BRIAN BANDA REPORTING LIVE FROM MASINTHA GROUND KOMWE KULI NSOKHANO WA UTM KWACHEMERATU LERO

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 ноя 2024

Комментарии • 43

  • @namalepetakeith1912
    @namalepetakeith1912 Месяц назад +1

    Despite her past flows (Akweni) politically let's appreciate how she has held together the UTM in this period

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 2 месяца назад +2

    Mayi kaliyati omwewo presdent wathu.mayi wolimba mtima kuyendetsa dziko lamalawi ndikusintha malawi

  • @MalizeniOliviaBridan
    @MalizeniOliviaBridan 2 месяца назад +5

    Kukovetion ndilikumbuo kwa kaliati maiolimba mtima wationetsera kukhwima mzeru votiyangai kwa kaliati

  • @goodwellnyalugwe9211
    @goodwellnyalugwe9211 2 месяца назад +8

    Cathy umaoneka bwino ndi natural pilizani si ambiri Masiku ano afuna natural

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw 2 месяца назад +6

    Nooo chifukwa chakuti chilima balibepo koma chilima kanakhalapo palibe amene akanapikisana naye

  • @gregomando
    @gregomando 2 месяца назад +1

    Kodi mukuyuza 3g network?

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr 2 месяца назад +3

    Ndechimene manganya sunapitile ku msonkhano waukulu, okuta ngati uwu ndichani? Ndipo skc ngati wangopita ku holiday foni nkuzimitsa kuti aturukila abale 😢 sindimvetsa ndipo mulungu mukanamukhululukila osamutenga nsanga kuti adzatikonzereko dzikoli mu 2025 limodzi ndianthu 7enawo anali othandiza kumabanja awo 😢 Chilima sindidzamvetsa until tidzadziwe choona chomwe chinachitika ndipo ndikupempha akuchurch ndi family ku chipani ndiamalawi okonda Saulos kuti asafooke, asaope, asatope ndipo mpaka mcp idzaturuke mboma.

    • @FlywellChazinga-z9v
      @FlywellChazinga-z9v 2 месяца назад

      Mmmmm mene akumunyozela Manganya muja or muli inu mukhoza kupitako?

  • @mathewsmbaluko8522
    @mathewsmbaluko8522 2 месяца назад +1

    UTM for ever❤

  • @martinthonje8523
    @martinthonje8523 2 месяца назад

    Am watching live from FAL hotel, Deira,Dubai UTM osaopa osafooka osaonesa kutopa kuti moto bhuuuu

  • @peterthawi
    @peterthawi 2 месяца назад

    brian kuseka kumeneko😂😂😂kufuna kuphyetsa mtima madame ako pa den

  • @FloraBanda-w7t
    @FloraBanda-w7t 2 месяца назад +1

    Musamaike background sound ikumajamitsa video aaa tisiyatu kukupangan follow 😊

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 2 месяца назад

    Moti Usi sanapezekenso uku ena mkumati Kaliati akusokoneza UTM.

  • @royveckphiri9386
    @royveckphiri9386 2 месяца назад

    Dalitso will be the presendent of utm

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 2 месяца назад +1

    Bravo!! bravo!! UTM

  • @georgemoffat5143
    @georgemoffat5143 2 месяца назад +1

    kaliyati ulufunaso ataima pa u president kkkkk timkanena kuti zamuwawa chakwera posankha Ausi amkafuna kuti asankhe iyee lero ndiinzoo akufuna uyimira utm

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 2 месяца назад +5

    Utm woye chipan chànga chafuko

  • @GraceChibwana-jq8gk
    @GraceChibwana-jq8gk 2 месяца назад

    mbambande!!! UTM forever

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 месяца назад

    Manganya si chipani cha UTM zimenezo iwe brian Banda

  • @AbdullahAjida
    @AbdullahAjida 2 месяца назад +3

    Mwe mtosye kajimboko

  • @martinthonje8523
    @martinthonje8523 2 месяца назад +1

    Forever in our hearts my vp your dream will never die rest well until we meet again

  • @YamzyAmos
    @YamzyAmos 2 месяца назад +1

    MA video anu amaimaima bwanji ahead

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 2 месяца назад +1

    Usi ayambitse chipani chake cha nthiko.

  • @PhilimonThegha
    @PhilimonThegha 2 месяца назад

    Live from south Africa utm oyeee

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp 2 месяца назад

    Aruta continua Aruta❤❤❤❤

  • @TamalaKambanje
    @TamalaKambanje 2 месяца назад

    Ana achepa motokuti buu!!!

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 2 месяца назад

    Utm bomaa

  • @UZIKASI
    @UZIKASI 2 месяца назад

    ❤ U. T. M

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 2 месяца назад +1

    Kkkkk kuvutadi kulibho kom mabg alibho

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 2 месяца назад +1

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @RargieMediaclassic
    @RargieMediaclassic 2 месяца назад

    Atolankhan muzilakhula zoyanjanitsa anthu osat kumalakhula zosokoneza ai kusakhala ndiopikisana nao ndichiganizo cha chipanicho chafuna poona ma followers omwe alinao mtsogoleriyo .

  • @Dauson-j5i
    @Dauson-j5i 2 месяца назад

    Zoona kusakhala opikisana naye sibvuto and amaziwa kuti ngakhale aononge ndalama zawo zomwe zimafusidya ku chipani kwa munthu akafuna kupikisana pa mpando wa uprezident zikhonza kungopita m mazi chifukwa ofunikira amaziwika kale ku DPP ndi ku MCP

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp 2 месяца назад

    Live from BT

  • @thomasmcbanda9794
    @thomasmcbanda9794 2 месяца назад

    Osaopa💪

  • @TamalaKambanje
    @TamalaKambanje 2 месяца назад

    Utm sizantha

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 Месяц назад

    Kukadakhal kt chilim alipo nakonsomukadamv kt chilima alowa popand opikisan nao ku mcp ku dpp chimodz modz zitat chakwer waf mwaziz kuth kulow chisawawa

  • @ShagaFologonya
    @ShagaFologonya 2 месяца назад

    Koma yaaaaa 2025 boma lapita ndithu

  • @LucianoKapepuza-sy9wx
    @LucianoKapepuza-sy9wx 2 месяца назад

    Boma ilo

  • @MikeManyamba
    @MikeManyamba 2 месяца назад

    Vuto si,makhala siliyas

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 2 месяца назад

    UTM 2025 boma

  • @thoccokay-v7s
    @thoccokay-v7s 2 месяца назад

    mbambande

  • @MwaleMussa
    @MwaleMussa 2 месяца назад

    Poor videos, too much stoppages