Это видео недоступно.
Сожалеем об этом.

BON KALINDO 14 JULY 2024 UYU NDI BIG MAN PA SUNDAY

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 12 июл 2024

Комментарии • 61

  • @MalawiTrendsTV
    @MalawiTrendsTV  Месяц назад +5

    Pepani audio yatulutsidwa ndika phokoso kena

  • @user-ri8em6my2e
    @user-ri8em6my2e Месяц назад +2

    Ine ndine mchewa original koma Chakwera eee akundiwopsaso nane UTM My vote 🔥

  • @FelixMwakhula-cm2yy
    @FelixMwakhula-cm2yy Месяц назад

    Big up the DC maka nkhani yaziphaso zovoterazo

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m Месяц назад

    Panopa kumalawi president wathu The DC kuyambila lelo amalawi tizimukhulupilila mu zonse amatiuza zimachitika

  • @AgnessMzengo
    @AgnessMzengo Месяц назад +2

    More life Mr Kalindo......... Mukuimilila mtundu wa a malawi..... ML &MB

  • @moosamlembe3939
    @moosamlembe3939 Месяц назад

    Big Bon kalindo amene ndimamudziwa ine ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @GeorgeZamala
    @GeorgeZamala Месяц назад +4

    Wa mkulu wa ife iweyo Kalindo more fire

  • @FrancisBanda-g9v
    @FrancisBanda-g9v Месяц назад

    Born kalindo lankhulani ise tikalankhula akuti dziko silanikoma ndise ma neba

  • @EsieChawanda
    @EsieChawanda Месяц назад +1

    😂😂😂😂😂 Amene ukuliwona dzikoli ngati lamako or lambuyako 😂😂😂

  • @Costance-nf7ue
    @Costance-nf7ue Месяц назад

    More fire kalindo wa ifeyo

  • @MadaHarison
    @MadaHarison Месяц назад

    MCP anthu oipa kwambiri

  • @ForsterThawan
    @ForsterThawan Месяц назад

    Mbambande inuyo mwanva kkkkkkkkkk kalindo iweyo umakwana

  • @limbanimtitima9170
    @limbanimtitima9170 Месяц назад +1

    Agogo a born kalindo amamupatsa miyambi yoveka bwino 😂

  • @GeraldChisokeza-er5cf
    @GeraldChisokeza-er5cf Месяц назад

    Boss ayankhula

  • @stanfordnsona
    @stanfordnsona Месяц назад +1

    Agogo a Kalindo anamuyankhula atafika mu chikangawa

    • @SiphoZungu-tt9iu
      @SiphoZungu-tt9iu Месяц назад

      😂 ndipomwe anayamba kumuyakhulira tuuu😅😅😅

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer Месяц назад

    Ife mcp sitikufuna ikapume nd a president awowo 🙌🙌🙌🙌

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi Месяц назад

    Ine zomwe ndikuziona 2225 wina WA MCP azaziombera ngati poo m'mphweyo zaka zm'mbuyomu chifukwa sakuganiza za ntsogolo kuti kodi bomali likadzasintha ife sazaganiza zoti njata koma ALLAH kuona zomwe muchita pangatalike Adzanva madando anthu ndalama kumakapezeka kunja kwaziko ife tikukutamano akusowa chakundya ayi zikomo kwambiri 😭😭😭😭😭😭😭😭😏😏😏😏😏😏

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Месяц назад +1

    More 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 fire DC

  • @user-ef4tr4ve9x
    @user-ef4tr4ve9x Месяц назад +1

    Born kalindo

  • @user-fh7sd6gp3f
    @user-fh7sd6gp3f Месяц назад

    Koma MCP ndiyankhanza akuti mugwirazano panalibe nanga bwanji anasankha nduna kuchokera KU UTM 😮

  • @user-fh7sd6gp3f
    @user-fh7sd6gp3f Месяц назад

    Next time mugwirazano pitani Kuma court kukasayinira migwizano yanu ngati umboni 😊

  • @MynessChirwa
    @MynessChirwa Месяц назад

    🔥

  • @MaryPanje
    @MaryPanje Месяц назад

    Bon kalindo ❤❤keep it up

  • @SovietMzungu
    @SovietMzungu Месяц назад

    Muzinenaso kuti akuba ndi awa chifukwa zongokambazo mkuoneka. Chabe ndi nkhwizi ndi boma la Chakwera, mulibe umboni kapena makufuna ndalama inuyo,

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa Месяц назад

      ngt mufuna maina mvelani ntanyiwa ndi bakili tv akumatchura maina osaopa munthu

  • @HalimaShafie-o7g
    @HalimaShafie-o7g Месяц назад

    Chilungamo mr kalindo ❤

  • @user-oy6dl1pv9e
    @user-oy6dl1pv9e Месяц назад

    Pambuyo panu apule tili limodzi ndiithu
    MULUNGU ali nafe

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Месяц назад

    Anakawuzani miyambi ndinthano zabwino muli muchikangawa forest

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Месяц назад

    Amenewadi awolela matewela azipita kwa achamawo 😂😂😂😂😂

  • @user-hg2cw1om1p
    @user-hg2cw1om1p Месяц назад

    ❤❤❤ We love you kalindo

  • @NelsonNdeke
    @NelsonNdeke Месяц назад

    Kalindo🎉

  • @Ben-i2u
    @Ben-i2u Месяц назад

    Iwe usazunguze mitu anthu ndichamba chako wamva

  • @user-wu8kp7ui5j
    @user-wu8kp7ui5j Месяц назад

    Audio ya lero sikunveka bwino

  • @NoliaMpempha
    @NoliaMpempha Месяц назад

    Fire

  • @AubreyTrust
    @AubreyTrust Месяц назад

    Katundu wamulungu kalindo

  • @lindananthalo5327
    @lindananthalo5327 Месяц назад

  • @MaliamMussa-p2e
    @MaliamMussa-p2e Месяц назад

    Kalindo yomweyo

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os Месяц назад

    Achewa agalu awa asatinyase zitsiru za wanthu

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e Месяц назад

    😂😂 awore matewera kkkkkkk

  • @user-rm2xv8ys1i
    @user-rm2xv8ys1i Месяц назад

    My dc

  • @gabbymagwaya5836
    @gabbymagwaya5836 Месяц назад

    kkkkk pakana awole matewera

  • @Ben-i2u
    @Ben-i2u Месяц назад

    Uyu chamba chimapweteka

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os Месяц назад

    Zoonadi ndi makape

  • @donaldlukhere1253
    @donaldlukhere1253 Месяц назад

    Please mute the video

  • @ellensambo6323
    @ellensambo6323 Месяц назад

    Ziliko

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala1493 Месяц назад

    galu iwe wachisuta galu iwe tiye iwe ife ochewa tikulamula basi 2030 woo

    • @GeorgeZamala
      @GeorgeZamala Месяц назад

      Uwalamulira ambuyako

    • @user-le9su3mt7r
      @user-le9su3mt7r Месяц назад

      Galu hiwe na chakwela satana wohipa

    • @chachaamoah3592
      @chachaamoah3592 Месяц назад

      Iwe ndi MCP yako munya.kupanda UTM kukusetani inu muli ndani.2030 yambuyako udzalamulira ambuyako omweo

    • @chadreckchibwithala1493
      @chadreckchibwithala1493 Месяц назад

      mnya mcp ilipo since kalekale n yizawinaso

    • @GeorgeZamala
      @GeorgeZamala Месяц назад

      @@chadreckchibwithala1493 muchita Kuba ma votitu kodi iwe ngati akudyesa chi banz uchisanza chimenecho ndipo tatopa nawo ulamuliro wa nkhanza ndi kupha. Pa zaka 4 wapanga chani

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga Месяц назад

    ndiwe opusa kaya ukufuna udindo wanama suupeza loko utanama motan

  • @AgnessMzengo
    @AgnessMzengo Месяц назад

    More life Mr Kalindo......... Mukuimilila mtundu wa a malawi..... ML &MB

  • @FelixMwakhula-cm2yy
    @FelixMwakhula-cm2yy Месяц назад

    Big up the DC maka nkhani yaziphaso zovoterazo

  • @Ben-i2u
    @Ben-i2u Месяц назад

    Iwe usazunguze mitu anthu ndichamba chako wamva