KWACHEMA ANTHU KUTHAWA MMA ROOM MU HOTEL | DR MICHAEL USI, MOSES KUNKUYU JOMO KUNO |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 сен 2024

Комментарии • 31

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 25 дней назад +1

    Mapazi anu a Mai Ntalimanja

  • @TonykalicheloKalichelo
    @TonykalicheloKalichelo 26 дней назад +1

    Kmtu mukasogoza chinyengo dziwan kt muzaphesa anthu

  • @user-zi8pj5ey4t
    @user-zi8pj5ey4t 22 дня назад

    Machine akuba awa

  • @ChidaPhiri
    @ChidaPhiri 26 дней назад +1

    Zonama zimenezo only njira yobela mavote muli mu mcp inu

  • @user-sh8bi2lk5d
    @user-sh8bi2lk5d 26 дней назад +2

    tizisiya kukukhulupilrani , chofikwa zomwe mumalemba ndixomwe zili mkati mwa cleep zimakhala zosiyana

    • @dziwetv
      @dziwetv  26 дней назад

      BRITHER SIMUNAONE ANTHU AKUTHA MU HOTEL KUTSIKIRA KUNJA ? ZASIYANA PATI ? WE TRY TO DELIVER OUR TOPICS TO REFLECT THE CONTENT,

    • @TakondwaSaidi
      @TakondwaSaidi 25 дней назад

      😂😂😂😂😂😂

  • @MoosaDawood-l5c
    @MoosaDawood-l5c 26 дней назад

    Mai inu muphedwa ngati mukunama

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h 26 дней назад

    Aaaaa zaziii bola ngati tizavote ndi chilichonse

  • @RaphaelKweve
    @RaphaelKweve 26 дней назад

    Nkhani post inaso zibwana eti?

  • @JOHNOlesmasCosmas
    @JOHNOlesmasCosmas 25 дней назад

    ndikutulukan coz mwayamba kulemba zabodza zosiya ndizomwe tikuonera kumakhala ufiti chan
    mwandibowa kwambiri

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 26 дней назад

    Muzavota katatu ngati simuzitenga bwino chisankho chikubwelachi.

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 25 дней назад

    Chikangawa imeneyo

  • @user-ev6bi7jr7g
    @user-ev6bi7jr7g 26 дней назад

    Sitikukukhulupirirani chifukwa m'makondera MCP

  • @chikublea8982
    @chikublea8982 26 дней назад

    Osawakhulupira zaboza zimenezo ndi tchito ya nrb imeneyo

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 26 дней назад

    Chikhulupiliro mulibe mwa inuyo, siinunso bungwe loyima palokha lero, mudzinamidzana nokha kumeneko. Ndipo 2025 muchileka tikungokuverani.

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 26 дней назад

    Boma liziyesesa please Maka anthu akumudzi zambiri zisamawapitilire

  • @user-rn7wv8ze3v
    @user-rn7wv8ze3v 25 дней назад

    Palibe chilungamo apo

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d 26 дней назад

    Komatu Inutu Inu a mec ngati mukukondela Lazaro kuti akhalesa papando dziwani kuti ngati mukudya athu akufa ndi njala chifukwa Cha BOMA muku lika kumbuyolo mudzalandila chilango chachikulu kwambili pa maso pa mulungu musaone ngati mulungu kulibe alipo ndithu

  • @stevezulu2108
    @stevezulu2108 25 дней назад

    Interpretation ya mzungu ....eeee invetsetseni.

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r 26 дней назад

    Muli kumoz ndi mcp izo timaziwa iiiya

  • @TressLuka
    @TressLuka 26 дней назад

    Palibe cha nzeru apa. Boma la anthu aku Lilongwe osati ifeyo a Amalawi ayi.😅 Za Chakwera izi.

  • @adamdiss1868
    @adamdiss1868 25 дней назад

    Njira yobela

  • @yusufbanda4980
    @yusufbanda4980 26 дней назад

    Cancer njochzka pogwrtsa ntchto poison wa njoka komaso kumadya mandmu

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 26 дней назад

    Mtalimanja ndi phwala

  • @MaxwellChiona
    @MaxwellChiona 26 дней назад

    Fallly wathuwathu Banda

  • @adamdiss1868
    @adamdiss1868 25 дней назад

    Zonama

  • @ChrisjuZiyaya
    @ChrisjuZiyaya 26 дней назад

    We as Malawians we don't trust nosense because all your plans anthu akuwadziwa so ossmatiyesa.

  • @JamesChiphwanya-tb3tq
    @JamesChiphwanya-tb3tq 26 дней назад

    Km Malawi ajomo mukuti ku bomako angasithe chani munthu osaphuzila olo A mwana oti wakula akugulitsa swani freezes lero mukuti ndi asogoleri amalaw😂😂😂