BON KALINDO WAYANKHULA ZINTHU ZACHINSISI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 сен 2024

Комментарии • 28

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 25 дней назад +1

    Na Born kalindo anakhala alimo anthu 10 olimba mtima ngati uyu ndithu chakwera anatura pansi udindo ndithu

  • @ThomsonJamu
    @ThomsonJamu 26 дней назад +1

    Kd inu akalindo simunakhapidwepo nthawi ya dpp

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 26 дней назад

    Onena adalipo ngati achina Bon kalindo, koma ineyo kusamva 🎉🎉🎉🎉

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 25 дней назад

    Mcp ndi boma ladziwanda

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 26 дней назад +1

    Wayambapo ukunama. Kwakuchela

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 25 дней назад

      Machende ako iwe ngati sukufuna usamavere

  • @jimmywhitecollins
    @jimmywhitecollins 26 дней назад +1

    Awa atitopesa

    • @user-zj1xx1ic2m
      @user-zj1xx1ic2m 26 дней назад

      Ngati akutopetsa kagone, ine sindinatope naye 😢😢

  • @user-fw2tg3ew3k
    @user-fw2tg3ew3k 25 дней назад

    Umm guys koma pachilungam a police pena amapanga zobowakoma

  • @PackPin
    @PackPin 26 дней назад

    🙏🙏🙏🙏

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 26 дней назад

    Kalindo akunen za mcp chifukw chakut mcpiyo ndiyomwe ikusewerets misonkho yamalaw

  • @EviChio
    @EviChio 26 дней назад

    Zathebazodi tikuzifuna coz makolo anthu anavutikila

  • @YusufSeleman-j4y
    @YusufSeleman-j4y 26 дней назад

    Munthu wamkulu kwambili

  • @ThomsonJamu
    @ThomsonJamu 26 дней назад

    Kodi mwayamba u prophet a Borne kalindo?

  • @MkandawileLloyd
    @MkandawileLloyd 26 дней назад +2

    Vuto mukupanga mademo amutendere chifukwa chakwera akupanga chomwe akufuna pangani ngati zakukenya

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 26 дней назад +1

    Kodi akalindo ineyo ndikudabwa nanu kwambiri muno mumalawi muli zipani zambiri koma inuyo pakamwa panu mumangotchula mcp yokha kodi zipani zinazi sizingapange chipongwe koma inuyo akalindo mulindivuto ndi mcp inuyo sikuti ndinu omenyela nkhondo amalawi koma muli against ndi mcp inuyotumukupanga kampeni ya dpp ndicho chifukwa chake poyamba tinali kukuvelani koma panopa tinasiya chifukwa tinawona kuti mumapanga kampeni osati kuthandiza amalawi ayi koma dpp yinapeza kampeni dayilekita wamphamvu pakamwa sipadusa mphepo pakamwa ammmmm kodi uli ndibanja munthu iwe or uliwekha koma ada kulnkhura munadusa pamunthu wankazi yooo

    • @user-zj1xx1ic2m
      @user-zj1xx1ic2m 26 дней назад +1

      Mumafuna kuti mitengo ndi yomwe izilongolora kapena miyala??? Nawenso uli ndi pakamwa ndipo ngati sukufuna kulongolora kagone galu mwana wa Hule wa MCP, pantumbo pakonso usandiyankhe galu😢

    • @geoffreykamoto-ex9wu
      @geoffreykamoto-ex9wu 26 дней назад

      Kodi nde kuti inuyo momwe ikupangila mcp zikukusangalasani more over Kalindo akaankhula chithu chimachitika so he is focusing on party that does nonsense

    • @user-zj1xx1ic2m
      @user-zj1xx1ic2m 26 дней назад

      @@geoffreykamoto-ex9wu Ana a chikangawa akudya nawo misonkho ya amphawi

    • @geoffreykamoto-ex9wu
      @geoffreykamoto-ex9wu 26 дней назад

      Ndipo kwabassi ameneyo ndi gulu la chikangawa uyu

    • @TressLuka
      @TressLuka 26 дней назад

      Iwe kapoli sukudziwa kuti dziko likuipa chifukwa chakupha kwa MCP komaso kuba ?