A Malawi Lyton Mangochi Musamukhulupilileso - Bon Kalindo

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 25 окт 2024

Комментарии • 49

  • @wilsonfelix6559
    @wilsonfelix6559 5 месяцев назад +11

    Bon kalindo yehova azikudalitsa iwe ndi vumbulutso tizazindikila bwino pasogolo❤

  • @chimajrbhahat2334
    @chimajrbhahat2334 5 месяцев назад +2

    Thank you, Mr Kalindo for your strong message. We love you

  • @AbdullCassim
    @AbdullCassim 4 месяца назад +1

    Born kalindo forever timenyelen ufulu ndife anthu anu osauka we love you 💞

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 5 месяцев назад +3

    Good Message Mr Bon kalindo number one

  • @NelsonDavid-bb9xm
    @NelsonDavid-bb9xm 4 месяца назад +1

    My legend Mr Born kalindo

  • @MussahListonichiocha
    @MussahListonichiocha 5 месяцев назад +1

    The DC Msilikali wathu,we love you brother keep fire for burning

  • @JosephNgona-f9v
    @JosephNgona-f9v 5 месяцев назад +1

    Born kalindo more fire be strong God is with you ndipo ndinu dolo

  • @francischikaya3146
    @francischikaya3146 4 месяца назад +1

    Amene azikumvera ndi anzako aku Mulanje kwanu.

    • @HamanjaManyela
      @HamanjaManyela 4 месяца назад

      This message is all about Malawians not about tribe

  • @SanudiJaymofred
    @SanudiJaymofred 5 месяцев назад +1

    Malawi 🇲🇼 Frist💪🌶️. Team kalindo

  • @MasterBlack-r2n
    @MasterBlack-r2n 5 месяцев назад +1

    inuyo akalindo ndi mtunda Wina Wina wovuta kudusamo. inuyo munabadwa masiku okwana ndipo ndikuganizaso kut anapitilira. Boooooooooooon Kalindooo Mwana wooopsa kwambili. Mulungu akuze malire amoyo wanu kut miyoyo ya amalawi osaukafe tipulumuke mmanja kwa azifwambawa😭😭😭😭

  • @194vo
    @194vo 4 месяца назад +1

    Mr nyoooooo

  • @krisquaxmwlikapah9184
    @krisquaxmwlikapah9184 4 месяца назад +1

    Thanks bon kalindo

  • @AlexZinga
    @AlexZinga 5 месяцев назад

    Strong message from DC

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 5 месяцев назад +3

    Amang,o chikupusa mulibe sselu

  • @Moses51
    @Moses51 5 месяцев назад +3

    The DC bon kalindo

  • @YohaneChinthomba
    @YohaneChinthomba 5 месяцев назад

    I don't trust anyone who called himself FREEDOM FIGHTER. We have to get a lesson from previous freedom fighters eg T. Mtamba, B. Mayaya etc.

  • @SimonBanda-b1f
    @SimonBanda-b1f 5 месяцев назад

    Chisankho chaku aKaronga a Mangochi anali patsogolo kuti MCP inabela komanso amati anali NDI umboni kuti MCP imagawa ma 2000mk/ ma 5000mk muma classroom.
    Koma pano kuli ziii (ndalama zimayankhuladi)

  • @HussainKabila
    @HussainKabila 5 месяцев назад +1

    ❤❤🎉🎉 bon kalindo Doro Mesa osat mangochi galu KWA bs

  • @AndersonchinseuPhirijunior
    @AndersonchinseuPhirijunior 5 месяцев назад

    Lyton munthu opanda kanthu ngt chakwela yemweyo mukundiuza kt angapange chilungamo? Zomwe akupang lyton akufuna kuzithandiza yekha km ndi chisilu kwambiri alibe kalikonse galu ameneyu

  • @francischikaya3146
    @francischikaya3146 4 месяца назад

    Zabodza izi. Bon kalindo galu wachabechabe.

  • @JimmyMaster-l1x
    @JimmyMaster-l1x 5 месяцев назад

    Magochi mawu onyasawo wabva iwe

  • @Freedomchennl47
    @Freedomchennl47 5 месяцев назад

    Lyton mangoch ufulu samenyela munthu opanda kena kalikonse ndiwe galu wachabe chabe panyoo pako tinakuziwan kale iwe maphaz ako nalo Boma laulendo kumangopeleka ndalama kwawina aliyense makhape noka noka

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 5 месяцев назад

    Komatu chakwela ngati ali mfiti wapha anthu kwambili, chifukwa sakumuchotsa minister yemwe akulephela cholinga anthu azivutika.
    Chilima ufiti wachita kusintha nawo nkhope

  • @mahmoudjohn2382
    @mahmoudjohn2382 4 месяца назад

    Amvekere dzina nde tapanga kale..mmmmmmm Ku Malawi kwazaza mbuzi

  • @BertharrySecurity
    @BertharrySecurity 5 месяцев назад

    Tilipambuyo panu Mr kalindo

  • @Edwardtolo
    @Edwardtolo 5 месяцев назад

    Mangochi ndi munthu wadyela komanso ndi Galu wachabe chabe satana munthu opanda nzelu chisilu chamunthu koma mukunama ife tilinayo wa president DC Kalindo opelekedwa kwa Mulungu osati iwe Galu wachabe chabe satana

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 5 месяцев назад

    Malawi siwomufela by Bon kalindo

  • @ErickMambelera
    @ErickMambelera 4 месяца назад

    Ulem wanu big osati ngalu lamuthu linja magochi

  • @lulukunkeyanih8271
    @lulukunkeyanih8271 4 месяца назад

    Mwana owopsa the Dc

  • @JamesChimera-hw1nv
    @JamesChimera-hw1nv 5 месяцев назад

    Osamanamizidwa inu ndale muzizidziwa bon karindo ndiwa DPP amadya mu DPP palibezomenyera ufulu apapa koma kusokola ndarama muziona khalani chete mudzadziwa Chilungamo

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 5 месяцев назад

    The D.C. ❤❤

  • @SolomonMatola
    @SolomonMatola 5 месяцев назад

    Omenyera ufulu adyera ndawaona

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 5 месяцев назад

    Pa Asoko ku mwai wa Abambo kkkk Rest House kuseri kwa Ekhaya kk

  • @shaibuJames-c3w
    @shaibuJames-c3w 5 месяцев назад

    koma dziko amalawi omenyera ma ufulu alero

  • @wysonmaya
    @wysonmaya 5 месяцев назад

    komatu Lyton mangochi mwatichitisa manyadzi mene timakukhulupililani muja kwatu kwa moto kuno mumatiyimilila koma apa chikhulupililo chataika

  • @MartinLuther-o2z
    @MartinLuther-o2z 4 месяца назад

    Lyton kuyaluka kuyaluka masana,sana

  • @rastaaustin4042
    @rastaaustin4042 5 месяцев назад

    uli chindele iwe chikalindo mose mkuyana waka maluzi yalikukukutani palije va kumenyela ufulu pa imwe ukavu wekha ndiwo wasuzga

  • @malvinhusted6245
    @malvinhusted6245 5 месяцев назад

    Lyton mangochi apa nde watamba masanadi 😂😂

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga 5 месяцев назад

    lweso zako udadya kare usatukwane anzako

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 5 месяцев назад

    Ndipo ine mwana wanga chilipilileni passport Chaka chatha m,pakana pano ndrama yochita kukongola ambuye atiyendele ku Malawi athu tapanikizika

  • @rastaaustin4042
    @rastaaustin4042 5 месяцев назад +1

    mwamupulata na audio iyo munyinu kutu muyowoyelepo aguluni inu mbava iwe kalindo

  • @williamcl8341
    @williamcl8341 5 месяцев назад

    Kumalawi kuno kuli ma activists?

  • @ChifundoJohn-w3t
    @ChifundoJohn-w3t 5 месяцев назад

    Lyton machende ako

  • @ElizahMadi
    @ElizahMadi 5 месяцев назад

    The DC

  • @MorrisMapiri
    @MorrisMapiri 5 месяцев назад

    Mudzawadziwa ndi ntchito zawo

  • @YasmeenYalabi-b2c
    @YasmeenYalabi-b2c 5 месяцев назад +2

    Tinanena ife kut mangochi wabwinyika chibanzi nde wayalukatu mau osasawo galu oipa iwe

  • @HalordDzampana-cq4qx
    @HalordDzampana-cq4qx 5 месяцев назад

    wakuba layiton