EDIWAD KAMBANJE LIVE ON YAO FM MADEMO ALIPO AMAKAWI OSAOPA CHAKWEKA MAST GO TO KASIYA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 окт 2024

Комментарии • 41

  • @Jasonnyatwa
    @Jasonnyatwa 3 месяца назад +5

    Asakheleso mademo Ake ophempha, boma ili siloliphempha mademo chomwe tikufuna chakwala atule Pasi udindo

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 3 месяца назад +3

    Go konkoooooooooooooooo,,,, wapolisi samala. Moyo wako ngofunikira kwambiri ndiye udzipatse ulemu wekha

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 3 месяца назад +2

    Mademo aketu tikufuna enien omwe tikapange not zongpchedxa zomwe zakhala zuchitika mbuyomu, tikufuna Mademo ngati omwe akuchitika ku Kenya 🇲🇼💪💪💪

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k 3 месяца назад +2

    Achoke achoke anati ronjeza kt ndika rephera kukwanisa zomwe ndaronjeza ziko ndizatura pansi udindo ndiye apa paribepo vuto kupanga mademo chifukwa anaronjeza ziko ndiye zomwe anati ronjeza paribe or chimozi chot tingaroze just go to kasiya man

  • @PatrickGonagona
    @PatrickGonagona 3 месяца назад +4

    Chakwera atule pansi mokakamizidwa don't ask him to resign but we want him to quit by fire by force 😳

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 3 месяца назад +2

    Tatopa ndi Chakwera Malawi wathu wawola ndithu achike basi galuyu kayafa

  • @isahMapemba
    @isahMapemba 3 месяца назад +3

    Tili pambuyo

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 3 месяца назад +1

    Bola osamangokamba apa then muzizalepheresaso kupangitsa 😡

  • @happymumba2261
    @happymumba2261 3 месяца назад +2

    💪💪💪💪

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 3 месяца назад +2

    Tili nanu limodzi guyz

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 3 месяца назад +1

    Komanso palibe ku perhaps fziko ndi Kathy si la chakwela

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 3 месяца назад +2

    Goh komkoooooooooh

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 3 месяца назад +1

    Edward kambanje power of speech Achoke galu amaneyo we don't won't chakwera mbudzi yachabechabe

  • @LongweLeya
    @LongweLeya 3 месяца назад +1

    Vuto ife ngati amalawi eni eni timaopa kulowa ku ma demo koma kulankhula pakamwa thoooo boma la manyi ili likadali kupanga zinthu mwa manyi enieni kodi vuto ndi chani kwenikweni mantha

    • @sylvesteralfred8355
      @sylvesteralfred8355 3 месяца назад

      Ndipo imeneyo ndimadandaula poona aMalawi amangokhala osafuna kupitako ku ma demo ndimadandaula kwambiri timaiwala kuti zinthu tisinthe zimafunika kutengqpo Action thru ma Demo

  • @HusseinMoffatt-mi1fl
    @HusseinMoffatt-mi1fl 3 месяца назад

    Zoonadiitu osafookayi chakwelandi mbudzi kobasi

  • @besterlumbe4404
    @besterlumbe4404 3 месяца назад

    Mademo akumalawi amakhala amasewera, maiko anzathu sachita kupempha chilolezo kwa dc amangochita basi,mukundiuza kuti mademo omwe akuchitika ku Kenya anakatenga chilolezo chochitila mademo? Amalawi turo 2much moti malawi yemwe wavutilamu tidikile mpaka 2025? Tiyeni amalawi tipite pa msewu mwaunyinji Chakwera ndi nduna zake zonse zitule pansi udindo basi enough is enough

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 3 месяца назад +1

    Go konko Malawi siife amantha osaopa osafooka osapepesa ❤❤

  • @Lee-lee-w1r
    @Lee-lee-w1r 3 месяца назад +1

    Chakwera azachoka pampando mowawa kwambiri. Zizakhala zoipila kuposa mmene Peter Mutharika adachokela

  • @JohnKalembo
    @JohnKalembo 3 месяца назад

    Chakwera atule pansi udindo alephera kuyendetsa dziko ndipo ndikuchita kuona kuchedwa pa 10

  • @sylvesteralfred8355
    @sylvesteralfred8355 3 месяца назад

    Dandaulo langa kwa aMalawi please tiyeni ku ma Demo mwaunyini kuti Chakwera achokepo

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 3 месяца назад +1

    Osawapempha absolutely ndiachamba aboma

  • @MaliamUma
    @MaliamUma 3 месяца назад

    Ifenso kuno ku cape Town city tilipo group pano tilowe pa sewu

  • @EdenNgulube
    @EdenNgulube 3 месяца назад

    Mall fire 🔥🔥

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 3 месяца назад +1

    By fire by force chakwe must gooooooooo!!!!!!!!!!!!

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw 3 месяца назад +1

    🫡🫡🫡🫡🫡🤝🤝💪💪💪

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 3 месяца назад +1

    💪💪💪💪💪

  • @PetroMatias
    @PetroMatias 3 месяца назад +1

    👊👊👊👊👊👊👊💪💪💪

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 3 месяца назад +1

    Tiyeni komko

  • @mariamahamadu8402
    @mariamahamadu8402 3 месяца назад +1

    💪💪💪💪💪💪💪

  • @KimDexonAdamson
    @KimDexonAdamson 3 месяца назад

    Tiyeni Tiyeni Tiyeni

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 3 месяца назад +1

    Zazii masatanic inu mkuwona mmene anthu afela kukenya poti masananic ngati pafa anthu inu mmasangasalala pephelo langa ndilakuti mkafe ndinuyo osati anthu wapa ambuye alowrlelepo kuti mkafe ndinuyo mmangoyambisa zipolowe inu mmathawa msakathawe ndipo tisave kuti anthu wamba amwalila kumeneko mmene mnayambila sitikuwonapo phindu tikungowona majelasi

    • @ZionekaMember
      @ZionekaMember 3 месяца назад +6

      Iwetu wadya zambiri koma ukunama anthu sangakumvele namapwala iwe m'mene ulili moyo pano ukusiyana chan ndikufa
      Ukuganiza kut anthu angamvele kapolo ngat iwe ndikukusaka step by step ma comments ako ukupanga zosemphana ndi generation
      Usaza ndalama zimenezo

    • @brainsmkumbwa6267
      @brainsmkumbwa6267 3 месяца назад +1

      Chisiru iwe, mbuzi

  • @YusufuKaifa-fr4wt
    @YusufuKaifa-fr4wt 3 месяца назад

    ❤❤❤ all malawian don't give up be strong enough Allah will help us malawian for fight inshaa Allah
    Support come from here south Africa love you all malawian ❤❤❤❤❤ game is over mr president

  • @lyiemax
    @lyiemax 3 месяца назад

    Powerful!!!!! Forward ever and backward never

  • @JaxyKumwenda
    @JaxyKumwenda 3 месяца назад +1

    Pa 10 kwatalika kwambiri

  • @YamikaniPrince
    @YamikaniPrince 3 месяца назад

    🎉

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 3 месяца назад

    Kunena zoona ku mademo sikukhala malonda ,chimenecho chibwana cha mchombo lende

    • @SamuelMponda-y3d
      @SamuelMponda-y3d 3 месяца назад

      Komatu mdala uja anakuuzani kuti ngati mufuna kubwerera m'mbuyo musankhe a lerowa. Munasankha. Ajawo anapanga zionetsero potapa mphamvu zaku mdima, chifukwa amaononga zinthu pamene nkhani yao inali kubwlo la milandu. Inuyo simuononga?