Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Kodi amati "Azi matala ofu fakiti" kapena ndimava udyo ndine😂😂😂
Eya amatelo😂
😂😂😂😂 all the best
Kkkkkk komatu amandota njira zanu za umbombo izi amamairi asazuzike nanu kusogoloku kuumilako I love you guys ❤️❤️❤️
Ine singalole kuti mukakhale nawo ku 47 adha nzanu munamupanga nkhanza.We lovez u 2
🤣😂🤣 eti mfunda nsapatozo,good work💥
Muyipanga bho videoyi
Unu c ndimakhumudwa nanu wakulu chikakula more fire
😃😃😃😃i like the way you are acting both of you guys keep it up i lafusi you
Perfect 🔥🔥🔥
Perfect 💏💏🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Mumakwanira😂
Mwasowatu amandoda
kkkkkkkkkkkk mumakwana ma guys
😂😂😂 mlendo paka alipire ya rent😅😅😅ankolo simuzatheka inuyo kkkk
Ndizovuta chifukwa mandota amachita umbombo ndiye nditakhala kuti ndiine singalore kuwatenga chemandota ku 47
Mm mm Koma mandota mene mumamapangila angalore
Koma Morogeni wajayilapotu mpaka kuonjezera madzi mu mpoto😂😂😂😂Che Mandota mumakwana
Sosateka kukala limosi kkkk mumatha keep it up never give up
Mologen waiphula... Keep the good work.. 🔥🔥🔥🔥
Pasi pa mbaula apo, tatengani pulusa 😆😆 koma mlendoyu sanamlandile ndthu
Koma man inuyo mmatha.
Mai mail mwaonjedzatu Ndi Amunanuwo Che mandoda umbombo choncho, asakutengeni mukhale PA rent pompo basi
Mulendo alipire rent akuyankhulitsa heavy
As matala of fact singalole.... Komabe poti choipa sabweza mdtha kulola
Wow 😲😲 that's great
Kkkkk ndiwe galu kwabasi Mesa wapungula nsima
Uyuyu aseh 😂😂😂😂
😂Che Mandota umbombo onse uja Pano mwawafuna kkkkk
Chilomwe mchiyankhulo chotseketsa kwabas ,ati musandiuze"'musandiuzeee .
very nice. apa che mandota ali mmadzi ine singalore kut andisate ku 47. azikhala ndi mayi a mayili omweo kklkkkkkkkkkkkk
😅 😅 I have liked adha mwawapanga introduce wo😂😂He is also good at acting. Timamva kukoma kobasi. Keep on entertaining us. Long live
Morogeni ndi dolo 🤣🤣🤣🤣Mandota squad mulibe manyaka
Moto chemandota
zilimo m'moyo zokumana nazo mologeni
Ndili ine ndingakuloleni ndi cholinga kt muphuzile kukhala ndi anthu bwino
Nayenso Morogeni kukhalabe pakhomo chonsecho akudziwa kut sakufunidwapo kkkkkkkkk, ugona ngat ng'oma
Moni kwa ma Maili. Ati mlamu bwerani tiphike. 😂
kkkk km anthu inuyo mumakwana ndipo mumativesa kukoma
Today l was at BCA n l jst come cross with that guy morogeni 😂 n ndi fana wabh hvy lero ndaseka kwambiri ati kundiuza azimatala ov fact undigulire Chip's
Km mandota mmmm zomwe munachita mu nkhuku zija zilipobe kkkkkk
Ine nditakhal morogen sindingakutenge iwe mandota mu2 waumbombo ngt iwe
Ai sikuyenela kupita nao muli ndi khanza
As a matala of fact 😂😂😂
Kuwonjezera bwanj madzi kkkk okhala mulendo
Mhuuu alendo kumasukatu , kukhala mologeni sindingalole
Inu muzakomola anthu sure kkk
Mologeni akhululuke choipa sabwezera basi
Munthu wankulu inuyo ndi 🔥 🔥 🔥 🔥
Mamaili muli pamavuto, 😂😂😂 i lafusi you koma gyz
Kma kankhani et🙌
😂😂😂😂 koma yah eeeee zovuta
Che mandota ndiwe ambombo kkkkk
Mandota kulandira alendo kwabwanji uku hahaha
Wow!!! So beautiful Doc.... Mologeni wayiphula hahaha 🤣😂...asamutenge mandota aaaaa amumvesa kuwawa kkkkkk
Iweyo ndi dolo ase keep up the good work 🤣🤣🤣💯💯💯
mandota and your friends 😂😂😂😂😂😂😂 You're people.am top fan of you
Mukakonzeka mundiuza.koma akubwera osakonzeka🤣🤣
if i was mologeni ndikanapweteketsa mtima mandota ndikumupatsa kumapeto
Suwa LA lowaa. As matala of fact😅😅😅😅😅😅🇲🇼
Music
Mandota sazatheka
Kodi mandota mukumuzuza bwanji mulendo 🤣🤣🤣🤣mpaka alipireso rent?
Ako ndmadzi otetha kkkk makwana bro
Ine takhala mologe ndikupondani popita nd ma mayili womwe 🤣🤣🤣🤣
Kukonda ndeu
Mulendo kumuletsa kudya mmmm
Sindingalore olo pang'ono.
Kkkkk ulemu wako mandota
Kkkk❤ alendo kuwonjezera madzi mupoto
Mologeni kubweza kkk
Osunga nzake saziwika wayiphula poyela yela
Muli bho heavy madala
Chemandota timakunyadirani kwambiri imakwana
Hahahaha koma guys mwapha keep it fire guys
Mumakwana ambuye
Muziona kocheza nanu😂
😀😀😀😀 achizumbi malenga lenga kkkkkk
Hahaha mbola mani mntakhala ine singailole mandota akhale 😂😂🙌🙌
Kwabiri kwake
Iiiii umbombo wake umeneu che mandota ayi sindingatenge😅
Hahahahaha koma mlendo waziona kkkkk
Kkkkk eeeeee kovuta kukuten baba khalidwe limenero mukhonza kukalamulira nyumba ili yanga
Wakalibu kuthawitsa mbale
Masha Allah 🥰🥰🥰!!! we loves it so much Allah apitilize kukupatsan nzeru Insha allah 🙏🙏🙏
Kkkkk akukhaulise kumene iwe ndi mamaidi wakoyo muzikhala pa rent pomwepo
Kutopa naro bwanja!?🙌🤣🤣
😂😂😂😂ndpo ine sndingalore mwandigoneka ndnjala kmazigulira ndekha chakudya 😢😢😢ndye zakoma kwa ine muzit tikakhale limoz 😅😅😅choipa sabweza bwelan muzakhale muphuzile kulemekeza mlendo ❤❤❤❤
Aaaa koma Mandota ukuwonjeza kkkkkkkk
Alendo aja aonjezera madzi kuno🤣🤣🤣🤣🤣
Eya nditha kulora coz choipa sabwezera💖
Whatchg from Maputo Mozambique, che mdt. Umakwana
😂😂😂😂ngati kwasala munthu yemwe ukutimvesa kukoma ndizisuzo ndiweyo ase plz pitilizani musafooke
Kma mologeni naye akubwela bho kwambili asi e matala ofu fakiti😁😁😁🤣🤣
Ayi asalore kuti chemandota apite nawo ku 47
Azi matala ofu fatikiti 😂.
Nditha kuvomera pofuna kumuphunzitsa kt asadzapangirenso ena
Love
Umakwa
Koma mandota sazatheka 🤣🤣🤣🤣
Zilibwino kwambiri
Ayi azingokhala mandota
amache maili amata nditu
Kkkkkk kod amailiwo tizaona ? Mmakwana
Azipita limozi kumoz nd ma mayili
Cmandota wafika level ya nyooo 🥳🥳🥳🥳🥳
Agerevaziyo 😂 😂 😂
Afunda mitengo yawoyo
🤣🤣🤣🤣🤣 Morogeni waiphura
Kkkkk che mandota lemekezani odutsa inu, kkk
Good
As a matala of fact mologeni sangalore
Kodi amati "Azi matala ofu fakiti" kapena ndimava udyo ndine😂😂😂
Eya amatelo😂
😂😂😂😂 all the best
Kkkkkk komatu amandota njira zanu za umbombo izi amamairi asazuzike nanu kusogoloku kuumilako I love you guys ❤️❤️❤️
Ine singalole kuti mukakhale nawo ku 47 adha nzanu munamupanga nkhanza.We lovez u 2
🤣😂🤣 eti mfunda nsapatozo,good work💥
Muyipanga bho videoyi
Unu c ndimakhumudwa nanu wakulu chikakula more fire
😃😃😃😃i like the way you are acting both of you guys keep it up i lafusi you
Perfect 🔥🔥🔥
Perfect 💏💏🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Mumakwanira😂
Mwasowatu amandoda
kkkkkkkkkkkk mumakwana ma guys
😂😂😂 mlendo paka alipire ya rent😅😅😅ankolo simuzatheka inuyo kkkk
Ndizovuta chifukwa mandota amachita umbombo ndiye nditakhala kuti ndiine singalore kuwatenga chemandota ku 47
Mm mm Koma mandota mene mumamapangila angalore
Koma Morogeni wajayilapotu mpaka kuonjezera madzi mu mpoto😂😂😂😂Che Mandota mumakwana
Sosateka kukala limosi kkkk mumatha keep it up never give up
Mologen waiphula... Keep the good work.. 🔥🔥🔥🔥
Pasi pa mbaula apo, tatengani pulusa 😆😆 koma mlendoyu sanamlandile ndthu
Koma man inuyo mmatha.
Mai mail mwaonjedzatu Ndi Amunanuwo Che mandoda umbombo choncho, asakutengeni mukhale PA rent pompo basi
Mulendo alipire rent akuyankhulitsa heavy
As matala of fact singalole.... Komabe poti choipa sabweza mdtha kulola
Wow 😲😲 that's great
Kkkkk ndiwe galu kwabasi Mesa wapungula nsima
Uyuyu aseh 😂😂😂😂
😂Che Mandota umbombo onse uja Pano mwawafuna kkkkk
Chilomwe mchiyankhulo chotseketsa kwabas ,ati musandiuze"'musandiuzeee .
very nice. apa che mandota ali mmadzi ine singalore kut andisate ku 47. azikhala ndi mayi a mayili
omweo kklkkkkkkkkkkkk
😅 😅 I have liked adha mwawapanga introduce wo😂😂
He is also good at acting. Timamva kukoma kobasi. Keep on entertaining us. Long live
Morogeni ndi dolo 🤣🤣🤣🤣Mandota squad mulibe manyaka
Moto chemandota
zilimo m'moyo zokumana nazo mologeni
Ndili ine ndingakuloleni ndi cholinga kt muphuzile kukhala ndi anthu bwino
Nayenso Morogeni kukhalabe pakhomo chonsecho akudziwa kut sakufunidwapo kkkkkkkkk, ugona ngat ng'oma
Moni kwa ma Maili. Ati mlamu bwerani tiphike. 😂
kkkk km anthu inuyo mumakwana ndipo mumativesa kukoma
Today l was at BCA n l jst come cross with that guy morogeni 😂 n ndi fana wabh hvy lero ndaseka kwambiri ati kundiuza azimatala ov fact undigulire Chip's
Km mandota mmmm zomwe munachita mu nkhuku zija zilipobe kkkkkk
Ine nditakhal morogen sindingakutenge iwe mandota mu2 waumbombo ngt iwe
Ai sikuyenela kupita nao muli ndi khanza
As a matala of fact 😂😂😂
Kuwonjezera bwanj madzi kkkk okhala mulendo
Mhuuu alendo kumasukatu , kukhala mologeni sindingalole
Inu muzakomola anthu sure kkk
Mologeni akhululuke choipa sabwezera basi
Munthu wankulu inuyo ndi 🔥 🔥 🔥 🔥
Mamaili muli pamavuto, 😂😂😂 i lafusi you koma gyz
Kma kankhani et🙌
😂😂😂😂 koma yah eeeee zovuta
Che mandota ndiwe ambombo kkkkk
Mandota kulandira alendo kwabwanji uku hahaha
Wow!!! So beautiful Doc.... Mologeni wayiphula hahaha 🤣😂...asamutenge mandota aaaaa amumvesa kuwawa kkkkkk
Iweyo ndi dolo ase keep up the good work 🤣🤣🤣💯💯💯
mandota and your friends 😂😂😂😂😂😂😂 You're people.
am top fan of you