Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Dziko silidzapereka mtendere kwa munthu. Kwa Yesu yekha kuli mtendere okhathamira.
What a nice songs may God bless u brother nyimbo iyi ukakhala kut ukubvela ukaganiza nyengo ukudutsa misozi kumatuluka ❤❤❤
On behalf of all Malawians based in south Africa we have excepted that Taimon is a 👑 in music.
mmmmmm Bro ndende ndine ase kwathu akadya ndy ndiiney mmmm
This guy is indeed genius,well done I salute your excellent work.Dont give up
Uthenga 🤗🤗🤗🤗 amen. Ambuye dalisan chonde nyengo zisinthe
That's great bro nice and powerful massage ,,,,,, continue ukutivetsa kukoma❤❤
You guyeee aaaaaaa!!! Luso lako landipatsa school, God bless u.
i really love you aise nyimboyi exactly zamoyo wanga mene ukuyendera
I love your songs ❤zikumandidalisa especially zikomo ndi dalisani
😂Umakwana iweyo iweyo ❤❤❤
Zofunika kwambiri mulichimbikitso kwambiri,,,bro continue
Ndisaname mukutivesa kukoma amalawi ndipo iweyo usasiye kutivesa kukoma❤❤❤❤❤
Uli bwino kwambiri plz keep it up with good music🎉🎉
Zosangalatsa kwambili,,kuimba modekha koma zodalisa❤❤
Kwambiri
Dalisani ambuye bizinesi yangayi,powerful mesege
Nyimbo zanu zimatichosa khawa bwana pitilizani❤❤
Mwayipweteka bro nyimboyi yooh. Respect
Sou Moçambicano mas gosto muito das tuas músicas força
Iweyo ndye umandimvetsa kukoma 💙💙
Saint Realest unabwera kuzakhala ndipo nyimbo iyi mmmmmmmmm.ilibhoo
Ulemu wanu .. powerful song
Watching from Zambia nice song
Awonjezere tsogoro lako Mulungu wa taimon
Monga ngati ine ndikudutsa mnyengo zomwezo, koma ndimadalila mulungu yekha basi
Please keep it upp!!!!! Don't change the beat, stick to it for your identity. Marvellous.
You next big thing in Africa here in Zambia we love you
Tás a falar a verdade irmão🙏🙏🙏
Ga 1:06 1:06
A bro mulungu apitilize kukusogorera ND talent yomwe ulinayoyi
Mukuyimbatu bro palibe opikisana nanu
Komatu munthu wankulu,mukundivetsatu kukoma,ine Domingos Eduardo Lapuquene kuno kumozambique,pitilizani bg.
Ndipo kachilungamo ❤
❤❤❤ imandibaya this is so touchble song
Dalitsani mbuye chonde Dalitsani ❤
Zabwino kumayamika......... touching song!
Aisy iwe ulibhoooo. Luso ili lofunika kulichemerera kwambiri
Meleka in this song ❤❤❤❤ anapitadi soja
Ulemu tuu muktivetsa kukoma mbuye dalitsani nyengo zisithe basii
wow bro may God bless you ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉
Zanga umatha kudandaula nice
Chilungamo ichi, keep it up brother
Ngati nde nyimboyi wayimbira ine 😢
Nice one bro yiri pa repeat
One is one day fada ndinu katundu 🔥
Koma guys Nep man ndi akatundu,,,, Chichewa anga chidzungu,,,,,,ndaikonda nyimboi,,,,,,, Nayeso Queen Sheba mawu ngati Ethel kamwendo Banda
Ili bwino kwambili imandipeza nyimbo imeneyi
Taimon my keep it up the good job
Muli ndi luso amwene
Mulungu azikudalisa kwambili aise umatha
Big up 🎉❤
Gods time is owez the best....Very talented
A good song with a powerful message
Mbamband fadah 💥📸
Chilungamo bro nyimboyi aliyese yimukhuza ndithu mphatso yimeneyo bro pitirizani
This boy he's coming good. Love his songs
Unalikuti nawe❤ keep it😢
Talented guy all the best bruuu🤙💥
God bless you and your family and your song
Powerful message,keep it up
I like it ❤❤
Eish 3 yrs agooo? Iwetu uli ndi luso
Beautiful song from Zambia
Big Kodi big mulikuti mwakwapulatu ineyo comment yanga ndikufuna ntakuonani big 🎉🎉🎉🎉
Chilungamo ichi mwaimva brother
Amazing❤❤
Brother keep it up mmatha
Nice song my dear keep it up
Nice voice & encouraging.
I love this keep it up
Chulungamo ichi bro, keep it up
Nyimbo zako zomanipanga tiyenayo bro
I don't like sad songs but I like this one very much
Ndipo dalitso I ntchito ya manja a taimon ndi luso munampatsa zisomo zikhale zochuluka dalitso I ma plan ake
Mbambande ❤
Continue with the great work
Brother this song ❤❤❤❤
Palibe yesu apa aaaaaa nyimbo or Satana sangasuthe😂😂😂😂
Za fire braz
Zoona zake bro nice
It's burning 🔥🔥🔥
Zokumba ndi mbweee nkhan nditerechede eish !!!
This is a big song boss 💥
Amen brother keep it up
This song must win award
Taimon ndiwe one
Sometimes it's good to listening good song like this
Nice bro🎉
Nice my bos
Very powerful brother
Never give up my brother
My favorite song ❤️🙌
Perfect❤
Talented❤it
Powerful brother 🛐
Very nice sumu/song
Dolo pakhani ya music
Amen ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
My favorite song ❤️
So touching bro yoj are talented🙏
My mates, kodi mau oti fada amatanthauza chani pls open up my eyes poti kuphunzira sikumathayi
Wow ❤❤❤❤❤❤❤❤❤