I love your songs my brother umatimvetsa kukoma osati zandale ndipo usasadzalole zachima Dan luh udzawononga tsogolo, umatiyika pa map nyimbo zako tikamawonela ndi anzathu osamva chilankhulo chakwathu amangovina nawo kamba ka ukhondo osati zojambulila pa phulusa
To my own side he is the best so far from Malawi and I love this gentleman songs 🎉 I patiently waited for the full song my cousins from Malawi like my comment
This song made me shed tears 😭😭😭it reminded me of someone 💔I wish u wello dear wherever u r💔 Whenever someone likes this comment I will be coming to watch again and again
Ena nde akumati Video silibwino aaa Guyz this is the best video with this type of song. Mukachurkaso zochita mu video ngati iyi zimabisa uthenga wamunyimbo. Kudos Timon💯
I really wish mukananditenga ... Kojambulaku ... Mumafunika kuchitika zambiri... Zogwilizana ndi message... But all in all ur the best bro ... Blessings on ur way ...keep it up
You deserve an award for gospel artist music 2024... you are preaching to many lives... keep the fire🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 burning as you are making a good history...iam very happy for this song...may God remember you in a special way
Nyimbo yopereka chilimbikitso mwauzimu, Mulungu apitirize kukudalitsani ndi kukulitsa malire a utumiki wanu a Tipa, kuno ku Mbulumbuzi Chiradzulu timakunyadirani🙏🙏🙏
A DAY IS COMING. TAIMON TIPA WILL BECOME ONE OF MALAWI'S GREATEST MUSICIAINS
Amen
I'm praying for this🥺
Ndipo live🥳🥳🥳🥳
Ndipo si kale😊
Biggies-wa ndi handsome plus alinkutchena🔥🙌
Anyways nice track keep it up✊🏻
Ndipaseni ma like ndipo nthawi yonse ndikabwera ndivera nyimboyi kutengera momwe achulukira ma like❤❤❤❤❤😂🎉
osadanda bro
My favourite ....
Amen
Zambia is proud of you bro 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇲🇼🇲🇼🇲🇼❤❤ I will be liking my comment alone kaili no one will ever like it ❤😂
Nyimbo zako zimandipasa chimwemwe pamoyo wanga,may God bless u dear🎉
" Ndiambiri okudalira ndipo akuchulukira ukazisiya adandaula" mawu awawa andilimbikitsa. Nice one iyiyi nyimbo mwakunga Bro🔥🔥🔥🔥💣
I love this song! Keep it up Taimon.
Aisee ndiwe Shasha u got talent anthu akuchedwa kuzindikira chimenechi this is great man
If you believe that this is pure talent from God like my comment
My artist
100%
100%
Yes bro
Proud cheba here love this song
This song.......eeeh🙌 amene tikudutsa nyengo ya nyimboy like my comment❤
I wish i could give million likes but am advertising it
Song of the moment big up
I love your songs my brother umatimvetsa kukoma osati zandale ndipo usasadzalole zachima Dan luh udzawononga tsogolo, umatiyika pa map nyimbo zako tikamawonela ndi anzathu osamva chilankhulo chakwathu amangovina nawo kamba ka ukhondo osati zojambulila pa phulusa
Nyimbo ili nd uthenga iyi Ndipo ngat ukufotokoza za ine 🙏🙏🙏 keep it up fadah
Ndipo mbali yakuno ngt wandiona ine
@@ChifuniroMisiyasimaka apopo poti ukazisiya anthu Ena adandaula... Ndalimbikisika kwambiri 🔥🔥🙏🙏
Nyimbo iyiyo olo kumaimvera daily singakutopese rather kukulimbikisa
This Man is completely talented. I love your music ❤❤.. sending love to you from your die hard fan from Zambia 🇿🇲 ku Chalo 🌏
Yes Nyimbo zanu Big zimandiwaza havy palibe nyimbo yako yomwe unapala Big up prz Malawi Mulandilen Mu2yo kuno Watifilisa kwambiri
Ili ndi luso losakakamiza lija.
❤️ big up young man.
To my own side he is the best so far from Malawi and I love this gentleman songs 🎉 I patiently waited for the full song my cousins from Malawi like my comment
This song made me shed tears 😭😭😭it reminded me of someone 💔I wish u wello dear wherever u r💔
Whenever someone likes this comment I will be coming to watch again and again
Zambians let's gather here 🇿🇲🇿🇲🇿🇲 to support this man 🙏
❤❤ We're here 🇿🇲🇿🇲🤦👍💕🇲🇼 Zambia Malawi
Here
Na nyimboyi mmmm repeat the whole day. Kuchita kumveka tseketseke
Your my favorite artist in Malawi your on high level dzina munapanga kale bro
Ase ndilibe mau ambili koma ochepa omwewo diyakhulapo base ❤❤❤❤❤❤ iwe umatha kuimba ase ine sindikonda zanyimbozi koma iwe wekha ndagoma nawe
Viewing from Zambia 🇿🇲 it's my dedication from my family. But I promise this year I shud overcome my dreams
Iwe ndi dolo kwambir
Congratulations 🎉❤
Apa ndapeza nyimbo ina ku playlist yanga. You're a blessing to Us ❤.
Proud of your music big man I like it
For example uli mu galimoto yako pamene paja 🔥🔥🔥ingamveke bwino
Ndipo chingakomeditu
😂😂😂 ine tikuivela mu mgalimoto ya mmaganizo zanga phee apa ndili pa chingeni
Iyiyi nde mwapha akulu big up fada
My favorite artist.chaka chake ndi chino.ishuta ndithu
Ena nde akumati Video silibwino aaa Guyz this is the best video with this type of song. Mukachurkaso zochita mu video ngati iyi zimabisa uthenga wamunyimbo. Kudos Timon💯
Anthu ena anabadwa Ali afiti kale
Those who are coming from tiktok let's gather here and show some love❤❤❤❤❤🎉🎉
Big up taimon tipa umayimba nyimbo zabwino kwabasi
Powerful song brother
That's great 👌Well done and may the good Lord enrage your territory👏👏
If you really like this song give me like
Iweyo ndi dolo kambirimbiri. Luso ilili ndi mdalitso wako adah
Kuswa kugwetsa basi , nice song
Awawa ndi akatakwe pamaimbidwe ndipo nyimbo zawo ndizopatsa chilimbikitso.kudos Mr Meleka n keep it up big man ❤❤❤❤❤❤❤
Nyimbo iyi yawona nyengo zanga ndipo ndi ambiridi okhomererawo 🙏🥰
Taimon you are the best musician.. Ndiwe doro aise
We got a talented one here in our country ❤❤❤❤❤
Ohh this is nicee❤❤❤
Keep fire burning 🔥
Keep up the good work nyimbo dzanu muli ma phunziro aphavu mulungu apitilidze kukudalitsan ndi mzeru
Komatu ukukamba zoona kungot nyimbo zako zose ndi zamathandauzo , koma iyi ngat ukundinena ine ayi zikomo wandimasuladi choona siine ndekhad
Nc song bg boss your number one music yachilimbikiso kwambiri 🎉🎉🎉🎉
Matipatsa chilimbikitso God bless you all time
WOW congratulations all guys tiuzeni zokhuza oyimba a gospel
😢😢😢😢 nyimbo iyi waimbira ine pena ndikuti bola ndingozisiya😢😢😢😢😢😢 udindo wakula ndakanika
Woow this song is nice
Receive your flowers 💐💐💐
Can't wait for the day you will blow pipo will see your talent continue hoping in Jehovah❤
Nyimbo iyiyi eeee muli uthenga wachilimbikitso ❤❤❤❤❤❤
I really wish mukananditenga ... Kojambulaku ... Mumafunika kuchitika zambiri... Zogwilizana ndi message... But all in all ur the best bro ... Blessings on ur way ...keep it up
Koma uyuyu nyimbozakezose ndi minyanga yokhayokha mmmm umathaaise
This song 🎵 ❤❤❤ achuluka okudelera Ena wokukhomelera kma tiyeee🎉🎉
Fadah uli luso kwambiri 🔥🔥🔥🔥
Am from Zambia I like this song I play 100x day
Nyamata woziwa kuyimba uyu🎉🎉🎉🎉🎉🎉 ulemu wanu
A very powerful song. The message is just good and on time. Keep it up brother.
Umatha aise iwe ndidolo kwambir nyimbo ikuchita kuyakhula mumtima kupelekaso chilimbikitso
Thank you Mr Meleka, mumati limbikitsa, mumatiphuntsa, mumatilalikira, mumatidalitsa kudzera munyimbo zanu. Keep it up,❤ Ife Tagwilizana kuchita mwanzeru ndithj
I like this guy ❤
Kamandisangala ako akuti TAIMON ka intro kekhako kakupala zokoma zili ku sogolo. So nice big up.
Ndigayile # yake
This is fact nyimbo iziveka ndi2 like this one
This is nice Hit Bigman.. work hard. The message is Just too great
I would like to meet this guy, you going places my guy
I really love his songs!!! Ipase moto sending love from Zambia 🇿🇲 ❤️❤️❤️❤️🔥🔥🔥
Big up brother
Almighty God, bless this lad for me. I have always enjoyed his music. Big up, day ndiyimozi nfanayi azafikapo pamene amafuna.
Ma views mmene akuphaphalikila ngat mvula ya matalalatu❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️
Uyuyu nthawi yake yakwana basi
@@chimwemweligomeka9188 ndipo chikaloza chimakhala chaloza
Ndipo nde yakwanadi eeeeee@@chimwemweligomeka9188
You deserve an award for gospel artist music 2024... you are preaching to many lives... keep the fire🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 burning as you are making a good history...iam very happy for this song...may God remember you in a special way
All those coming from mikozi let's gather here and give the guy a shout out
Mtima wako watopa thupi lako lafoka pena ngati ungozisiyaaaa 😢 ndiambili okudalila ndipo akuchulukila ukazisiya adandaula,,,,,,pamenepooo Ambuye titsogoleleni
Dolo🎉❤🎉
Silidutsa tsiku osaonera nyimbo iyi🔥🔥🔥 keep it up 💃💃
One of my favorite song
Nyimbo iyi ndi painkiller 😢,,Taimon never disappoint 🎉
Wabwera taimon
Nyimbo iyi imandpasa chilimbikiso mmoyo wanga.... God bless you bro...osalora satana akulamure...
Siine ndekha ndikuonera nyimboyi, dnipo siine ndekha ndaipang Like.
Ndikuyamikire ulimoyo bro...... UMATHA AND KEEP IT UP 🔥🔥🔥
You are talented
Am speechless bro mwaganiza kwmbr 💪💪🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Iyi ndi one of the songs we need, pure music kutilimbikitsa brother keep it up
Almost number 2 on trending Timon you are on your own fire my bro love from Zimbabwe
Talk about God given talent? This is the definition 💯🔥
Ikhale National Anthem bwa?
Yasenza mavuto atonse 😅😂
VOLUME IKWELE Taimon T maka maka azibambo wa mmmm kumangozipha ngati mabvuto ali nao okha ''Si we wekha'::🎉🎉
Kunena mwachirungamo ndima konda adh awa amamenya ma hit abwino hvy keep up good job bro 🙏
Nice song bro with meaning we really appreciate on this truck wish you all the best
Osadzilembeka malire ,uyuuu nyimboyi waimbila ma fans ake lunso koma ili aise pitiliza
great message,yandigwira mtima,big up Taimon
So educative song my brother,wandisangalasa ndi nyimboyi. Ndikumakufunira zonse za boo.
Man ndavula chipewa coz it's mwang'alula 2 much. Congratulations go ahead .
Taimon wandiimbira ine ndithu ummm mulungu akupatse chosowa chako
Chipanda nyimbo iyi mnakasiya ntchito, koma yandipasa chilimbikiso kuti ndilimbikile magobo
Zosatheka kumangolira km nafe tikudutsa momwemo 🔥💥 iweyo wabwela 🔥
Nyimbo yopereka chilimbikitso mwauzimu, Mulungu apitirize kukudalitsani ndi kukulitsa malire a utumiki wanu a Tipa, kuno ku Mbulumbuzi Chiradzulu timakunyadirani🙏🙏🙏
I like you aisee ,,,,, continue nyimbo zako zimandiphunzitsa ndisaname
Akuru awa amatha kwambil nyimbo Ngati Izi ndizoenera kupita Ku world 🌎 Koma Vuto amalawi eshiiiii ❤❤❤
ur a good adviser boss. keep it up
Ndkaona anthu amene akumandidalira kumbuyo kwangaku, nyimbo iyi siingachoke pakamwa panga, big up taimo
Umayimba bho kwambiri 🔥🔥
You' re the best Taimon,I wonder why people don't recognize you,but it's my prayer that one day you'll become famous in Jesus name 🥰