Taimon Tipa_Wanga (official music video)
HTML-код
- Опубликовано: 27 июл 2024
- The song talks about a Man who is deeply in love with a lady.The man would like to build a life with this woman and have kids as beautiful and as good mannered as she is.
Видеоклипы
Sindiziwa ky bwanji Ada awa sachuka kwambiri koma mwanayo amathaa
Sanalowe sataniki bro osadabwa onamuonera DNA amatchuka?? Nyimbo zake ndi katutuso bro
It's enough for us to enjoy his song, samafuna kuonjezera zoti azapwetekedwe
Slower Satanic basi atchuka
Ndipo nane mafuna zanene mene amaimbira DNA muja but satchuka e same dis guy conde usalowe satanic zingoimba ada eeeeeeeee
Kutchuka sikuimba bwino ayi...kma nthawo
having music by taimon pita the first hand in Mozambique 🇲🇿🇲🇼 may God bless you
Uyuu osamamuphweketsa Nd artist number one
Bwana taimon inuyo ND kawawa❤❤❤❤wat a video is this wow🎉🎉🎉🎉🎉
thamanga mwana muna zawenu kutukwanitsa powerful song .
Ilibho kwambili nyc song wanga wanga
Popeza akamapangama promote akumatenga okhaokhawo apansi panja, koma kukanapanda zimenezo Taimon yu anaenera kupangidwa promote ndthu eeesh this guy is genius
Taimon tipa iyi yokha wapha ulemu wako respect
let's give him support munthuyu ndi wa ku Malawi konkuno 💪
Uyu amatha ❤❤
Mwapha🔥🔥🔥
Luso losakakamiza amwene... mbambande
Mwakunga malume. Mutha kudzatiimbira pa wedding monga top fan
Saname great song iweyo umatha
Iwe ndi Dolo,,,keep it up
Big up brother Taimon this is fantabulous song
Mwaphaaa boss❤❤❤❤
Tipa🔥🔥🔥🔥🔥
Aise nyimboyi wapha, beat selection nde ndi mwala 🔥
Video nde ndi 100🔥🔥🔥
Ndapanga like sanaonere 🔥🔥🔥
❤❤more fire pa easy basi
Uli fire Fatah ipondeni
Yabwera mu nthawi yake nyimboyi inu simukhumidwisa 🎉🎉
Very good and interesting song Malawi watsopano is what we al need
Apa Tymon wafika🔥🔥🔥
Iweyo ndwe katundu umaswa ❤❤❤❤❤
Unabwela iweyo🔥🔥🔥
Saname brother nyimboyi mwayipa yt yoooo🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Awanso ndima level ena,umatha Taimon
Iwey luso ndi ❤ camera perfect
Chinyimbo mbambande❤❤❤❤❤❤
May your career keep on growing...... much love 💕 for you Taimon🙏
mwaphatu man hit 🔥🔥
Nice song 🎵 my brother
Wabweraso iweyo Tai🔥🔥🔥🔥🔥
eshiiii koma iweyo mm mm umatha aise. receive your flowers❤🔥❤🌷🌷
Wacha, Wapsya, Taimon that's Maturity at its BEST 😊
Kuyimba mmatha bro and ur videos very fantastic serious
Bro wumakwana 🔥🔥🔥🔥♥️♥️
❤❤❤ ndie iwey amene umakhala uli iweyowe
Chitaimon chimatha kuimba kwambiri
Koma mwana uyu mmmm 🔥🔥🔥🔥
Umatha kuimba aseh❤🔥
Fire 🔥 mfana oopsa
Taimom inuyo umakwana 🔥
Kudzichepetsa Kuja sikupusa ❤
Katswiri kwambir iweyo bro 🔥🔥🔥🔥🔥
Mukukwana mafana ❤❤❤😂
Nice one
Mbambande Taimon
Nice song... video on point 🔥🔥
Wow wow this is nice ❤❤❤
Nice song ,,,,big up
Za power bravoo
Big up brother nice song
❤❤❤..Nyimbo kawawa big up
Inu nd 1 🔥🔥
Ase Iweyo Umatha kuimba ..Respect ✊️🔥
Ichichi chikuvaya man❤
Nice big up🥳🥳
Nice tune
Absolutely that's amazing bru keep burning my bru🔥🔥🔥
umatha anse 🎶💯
Hinddee Taimon umatinvesa kukoma nd nyimbo zako❤❤❤
Iwe ndi 1 🔥🔥🔥🔥🔥
NYC mlw good music
Ungotola Tune yomweyo uwona kusintha bro uli bho heavy and i like your style
Umatha bro🥳🥳🥳
shasha🔥
Nice song, video so nice as well !👍
Mwakwapula man
Gud job bro
Mumakwana bro nice song
❤❤❤❤ Umantha
🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤
You did a great job, congratulations, the video was worked o
This is fantastic
You're a genius bro
This is💥💥💥💥💥
Cool guy 🎉🎉
Wow that's awesome 👏
Uli mwala aiseee Kuno ku
Eeeeeh! Yaphedwa❤❤❤❤
big up taimon size ya tanzania iyii 🥰🥰🥰🥰
Ndimaona ngati ndaona ndekha, this tune ndi ya Mbosso
Nice bro
Mwajambula ankolo
Iweyo waza aise
Outstanding Taimon
Nice tune🔥🔥🇲🇼
Brother brother this is Great STAFF ❤❤
DOLO kwambili Mwana wakwathu❤❤🎉
Ngini ili bhooo broo I love your music
Ase umatha big up
Really nice one
Mkazi ndmwala
I love 💕 this song Mr Taimon😔🌹
Number one nice song ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Come on guys everything is OK from video and oudio perfect wamenya bho
Taimon ali mu lane yake yake nyimbo yokoma 🔥🔥 Bless up
Nyc song aua
Uyu ndi dolo kwambr
Nice brooo love ❤️