Koma Mimi inuyo aaaa, munabwera kudzatilimbikitsa ndithu🥰, malamgizo abwino achilimbikitso,like my comment I want to come again fokika mmawa tikwanitse 5 million viyuzi🔥🔥🔥🔥🔥
Ai mama MC iyinso ndie mwaimba ndithu God Bless U .....guys zoonadi tiyeni Tithamange basiii maiwa akunena zoonadi ndithu ....mungoyesa ngati mmene anzanu tikuyesera ....God again bless u all
Your musical intelligence never fails you. Great power and control are all there. Your booming voice and bags of character in your tone unceasingly amuse and bless us. May you live long Miracle
Hit 🔥 ingokhala national anthem ya 🇲🇼 Malawi basi🙌🙌🙌.. Muona mmene anthu tingamalimbikilile mwatokha. Yakalei mmmhh ipume kae ili too much 😔. Miracle iyiyi olo ba neba aziimba nawo. Congratulations 🎊 🎈
Muturity in composition now, big up to audio producer and team for great video. Grace chinga legacy lives on Song which reflects our daily lives Good citizens make good Christians. We thank God for everything.FEAR OF LORD IS THE BEGINNING OF WISDOM!
Apapaa nde you are bringing back Grace Chinga. Nyimbo zoti you can sing along and learn something. Keep it up!!
Grace must be so proud honestly
Sangafike pa make
zabwin zonse
I don’t know how to thank you enough every one watching this song daily on this channel will testify in Jesus name God bless you all lovely people❤
You are a true copy of Grace. Keep it up
Love you baby girl
This is what we call creativity right, & a replica of ur mum... Si zija za milandu zija
Thank you as for me l watch, 10 times a day because it touches my heart ❤ 💙 💜 💖
We love your music
Koma Mimi inuyo aaaa, munabwera kudzatilimbikitsa ndithu🥰, malamgizo abwino achilimbikitso,like my comment I want to come again fokika mmawa tikwanitse 5 million viyuzi🔥🔥🔥🔥🔥
❤❤❤
❤❤❤❤
Thank you Chinga for the encouraging song I appreciate your work, much love from Zambia.
This song deserve million view in a month.
Miracle beautiful encouragement
Ladies tchukumani osaziyang'anira pansi.
Thank you lovely people for the support the love I appreciate let’s keep on viewing everyday until we make it 💃🏻💃🏻💃🏻💃🏻🙏
Nice and powerful!!!!!
Iyiyi mpakana 1 million views
Wow!!! The way I love this song, continue teaching through songs .this is powerful
Am Zambian and In ❤with your songs 🎉🎉🎉🎉
Ndipo it's on my status everyday nyimbo iyiyi waiumba
Your loved by many dear keep the fire burning
Can someone like my comment ndikabwelenso cos this is wow
Thanks alot
For sure bro,apapa ndiye was waiting bomba mwanayi
@MiracleChinga limbikirani sister, this is the great hit,pitilizani ndithu Peter from RSA
lero ndimati simpita Ku business but after listening to the song basitu ndanyamuka
This is nice, quality video,the outfits were giving,nyimbo yopatsa chilimbikitso
Uthenga wabwino,kutchena,vedio kukongola,chivoice mbambade,production yabwino aaaa mwapha nyimbo iyi 100 pa 100
Everything on point
Ndipo 100%
Mwatilimbitsa mama tithamangadi
Proud of u dear.... ndithamange inee🙏
Miracle nyimbo mwapha iyiii it's so encouraging we really have to be self empowered and hard working 💪
Powerful message miracle❤❤
Abale pangani zoti ndibwelenso❤
Bwerani basi
Ai mama MC iyinso ndie mwaimba ndithu God Bless U .....guys zoonadi tiyeni Tithamange basiii maiwa akunena zoonadi ndithu ....mungoyesa ngati mmene anzanu tikuyesera ....God again bless u all
Miracle nice composition. Iyiyi wapha Mwana Iwe. Your mum is happy
Wow ine chimwemwe mu mtima sikadza kokhasooo tithamangebeee basii yesu wathu pa pambalipaaa
Miracle chinga wow...her fans lets gather here😍😍
We are here already
Tilipo kale ❤
Nyimbo yolimbikisa iyi God continue bless you Mimi
Amen amen 🙌🙌🙌
Tilipo
Your musical intelligence never fails you. Great power and control are all there. Your booming voice and bags of character in your tone unceasingly amuse and bless us. May you live long Miracle
Credit to the producer he understood the assignment... this is nice Miracle 🔥
Ihave never loved this girl's songs but today I can testify that ihis is first song to like god bless u❤
Nyimbo iyiyi uphula nayo aseh. NGOs will come for it. Well done mamie
This is wonderful talent, God ur so great. This is What we expect from u miracle.
Koma mulungu yemwe amakupasa nzeru zomalemba nyimbo chonchi zi mmmm timuyamike nyimbo mwabebesa iyi it's as if mwaimbila inesotu mimi🎉
Nice wow tithamanga nawo nyimbo mwaimba bwino, kuvinaso kwabwino,voice yabwino, mulibe Za diku diku zija😍😍
Miracle zomwe wayambazi ndayamba kukonda nyimbo zako🔥🔥🔥 uku ndiye kubwera🔥🔥🔥🔥 poangira vn ndipati ndoyipatse moto bwino 🔥🔥🔥
Eti vn wandiwaza bwanji
Eeeesh in love with this one nsaname....kupempha kutukwanitsa😍😍😍😍😍😍
I feel like Grace chinga is still alive keep it burning 🇿🇲🔥👑💪
Miracle iweyo apa nde wapsa basi palibeso kubwelera m'mbuyo , go miracle we love you❤❤❤❤
Ndalimbikitsika, inetu ndi nthamanga once again congratulations mami mwapha nyimboyi🎉🎉🎉🎉
Nyimbo yabwino iyi Miracle indeed, Mulungu azikutsogolera
Hit 🔥 ingokhala national anthem ya 🇲🇼 Malawi basi🙌🙌🙌.. Muona mmene anthu tingamalimbikilile mwatokha. Yakalei mmmhh ipume kae ili too much 😔.
Miracle iyiyi olo ba neba aziimba nawo. Congratulations 🎊 🎈
This song is very nice 👌,,,,or munthu ukamvera kumati koma yeah ,,,,Well done Miracle
Lozereni poti mkomente with an audio, funa my'imbe likhweruuuuuu🥳🥳🥳🥳🥳🥳
Well done Miracle 👏 🔥 This is a noce song,very encouraging.Ambuye apitilize kukhala thandizo lako mu dzina la Yesu.
Apapa Grace chinga uja alimoyo ndinthu miracle wadza sure
Powerful song ndipo muli chi message 🔥 🙏 pangani zoti ndibweretso good people 🥳❤️💃
Thank GOD watipatsa zochita,,, kusatulutsatulutsa kwako kwa nyimbo kwabala zipatsobzabwino...... Nyimbo yabwino
Nkhope ngati ya mayi ake ,,❤RIP CHINGA ,
WATCHING FROM DURBAN RSA❤❤❤
Thanks alot for 44k views let’s hit 200 🎶🎶🎶🎶🔥we can do this people
Yes we can do ❤❤❤❤❤ in Zambia 🇿🇲 we are with you mama mitrick
Yes we can do ❤❤❤❤❤ in Zambia 🇿🇲 we are with you mama mitrick
Ndiye iyi ndi nyimbo yapatali. Akudslitseni Yehovah.
I like the vibe in you ❤ maka the confidence 😌 the music video s good as well
Don't worry mama
Osati nkhondo mwaimbayi mungaimalize chanichani zama vuvu zija... Iyiyi ili mwala ... Dope hit
Ndangoona pa Mikozi basi tu akuthamanga mzaonere🥳🥳
Been smiling throughout the song, beautiful characters and nyimbo yolimbikitsa
Wandipatsa chilimbikitso mwana iwe, 😢😢 misonzi yachimwemwe😊,
Watching from Moçambique. I love everything about the song. I am just repeating it.
God bless you for encouraging me.
My Zambian people let's gather here we have a meeting 🇿🇲
Let's gather here Zambians miracle fans.Miracle you're a vibe mami
Tilipo,,love u Mimi
Wow, miracle this is so on point , everything on point , God bless u
Iyiyi mwapha amwali ndipo zonse so on point tu
Miracle 💕 iweyoo mhuuu ine mpakana misonzi kumukumbukira Grace eeeeiish Grace sanafeyi
Grace Chinga is still alive through you Mamie
This is most of the amazing songs
Nice one nyimbo ili bwino iyi ❤❤❤❤❤ My God continue bless your talent like mother like daughter
Ma dance mpaka mlenji
Mulungu odzwa kudalisa aonjezere luso mwaiwe❤❤❤
Nice song miracle am happy for this song
God bless u😍😍😍
Iyi nde yabwera ,,inde tithamanga mimi❤🔥🔥1M today
Go girl go, this is very beautiful,apapa tikulimbikitsika
Miyala ija is very important,ikachuluka umamanga nayo nyumba, beautiful Miracle Chinga...
Dolo kwambr Chinga .... full of maturity 💪💪💪💯
U have really encouraged me🎉🎉🎉🎉🎉 miracle fans let's gather here❤❤❤
Nyimbo iyi🙏🙌🙌aayayayayayayaaaaaa,Mawu ndilibe
Miracle this is nice 🙌🔥
Ngat ndilire mwamva Inu mmmhhhh very beautiful
Ineyo ndilibe zoyankhura ndingoti miracle kukazakhara kotheka tsiku Lina uzanditenge munyimbo zako
Miracle iweyo umatha ndikungobwerezabwereza kumvera eshiiiiiii
Nyimbo mwakazinga iyiyi mamie🥳🥳🥳🥳🥳🥳
Nyimbo zako ine ndiye sizimandisangalatsa .....koma na iyiyii aaaah wabwera iweyo ...ndikumaivera tsiku lonse! 🤸💃💃keep the fire burning🔥🔥🔥
Iyi nde miracle wapha muli uthenga umu
Na iyi yokha kuika Pa repeat basi keep it up to give us a good gospel music ❤❤
Welldone miracle chinga so God voice
Mulungu knew Grace was a blessing and then blessed us with Miracle 😭😭❤️❤️❤️🙏🙏
I look at this video and am very proud of what your journey has been like this far. Very proud. Nice one Miracle!
Ambuye apa pokha Grace Chinga munamulemekeza. NICE Mimi
Nyimbo waimba iyi so encouraging to women and girls
Nyimbo iyi imandifikitsa patali ine eeeeesh ❤❤❤❤
Ayi apapa ndikupatsani mendulo ya ulemu mama- motivation song keep it up
Eeeh uyuyu amatha.. this will be my daily anthem sure..
Watiziximutsa mam.....ndaonera ka 50 woww nice song girl.
Powerful ... your song is so encouraging❤❤❤❤❤ apapa ndikuthamanga molimbikila love you❤❤
This is a beautiful piece and there is so much creativity. Zomadikula mwachikunja zija mulibemo zomwe zikuthandizila kubebesanso nyimboyi
Anafe kuyamikila sitidziwa koma apa big up Miracle
This is beautiful, message on point... congratulations for such a beautiful music.
Apa nfanayu waitolera sopano...this is the level we ve bn waiting to see you in..kudos Miracle
This is good music @miracle!!! Well composed and the video altogether is a top-notch!!!
Wooow nyimbo yabwino iyi Miracle tiyeni tizithamanga azimayi tidalire zathu zaweni zidzetsa mnyozo
On behalf of all your Zambian fans we love u nd yo music 💚💃
Wow🥰🥰this is great Miracle....Mulungu apitilize kuyikizabe nyimbo za pamwamba mwa iwe ....iyiyi wapha 💯
Muturity in composition now, big up to audio producer and team for great video.
Grace chinga legacy lives on
Song which reflects our daily lives
Good citizens make good Christians.
We thank God for everything.FEAR OF LORD IS THE BEGINNING OF WISDOM!
wabwera mimi...congrats❤❤ uthenga wabwino
Miracle ayi zilibwino kwambiri. Ambuye alemekezedwe. Proud of you❤
Great composition and great tune. I love this song Miracle
Nice nyimbo,zonse zili wow, keep it up🥰
Super super 🎉🎉🎉🎉.. congratulations.. Ambuye apitilize kukupatsani nzeru ndi zina zonse uthenga wanu ulibwino kwambiri.
Ndipo nyimbo yokoma kumvera ndikuonera komwe....good message to us ladies
Wow nyimbo Ili bwino iyi pitilizani mama kutumikila mulungu kudzera mayimbidwe
Mbamband❤❤❤Mulungu aonjezera nzeru zakuya nyimbo yachiphunzitso
Uliboh, ndimakufila kwambiri ❤
I love the outfits.... Well done Mimi❤
Ineyo nde ndungowonera daily tu eeeeee
I love the song
Wow , I feel the presence of Grace chinga. Keep up the good work miracle.
Kumayambililo ndinkayesa umayimba chifukwa mayi ako analo oyimba koma nditamvela nyimbo zako ziliwili zakumapetozi ndinaona mphatso yamayimbidwe ulinayo ndipo your gifted
This is amazing 💕💕
Njala kuchita kuthawa ngati ndisasiye kuvela
Wowooo among all your songs this is my first song to like, it's got a true meaning keep it up
This is nice...so encouraging! May God miraculously bless you.
Iyi yokha ili bho.100%from me.keep the fire burning.the world needs pple like uu