ZIMENE ZACHITIKA KU MAJETE GAME RESERVE PARK PAMENE A PRESIDENT CHAKWERA AMAKAONA ZINYAMA LERO

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 15 ноя 2024

Комментарии • 106

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya 2 месяца назад +7

    Koma inu anthu assembles of God tawululani, munthuyu analidi m'busa? Ine zimandikaikisa, anthu akufa ndi njala, iye nkumayendera nyama zoona?Ambuye tiyang'anireni a Malawi 😢😢😢😢😢😢

    • @HappyAnt-uz5je
      @HappyAnt-uz5je 2 месяца назад +2

      Ine ndakayika

    • @DeliaKaduya
      @DeliaKaduya 2 месяца назад +1

      @@HappyAnt-uz5je ndipo ine ndimakhala ndi mafunso opanda mayankho pa m' busa ameneyu

    • @HussainHhu
      @HussainHhu 2 месяца назад +1

      Uyu ndigaru ndithu

    • @ComradeComrades
      @ComradeComrades 2 месяца назад +1

      Eti etiiii iiiih koma chikangawa chimenechi kaya nde thengo chikuyendelali chufuna chikaphekono ndani

    • @jamessheki4293
      @jamessheki4293 2 месяца назад +1

      Eee mulungu atikhululukire mwina ndi chilango

  • @mlfmalawi4393
    @mlfmalawi4393 2 месяца назад +1

    This is a nice president that Malawi never ever had before, my vote!

    • @mphatsobwanali5981
      @mphatsobwanali5981 2 месяца назад

      Galu wa munthu mbamva, wokupha ngati uyuu chikangawa

  • @JamiesonKaunda
    @JamiesonKaunda 2 месяца назад +5

    Sitinakhale ndipo sitizakhala ndi chitsiru cha president ngati galu ameneyi mmalo mokaendela anthu akufa ndi njala lero akukaona nyama shame on you chikangawa.

    • @DeliaKaduya
      @DeliaKaduya 2 месяца назад +1

      Zizamuvotera nyama zake zomwezo 2025

    • @EmmanuelMphande-f4l
      @EmmanuelMphande-f4l 2 месяца назад

      😂😂😂

    • @tasmania527
      @tasmania527 2 месяца назад

      @@DeliaKaduya Ndiwe chitsiru chamunthu ndipo chaulesi. You don't deserve kukhala nzika ya ku Malawi. I can't understand you're insulting the president for your stupid laziness. Ulira mpaka uzafe galu iwe.

  • @IbrahimJackson-i8h
    @IbrahimJackson-i8h 2 месяца назад +2

    Koma abale Chikangawa ai anakoza Malo moti apite akaone kanthu akufa ndi njala aja ali mutchile pano kuyendela zinyama

    • @tasmania527
      @tasmania527 2 месяца назад

      Njala ya kumwera kokha. Dziko limafunika zambiri kuti litukuke osati kungokhalira nsima, za chamba basi.

  • @EdnahShantell
    @EdnahShantell 2 месяца назад

    Anavota karetu galimoto la tsku transport inanyamula mavote ndipo ali ku South Africa 😅 titha pyiti alamulire Nyama zomwezo, ukachoka kumeneko upite ku chikangawa ukaonenso unaphera athu 9 paja galu

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 2 месяца назад

    Kikikiikiki PLUS Hahaha kenako ti
    Mva kuti akuyenderanso Anthu midzimu wongwira mbewa zambiri Midzimu ndi Abwampini èeeeeee l don't think he has peace koma Ziliko😅😅😅😅😅

  • @MacmillanMkambeni
    @MacmillanMkambeni 2 месяца назад

    Nice move

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 месяца назад

    Allah akuona amalawi tisadandaule

  • @HarveynsonthiNsonthi-u4n
    @HarveynsonthiNsonthi-u4n 2 месяца назад

    Ambuye kumwambako muliko mukuona ,ana anu akubvutika chifukwa chamunthu modzi yemwe akumva zake zokha inu ndi mwini zonse muchite mwakufuna kwanu dzina lanu lilemekezeke

  • @AbudulJohn
    @AbudulJohn 2 месяца назад

    Munthu wa Nyawu simunthu koma ndi satana chifukwa chake samava or tithayankhula chifukwa nyawu alibe chisoni.
    Ndiye ali busy kuyendela nyama malo moyendela anthu omwe akuvutika madelamu

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 2 месяца назад

    Mr Chikangawa atopa

  • @RejoiceMollande
    @RejoiceMollande 2 месяца назад

    May God have mercy

  • @Richardbanda-hg6pt
    @Richardbanda-hg6pt 2 месяца назад

    Thanks

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er 2 месяца назад

    Kuchikamwako kutsekerera ngati zikuchitika zamzeru,Matongo anu nonse muli pameneponu pulasinso mkazi wakoyo machende aka.anthu akudya chitedze uko iwe kumapanga as kumtumbozo mnyamaako

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 2 месяца назад

    Komatu muthuyu ndiwabwino mumbili yamalawi ndi president oyamba kusamala nyama dzatchile kutsiya athu ovota awa ndi amuna chikangawa

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 2 месяца назад +1

    M'malo mokayendela anthu womwe akudya chitedze ndi chitimbe chifukwa cha njala . president ali busy kukayendela zinyama😢😢😢😢

    • @tasmania527
      @tasmania527 2 месяца назад

      Muzilima osangoliralira foseki.

  • @SteveMasuli
    @SteveMasuli 2 месяца назад

    Anthu akufa ndalama ukuonongela kukaona nyama

  • @AmosfranciscoNevila
    @AmosfranciscoNevila 2 месяца назад

    🎉🎉😢😢😊

  • @marypatriciamakuru226
    @marypatriciamakuru226 2 месяца назад +1

    Ayayayaya Koma sindinaone one shaaaaaa

  • @LoydKamtedza
    @LoydKamtedza 2 месяца назад

    Chikangawa kumpheto kwako mwana wa hule iwe ndi Monica machende ako

  • @AbdulNyambi
    @AbdulNyambi 2 месяца назад

    Kodi chisilu chimenechi kusavinidwatu makamaka ayendela bwanji nyama Malo mokayendela anthu akufa ndi chiteze zisiru Zina zikuwombera manja zopusazi

  • @AnthonyChirwa-t4g
    @AnthonyChirwa-t4g 2 месяца назад

    iwe chikangawa uzafunaso athu okuvotela mwina ng,ombezo ndipo kuzavotela iwe chakwela bola kuvotela manyi galu kwabasi athu akufa ndinjala iwe basi kukaendela vinyama amalawi mthuuyu ndiwakuphadi Mr chikangawa ndipo ndiwe ozikonda ngati machende ako

    • @tasmania527
      @tasmania527 2 месяца назад

      This shows that you're useless to the country as its citizen. You got nothing to contribute dude.

  • @AnthonyChirwa-t4g
    @AnthonyChirwa-t4g 2 месяца назад

    utichimwisa iwe ife Garu

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 2 месяца назад

    Kkkkkkk koma awa kugundika kwabas kuononga minsokho yanthu zaziiiii mbolo yosadulayo galu

  • @SteveMasuli
    @SteveMasuli 2 месяца назад

    Anthu akunsanje bwanji akukugonesani

  • @NtchindiChirwa-l8o
    @NtchindiChirwa-l8o 2 месяца назад

    Olo mutukwane chakwera 2030

  • @EmmanuelMphande-f4l
    @EmmanuelMphande-f4l 2 месяца назад

    Tinkanena iwe pumbwa uyu sangathe kuyendesa ziko si izo ali busy kukayendera nyama nga ndizimene zinamuvotere nyamazo ayiwalilathu kuti ndi anthu anamuvotera

  • @GiftJulius-ro9ev
    @GiftJulius-ro9ev 2 месяца назад +1

    Boma ndilomweli....

  • @MavusoNdhlamini
    @MavusoNdhlamini 2 месяца назад

    Fantastic president mwatipatsa mphamvu mu conservation sector.

  • @oswardzenizeni1458
    @oswardzenizeni1458 2 месяца назад

    Gurani chimanga athu akufa ndi njara

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 2 месяца назад

    Ndipo chakwera ndi garu wamunthu tikuyankhula izi mopamda mantha.

  • @ntombiunice8637
    @ntombiunice8637 2 месяца назад

    Well done Mr president

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 2 месяца назад

    Ambuye mulungu bwanji simukumupha chakwelayu ndi mphavu zanu?

  • @michaelcharles-p9v
    @michaelcharles-p9v 2 месяца назад

    Kkkkkkkkkkkkkkk eshiiiiiii

  • @mbelengamavuto2517
    @mbelengamavuto2517 2 месяца назад +2

    Inu anthu akufa ndi njala

    • @BeatriceSaulosi
      @BeatriceSaulosi 2 месяца назад

      Koma ndipo inu malo mokayendela athu omwe akufa ndi njala iwo alibe nazo ntchito 😢😢

    • @IshmaelNgeyani
      @IshmaelNgeyani 2 месяца назад

      Mboreyako chakwera nyiniyamako Monica mqundu wake

    • @IshmaelNgeyani
      @IshmaelNgeyani 2 месяца назад

      Nyini yake kamtukule hule

    • @IshmaelNgeyani
      @IshmaelNgeyani 2 месяца назад

      Kukondwerera mdziko muli Njala Zachamba jb mutipo bwanji bwanawanga ndimakunyadirani Mr jb

    • @tasmania527
      @tasmania527 2 месяца назад

      @@IshmaelNgeyani Ndiwe chitsiru kwambiri ndipo ndiwe bulutu otheratu. Akamati mfiti amanena anthu ngati iwe. Why blame Chakwera for the problems created by Muluzi and the Mutharikas? Get your life well bro.

  • @kondwanivyalema9449
    @kondwanivyalema9449 2 месяца назад

    Ndi galu kwabasi munthu uyu magazi a saulos Chilima akumuzuza kuti awonese uchisilu wake pompha mzake wosalakwa

  • @FatimaUmali-pc8sy
    @FatimaUmali-pc8sy 2 месяца назад

    Kkkkl koma Zina ukazimva mtima😅😅

  • @CathrineKumwenda
    @CathrineKumwenda 2 месяца назад

    Thank mr presedent

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 2 месяца назад

    Ambuye ngati mumalanga munthu langani ameneyu😅😅😅😂😂😂

  • @SteveMasuli
    @SteveMasuli 2 месяца назад

    Abida ukuwonatu bambo wakoyi

  • @WisdomGavu
    @WisdomGavu 2 месяца назад

    Lazalo

  • @ChrissEli-vr1nn
    @ChrissEli-vr1nn 2 месяца назад

    Mmalo mukaona anthu akufa ndinjala KU machingaku kmanso komweko KU chikhwawako anthu akuvutika osakaona momwe akuvutikila apule inu ndiochimwisa

  • @MikeEdwardChitopa
    @MikeEdwardChitopa 2 месяца назад +2

    Km uyu ndimamina basi anthu akufa ndi njala iwe busy kuchedza ndi mikango km dziko lapansi mamvuto

    • @tasmania527
      @tasmania527 2 месяца назад

      Ungokhalira kulira basi. The country needs innovative ideas in order to prosper osati kungokhalira kusangalatsa makape aulestsi ngati inu.

  • @ShorayChimera
    @ShorayChimera 2 месяца назад

    It's a vakeshini 😢

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu 2 месяца назад

    Chikangawa Lazaro fiti agalu nyani Kodi lwe chakwera anthu akufa ndi njala bzy kumayendera uchi ndizinyama mbuzi ndichimonica chakocho

  • @JacquereenPereira
    @JacquereenPereira 2 месяца назад

    Moti mukaendele Athu dzopatala mulaone athu mene akufela kusowa makhwala Chikangawa alibentendele ndi chifukwa akungo enda enda keneko Muva akukaendela Gule wankulu

  • @MikeKampotah
    @MikeKampotah 2 месяца назад

    Tamuoneni akuchita Matha akuona ngati mankango umuluma

  • @JEFFERYJUMA
    @JEFFERYJUMA 2 месяца назад

    President opanda mapwala uyu munthu wamapwala amayamba Kaye chakudya nyumba

  • @FysonMkuzura
    @FysonMkuzura 2 месяца назад +1

    Koma akulu akulu munthuyutu sizikuyenda ndithuu ,inu m'malo mokaona anthu mmene akuvutikira akawona 😂😂😂

  • @IshmaelNgeyani
    @IshmaelNgeyani 2 месяца назад

    Awayendera bwanji pamene anthu omwe alindinjalawo a mcp akachititsa nsonkhano akuwalandira chonsecho akudya chitedze ndi zomwe akufunatu kaini chikangawa sikusinja kumamuombera mmanja pazopusa ifetu sitidya nyama koma mgayiwa ubwera ndi adad 2025 museptember

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 2 месяца назад

    Komatu azungu amenewa asakhale akumaba miyala mziko muno. Ndakhala ndikumva mphekesela yoipa kwambili yokhuza azungu amenewa

  • @mphatsobwanali5981
    @mphatsobwanali5981 2 месяца назад

    Shame on you chikangawa muthu oiyipa uyuu

  • @PaulineKamwana
    @PaulineKamwana 2 месяца назад

    Zomwe akuchita uyu charakweyi nzopangitsa kt anthu amuchimwire Mulungu 😢 munthu wanji wosamva chisoni ndi momwe alili Malawi mu😭 shame on you

  • @PatrickLigomeka-c8b
    @PatrickLigomeka-c8b 2 месяца назад

    Upurezideti wochita kutara ndichocho kkk

  • @AllieJonassi
    @AllieJonassi 2 месяца назад

    Mwana wa hule uyu obadwila kuthengo

  • @tisuhmakhwah7085
    @tisuhmakhwah7085 2 месяца назад

    Mwaononga zingat pa ulendo umeneu?

  • @Thewarrior7093
    @Thewarrior7093 2 месяца назад

    Galu nyani chakwera amakaona nyama zinzake

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft 2 месяца назад

    Ambuye akuyendere mwapadera chakwera, ndipo akukumbutse chomwe unakhalira president

    • @tasmania527
      @tasmania527 2 месяца назад

      Don't speak in parables, your frustrations from your failures should not equate to blaming the president for what you lack in your life. Anthu ngati inu ndinu omvetsa chisoni kwambiri.

    • @VictoriaWilliam-ms2ft
      @VictoriaWilliam-ms2ft 2 месяца назад

      @@tasmania527 omvetsa chisoni ndiweyo ukuyankhira ngati ndani? Iwe ndi chakwera?

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw 2 месяца назад

    M'malo mothamangila kukawona anthu akufa ndi jala kutaya thawi kukawona nyama koma uyu mamina anazazadi m'mutu

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 2 месяца назад

    Koma kupuma palibe m'bambo uyu eeeh daily kuyenda?

    • @HappyAnt-uz5je
      @HappyAnt-uz5je 2 месяца назад

      Kwinakutu mkutesa Kuti mwina mtendere akhale nao

  • @EliasMandalasi
    @EliasMandalasi 2 месяца назад

    Machende Ako chakwela

  • @MikeKampotah
    @MikeKampotah 2 месяца назад

    Zovetsa chisoni mwapeza mwaiwokaona nyama zakutchile

    • @tasmania527
      @tasmania527 2 месяца назад

      Mulibe zochita inu, mungokhalira kulira ndi kutukwana. Chakwera alibe mnzake and deal with it.

  • @FrankMsiska-i9j
    @FrankMsiska-i9j 2 месяца назад +1

    Boma ndilomweli

  • @RejoiceMollande
    @RejoiceMollande 2 месяца назад

    Anthu akufa ndi njala akudya chiteze your busy kukayendera nyama for what pilizi?

  • @HanafiBadat-i8s
    @HanafiBadat-i8s 2 месяца назад

    Chikangawa yomweyo galu iwe

  • @EmanuelPintopinto-g3b
    @EmanuelPintopinto-g3b 2 месяца назад

    Nkango osangokugwira ukutafune satana iwe

  • @tatindalama5573
    @tatindalama5573 2 месяца назад

    Kusowa chochita.

  • @JeseGwile
    @JeseGwile 2 месяца назад +1

    Good job mr president 2030 buuu

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa 2 месяца назад

      Good job for what😂😂😂😂

    • @ComradeComrades
      @ComradeComrades 2 месяца назад

      YOU ARE VERY STUPIT DO YOU KNOW THE MEANING OF GOOD JOB. PEOPLE ARE DYING OF HUNGER KUDYA CHITEDZE MBUZI YOTCHEDWA PRESIDENT ILI KUMENEKU MUTU WAKO NDOZAZA NDI MAMINA NDITHU.

  • @partmaulidiPatrick
    @partmaulidiPatrick 2 месяца назад

    uyu nde jabulosi kuthupiku akumatipusitsa ngat munthu koma satanaothelatu galu kwabasi

  • @GodfreyKampezeni
    @GodfreyKampezeni 2 месяца назад

    Mbori yako manganya ndi chikangawa

  • @liz9425
    @liz9425 2 месяца назад

    Useless man

  • @liz9425
    @liz9425 2 месяца назад

    Bwanji sanadyedwe konkooooo

  • @SayidiMisessa-x6y
    @SayidiMisessa-x6y 2 месяца назад

    Simdawonepo nkadzi wa president opanda zochita nziko ngati uyu😂😂😂😂 osakhala ndichochita chinachake chothandiza nziko,,, aaaa londolondo ngati ngumbi 😮😮😮

  • @AbdulNyambi
    @AbdulNyambi 2 месяца назад

    Kodi chisilu chimenechi kusavinidwatu makamaka ayendela bwanji nyama Malo mokayendela anthu akufa ndi chiteze zisiru Zina zikuwombera manja zopusazi

    • @tasmania527
      @tasmania527 2 месяца назад

      Ndinu anthu opusa osafuna kulimbikira kulima.

    • @AbdulNyambi
      @AbdulNyambi 2 месяца назад

      @@tasmania527 ulimbikila bwanji zisakutheka misonkho ndi MA sticker MA boarder zomwe zikuchitikazi ukati upite kunja kukawoda zinthu zosayenda kulimako fertilizer akudula amanama kut akhala osika mtengo koma pano anthu akulephela kugula

  • @partmaulidiPatrick
    @partmaulidiPatrick 2 месяца назад

    uyu nde jabulosi kuthupiku akumatipusitsa ngat munthu koma satanaothelatu galu kwabasi