ZOMWE WAYANKHULA PETER MUTHALIKA LERO PAMENE AKUCHITISA NSONKHANO WAKUCHIPANI CHAWO KU BLANTYRE

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 14 ноя 2024

Комментарии • 171

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 часа назад +6

    Welcome Dad respected leader what Malawians waiting, we love u Dad for gd heart u got God must continue bless u and give u long life.

  • @LovenessJere-up6ie
    @LovenessJere-up6ie 2 часа назад +5

    APM President odekha,, odziwa kusamalira, obadwa mtsogoleri,,, Ambuye apitilize kukutetezerani nthawi zonse❤ next year my vote

  • @MaryNyirenda-nq3mh
    @MaryNyirenda-nq3mh 2 часа назад +18

    inuso nyimboyo mumawonjeza nanga timva chani sono tizimvera nyimboyo tasiyisani nyimboyo nanga

    • @KhooMadex
      @KhooMadex 2 часа назад

      Ineso zimandibhowa msaname aaaa

    • @edwardndhlovu1051
      @edwardndhlovu1051 2 часа назад

      Eti eti

    • @alinafesalima5597
      @alinafesalima5597 Час назад

      Ada awa ndi achisilu samamva kuzuzulidwa nyimbo imamveka kuposera zimene anthu akufuna kumvera

    • @isaacsnowden7725
      @isaacsnowden7725 Час назад

      Love this channel but honestly sound yanu itamabwera before then after program yomwe mukutipatsira
      Tili ndi nyimbo zambiri plz

    • @fredahgates2165
      @fredahgates2165 Час назад

      Za nyimbo zanuzo sizimakhala bwino or pang ono komaso ndo programyi sikugeirizana

  • @ChikumbutsoChomali
    @ChikumbutsoChomali 2 часа назад +4

    Adad aife munthu osamala Ali yense munthu opanda khaza munthu wachikondi osayang'ana mbali ❤❤❤❤ God bless you dad timakunyadilan Mulungu apitilize kukupasani moyo wanthaz ndi wautali.

  • @NicksonFaduweck
    @NicksonFaduweck 2 часа назад +3

    Volume please yasika kwambir tikufuna tizimVa zikukambidwa osat ka tone ko ai

  • @KelvenNakhalare
    @KelvenNakhalare Час назад +2

    Tithokoze chifukwa chotipasila program imeneyi koma sound inaonjeza Moti palibe chomwe tikumva

  • @ChimwemweSauka
    @ChimwemweSauka Час назад +1

    Welcome APM next year you will go to state house, God bless our president and protect him.

  • @RoseSosola
    @RoseSosola Час назад +1

    What is happening at DPP is very encouraging. Keep it up guys

  • @DanChirwa
    @DanChirwa 48 минут назад

    Welcome come Dad we us Malawians we are very proud of you and our God may protect all the time where ever you .❤❤

  • @MasaukoSalijeni-wb6hp
    @MasaukoSalijeni-wb6hp 2 часа назад +2

    Nice reporting, but the background music spoils all

  • @FaheemChipojola
    @FaheemChipojola 2 часа назад +1

    Pamenepa ndekuva sound osati sonkhano please mukamatipatsila ma video yo sound muzichotsapo kaye

  • @EmmanuelMzungu-fd4rm
    @EmmanuelMzungu-fd4rm Час назад +1

    Adar woyeeee palibenso ambuye adzikutetezani timakupemphererani ababa

  • @MussaidanaAboubakar-fz5hv
    @MussaidanaAboubakar-fz5hv 2 часа назад +1

    Komano ka sound kaniko kakumasokosera koposa zomwe zikulankhulidwa

  • @AgnessChapinga
    @AgnessChapinga 2 часа назад +2

    Ambuye kumwambako mumupase moyo wautali apm❤

  • @HassanDuwah
    @HassanDuwah 2 часа назад +1

    It's too high the sound please

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 32 минуты назад

    Long live APM we love you

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s 49 минут назад

    Our beloved leader who focuses what comes aheard if people choose badly that foretold them,that they will face an animal called NYEKHWE iyo yodya nayo nyemba za chitedze,nayutu munthu wa mtima okonda amalawiyu,APM.Mulungu akubwezereni udindowu mwafuna kqake,dzicepetseni pamaso pake ndi amalawi onse,otsatira chepetsani zosayenera

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm Час назад

    Can't APM address some meetings standing ?

  • @DanielDoctor-t3p
    @DanielDoctor-t3p 2 часа назад +2

    Apm 2025 boma❤❤❤songolelil wazonse udindo wochokera kumwamba

  • @SuzgoMkandawire-ss4kh
    @SuzgoMkandawire-ss4kh 11 минут назад

    Makosana machende anu background sound too much mpaka osanva zomwe zuyankhulidwa

  • @AliPonda-m4s
    @AliPonda-m4s 57 минут назад

    Wellcom my lovely president

  • @kephermanase8656
    @kephermanase8656 2 часа назад +1

    Koma kanyimboko kauonjeza kakulepheretsa zolinga za program yanu man

  • @Goefreasima
    @Goefreasima 49 минут назад

    Dad 👨‍👩‍👧 we waiting for you elections 2025 boma Movaya l love ❤️ 😍 💖 we don't need chikangawa

  • @SambulaniMaliki
    @SambulaniMaliki 2 часа назад +1

    Makosana anthutu anayamba kake kukudandaula za sound yomwe umaikai Koma sukusintha akutukuka anthu ndithu ,ubwino wake nkhani yofanana Ku utube Kuno imatha kupasidwa ndi ma media ambiri, mvera zomwe ma followers ako kukupempha check momwe dziwe tv imachitira

  • @Langtonmilazi
    @Langtonmilazi 52 минуты назад

    God bless you papa Malawi ❤

  • @elliottndalama2509
    @elliottndalama2509 Час назад +1

    kodi mumafuna tizimvela zonenedwazo? kapena sound yo?

  • @charlesmagola4030
    @charlesmagola4030 2 часа назад +1

    sound ya background too loud sitikunva kanthu

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko 49 минут назад

    Mulungu apiririze kusunga moyo wa president wathu Peter muthalika

  • @McMillanGondwe-o4h
    @McMillanGondwe-o4h Час назад

    Background sound its too loud

  • @HestingsChibalo
    @HestingsChibalo Час назад

    Sound sound please

  • @ThomasGondwe-g4x
    @ThomasGondwe-g4x 2 часа назад +1

    Timakudarila maka tchanelo yanuyi potipasira zochitika zosiyana siyana
    Pepho langa ndilokuti saundi yanyimbo ikukwera kwambili zokambilanazo zikuveka pasi pasi zikomo mabwana athu pitilizani kutipasila

  • @jameslweya-eo1uj
    @jameslweya-eo1uj 16 минут назад

    Ambient sound

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 2 часа назад

    APM our vote our trust our possibility our future and he is a good advice masiku akuthera kuchiseko awa ulendo opita ku 2025 wayandikira tikachose phutsi tchentche APM we love you Long live 🎉🎉🎉🎉🥳🥳🥳♥️♥️♥️💯 percent

  • @MonalisaMwale-c5k
    @MonalisaMwale-c5k Час назад

    Boma ilo ndimangowakonda Adad mopanda chifukwa🎉🎉🎉

  • @HenryLipalapata-b2m
    @HenryLipalapata-b2m 2 часа назад

    The background is disturbing, plz next time muzasayikenso that sound

  • @SHUNEX-zo8vc
    @SHUNEX-zo8vc 2 часа назад

    Makosana pena nyimboyo kumabweza volume timakonda kumvera ma program anu km vuto ndi sound umakweza kwambiri

  • @sungananigondwe2807
    @sungananigondwe2807 2 часа назад +1

    Ase ukamapanga post ma videos ako kanyimboko uzichotsa kaye chifukwa kamasokosa

  • @BoyneMalenga
    @BoyneMalenga Час назад

    Adad Kodi panthawi ya ulamulo wanu a police amapanga ngati zongowonelela anthu akuyenda ndizikwanje mu town malawi wafika potani Kodi ndine Boyne James malenga

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 51 минуту назад

    Mulungju mumupase peter munthalika moyo wautali kuti apulumutse malawi ku mimbuliyi

  • @MikeKathumba
    @MikeKathumba 2 часа назад

    Ka instrumental musicko kamasokosa kwambiri sidzikumveka zomwe zikuyankhulidwazo

  • @WhiteMmadi
    @WhiteMmadi Час назад

    Nyimbo zimasokosa nanuso,you have to reduce volume 😅

  • @user-chimenyaMTV
    @user-chimenyaMTV 2 часа назад

    Please reduce the background song it's too much sitikunvakathu

  • @YousufuJohn
    @YousufuJohn 2 часа назад +1

    President wadziko lamalawi kuyankhula

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 2 часа назад

    Osawayankha..chimwendo alibe mfundo koma kutukwana..inu mulinpheeee osawayankha..okha akudziwa kutu chao oalibe ndi chifukwa akufuna kubela..koma mulungu azitembenuza...inu chaka cha mawa bomaaaaa

  • @SuzgoMkandawire-ss4kh
    @SuzgoMkandawire-ss4kh 30 минут назад

    Sound yanuyi yachuluka

  • @VincentKalata
    @VincentKalata 2 часа назад

    Sound plz ikwele

  • @isaledambe
    @isaledambe 2 часа назад

    Eish! Background sound/music should be stopped. Its too loud and not necessary! Next time please!!!

  • @MasterBlack-r2n
    @MasterBlack-r2n Час назад

    nice but background sound too loud

  • @sweeneykamwendo6251
    @sweeneykamwendo6251 Час назад

    Background sound sucks Chief

  • @SimonSteenkamp
    @SimonSteenkamp 9 минут назад

    Koma mukamapanga live ngati iyi musamayikepo bit yanuyo cz palibe chomwe tikumvapo

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 3 часа назад +1

    Connection ya MCP ndi nyau. No matter they are failing in everything. Akulephera kukonza msewu wa M1; kuyendetsa zisankho; akupangitsa ndalama ikhale ya mpamvu; kubweretsa fetereza kamba ka nyau(=ufiti).

  • @TedJamesMiguel
    @TedJamesMiguel Час назад

    Inuyo ndi ngwazi basi alole. Mulungu kukhala moyo nthawi yaitali mpaka 2025 chifukwa takonzeka kuakakuvoterani

  • @NoxenockKatsara
    @NoxenockKatsara 3 часа назад +1

    Dppp my vote

  • @Esa-u3t
    @Esa-u3t Час назад

    NDE CHINYIMBO CHANU MKUYIMBATCHO TINGAMVE BWANJI NANUSO M'MAONJEZA ASAA

  • @MussaZakeyu
    @MussaZakeyu 55 минут назад

    Sound is to much

  • @jackmambo2638
    @jackmambo2638 2 часа назад

    Sound yanuyo it’s hi we can’t hear

  • @MaryNyirenda-nq3mh
    @MaryNyirenda-nq3mh 3 часа назад +1

    Aliyese odana ndi APM wusanza magazi or manyi mukhawula Apm 2025 boma tikulitengaso kwa agulukunyinda awa anthu okuba okupha adyera ozikonda amfiti anthu opanda chisoni

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm Час назад

    Palibe chikumveka chifukwa Cha phokoso lakanyimboko . Dzofunika kukonzapo apa

  • @FrankBanda-w4f
    @FrankBanda-w4f 2 часа назад

    Makosana plz sound yakwela

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 3 часа назад +1

    Long life Apm 🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏💙💙💙💙💙💙

  • @fredahgates2165
    @fredahgates2165 Час назад

    Nyimbo yanuyi ndi zochitika zinazi sizimafanana uchose zimenezi,komaso mau anu omakhala ngati tikumvesela muchitini aja muchose muzingitipasila program basi

  • @ELLENZAPS
    @ELLENZAPS 2 часа назад

    Ma vote NDI Anu Adad Koma awa akufuna kutiberawa ndye kAa muwona zochita Kut mbavazi zisadzabepo

  • @MikeKathumba
    @MikeKathumba 2 часа назад

    Viewing sili bwino .mukanachosa kaye barner mukuiikayo tifuna tiziona live

  • @fraiserkapito-yb2ob
    @fraiserkapito-yb2ob 2 часа назад

    Komatu muzipanga balance kanyimbo kanuko ndi voice ya anthuwo.
    Coz the important thing is the message not your sound so next time improve on this

  • @lukeseyama1472
    @lukeseyama1472 Час назад

    Remove your music on the videos you post

  • @WilliamChikomo
    @WilliamChikomo Час назад

    Kanyimbo kakumveka pansipo kakusokoneza sitikumva bwino bwino zikuyankhulidwa

  • @UnjiunjiGeneral
    @UnjiunjiGeneral Час назад

    Too much noise from the background asahh

  • @EsterManiya
    @EsterManiya 3 часа назад +1

    Our trump our trust

  • @JamesBrown-gx8my
    @JamesBrown-gx8my 2 часа назад

    Repost your video please and remove your song

  • @ElizabethMwale-z3s
    @ElizabethMwale-z3s 2 часа назад

    Koma ine kanyimboka kandikwana, si tikumva zolankhulazo

  • @GenWealth728
    @GenWealth728 Час назад

    Nyimboyo bwanji kodi...palibepo chikuvekatu apa...tungova nyimbo

  • @SaudhaKatete
    @SaudhaKatete 2 часа назад

    Live from Johannesburg please sound ife siti kumva

    • @WhyteSmart
      @WhyteSmart 2 часа назад

      Sound ikumakwera kwambili

  • @chifundochiwaula998
    @chifundochiwaula998 2 часа назад

    Sound ilipansiyo mudzitsitsako tidzinva zoyankhuludwazo

  • @tituskalulubanda
    @tituskalulubanda 26 минут назад

    Nyimboyo mwatipweteka nayotu. Next time take It down please

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 2 часа назад

    Adad inu mtima malo..akukutukwanani.. inu pheee..alibe chonena kuposa kutukwana..

  • @MarthaBanda-g4f
    @MarthaBanda-g4f 2 часа назад

    Welcome back a dad

  • @apatsajana
    @apatsajana 2 часа назад

    Nyimboyo yachaniso Mesa mwati tinvele zomwe ayankhula lero

  • @FortunateMwamusamali
    @FortunateMwamusamali 43 минуты назад

    Sound eshh

  • @EDSONMahamand-v2z
    @EDSONMahamand-v2z 31 минуту назад

    Nyimbo mwaikayi ikubila mawu athu oyankhua ulendo wina musazaike

  • @StandBwanali
    @StandBwanali Час назад

    A P M my man ❤

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 2 часа назад

    Chinyimbo chanuchi mumasokosa nacho mumachiyikiranji kodi

  • @MayesoBikefa
    @MayesoBikefa 2 часа назад

    Good disicion to cabinet of dpp

  • @FaroukSaliem
    @FaroukSaliem Час назад

    Tathimisa nyimboyo galu iwe tikufuna tizimva mawu adad

  • @petrosmilanzi7067
    @petrosmilanzi7067 59 минут назад

    Zoona nyimboyi mmm paka zomwe akuyakhula sizikuvekatu

  • @AaronKampira
    @AaronKampira 2 часа назад

    🎉Km inuyo mmmmm ayi. Ndimangonva ndadziona ndekha

  • @MlambeLodge
    @MlambeLodge 2 часа назад

    Mumakwana adad ili offer my vote

  • @nomamoyo4519
    @nomamoyo4519 2 часа назад

    Welcome APM

  • @LacksonPhiri-z2t
    @LacksonPhiri-z2t 2 часа назад

    No more in power sleeping on duty

  • @BrightonNdalama-x2b
    @BrightonNdalama-x2b 2 часа назад

    Kodi waika nyimbo ikunveka pansi pansiyo sakunva kuti ikusokoneza???? Aaaaa plz tachotsani plz

  • @planmalawi-sm2cw
    @planmalawi-sm2cw 2 часа назад

    Kanyimboko muchepetse volume

  • @planmalawi-sm2cw
    @planmalawi-sm2cw 3 часа назад

    Wise people keep it up apm

  • @sthoramexjrsa902
    @sthoramexjrsa902 2 часа назад

    Sound yakeso nde yaukapet munakangosiya fokofu👺👺👺

  • @ChristopherKawilam
    @ChristopherKawilam 44 минуты назад

    Kanyimbo ako mukchosa sikulakwisa Ayi

  • @KingChako-s7z
    @KingChako-s7z 2 часа назад

    Apm ananena kuti mukhaura zowona bakili anati vuto raamarawi ndikuyiwara sanga zowona koma amarawi muthu wina aliyese alindizofowoka zake koma apazanyanya

  • @IbrahimJackson-i8h
    @IbrahimJackson-i8h 2 часа назад

    Sounds it's too high

  • @InnocentNitamanMilanzi
    @InnocentNitamanMilanzi Час назад

    Mfiti sinayambepo yavomereza kuti imatamba

  • @NelsonBanda-j1f
    @NelsonBanda-j1f Час назад

    Great

  • @DoreenKundembo
    @DoreenKundembo 59 минут назад

    Bambo athu athu adad ndpo mulungu akuze malire amoyo wanu adad

  • @BlessingsTembo-y6x
    @BlessingsTembo-y6x 2 часа назад

    Nyimbo imene mwaik yasokonez kwambir

  • @BrendaMaluwa
    @BrendaMaluwa Час назад

    Kanyimboko kakusokoneza sizikumveka bwino