NAMADINGO VS LULU ASAMBWAZANA DZULO PA LIVE VIDEO CALL ANTHU AWA TSIKULINA AZAMENYANA NDITHU

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 15 ноя 2024

Комментарии • 22

  • @CosmasChikwindi
    @CosmasChikwindi 18 часов назад +5

    Onsewa alibwino koma mumawapangitsa kuti azidelana ndinuyo wanthu owatsatila.

  • @MartinNgoma-tp2jk
    @MartinNgoma-tp2jk 5 часов назад +1

    Chilungamo kaimbidwe Dolo ninamadingo koma wankulu ndilulu lulu analela namadingo😊

  • @TchakaChisuse
    @TchakaChisuse 5 часов назад +1

    Namadingo ndikape sangamake kwa lulu ndiopo lulu ndioyimba kuchokela paka time or mafunyeta adakamba kuti lulu ndiyimba wamkulu namadingo akaona lulu ndi bambo ake pa muzick industry

  • @Debbie2004-x9q
    @Debbie2004-x9q 12 часов назад +1

    Comparison is a thief of joy. Be happy when your fans are appreciative of you

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 18 часов назад +4

    Namadingo ndi dolo koma amazipopa matama too much

  • @AlinafePililani
    @AlinafePililani 16 часов назад +2

    Apapa basi namadingo wandiwaza❤❤❤

  • @jamestsabola1376
    @jamestsabola1376 18 часов назад +2

    Koma namadingo ndiwolakhula muzipopa mozikweza pomwe lulu ndiwozichepesa kwambili samafuna zomalimbana

  • @KondwaniBanda-ul8sj
    @KondwaniBanda-ul8sj 14 часов назад +1

    Zaine ndine mukukudziwa komwe kunachoka luso lanulo koma kuzichepetsa ndi kwabwino kunali madolo awa asabwelepo

  • @usherjamson174
    @usherjamson174 4 часа назад

    Was very nice 🎉

  • @AlexMduladulaMafuleka
    @AlexMduladulaMafuleka 18 часов назад +2

    Zongotha Bundle za ziii

  • @DimplesDumplingHouse
    @DimplesDumplingHouse 10 часов назад

    Kodi namadingoyu akudwala?

  • @JamesUlambo
    @JamesUlambo 17 часов назад +1

    Namadingo azatha ngati moto wa mapesi

  • @sungananigondwe2807
    @sungananigondwe2807 13 часов назад

    Namadingo ukhalike eeeh 😂😂😂

  • @ThomasPatrick-n3n
    @ThomasPatrick-n3n 9 часов назад

    Lulu ndidolo sangafanane ndinamadingu namadingu ndi wamakwaya

  • @SabitSamohgruva
    @SabitSamohgruva 13 часов назад

    Namadingo kuyankhulitsa mkulu uyuyu mmmmm

  • @Emmanuelkalinde-v6i
    @Emmanuelkalinde-v6i 13 часов назад

    That's Lulu l know is a man of small words

  • @owenmoses9434
    @owenmoses9434 16 часов назад

    Namadingo kachaso akupweteka

  • @GeoffreyDyton
    @GeoffreyDyton 18 часов назад +2

    Lulu wayankhula zanzelu ngati muthu wankulu

  • @AlufeyoBanda-cv2we
    @AlufeyoBanda-cv2we 14 часов назад

    Choking apa chiwanda chikuchokeni kudanitsa basi

  • @MarriamShakira
    @MarriamShakira 14 часов назад +2

    Lulu ndimunthu woupesa tima namadengu matama akuwachulukila inuso anthu amafuso simulibwino ai

  • @georgeabigailmaseko-ts3fq
    @georgeabigailmaseko-ts3fq 18 часов назад +2

    Namadingo amadzifila heavy 😢

  • @SmartGotkeyTV
    @SmartGotkeyTV 19 часов назад

    Masapusi 😊