Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Zaziiiii
Alibe chikondi inakula ndi dyela
Sisiliyas. anoneka. ngat analibe. chikond masku. okuthaitha. akanyenela. kumvomeleza. kuluza. kwao
Usingpdziwandale momwe Wapangila ndale munthu uja ndi akatindu. Muona utm isokonekera. Iye anauza anthu ake onse kt avotere kabambe. Mpomwe Wapangila kt kambambe asamukulire mtima. Munjira Ina kabambe chimuvuta chipani ngati Savana ndi usi. Akapitiliza zone a mgwiriro ntchito ndi boma. Usi. Kambambe zimuvuta chifukw anthu Ali nkabambe mwini wake ndi usi izi ndie tomato ndale za smart zomwe John tembo amasewera utm itha kutha ngati kabambe savers usi ndithu. Usi moto
usi sangatsogorere chipani muthu waonetsa kare kurephera akungwilizira
Munyamata iwe wayamba bwino zaonesa uli ndi nzeru kuposa nkhalamba zalephela ku convention ya utm
Ndipo zoonad akaliati ngat audio imenei ndiyao alakwitsa kwambir awoneka uchitsiru wao
Zoonadi mau brother
Ai mzokaikisa pachichewa pali mau oti kuthamanga sikufika