Kalindo amadana nae kaya chilungam mchowawadi guyz Kalindo amamuuza Chilima choka kumeneko anthu oipa amenewo ai RIP Chilima Bon Kalindo may Good Lord protect u oga
Plz Booon kalinde musiyen Mary chilima akulira ndipo azalira pa kale ndipo asayerekeze kupanga ndale, politics is a dirty game musiyeni azipanga zina than this so called Malawi politics azafaso ngat mamunawake
Vuto ku UDF akungoona zoti MCP inathesa mulandu wa bambo a Atupele ndiye kuona kwaine ndi mbali imodzi yothokoza osadziwa kuti akulowera ku pompho. UDF forget about za kukhululuka kwa Chakwera ku mulandu wa a Chair. Sizikugwilizana ndi ku chipani kwanu.
Anthu ambiri amathandizika kwambiri komanso ndi munthu yekhayo amene waima pachilungamo limodz ndi mtanyiwa komanso bakili muluz tv Anthu Amenewa kwa ife ndi hope yathu chikangawa party tatopa nayo
Koma ganizo langa Mary chilimayo ndiifa ija mmmm savetsa nde aaaa asamale ana aja akuziwa bwino lomwe momwe zikuyendela dziko muno ndematha alinawo ndithu
Iiwe mr DC ndi ine tikugwirizana sindingakhale pamozi ndi mcp kukhala pmozi ndi mcp ndichimozimozi kukhala ndi fumu helodi . Manganya umuzedi muzako akuoneka ayamba misala apite nayo ku mental health akamuyeze mwachangu mr ngongole akuononga misonkho ya Malawi zazi zimene akupanga. Ndege kuchikanga ambiri amuboma yawapangisa misala ndipo ayaluka
Koma pliz mukadapeleko ulemu pa imfa ya malemu chilima ,apapatu zikungosonyeza kuti ichi sichison ndi chilima koma kupepuza inmfayi.ambuye ndi wachifundo akudziwa ndipo tsiku lina adzayankha.
Sir Bon kalindo live Mart chilima alone .if she is hesitant to begin utm.politics .she knows what's under it as a wife @ Zizimba zake za chipanizo zikumuopsya..ndiye inuyo a Bon kalindo khalani.president wa utm.kuti mupulumutse malawi..zizimbq zake muzitha chifukwa inu ndi inu munthu woopsya kwambiri .sichoncho a a Bon kalindo..mwana qoopsya wa ku Malawi
❤❤❤iweyo uli pa number one ndizako wa bakili muluzi uja mumatiimilira usasiye kutiyakhulira Mr kalindo
Bon kalindo man of the moment the number one don't give up my brother
Mwana woopsya wa kumalawi Bon kalindo lowanso utm.ukhale president..Booon.kal8ndo
More fire 🔥 mr president bon kalindo we trust you the DC that is true 👍 my guy 👦
I wish you to be a president your really legend ❤
Kalindo amadana nae kaya chilungam mchowawadi guyz Kalindo amamuuza Chilima choka kumeneko anthu oipa amenewo ai RIP Chilima Bon Kalindo may Good Lord protect u oga
Uyu ndi Julias Malema waku Malawi, straight talk 👍
Nice one thanks brother keep it up please
Pajatu aMalawi sitichedwa kuyiwala. Dzuka Malawi dzuka. 😢
Pa Mary chilima Bon wanena chilungamo iwedi ndi nyooooh ukasankhidwa ndi anthu ndi bwino osati 😂😂😂😂😂
Ndikuvomerezana nanu please Mary am on my knees rescue Malawi wavunda
Keep on doing it Dc
.. azazindikira bwino pasogolo
Plz Booon kalinde musiyen Mary chilima akulira ndipo azalira pa kale ndipo asayerekeze kupanga ndale, politics is a dirty game musiyeni azipanga zina than this so called Malawi politics azafaso ngat mamunawake
M'malawi mulidi mavuto maka ku mudzi😢😢😢 ngati atsogoleli kulibe, chonde Mulungu akuoneni coz akudandaula Misokho yao😢😢😢😢
Vuto ku UDF akungoona zoti MCP inathesa mulandu wa bambo a Atupele ndiye kuona kwaine ndi mbali imodzi yothokoza osadziwa kuti akulowera ku pompho. UDF forget about za kukhululuka kwa Chakwera ku mulandu wa a Chair. Sizikugwilizana ndi ku chipani kwanu.
Zoona simukunama amenewo asabwere ife sitikuwafuna mumuuze atupere waganiza bwaji ife zikutinyasa
KOMA AMALAWI BORN KALINDO DAILY AMAONEKA OPUTSA NDIOBALALIKA POLAKHULA KOMA TSIKULINA MUTHUYI AZAKHAKA WADZERU NDIPO KUCHENJERA KWAKE WAONEKAT MU NGOZ YA CHILIMA AKAMUUDZA KUTI TULUKANI ,MUGWILIZANO TULUKANI BWANA ANTHU ADAMUYESASO OSAZINDIKIRA MPAKA ADATI MKAZ NGAT SAKUFUNA USAKAKAMILE CHIFUKWA TSIKULINA AMAKUPHA KUKUTHILILA POISON , LERO BWANJI? CHILIMA ALIKUTI ? SADAMUPHERE KUCHIKANGAWAWA MWAKHAZA MCP YOMWEYO? KOMA ANTHU SIMUKUMUMVERA TSIKULINA MALAWI MUNO MUZAOPSA BORN KALINDO AMATIUNIKIRA KOMA IFE AMALAWI TIMAZITENGA ZOPANDA PAKE OWOOH
Munthu amuphera mai ake , basi komweko wonders shall never end
Bwana bon kalindo makamaka chimwendo banda ntchende lamunthu
😂😂😂😂 manganya akutipangisadi manyazi. komaso chikangawayu atipha
Koma bon 😂😂the DC😅
Champion wa democracy udf .mwini wa democracy anali chihana enao anagweramo.chifukwa chake wakapanga zimenezo
Mungonkhala président ndinu bwana
Anthu ambiri amathandizika kwambiri komanso ndi munthu yekhayo amene waima pachilungamo limodz ndi mtanyiwa komanso bakili muluz tv Anthu Amenewa kwa ife ndi hope yathu chikangawa party tatopa nayo
Komasotu ku bomaku Muthu umakhala wazeru ngati sunapiteko ukango lowa boma zeru zukhala ngati zimabalalika
Ndithu ndinu Muthu okonda dxikolanu bwana timakunyadiran
Bon kalindo adakumanabe mpando kayambe kugurisa karongonda masaya kutupa ngati wakumaguru
Nyini yamako
Amako ndamene anawamana pando , patumbo pako iwe
KOMA INU NDIMUNTHU WANKULU UMAYIMILILA KU
MALAWI
Maganizo Ako amenewo ubwino wake wati dxikoli ndi democracy
Iwe tapita uko wosankha mitundu iwe
Machende ako bon.icho ndichisankho chako.kusapita Ku conversation ya udf ndiwe ndani Ku udf machende ako MCP ikupita Ku conversation ya udf
Nanga iwe mamchende ulibe galu iwe mbolo yosadulayo galu
Iweso machende Ako galu iwe
Achisiru inu yang'anani nkabudula mwanumo
Koma ganizo langa Mary chilimayo ndiifa ija mmmm savetsa nde aaaa asamale ana aja akuziwa bwino lomwe momwe zikuyendela dziko muno ndematha alinawo ndithu
DC go ahead we are praying for you ❤❤❤❤❤
Proud of you DC
😂😂😂😂uthenga wopanda chigamba kupita kwa manganya
Ndi iweyo amene uliwokhumudwa osati a Malawi 🇲🇼 chifukwa dziko likufuna mtsogoleri wachinyamata osati mnkhalamba yakoyo nonse musapezekeko.
Honestly ,democracy could start within the party…so UDF leaders mukanamvera…this is just advise
Inu asiyen a mary paja wnanena kale kt sakufuna kupanga za ndale
Ndipo inu museyen Mary plz anthu muzikhala ndifundo muja anafera amuna ake. Kms abon siinu abwino. Muuzen mary sizoona iweyo imira u President
Keep it up telling us the truth
Iiwe mr DC ndi ine tikugwirizana sindingakhale pamozi ndi mcp kukhala pmozi ndi mcp ndichimozimozi kukhala ndi fumu helodi . Manganya umuzedi muzako akuoneka ayamba misala apite nayo ku mental health akamuyeze mwachangu mr ngongole akuononga misonkho ya Malawi zazi zimene akupanga. Ndege kuchikanga ambiri amuboma yawapangisa misala ndipo ayaluka
Amalawi ake atiwo akutumao let's meet 2025
Kalindo adamumana ulendo ndiye zidamuvuta
Abon kalindo mukuyimilira Amalawi ake ati,munalephera chisankho kudera la kwanu monvesa chisoni,lero mukasuta fodya wa mkuru kumati ukuyimilira Amalawi ake ati? poti unakanidwa kale,kuzolowera kudya maboza basi,dpp yakupepelesa plus chamba,anthu ozindikira anakutuluka kale,zasala ndi mbewa zokha kumakuchemelera😂😂😂
DC samaonetsa mano zopusa zikamachitika , wina aliyense zikumuwawa ngakhale mmalawi yemwe ali kunja
The late right honourable Saulos Chilima rightly said chipani cha UTM sicha kumtundu kapena kubanja, ndi cha aliyense
We need Mary chilima here❤❤
The DC Mwana owopsa kwambiri from Jezza village
Mr Bon can w
This massage be sponsored to broadcasted on radios
Akulirabe musiyeni,
Koma inuyo mungakhale ndi muthu Ufuna kukuphani
Winniko galu wachabe chabe palibe zelu na gogo wako Peter
Nyozan winiko akuyakhula si peter wakulakwiran chan
😂😂😂 iwe dikira 2025 pa 16 osamangorubwarubwa apa palibe chomwe ukudziwa
Ang'alule amewa mbuzi za anthu
Ayi asithe zawunsiluzo
Mary asalowe ndale ,adzafela zayen ndale za Ku Malawi ndi zoyipa
😂😂😂 ndimzako kumene manganya yo
Ng'alula anthu aziva tikakhala enafe ndiye tikuziwa ndipo tikuva chomwe mukuyakhula
Kalindo ena olo adane nawe ukunena zoona
Osabweretsa mpungwempungwe dziko la Malawi ndi la Mulungu .
Koma Mary yo angaloredi uh coz nayenso awopa eh eh dzikoli layipa ndipo zinthu sizili bwino
Mcp ndi bwalo or group la kupha
tiuzireni amenewo amuyiwara Mr chikangawa?
The DC mwana ovuta kwambiri
Za mery chilimazi ndizopoila uku ndkusokoneza chipan nga iye sakufuna osamukakamiza
Omenyela ufulu amakhalatso ndi mbari Kodi? Kkkkkkk
Sitikufuna sitikufuna MCP muwaitane pliz pliz pliz pliz pliz pliz pliz pliz pliz pliz
Uthenga opanda chigamba 😂😂😂😂😂😂😂
I love Dc❤😂
Kodi alomwe mumatitenga ife ngati zitsilu zanu eti tisiyeni tizipanga ziganizo patokha anthu anji ongo funa usokoneza mitundu ina
Team DC im proud of you
The DC mwana ooopsya kwambiri
Nsanje ikuphani akulu kkkkkk
Ndipo achita awawa
Iwe ndichitsiru kwabasi mesa umanena kuti utsogoleri umafunika experience nde Mary Chilima alindi experience iti pandale kapena utsogoleri?
Umbuli wachuluka tanthauzo la Democracy sukulidziwa,mdani wa UDF ndi Dpp ngati sukudziwa.
Apapano ma organizer mwapanga zopusa😢😢😢
Koma pliz mukadapeleko ulemu pa imfa ya malemu chilima ,apapatu zikungosonyeza kuti ichi sichison ndi chilima koma kupepuza inmfayi.ambuye ndi wachifundo akudziwa ndipo tsiku lina adzayankha.
kung'alula
Ndipo live the DC
🔥
Malawi wakeuti umadziimilila bwanji.kwanu adakuka.kuump
Akalindo akunena zoona.
Marry chilima nde chani?
Powerful ❤❤❤❤❤😂😂😂
🎉🎉
Kupeza zina zochita bwanji guys uyu atipusitsa
Sir Bon kalindo live Mart chilima alone .if she is hesitant to begin utm.politics .she knows what's under it as a wife @ Zizimba zake za chipanizo zikumuopsya..ndiye inuyo a Bon kalindo khalani.president wa utm.kuti mupulumutse malawi..zizimbq zake muzitha chifukwa inu ndi inu munthu woopsya kwambiri .sichoncho a a Bon kalindo..mwana qoopsya wa ku Malawi
Koma UDF kupanga chiphyera mtima uku. Ati a UTM amve kuwawa. Mwaponda mwala. Mawa winanso asowa ngati mukuona nhati inu sidzingakupangikireni zaona Biyeni.
Kma nkuluyu eeee ndi 1
Zoti chipani cha UDF chayitana mcp kusokhano wawo wawukulu ndizaboza
Kodi akuluwa alibe zina zochita kupatula kuyankhula pa social media? And muja adayambira kuyankhula muja zikuwathandza😊
Akulu izi amalankhulazi zikupindulila aliyense omvetsetsa komanso opanda mbali mu politics inuyo muzazimvetsa mtsogolomu
Ndiwe opusa ngat umawona kt Boni kalindo amayakhula zosakusangalasa bwanj umabwela kuzavela zoyakhula zake
Iweyo uzipanga zakho usalimbane ndikzlindo ife Okonda malawi timakonda bon kalindo
Iweo ndamene uli zoba chifukwa unayambira mkale kumusata pamene sumamumvesesa
Kumati inuyo ndinu okhumudwa osati aUDF ayi manyazi bwanji
Bon kalindo ng'alula baba
Chilunga chako chaboza unakhalapo mp ku Mulanje unapangakochani cholozeka kwa anthu
Umafuna akugulile galimoto
inuyo zanu pangan DPP 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Zama bodzatu pano ayi garu iwe
Iwetu ndiwa Dpp suungatipusise wamva
Ife mcp tingoyidyera basi sitingavotete chipani choyipa ngati chimenechi, ndalama za phweka tiwadyere basi.
Azalowa no Tonde? Or?
Mwaveka bwana athu aku malawi