BON KALINDO LERO PA 25 JULY 2024 |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 6 сен 2024

Комментарии • 96

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Месяц назад +1

    I support The DCs mwana woooopsa kwambiri

  • @CharlesMasamba-h8d
    @CharlesMasamba-h8d Месяц назад

    Malawi kaya tingati chani kayaaa
    Amanga mwana osalakwa lero ku balaka mkumakamuimbila mmanja chikangawayo

  • @ChikumbutsoChomali
    @ChikumbutsoChomali Месяц назад

    Iwe ukutiimilira Bon umakwana a opposition akugonadi adzuka thaw itatha

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Месяц назад

    Ku Malawi kuno , Multiparty atikanika ,tiyeni tivomeleze, zonse tingosiyila Malawi fisrt ,aaa zipani zosusa khalani pansi yisiyeni MCP yitizunze mpakana kubwera kwa Yesuu

  • @CharlesMasamba-h8d
    @CharlesMasamba-h8d Месяц назад

    Ineyo mkumati ndiye mmalawi wina kumaombela mmanja this boma

  • @user-ic1zy4zj1c
    @user-ic1zy4zj1c Месяц назад

    Kodi Boon kalindooo the DC, sakumusaka ngati wa Bakili Muluzi TV bwanji?

  • @MillionNankhonya
    @MillionNankhonya Месяц назад

    Ndipo ineyo opposition ikumandipweteketsa mtima mmene akugonera

  • @PhumsyMbewe
    @PhumsyMbewe Месяц назад

    The DC🔥🔥🔥🔥💪💪

  • @ThandiMbewe
    @ThandiMbewe Месяц назад

    A opposition sangamve chifukwa iwoo Ali ndi ndalama sakuwona vuto, ndipo ndimomwe akutipangisa ife kulila

  • @kingstonekalonga8435
    @kingstonekalonga8435 Месяц назад

    Nankhumwa ndichisilu akukakamira opposition koma salankhulapo kalikose galu wamthu kwabas bon kalindo mumatiimirira koposa Allah azikudalisani ❤❤

  • @user-pw6fs4zs8k
    @user-pw6fs4zs8k Месяц назад

    Opposition kulibe kuno ziko la Malawi ndilovesa chisoni

  • @BlessingsMakalani
    @BlessingsMakalani Месяц назад

    Ndi dzoona bwana DCC

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w Месяц назад

    E ndimakape tavomera vuto amalawi anasankha kusamvera ndiye akhaure zenizeni iyoooooooooooooooooooo

  • @SwadickSalanje
    @SwadickSalanje Месяц назад

    Malawi panopa yili wez😢😢😢😢😢

  • @chiwaulaashraf4696
    @chiwaulaashraf4696 Месяц назад

    Dont blame opposition you voted change yourself. Anthu amitudzu inu

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Месяц назад

    Apolice amakumanganiwo akukanika kupasidwa ma pension awo

  • @evansjohn7766
    @evansjohn7766 Месяц назад

    Ma GEN Z palibe ku Malawi.

  • @greymasha838
    @greymasha838 Месяц назад

    Nkhaniyo ndiooona bwana DC

  • @SamuzySamuel
    @SamuzySamuel Месяц назад

    Malawians too much sleep don't give chance that guy.

  • @annamazingashaibuh6276
    @annamazingashaibuh6276 Месяц назад

    Ndipoo eee ku malawi chiletsoo uhmmmm

  • @MoosaBanda-su3zp
    @MoosaBanda-su3zp Месяц назад +7

    Yes tilibe opposition kuno athu ake ndi ogona apangisa kuti chakwela mbuzi imeneyi ilamulileso chaka chamawa

  • @LexiousMwale-gk3nk
    @LexiousMwale-gk3nk Месяц назад

    A opposion naonso ndiokonda kudya mabanzi, ali ndwiii azitinyamsa nthawi ya lampeni.

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Месяц назад +3

    Opposition ikupsyetsa mtima kwambiri.

  • @VictoriaWilly
    @VictoriaWilly Месяц назад

    Ndipo Boni Kalindo mukunena zoona, penapake awa osusa boma awa anyanya kufasa zedi. Kodi akalowa Boma achita zokupsa awa kufasa kumeneku?
    Asaaa pheee ameneyi atithandiza koma?
    Anthu akuvutika malo moima ndi omenyela ufulu kudzudzula awa akuononga dziko awa koma ayi ali chete akudikila ena awamenyere nkhondo iwo azangolowa boma.
    Zikundiwawa kwambiri..... Osusa nonse gwilanani manja chonde

  • @KhumboMunthali-jx5me
    @KhumboMunthali-jx5me Месяц назад

    Ayendereni amenewa tatopa ndi njala ife

  • @jixonromeo4111
    @jixonromeo4111 Месяц назад

    Zawo ndizimodzi chifukwa chake akukhala chete best way kungopangidwa chipani china

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk Месяц назад

    Zooona kalindo ma salary akutipatsa mma company WA ngat akupatsan mwan WA zaka 10 kt akagure kamba...km boma lathu likungoyang'ana.....ndye nkumat tiyen tikalembetse tikavote....ine nde ayi!!!!!

  • @JasperKaleni-dx6nn
    @JasperKaleni-dx6nn Месяц назад

    The DC❤

  • @TapiwaKhwisula
    @TapiwaKhwisula Месяц назад +1

  • @hendreson
    @hendreson Месяц назад +1

    Well spoken

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Месяц назад

    That's true our opposition leader they are week.

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Месяц назад

    Inuso mumakonda kumamenyela ufulu apolice ineyo sizimandisangalasa apolice so ndi athu oipa kwambili

  • @VictoriaWilly
    @VictoriaWilly Месяц назад

    Osusa boma kufasa kumeneku mukuti sanapakidwe bibi ku maso awa???
    Si za Normal izi ayi kkk

  • @AlomweWathu
    @AlomweWathu Месяц назад

    auzeni

  • @HASSANHASSANTDL
    @HASSANHASSANTDL Месяц назад +1

    Opposition ya amalawi atulo toomuch DC DC ulemu wanu bigger ndimakunyadila kwambiri zangovuta a opposition ndimakape toomuch

  • @khambisan
    @khambisan Месяц назад

    Fire 🔥🔥🔥 the DC fanaoopswa kwambili, khambisan

  • @DanielnachanzaBanda
    @DanielnachanzaBanda Месяц назад +1

    Vuto ndi iweyo bon kalindo ndiamene anawauza amalawi kuti akavotere alliance lero ndiye bwa

  • @user-wu8kp7ui5j
    @user-wu8kp7ui5j Месяц назад +6

    The DC 🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @evansjohn7766
    @evansjohn7766 Месяц назад

    Ndinakuuzani kuti a malawi ngoziwa kupempha pempha basi,kkkkkkk.....koma kuti aonesetse zomwe zikucitika ai,kugwila ntchitonso ai manja lendewele basi.

  • @GiftRashid
    @GiftRashid Месяц назад

    Kugona kwa position musadabwe ai akugwiritsa ntchito chichewa choti malawi siwomufera mawu amene anayakhulaso bon kalindo kuti malawi siwomufera video yakeso ndili. Nayo

  • @mathewsnachuma8086
    @mathewsnachuma8086 Месяц назад

    Nkhani ndi greedy mostly ku DPP

  • @YOMALO.
    @YOMALO. Месяц назад

    Angalichose bomali ndani? Liimanso 4 years.

  • @MatressKanyenga-f1z
    @MatressKanyenga-f1z Месяц назад

    The dc mwana wachabe kwambili 🎉❤❤❤😅

  • @RaphaelKweve-u5s
    @RaphaelKweve-u5s Месяц назад

    Nkhani imodzi mukumayitumiza kambiriri !,,,,Why?

  • @Vascomw
    @Vascomw Месяц назад

    The DC

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz Месяц назад +1

    Kulibe opposition ku Malawi

  • @bysongeorge3243
    @bysongeorge3243 Месяц назад +2

    Ndimanena nthawi zonse kuti ku Malawi kulibe opposition. Angoti phwii ati kudikira chisankho chaka cha mawa. Tidya mchenga ku Malawi chifukwa cha anthu amenewa.

  • @AbdulrahimoMassamba
    @AbdulrahimoMassamba Месяц назад

    Zoona opposition kulibe ku Malawi, komanso a malawi ndi opweteketsa.sitingawakhulupilire anthu amenewa.chifukwa maiko ambiri opposition ndi imene imalamula mosigozana ndi boma.koma kumalawi mbola zokha zokha.

  • @capitalaction4107
    @capitalaction4107 Месяц назад

    🔥🔥🔥mumatiimilira our own mr P

  • @swintonchirwa1897
    @swintonchirwa1897 Месяц назад

    Si Apolisi ndi ayufi

  • @greymasha838
    @greymasha838 Месяц назад

    Ayi zikomo ndipo zoonadi ngati tikuzuzuka tikuzuzikaso chifukwa cha opposition nkhaniyo ndiyoona

  • @EusébioLucianoGaiondo
    @EusébioLucianoGaiondo Месяц назад

    🔥🔥🔥🔥

  • @PatrickMbenje
    @PatrickMbenje Месяц назад

    Opposition is very weak and we don't have any hope

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn Месяц назад

    Opposition kapenakuti zipanizosusa ndiyekuti kumenekonso kulimilandu amawopa kususa kutinso angawafukulezambili,Wina aliyensekumeneko ali ndi milandi ndipamenezikuvuta😂😂

  • @ChikondiKachaso-ox5ng
    @ChikondiKachaso-ox5ng Месяц назад

    Zimene amanena a bon kalindo ndizoona koma amalawi akufuna maDemo azaone mkwiyo uli mwa amalawi

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeon Месяц назад

    The deceeee more 🔥

  • @daviekamwendo9793
    @daviekamwendo9793 Месяц назад

    Mwana oopsa kwambli🔥🔥

  • @irenioeugeniosumila6647
    @irenioeugeniosumila6647 Месяц назад

    Thulussani zonse

  • @UmaliJuberge
    @UmaliJuberge Месяц назад

    🎉🎉🎉🎉

  • @ashahaduiduluzi9521
    @ashahaduiduluzi9521 Месяц назад

    Adzutseni😮😮😮😮😮😮

  • @user-rx7zz9mx4z
    @user-rx7zz9mx4z Месяц назад

    Nawo a opposition akuopa kumangidwa ndi kuphedwa 😂😂😂😂😂

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Месяц назад

    Akalindo ayendereni anthuwa mwina mkusintha....kukenani tidafika kapena

  • @user-bw7bd5jt9h
    @user-bw7bd5jt9h Месяц назад

    Zoona a opposition Ali phee as if zinthu zikuyenda ma pensioners akuvutika kwambiri

  • @DanielnachanzaBanda
    @DanielnachanzaBanda Месяц назад +1

    Bodza

  • @KomwaChimwemwe
    @KomwaChimwemwe Месяц назад

    M'makwana a DC

  • @LexzoMagwax
    @LexzoMagwax Месяц назад

    The DC mwana ooopsa kwambiri

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Месяц назад

    A opposition nawoso ndi mbava palibe amene sakuziwa

  • @GeoffreyMaulana-rh5rx
    @GeoffreyMaulana-rh5rx Месяц назад

    Anthu akebso zitianalamulilapo Malawi ngatiboza

  • @evansjohn7766
    @evansjohn7766 Месяц назад

    Opposition palibe and sakuzidalila so pomwe akutelo ndekuti mphambvu zoti angawinenso alibe ciyembekezo.

  • @AliceChipeta-pc3nb
    @AliceChipeta-pc3nb Месяц назад +1

    Ausi chonde pitani kukasungu Ku prison mukaoneko

  • @HarryKandani
    @HarryKandani Месяц назад

    Bwanji osamanga aja ankakuwa kuti pastor chikangawa aja

  • @BMDMasulani
    @BMDMasulani Месяц назад

    Opposition kulibe ndidzitsilu dzikudikila nthawi Yao yodzaba

  • @KumbukaniKafatia-cd2hq
    @KumbukaniKafatia-cd2hq Месяц назад +1

    Chilungamodi kuno nchovuta

  • @WhitemanNumbers
    @WhitemanNumbers Месяц назад

    Zomwe akupanga a opposition ndizogona kwambiri

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz Месяц назад

    The DC Bon Kalindooooo ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @emmanuelmpenda2673
    @emmanuelmpenda2673 Месяц назад

    Kalindo n bakili tv akatundu

  • @giftmakoyo1441
    @giftmakoyo1441 Месяц назад

    Munawachosa mboma ndiye mumafuna azitani mesa ndizimene munavotera

  • @MuhammedNtaba
    @MuhammedNtaba Месяц назад

    The DC❤❤❤❤❤

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope Месяц назад

    Okumva amva osamva asamve koma chilungamo chauzidwa

  • @KanjokaBreugam
    @KanjokaBreugam Месяц назад

    Zawo ndizimozi ndalama zomwe zikubedwazi akudya limozi

  • @BatsonKadzuwa-tl3rp
    @BatsonKadzuwa-tl3rp Месяц назад

    ❤❤❤ The DC

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Месяц назад

    Boma lambava

  • @braveglorymwanzagolah4899
    @braveglorymwanzagolah4899 Месяц назад

    The DC kuswa Kuswa

  • @TimothyNkhutembaChirwa
    @TimothyNkhutembaChirwa Месяц назад

    Zowona bwana

  • @Kay-racle_mw
    @Kay-racle_mw Месяц назад

    🔥🔥🔥

  • @TemboHaswell
    @TemboHaswell Месяц назад

    Tandigayile number yako ndikuponyele yamadzi. ndiiwe katundu bon❤✨🔥🔥

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Месяц назад

    Good Messnge Mr bon kalindo ❤

  • @hastinngschikafa-zf9bc
    @hastinngschikafa-zf9bc Месяц назад

    Dolo

  • @julietphiri5510
    @julietphiri5510 Месяц назад

    sakunama Bon, opposition is indeed very dull

  • @Lastontano
    @Lastontano Месяц назад

    Winiko ndi wamisala

    • @Extratremendouszeus
      @Extratremendouszeus Месяц назад

      How???

    • @Dysonkhofi
      @Dysonkhofi Месяц назад

      Wamisala anaona Nkhondo!!
      Kumbukira za Chilima,amkamuuza bwana chokani kumeneko,Pakadafunda padajiwitsa galu, Lero ndi Malemu.

    • @MaritaBanda-p4z
      @MaritaBanda-p4z Месяц назад

      wamisala ndi chakwera pamoz ndiweyo