Kugawa ndalama ndizoputsa. Mugawa kwa athu angati ndalamazo. Kodi osauka muwakwanisa? Osangoponya ma company zithu zitsike ma price. Fetrizer sugar sopo. Company ya Bakhresa kuti itsise ufa.... zipatala odwala akudya kabichi opanda.mafuta or tomato mulibe. Why ndalama zo osatsiya malo ngati amenewo bwanji
Opusa nonse mukufunika zikwapu, chimene mukufuna nchani ntsogoleri azingokhala phee kusanjika kuti Inu muzipeza zonyoza, koma anthu opusa alipodi, a Bwana VP akugwira ncthito yotamandika stop your canal mind. Our Malawi must change bwana VP give us some more these dull minded dudes will come to the point of appreciation si ntsogoleri amasunga Ndi a misala omwe.
koma what we should know is that those on higher positions are the ones who are on fore front in the issue of corruption. Then how can you say that it will come to an end.
Man kumusankha munthu pokhala vice sizitanthauza Kuti amafanana iyayi koma Pali zifukwa dzina anamusankhira iyeyo usiyo,,,,,,, koma msatenge usi kumati akufanana ndi chilima limenero nde bodza man
I think you have nothing to say,iwe ungayankhule speech yanji kwa Ife can you give us pang'ono chabe.Abwana VP ✊✊✊✊✊✊✊✊ ine siine mmodzi omazati eeeeh! Anali abwino ndikuuona ubwinowo ukuchitika.wanzimu okanika iwe usinthe mind yako, a VP akuongola mitu youma ngati wakowo .Ngati ulibe comment pliz do not comment.
Momwe adapangira chibwibwi atamufusa za kuti adali kuti momwe amamwalira skc muzamvere interview yake guys pa times exclusive china chake chachikulu chidachitika
Why can't you Civic educate them, if you yourself have Civic education.. you are bad spirited who are always against leaders as if you can.Our late Bingu was right some of you Malawi and don't value your Leaders 😢😢
Dr.Usi you are a passinate leader. Theo bless!
Ambuye kumwambako ulandireni mzmu wa SKC, ndipo vumbulutsani zobisika zonse zibwere poyera, SKC continue resting in peace
Amen
I have been so much impressed with that VP speech 🎉
Well done sir for that articulated speech.
Mau amulungu amat,aliese adzafa,zachilima anthu tinalira ndpo tinavomeleza kt pot aliese alinda komweko nanga titan,,,mmmmmmm tieni amalaw anzanga maso patsogolo move forward,,,sindingadyeko mobwafula pazomwe akuyankhula Dr usi ,coz akuyankhula zoona,,,God bless mw
Smart guy, no hate speech. Bravo bwana VP
Very SMART leader ✌️✌️✌️
Title of this movie (sewero) pliz 😢share 😮
Kugawa ndalama ndizoputsa. Mugawa kwa athu angati ndalamazo. Kodi osauka muwakwanisa? Osangoponya ma company zithu zitsike ma price. Fetrizer sugar sopo. Company ya Bakhresa kuti itsise ufa.... zipatala odwala akudya kabichi opanda.mafuta or tomato mulibe. Why ndalama zo osatsiya malo ngati amenewo bwanji
Uzapange ukazalowa iweyo o VP, umbuli uzatha liti kusayamika kwakoko?
Mozambican men
Usi is going to be president of republic of Malawi
Poverty makes people deaf and blind.....
Exactly 💯%
Inu ndiolemera? Everyone has right.. achumanu zikhalani pa FB pa😂
Opusa nonse mukufunika zikwapu, chimene mukufuna nchani ntsogoleri azingokhala phee kusanjika kuti Inu muzipeza zonyoza, koma anthu opusa alipodi, a Bwana VP akugwira ncthito yotamandika stop your canal mind. Our Malawi must change bwana VP give us some more these dull minded dudes will come to the point of appreciation si ntsogoleri amasunga Ndi a misala omwe.
More fire Dr Usi ❤
Komatu mukutha mau amalawi Kodi mukanakhala inu mukanatani koditu mukamaonela mpila umati azakowo satha kusewela koma lowatu iwe ngati uthe kutinya musiyeni manganya ayankhule mukanakhala inu akanakukondani ndindani musamangonyoza penapake muziganiza amalawi
Zoona km anthu samadziwa kt mpira umakoma ukamaonela anzako
✊✊✊✊✊✊✊✌️✌️✌️
Vuto ku Malawi kuno andalewa amatifuna kampeni ikatsala pang'ono.
Kutukwana kapena kupeka nkhani zopasula sikukudalitsani sikudalitsa Malawi, kaduka ndi nsanje sikutengerani patali. Muphilika ndi kaduka
koma what we should know is that those on higher positions are the ones who are on fore front in the issue of corruption. Then how can you say that it will come to an end.
Ndalama mugawa kwa athu angati..... ovutikawo alipo angati muwakwanitsa?
Zikakoma kumayamikila....ana azanu ophunzira awaa.. school ndidhilu 🎉🎉....asafuna akakolope kunyanja 😂😂
Pafupifupi wina aliyense amene wavala cha UTM chikuwoneka chanyuwanitu ndekuti anthu onsewa amadziwa kusamala dzovala mofanana eti? Enawonso aphatikiza chawo mkati, cha UTM pamwamba, kumazizira ndekuti?
Unity brings progress . Unite Malawi for a common goal.,... prosperity
Amfumu mupitenso Ku immigration plz
Zama Dr izizi❤.. wina alire asalire😅.... tiyeni abale anga koyatsa ma kandulo😂
Neef inayamba 2020 koma zaka zonsezi mumakanika kupeleka ndalama zangongolezo .Lero chifukwa choti campaign Yatsala pang'ono kuyambika mwayamba kuwanamiza anthu kuti alandira ngongole
Ndipo zoona a malawi kupusitsidwa sikuzatha ayi😂😂
more fireeeeeeee USI
Koma chitsilu ichi chilinde mfundo bwanji osangopitiliza Tikufelanjiyo bwaa?😊
I'm following, Salam alaikum
Walykum sallam
Athu ndikumawombera mmanja zimenezo koma malawi kugona kwakeko iiiiiiiiiiiiiiii musapusitsike ndi ameneyooooo yudasi ameneyo 😂😂😂😂😂😂😂😂
Ndipo😂😂😂😂
Umphawi ndi mavuto zedi kumangoombera mmanja ndi Za zii zomwe
Canal minded people,asiyeni anthuwo akudziwa chimene akuona komaso akumva inuso mukazakhala pa udindo tizakumvani.
Choka galu iwe unamupha chilima kufuna mpando chitsilu manganya
Mukukamba zamanganya lnu lnuso ndi fiti mukukondwera mene manganya anamuperekera chilima kumuphesa kwachikangawa kufuna udindo agalu lnu 😢😢😢skc tizalirabe lfe 4ever
Kukamba zopanda umboni. Dikirani report lidzakuwuzeni zenizeni.
Muli ndi umboni? Musachimwe ndi zinthu zomwe simuzidziwa
Ngati ndi nsanje mufa nayo..chilungamo amachidziwa ndi Mulungu..Lekani kufalitsa nkhani za bodza..kodi mukutokota ngati ndan..anuwake anamalira ananena kuti musamafalitse nkhani zopanda umboni...Muli busy ku lubwa lubwa azanu akusangalala..
Ine ndikwathu kumeneko manganya osanamiza anthu , ma drama uzikapanga ku blantyre kupusa eti??
It's too late to apologize akutaya nthawi pachabe
Tikuferanji@ Malawi
Palibe chamzelu,avutika atu for the past four years,nde lelo muziti chani?
Munthu wanjala umpase ngongole abweza, tayankhulani zamzeru apa
Chilima uja anali dolo kwambiri politics yake imakoma 😂😂😂 za bwino sizikhalisadi 😔😔😔 Michael usi alikutari kwambiri kuyelekeza ndi chilima
Very far
Ndiwe kape ase zokut aliyese ali unique sumadziwa
Iwe osadabwa Kuti Chilima dolo ukumunenayo adamusankha Usi Kuti akhale wachiwiri wake,iwe ukuganiza Kuti adangozipanga basi? Michael Usi simunthu Wamba aise. Utha kumanva ma speech Ake sanyoza munthu komaso amakamba zomanga nthawi zonse
Man kumusankha munthu pokhala vice sizitanthauza Kuti amafanana iyayi koma Pali zifukwa dzina anamusankhira iyeyo usiyo,,,,,,, koma msatenge usi kumati akufanana ndi chilima limenero nde bodza man
Azungu amayambitsa zipwilikiti mu africa, anthu nkumafa kenako amabwera nkumati tikuthandizani ndi nsima after kuotcha nkhokwe zaanthu
Uyu ndinamukaikira basi😢
Speech yoloweza
Namasewero
I think you have nothing to say,iwe ungayankhule speech yanji kwa Ife can you give us pang'ono chabe.Abwana VP ✊✊✊✊✊✊✊✊ ine siine mmodzi omazati eeeeh! Anali abwino ndikuuona ubwinowo ukuchitika.wanzimu okanika iwe usinthe mind yako, a VP akuongola mitu youma ngati wakowo .Ngati ulibe comment pliz do not comment.
@@InnocentMtafyaamwene koma ndye musaka athutu osapanga zanu bwanji anthu akulemba zomwe akuziwatu mukalandila ndalamazo mutigawireko🤣🤣🤣😂
Nkhani ya njala simunayankhe zanzeru chonsecho yomwe Ili yovuta kwambiri Ndi imeneyo anyway andale nchimodzimodzi
Luke 19 vs 29 to 31
aneef ayambe lero three 4 years yadusayi munali kuti za campaign basi amalawi nawo kutengeka
Ndipo zoona
Neef yoyamba 2020 akubwera pamsonkhano kumati anthu atenge lero 😂😂😂😂😂
Anthu akukondwera ngongole ya Neef sakuziwa kt angofuna kutipusisa komanso atilandenso katundu yemwe analinayo poyamba
😂😂😂
Eti eti ndithu
Kod ma tshirt a utm akungovalira mwano chiani
Kodi iwe manganya ukufuna kuwoneka WA nzeru chitsilu iwe mpake unapha chilima Kuti ukhale vice
Big man respect
Malawi ndidziko lophweka kulamula. Coz Malawian amafuna nsima ulimi zitukuko
Awa mesa ayambanako UTM
Zoyankhula za ausi ndizopanda ntchito chikufunika ndichakuti abwere poyela anenekuti alimbali iti UTM or MCP chifukwatu akuzemba zakutuluka mumgwilizano watonse
Ndiwa mcp simukuona mmene akuchemelera Mr chifunga😮😮😮😮
@@CharityMhone-uk9ymzosakoma
Ada awawa koma yaah
Malawi sizatheka ndichifukwa umphawi sudzatha chifukwa timangowombela manja ndi manyiwomwe uyu akuyakhulazi ndidzichiyanu galu ameneyu
Za nziiiii
Manganya ndi munthu wanzeru Koma zizichitikatu ajamani
Usi kumavala Bwinotuu monga vp
Iwe bwanji sunamukonde chilima....
Momwe adapangira chibwibwi atamufusa za kuti adali kuti momwe amamwalira skc muzamvere interview yake guys pa times exclusive china chake chachikulu chidachitika
Guys ndifuseni ine 😢za usi kuti mudziwe gwi Lani mau awa odya zake alibe m'mulandu
Manganya nayo zaziii kalibe ndi fundo aMalawi akungoyimbira mmanja zili zonse thus why munamuyika mpando chakwera kufera ubusa ndi izo mwaziona kungokhalira kugwetsa kwacha basi
Munali kuti nthawi yonsei kt mutipase ndrama zazii , mulungu akukuonani kumwambako
President iyeyo bwanji zakunena zoti anthu apasidwe ngongole kumangomvera kwama disciples paja ndale ndi bodza
Koma manganya pena ukupanga mawiniko
Akulu akulu ati ama candle zopusa basi usi yemweyo
Ndeeee chan akulu musapusitse
Galu ameneyo
Inuso basi tikhalira yomweyo ingochipisani sugar ndi feteleza agalu inu
Koma amalawi sindiwamvetsa ndithu kodi manganyayi ndiwachipani chanji koma 😂😂😂 koma guys
Nayeso wayambaso maboza😂😂
💪💪💪
😂😂 akupanga sewelo uyo
ndizosakhalisa akangoluza chakwela basi zathela popo bola mukana dikila
Zambiri mungitcholera mumatumba mwanu basi
Speech imodzi kom ka 100😅😅😅
Katundu VP
We mlawians have problems we have no. directions I understand. is. Poverty.
Malawians Luck Civic Education to make them see common sense be common.
Why can't you Civic educate them, if you yourself have Civic education.. you are bad spirited who are always against leaders as if you can.Our late Bingu was right some of you Malawi and don't value your Leaders 😢😢
Umphawi sizinthu.. hahaha 😂
Ausi anthuwa mukawalonjeza ndalama sizithandiza kanthu bwanji osamakamba zafeteleza mbewu zosiyanasi siyana kut muwapatse anthuwo koma mulibize kulankhula zaziiiii
Apatseni mbewu azadzale anthuwo
Zasewero
Koma ogwetsa denge alibe khaza koma omenya khalamba ndiye wakhaza
Neef yo mesa ndi ngongole ukupangira campaign yo😂😂😂😂 iwe masero nde Mbali yako
Ndale sikukolana kkkkk tikufelanji waibhebhesa Manganya
Fundo zamanya zochulusa kusekesa
Tisakwela abulu
Speech yachibwereza kod?
Jxt be smart & be a good manipulator you may receive full support.
Uyu namasewelo😂😂
Mmakwana bwana
Manganya ndiwe wa mcp2. Pamtumbo pako.
B very careful, anthu openga bola musamakomente .
Bwerani bwana kuno mutithandize ndine mwana wa anzanu malemu Dick chapweteka
Alibe fundo uyu
Your very young in politics
Mbambande bambo asikono
Why sunamukod chilima fit
Ndifusileko m. Bale wanga
Fundo zopusa sewero ndikuramura dziko siyanisan
Apanga amene akubwerawo
Pa nyini pa mako manganya unapha chilima lero ukufuna kugulitsa chipani Ku MCP ukuona Ngati sitikukuona tikudyera uzakhumudwa
Umbuli umenewu
Kkkkkkk koma Manganya mpaka mama kufunana za ku chipinda tsopano
Palibe unhachite oipa opha chilima
Koma umphawi sizinthu konnse😂
Tikuferanji ya 2006 😢
Usi anatuluka kare mutotse
Usi ndi kape
Tikuferanji amalawi 😂😂😂😂
Immigration/road traffic/MRA...e.t.c poor srvice and very corrupt intities
Zazi iwe mesa ukuziwa kuti njara inayamba kale after kulowa boma lanulo
Sewelo lokha mupaka zovinidwa ku vice president 😢
Year he is true son of Mws