Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Ndichifukwa chake mpira wakumalawi supita patsogolo ndale,dyera,kuzondana,kuponderezana,kuyendana,mmaphazi
Ndye zosakoma bwanji hmmm
Tisonkha ifeee amalawi tooonse atipase zithu zathu mamaka ife masapota tisonkha basi
Kkkk makape inu mumazinga Ngati madolo muziyenda pansi wokasewera Mpira
Kkkkkkkkkk ndipo ayendedi pasi amazitama anthuwa kkkkk
Vilije ntchito malanani mwekha
Chonde khululukani😊
Ndawa kukuona ku game ya bullets tizakupha
Mmmm zosayenda
Adana nayo bwanji ndipo achepesa akanawauzatso kuti asasewele kwa za 5
Ndale basi
Mmmm alipira
Mmunadana nayo team yo zikuvutani
Mbola
Umenewu ndiye timati umbili uja ndi umenewu timu inagulisidwa kwa ena ndiye zikugwirizana bwanji pamenepo amayenela kulipila ndi anthu amene amayendesa akalewo ukutchedwa big bullets not nyasa bullets 😂
Mpira waku malawi mmmm
Nkhuyu zodya mwana zimapota wa mkulu
Ingobwezani ndalama zo basi
Kungodana nayo bas
Zabwerera
Mwanayo mwanayo 🤣🤣🤣
Kkkkkk😂😂
Zakhala bwno😂😂😂
Iiii zosa yenda
😂😂😂😂
Zamkutu