Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Shinkangawaw wayamba BP inankwella shifunkwa sha shinkangawaw
Thanks mr moses
Takunyadirani a busa, Mulungu amene mumamupembeza akudalitseni.chigonammalunje Mulungu akuoneni
inuyo topani ifeyo wathu atiwawa ndinthawi yanu ambuye akusungeni musazafe zikomo
😂😂😂 mumakwana abusa
Dzina lokhalo Chigonammalunje Yaya
Ubusa osokoneza basi
Anless black box idzatuluke ndi umboni
Azibusa tiuzeni zaufumu wakumwamba zandale aaatatopa nazo
Abusa ometa mbalimbali antundu wanji anthu angawalangize chani Za ufumu was kumwamba iyeyu Ngati wayamba ndi iyeyu kumeta Mbali?
Koma ine za chilima idzi zinanditopesa lidamupha dyela lake
Mwalankhulatu achimwene mpaka dyera nde kt inu mukudziwapo kanthu kd kumaliro kuja anafuna yekha kupita kapene anatumidwa ai zikomo mulungu akuoneni inu pamodzi ndi abwana anu