BON KALINDO KUNG'ALULA MA UDINDO ATSOPANO OMWE ASANKHIDWA__2 January 2025

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 19 янв 2025

Комментарии • 70

  • @KuhleKiviets
    @KuhleKiviets 18 дней назад +6

    Two separate positions: Minister of Higher Education and Minister of Basic and Secondary Education? Honestly, for a country like Malawi, do we even have the resources to sustain all these roles? It raises questions about prioritization and efficient use of our limited funds.May God Guide us

  • @FrancisKavinaoyeraa
    @FrancisKavinaoyeraa 18 дней назад +1

    Thats true indeed Mr DC ..May almighty God help Malawi

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 18 дней назад +3

    Mbusa, Chipiku angatiuze chani mfundo alibe Chikangawa 😅😅😅😅😂😂😂😂

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 18 дней назад +1

    Nkhani ya cabinet cholinga ndi kugawana ndalama za misonkho ya a Malawi omwe akuvutika koopsa ndi boma ili

  • @SandraChibaka
    @SandraChibaka 16 дней назад

    Mr chikangawa 😅😅😅 mwabalalikaa etiiii??

  • @GiftMusorola-l2o
    @GiftMusorola-l2o 17 дней назад

    Kodi chimanga akugawa manganyawu Ndi cha born kalindo?

  • @RabeccaMkandawire-i9j
    @RabeccaMkandawire-i9j 18 дней назад

    Happy New Mr DC

  • @ShamzyMbawe
    @ShamzyMbawe 17 дней назад

    Big up dccccc

  • @DalitsoMbewe-u1y
    @DalitsoMbewe-u1y 18 дней назад +2

    Muuzeni opusayoo,kusapita ku sukulu akuluwoooo,Mr DC ,mungaluleni mbuliyoooo,ndimbuzitu yamunthu,31 ministers,?,kaziko kakangonongono ngati kameneka

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 18 дней назад

    😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂yomweyo Chikangawa party

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i 18 дней назад

    The DC one day is one day you gonna drive 🚗 this country mr president bon kalindo ulemu wanu big

  • @ThanksKamlanje
    @ThanksKamlanje 18 дней назад

    😂😂😂 akupambuka chisawawa chakwera manyi wokhawokha the DC karindo powerful 💪

  • @ConnexKhomba
    @ConnexKhomba 18 дней назад

    Nduna Osez mafuta aulele salary zimagalimoto zopuma achitetezo ma alawasi eeee 😢😢😢 chakwela zikomo

  • @Patricia-l7m6u
    @Patricia-l7m6u 18 дней назад

    Happy New year the DC

  • @EmmanuelNakoma
    @EmmanuelNakoma 18 дней назад +1

    Kkkkkk the DC ati kuli manyi okha okha

  • @ChinsinsiKantumba-p1u
    @ChinsinsiKantumba-p1u 18 дней назад

    🔥🔥🔥🔥🔥 DC

  • @dorothymkandawire
    @dorothymkandawire 18 дней назад

    The DCcccc happy new year😂😂😂😂

  • @BORNFACESIMBOTA
    @BORNFACESIMBOTA 18 дней назад +1

    Chakwera ndi mbunzi hvy yoh

  • @InnoMwikho
    @InnoMwikho 18 дней назад

    Born kalindo mwana opsa kwambli The DC

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 18 дней назад

    Kkkk the Dc 🔥 fire 🔥

  • @MercyChidzombe
    @MercyChidzombe 18 дней назад

    Thanks alot the DC manyiwo ali kt

  • @ussimasi2458
    @ussimasi2458 18 дней назад

    Dziko lovesa chisoni 😢😢

  • @wilfredluwinga
    @wilfredluwinga 17 дней назад

    The DCcccccccccc🔥

  • @BasheelKakaza
    @BasheelKakaza 17 дней назад

    Muying'alule bs Dc

  • @andrewmtendere3167
    @andrewmtendere3167 18 дней назад

    machine awa🥰🥰

  • @thomasthomson-rn5ch
    @thomasthomson-rn5ch 17 дней назад

    Mzimu wa chilima wakalipa

  • @andrewmtendere3167
    @andrewmtendere3167 18 дней назад

    amachokera kwa keneth kamvubweee,,,,,the dc southern africa T/A mabuka

  • @LameckMatabwa
    @LameckMatabwa 17 дней назад

    Abale munthuyi azakhale president wanthu

  • @STEVENMANGANI-o6e
    @STEVENMANGANI-o6e 18 дней назад

    The DC MWANA OOPSA KWAMBIRI BOOOONI KARINDOOOOOOOOOOOOOO

  • @Hendersonspoon
    @Hendersonspoon 18 дней назад +1

    Chalakwe ndichimzimu osa

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly 17 дней назад

    Vuto kumalawi kulibe anthu that's why chalakwe akupanga izi

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 18 дней назад

    ❤❤❤❤ DC

  • @JohnChiyazu
    @JohnChiyazu 18 дней назад +1

    The DC NJEDZA VILLAGE T/A MABUKAAAAAAAA

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 18 дней назад

    Manganya ndiwankhaza samayenera kumangitsa anthu choncho as vice president

  • @razackibrahim5880
    @razackibrahim5880 18 дней назад

    The dc ❤❤❤❤😂😂

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 18 дней назад

    Vuto lopanga Cabinet Reshuffle musanamwe magadzi ndi Mikodzo monga pa mwambo wako Chakwera,ndizimezo mmalo mochepesa ma Unduna ukukhadzikitsa mpaka 31 😂😂😂😂😂 Dziko lake liti.
    Mbabva ndi Mbabva basi .
    Chikangawa serial killers

  • @DuncanKazinkambani
    @DuncanKazinkambani 18 дней назад

    Bon Kalindo the DC ndimakupemphelera kwa MULUNGU apitilize kukupatsa mphamvu zoyankhulira chilungamocho pitilizani ntchitoyo

    • @ThomaslowrenceChizombwe
      @ThomaslowrenceChizombwe 18 дней назад

      mulungu musamamuike mu zinthu zandale,muzingopanga zandale osat kumuikamo yehova mu zinthu ngat zmenezi

  • @faithgama5972
    @faithgama5972 18 дней назад

    Happy new year DC😂😂

    • @HendresonNambazo-u4i
      @HendresonNambazo-u4i 18 дней назад

      Mulungu Munthu uyu anamuyang'anila kumbari ndithu chifukwa samva zokamba za anthu

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 18 дней назад

    The truth shall set us free.

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 18 дней назад

    Komanso ndamva kuti ma mp awonjezeledwa akuti panopa ndi 200+

  • @AlexanderTraffick
    @AlexanderTraffick 18 дней назад

    Ndimadziwa ine .kkkkk

  • @manasemaposa
    @manasemaposa 17 дней назад

    Chipiku experience

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 18 дней назад

    Ali ndi maganizo ongoononga. Akufuna anyeletu. Akatelo onsewo aziyendera ma vx, mafuta ngambwingambwi. Ma bodyguard pomwepo.

  • @thomasthomson-rn5ch
    @thomasthomson-rn5ch 17 дней назад

    Chalakwe😅

  • @EmbersonMchacha
    @EmbersonMchacha 17 дней назад

    The DC wabwera

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 17 дней назад

    Achina chikangwa mcp machimo

  • @MdalaBonomali
    @MdalaBonomali 18 дней назад

    Happy new year the DC ❤❤❤

  • @user-hh8eu8dr4u
    @user-hh8eu8dr4u 18 дней назад +1

    Malawi is a sad nation with useless leaders, Malawi is sad

  • @DonaldMunthali-d5i
    @DonaldMunthali-d5i 17 дней назад

    MBWELELA ZA NDUNA MANYI OKHA OKHA PALIBE CHAZERU NDUNA ZONUKHA MSETE ZOKHAZOKHA TSOKA CHIPANI CHA MCP CHIFUKWA OYIPAYO WASIKILA. KOMWEKO

    • @SandraChibaka
      @SandraChibaka 16 дней назад

      Ekizakitire.... Chimpheeee ichiiiii manyaka awaa ... Thanks God tivote changu 2025

  • @Harrychokanda
    @Harrychokanda 18 дней назад +1

    The DC 😂😂

  • @Rozaliohnjenjema-p3q
    @Rozaliohnjenjema-p3q 18 дней назад

    The Dc 😂😂😂😂

  • @MosesTangwe-q8o
    @MosesTangwe-q8o 18 дней назад

    Uyu mukhaula nae

  • @StarchJonas
    @StarchJonas 18 дней назад

    Dziko likulamulidwa ndi anthu osadziwa direction

  • @PHILLIPMmwenye
    @PHILLIPMmwenye 18 дней назад

    Palibe chomwe chachitikapo yapo yoooh mbola

  • @HaroldBerson-z2j
    @HaroldBerson-z2j 18 дней назад

    Chakwera ndi mafiya

  • @YusufMoyo
    @YusufMoyo 18 дней назад

    Wabalalika chakwela

  • @AbdurashidBwanali
    @AbdurashidBwanali 18 дней назад

    Zaziiiii

  • @stormchatepa134
    @stormchatepa134 18 дней назад

    Nyo

  • @iangondwe6857
    @iangondwe6857 17 дней назад

    Bon kalindo I don't understand you coz you only point zithu zolakwika zokhazokha zabwino palibe

    • @AllanNyirongo-t7x
      @AllanNyirongo-t7x 15 дней назад

      yes most of the things that are done with this government are bad than the good ones

  • @LIMBANIALISON
    @LIMBANIALISON 18 дней назад

    DC 😂😂😂

  • @MilacleSankhani
    @MilacleSankhani 18 дней назад

    Satana anayenda wapasi kuno

  • @Vincentmandota
    @Vincentmandota 18 дней назад

    Tikadali ku Bagamoyo basi

  • @CharlesJames-f1w
    @CharlesJames-f1w 18 дней назад

    Machado.md.samanyasi.chikangawa