Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Very excellent advice to the rich! I salute you! Keep it up!
Great advice to those who exposes their worthy to the world through the socia madia..thank you Born Kalindo.
Paja bon kalindo amabwela ndi warning mu January ndakumbukila ya a chilima mmmmm mpinganjila take care
Am agree with the dc
Ndipo zoona
James sukunama.....i remember everything.....bro ndipo Live
I was there kumvetsera ndipo ndeanamuuzadi Chilima kuti awaturukedi achikangawa koma mphuno salota ndipodi wamisala anaona nkhondo komanso Kalindo amatiyankhulira kuti tichiteko kanthu koma sitipanga kanthu aaa 😢
Wamisala anaona nkhondo 😂😂😂😂
Komadi kalindo akunena zoona mkazi wa mpinganjira California waonjeza kwambiri
Dpp my vote no matter what
Me too
Moto
100%
@@WhiteKandirinyu 💙💙💙💙💙💙
Mcp forever
Chimene atapange tsiku Limenelo amafunq dziko Lomse lidziwe😂😂😂😂😂😂😂
Oooo bwana limu ndi muli kkkk koma DC aaaa ndamulephela❤❤❤❤
❤❤❤ Apm my vote osati chikangawa
UTM my vote kabambe🔥🔥
🔥🔥💯
Ndipo live 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Munthu yemwe amakuuzani za nzeru ndiye kuti amakukondani. Ulemu wanu Bwana Kalindo.
For sure
The Dc you are number one always I will supported you the Dc
Salute ur the dc ...umalangiza....ndipo supanga ...sanje......koma kulangiza....god bless you
One of the best audios from him, I just love the advice
A Kalindo Malume anu anakwatila m,tsikana ndipo muwasiye kkkkkk chuma ndichawo.
Happy New year Mr Bon Kalindo.Mr Bon Kalindo ndimakunyadilani kwambiri mumayankhula chilungamo, Ambuye azikutetezani
Kkkkkkk koma mpaka showbizzie
Mwana oophyadi kwambiri The DC kkkkk koma ndaseka kumapetoko
😮Zoona alomwe ndinu odzikondadi.
Nde mwati uncle crossroads 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣.... Ndi kalifoniya eeeh bon kalindo
I once said bwana mpinganjira ali pa big trap akuyeneka ku samala....
Mkazi woyipa amene uja in my opinion.
Zoonadi hule uja waonjeza, pajatu amakawozekedwa ku Equatorial
Chitsazo kulii bwana msimbi ku mchinji ndi wa pheeee alomwe kuziva kkkkkk
Uthenga wa lero unali mbambande Mr bon🎉
Dpp my vote mr Bon kalindo ulemu wanu
Ndipo Triphoenia apangitsa kt chuma cha triphoenia kt anthu ayambe kuchifufuza ndipo ziwapasa mavuto
Bwana Limu bwana Muli Brothers imeneyo kkkkkkk
Akavera voice iyi aziganiza kut akudana naye kom truth Mr pinganjir
Absolutely
Chelimu my votee❤❤
God bless you Brother...staystrong! U.N.I.T.Y
Ulangizi zabwino kwambiri ❤
Chete kudikila the Dc kalata yawo yomangidwa...😂
Thanks for advising the Rich.
Kabambe woyeee
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Chirungamo ichi bon kalindo mkadzi amuyankhule sakupanga bwino
Ine mpana ndinanena kuti mkazi uyu ndi wamatama kwambiri
Respect Mr DCHappy new year
No comment coz atimagitsa ndilibe nkhuku 😂😂😂
Kulira Kwa a kalindo , komanso muziziwa kuti mkaziyo alinso ndi zake
Happy new year Mr Bon Kalindo,dzikomo kwambiri potilimbikisa
10 may once said this mpaka anamumanga,a California mumumagitsetu the DC 😂😂😂
Muthuyi akukamba zowona...bwana sithani malangizo awa ndiawulele
Anganga ulemu wanu ❤❤❤❤
The other guy said the same thing ku fb ndizija anamumangisa akuwalangiza amai aja😂😂😂😂😂
Eetu ukarankhura umakathera kundende
Ndiopusa..anayamba kelemera ndi iwowooo..za ziiiiii
Iiiih amene uja anaonjeza kunyoza pamene uyu akupeleka malangizo
Aseeeee uyu ndi DC uona ngati wina angamumangitse!!!?😮
Azimay Pena tili nkusokoneza zinthu matama andione anditame
Happy new year ❤❤
Crossroads lol mwaliyika nchizungu dzina lija 😂😂😂😂😂
Kunena chilungamo guys the Dc akuyankhula zoona bwana Thom nd mkadzi wawo zomwe akupangazi ayi sizabwino
Happy new yr Mr bon kalindo we love u
Taziwe bwana limu wo ife
Koma iweo kalindo ndiwe katundu. I admire you
Dpp my vote
First to commentbin 2025
Che crossroads
Number one bro ❤❤❤
Mkulu uja aaaah ndiwa shupu kwambili even ma speech ake okhuza za mpira aaahh
Ndipo enafe tinkangova kuti kuli a mpinganjira koma sitimawadziwa koma pano tinawadziwa ndipogona pawo pomwe tinapadziwa😢😢
Anachita mistek kukwatila hule uyu ineo sidikukondwana Mai amenei
Happy new year big 🎉
Happy new year big mr bon kalindo ❤❤❤❤
Great advice Mr ngt amamva amva
Ulemu wanu bwana dc❤❤❤
Koma iyi mwanena chilungamo kwambiri❤
Mr bone kalindo big up big boss's mumatiimilila
Ulemu wanu dc happy new year
Wayitha aise kusintha apap umavadi good
Kkkkkkkk koma kalindo 😂😂😂😂😂😂 ulemu wanu
Koma lero ndie eeeee uthenga uphuzitsa
Mkazi ndiopoila kwambiri akaona Dolla Mutu simugwila ...Koma samadziwa komwe zachokeraa
Excity bro naa mzimayi mmm
Happy new year Dc
Born kalindo,ndiwe munthu wamtima woona patali zed.
😂😂😂 koma bon kalindo eee wang'alura California
Chaswa mfundo 👏🏾
Kalindo malangizo abwino kwambili 🙏🙏🙏🙏🙏
Happy New years
😂😂😂😂 ndangoteee . Koma ameneyu akuthandiza kwambiri
Kkkkkkkkk bwana Limu ndiye ndan
Mulli brothers
Aaaaa kkkkkkk
Limu ndi muli brothers!
Muli kkkkkkkkkk
Kkkk😂😂😂 kodi simu nalankhulepo chining'a eti
Uyu nde muthu karindo
❤❤ kabambe my vote
A crossroads mwati😂😂😂😂😂😂
Kkkkkk koma kalindo bwana limu ndi muli ameneyo
Happy New year
Munamanga ten May nkhani zake zomwezi nanga uyuso mumumanga kapena bwanji koma wayankhulazi ndizoona mr crossroads be careful
The DC umakwana Big up
Iweeeeee ndikatunduuu ing'alulee
Happy new year🎉🎉🎉❤❤😮😊
Am agree with you born kalindo
Nalikalizi😂😂😂
Ndipo big munena zoona eti mpaka kujambula dzindalama et zoti ali ndalama timadziwa kale
We luv you Mr dc❤❤❤
Ichi mumati mchovuta koma mmmmmm muli medulla mbwiyeeeee inu ndi 1😅
Komad apapa nanenso ndayamba kuona kuwala pomwe tikuyandikila munyengo yoti ndikasithe President member of parliament and councillors
Limu/Muli 🎉🎉 happy new year DC🎉🎉
Happy new year Mr Dc
Kkkkkkkkk respect mr bon kalindo❤
Good massage bwiiyee
😂😂 a lhomwe
My best brother mr bon karindo THE D C ❤❤❤
Ulemu wamuyaya boss
Soona akupanga ngatiMwana mamuna akeAli 😅😅😅😅😅😅😅😅😅
Nice advise, powerful
Mumakwana amkolo❤
Happy new year Bon Kalindo ❤❤
Uyu ndiye kt samagwidwaso
Sangamange
Very excellent advice to the rich! I salute you! Keep it up!
Great advice to those who exposes their worthy to the world through the socia madia..thank you Born Kalindo.
Paja bon kalindo amabwela ndi warning mu January ndakumbukila ya a chilima mmmmm mpinganjila take care
Am agree with the dc
Ndipo zoona
James sukunama.....i remember everything.....bro ndipo Live
I was there kumvetsera ndipo ndeanamuuzadi Chilima kuti awaturukedi achikangawa koma mphuno salota ndipodi wamisala anaona nkhondo komanso Kalindo amatiyankhulira kuti tichiteko kanthu koma sitipanga kanthu aaa 😢
Wamisala anaona nkhondo 😂😂😂😂
Komadi kalindo akunena zoona mkazi wa mpinganjira California waonjeza kwambiri
Dpp my vote no matter what
Me too
Moto
100%
@@WhiteKandirinyu 💙💙💙💙💙💙
Mcp forever
Chimene atapange tsiku Limenelo amafunq dziko Lomse lidziwe😂😂😂😂😂😂😂
Oooo bwana limu ndi muli kkkk koma DC aaaa ndamulephela❤❤❤❤
❤❤❤ Apm my vote osati chikangawa
UTM my vote kabambe🔥🔥
🔥🔥💯
Ndipo live 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Munthu yemwe amakuuzani za nzeru ndiye kuti amakukondani. Ulemu wanu Bwana Kalindo.
For sure
100%
The Dc you are number one always I will supported you the Dc
Salute ur the dc ...umalangiza....ndipo supanga ...sanje......koma kulangiza....god bless you
One of the best audios from him, I just love the advice
A Kalindo Malume anu anakwatila m,tsikana ndipo muwasiye kkkkkk chuma ndichawo.
Happy New year Mr Bon Kalindo.
Mr Bon Kalindo ndimakunyadilani kwambiri mumayankhula chilungamo, Ambuye azikutetezani
Kkkkkkk koma mpaka showbizzie
Mwana oophyadi kwambiri The DC kkkkk koma ndaseka kumapetoko
😮Zoona alomwe ndinu odzikondadi.
Nde mwati uncle crossroads 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣.... Ndi kalifoniya eeeh bon kalindo
I once said bwana mpinganjira ali pa big trap akuyeneka ku samala....
Mkazi woyipa amene uja in my opinion.
Zoonadi hule uja waonjeza, pajatu amakawozekedwa ku Equatorial
Chitsazo kulii bwana msimbi ku mchinji ndi wa pheeee alomwe kuziva kkkkkk
Uthenga wa lero unali mbambande Mr bon🎉
Dpp my vote mr Bon kalindo ulemu wanu
Ndipo Triphoenia apangitsa kt chuma cha triphoenia kt anthu ayambe kuchifufuza ndipo ziwapasa mavuto
Bwana Limu bwana Muli Brothers imeneyo kkkkkkk
Akavera voice iyi aziganiza kut akudana naye kom truth Mr pinganjir
Absolutely
Chelimu my votee❤❤
God bless you Brother...staystrong! U.N.I.T.Y
Ulangizi zabwino kwambiri ❤
Chete kudikila the Dc kalata yawo yomangidwa...😂
Thanks for advising the Rich.
Kabambe woyeee
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Chirungamo ichi bon kalindo mkadzi amuyankhule sakupanga bwino
Ine mpana ndinanena kuti mkazi uyu ndi wamatama kwambiri
Respect Mr DC
Happy new year
No comment coz atimagitsa ndilibe nkhuku 😂😂😂
Kulira Kwa a kalindo , komanso muziziwa kuti mkaziyo alinso ndi zake
Happy new year Mr Bon Kalindo,dzikomo kwambiri potilimbikisa
10 may once said this mpaka anamumanga,a California mumumagitsetu the DC 😂😂😂
Muthuyi akukamba zowona...bwana sithani malangizo awa ndiawulele
Anganga ulemu wanu ❤❤❤❤
The other guy said the same thing ku fb ndizija anamumangisa akuwalangiza amai aja😂😂😂😂😂
Eetu ukarankhura umakathera kundende
Ndiopusa..anayamba kelemera ndi iwowooo..za ziiiiii
Iiiih amene uja anaonjeza kunyoza pamene uyu akupeleka malangizo
Aseeeee uyu ndi DC uona ngati wina angamumangitse!!!?😮
Azimay Pena tili nkusokoneza zinthu matama andione anditame
Happy new year ❤❤
Crossroads lol mwaliyika nchizungu dzina lija 😂😂😂😂😂
Kunena chilungamo guys the Dc akuyankhula zoona bwana Thom nd mkadzi wawo zomwe akupangazi ayi sizabwino
Happy new yr Mr bon kalindo we love u
Taziwe bwana limu wo ife
Koma iweo kalindo ndiwe katundu. I admire you
Dpp my vote
First to commentbin 2025
Che crossroads
Number one bro ❤❤❤
Mkulu uja aaaah ndiwa shupu kwambili even ma speech ake okhuza za mpira aaahh
Ndipo enafe tinkangova kuti kuli a mpinganjira koma sitimawadziwa koma pano tinawadziwa ndipogona pawo pomwe tinapadziwa😢😢
Anachita mistek kukwatila hule uyu ineo sidikukondwana Mai amenei
Happy new year big 🎉
Happy new year big mr bon kalindo ❤❤❤❤
Great advice Mr ngt amamva amva
Ulemu wanu bwana dc❤❤❤
Koma iyi mwanena chilungamo kwambiri❤
Mr bone kalindo big up big boss's mumatiimilila
Ulemu wanu dc happy new year
Wayitha aise kusintha apap umavadi good
Kkkkkkkk koma kalindo 😂😂😂😂😂😂 ulemu wanu
Koma lero ndie eeeee uthenga uphuzitsa
Mkazi ndiopoila kwambiri akaona Dolla Mutu simugwila ...Koma samadziwa komwe zachokeraa
Excity bro naa mzimayi mmm
Happy new year Dc
Born kalindo,ndiwe munthu wamtima woona patali zed.
😂😂😂 koma bon kalindo eee wang'alura California
Chaswa mfundo 👏🏾
Kalindo malangizo abwino kwambili 🙏🙏🙏🙏🙏
Happy New years
😂😂😂😂 ndangoteee . Koma ameneyu akuthandiza kwambiri
Kkkkkkkkk bwana Limu ndiye ndan
Mulli brothers
Aaaaa kkkkkkk
Limu ndi muli brothers!
Muli kkkkkkkkkk
Kkkk😂😂😂 kodi simu nalankhulepo chining'a eti
Uyu nde muthu karindo
❤❤ kabambe my vote
A crossroads mwati😂😂😂😂😂😂
Kkkkkk koma kalindo bwana limu ndi muli ameneyo
Happy New year
Munamanga ten May nkhani zake zomwezi nanga uyuso mumumanga kapena bwanji koma wayankhulazi ndizoona mr crossroads be careful
The DC umakwana Big up
Iweeeeee ndikatunduuu ing'alulee
Happy new year🎉🎉🎉❤❤😮😊
Am agree with you born kalindo
Nalikalizi😂😂😂
Ndipo big munena zoona eti mpaka kujambula dzindalama et zoti ali ndalama timadziwa kale
We luv you Mr dc❤❤❤
Ichi mumati mchovuta koma mmmmmm muli medulla mbwiyeeeee inu ndi 1😅
Komad apapa nanenso ndayamba kuona kuwala pomwe tikuyandikila munyengo yoti ndikasithe President member of parliament and councillors
Limu/Muli 🎉🎉 happy new year DC🎉🎉
Happy new year Mr Dc
Kkkkkkkkk respect mr bon kalindo❤
Good massage bwiiyee
😂😂 a lhomwe
My best brother mr bon karindo THE D C ❤❤❤
Ulemu wamuyaya boss
Soona akupanga ngati
Mwana mamuna ake
Ali 😅😅😅😅😅😅😅😅😅
Nice advise, powerful
Mumakwana amkolo❤
Happy new year Bon Kalindo ❤❤
Uyu ndiye kt samagwidwaso
Sangamange