JOSEPH NKASA WAPANGA ZA ATCHEYA BAKILI MULUZI CHAKA CHINO

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 янв 2025

Комментарии • 114

  • @AugustineMwamadi-k1n
    @AugustineMwamadi-k1n 8 часов назад +2

    Palibe kanthu ngati akuyimba ndicholinga CHOTI amupase kangachepe koma zimene wayimbazo ndi zowwona and a cheya anasiya ndale he is no more a politician ngakhale zitabvuta chotani sangakhalenso president koma kuyamikira pa zabwino zimene wina anachita ndibwino history is the best teacher ❤❤❤❤❤

  • @BlessingsChikankheni-r4f
    @BlessingsChikankheni-r4f Час назад +1

    Bakili is the only president who knows how to associate with the poor bravo Nkasa

  • @EdwardAbu-s7s
    @EdwardAbu-s7s 7 часов назад +3

    Zoona ndibwino kumamuyamikadi munthu alimoyo ❤❤❤

  • @JussabRobert
    @JussabRobert 5 часов назад +1

    Mkasi is the best artist coz iyeyo sawona mbali, palipose amapezeka akfunika 🎉

  • @CentTiger
    @CentTiger 8 часов назад +3

    Zina kambu Zina lekuu, izii ndizoonadii Acheya tiziwayamikadii, his father of democracy in Malawi!!

  • @DencoMtepuka
    @DencoMtepuka 8 часов назад +1

    That's the way to go legendary nkasa

  • @QueenWahera
    @QueenWahera 18 часов назад +3

    Mkasa ndalama zidzakuchotsetsa Mano🤣🤣🤣🤣

  • @KhadijaMsosa-d7z
    @KhadijaMsosa-d7z 16 часов назад +4

    Hahaha osati ampatsa galimoto ija😂

  • @AsitalaSitaziyo
    @AsitalaSitaziyo 9 часов назад

    Ndibwino munthu akamachitazabwino kumayamika sikutimukayamikira ndiyekuti mwanyozeka ai here so siumunthu so.❤

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 19 часов назад +3

    Ndi chfukwa maiko amamanga zipatala zamisala anthu ngt Nkasa adzipita kumeneko

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 2 часа назад

    I respect him Malawi was better when he was a president. Kunalibe kusankhana mitundu .

  • @MikeChimwalaa-qd4vr
    @MikeChimwalaa-qd4vr 8 часов назад

    😅😅. I respect nkasa,, especially when he keep his hair (afro😅😅😅😅,, u already known he's mose waleloo basii...

  • @FrankSubili-fv2sf
    @FrankSubili-fv2sf 3 часа назад

    Galimoto yake munayenera kumupasa munthuyi Atcheya palibe kanthu padusa nthawi yaitali lonjezo lilipobe

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 5 часов назад

    Atcheya boma❤❤ulemu wanu

  • @IdrisaJetu
    @IdrisaJetu 8 часов назад

    Uyuyu liliki ya chakwera anawasungira kare😂😂

  • @Momweekly
    @Momweekly 7 часов назад

    Antcheya was the best out all presidents in malawi

  • @mynafavourchapalani5741
    @mynafavourchapalani5741 8 часов назад

    Zooona nkasa a tcheya is a peaceful maker

  • @AmiduYassin-v2e
    @AmiduYassin-v2e 36 минут назад

    Kkkkkkkk km mkassa ay umakwana kkkkk

  • @YassimineRasheed
    @YassimineRasheed 7 часов назад

    Siyeni dzanu chimene amafuna sanachipeze mmmm Koma nkasa ayi

  • @CedricSpy
    @CedricSpy 19 часов назад +2

    Tikamati Mkasa mutu wake sugwira inu mumaona ngati timamuda

  • @Madachibwe-y4l
    @Madachibwe-y4l 6 часов назад

    Zandale ukhoza kungopusa nazo ndiwe osatsatira anthuwa ndi amodzi😂

  • @edenngoma8214
    @edenngoma8214 6 часов назад +1

    Mkasa ndishasha ,kalipo kamene wapatsidwa ameneyi

    • @JosephineLongweSelolwane
      @JosephineLongweSelolwane 4 часа назад

      That's true....A Malawi timakonda kuyamikira munthu wokufa oti samva kuyamikirako..Mkasa akutiphunzitsa kuyamikira munthu ali moyo kuti mwini wakeyo amve.

  • @getrudemsemwe8346
    @getrudemsemwe8346 10 часов назад

    Atcheya is a great leader munthu okonda dziko lake

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs 18 часов назад +2

    Kd nkasayi chimene amachifuna amachiziwa

  • @emmanuelnamangwiyo9350
    @emmanuelnamangwiyo9350 6 часов назад

    Soldier 1, Nkasa 2 , Namadingo 3

  • @PatrickNampota
    @PatrickNampota 6 часов назад

    Ana achepa uyu amatha kkkkk

  • @macleanldzimkambani7773
    @macleanldzimkambani7773 6 часов назад

    Koma ndaseka 😂😂😂 akuti "Kodi anduna azamagetsi alipo apa?, ndikamachokapa magetsi akhale ayaka pano". No wonder kwawo amkafuna kupite 66kv line to supply domestic customers😂

  • @MayamikoJeke-d5m
    @MayamikoJeke-d5m 39 минут назад

    Ulamuliro wa a Chair unali bwino kwambiri

  • @GracieRejoice
    @GracieRejoice 16 часов назад +1

    Ndi Mkasa yekha yemwe amadziwa kut kuimba ndi business basi sizifunika kumutengera uyu utha kuchimwa mmayankhulidwe😂😂

  • @makomberodgers3791
    @makomberodgers3791 19 часов назад +2

    Akufuna amugaiyile Ina yake mkasa ndi mbuzi kwabasi

  • @jameschibisa1433
    @jameschibisa1433 11 часов назад

    🎉 nanunso ankasa tikuyamikireni chifukwa choti mwadziwa ubwino wa Dr bakili muluzi nyimbo ili bwino ndithu....

  • @TapiwaBlack
    @TapiwaBlack 16 часов назад +2

    Wasowa kopita mkasa

  • @kondwaninampeya5780
    @kondwaninampeya5780 13 часов назад +2

    Maluzi musiye nzako

  • @erickhowoya9894
    @erickhowoya9894 3 часа назад

    Nice song with good mesaage but producer didn't do a good job sikumveka bwino nyimbo.

  • @AbdullRasheedThomas
    @AbdullRasheedThomas 5 часов назад

    Ulemu wanu boss inu nde mukukamba zoona

  • @Ntatesibusisombata
    @Ntatesibusisombata 6 часов назад

    If you always you take things in personally you will never be a politician ndale ndikanyama kowopya sikawoneka chisawawa

  • @Angel-dt6oe
    @Angel-dt6oe 3 часа назад

    Akufuna ndalama ya January uyo not kuimba kwabwino palibeso nyimbo apa

  • @EsayaMagaloni
    @EsayaMagaloni 2 часа назад

    Zili bwino iyi ndiye dimokalas ufulu

  • @PatrickJemus-q8w
    @PatrickJemus-q8w 6 часов назад

    😂😂koma nkaza

  • @AbudullHamuza
    @AbudullHamuza 8 часов назад

    Kkkkkkk koma kumayamikila❤

  • @ChrispoGawani
    @ChrispoGawani 9 часов назад

    Awa ndiachisilu kwabasi chifuna iye sachidziwa zokuba basi nkasa Mutu wake sugwira antaaaa ndinasiya kumukonda ine uyu sapanganika

  • @JazakaPhiri-j3h
    @JazakaPhiri-j3h 18 часов назад +1

    Munthu opepela uyu komanso zinakakhala kuti ndiku mpingo ndiye kuti tinakati mabukhu amusokoneza mutu ndiye poti kuzoimbazi ndiye kuti mwina chamba akumachita kumwa osati kusuta

  • @WysonSadiki
    @WysonSadiki Час назад

    Kuimba kapena kuyankhura iwe Nkasa?

  • @HendersonLapken
    @HendersonLapken 9 часов назад +1

    Ali ndinzeru bwanawa

  • @MMK-p3y
    @MMK-p3y 8 часов назад

    Uyu ndi katswiri. Amatha kupanga compose nyimbo eeeh

  • @Virdimir
    @Virdimir 5 часов назад

    Kkkkkk mkasa sazatheka guyz kkkk

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 10 часов назад

    Maluzi adakoza apapa ndie kuti mdalama za chikangawa wadya zatha pano akufuna atcheya apise muthumba

  • @EmmanuelChakalamba
    @EmmanuelChakalamba 7 часов назад

    Nkasa usamatiyese ifeamalawi ngatiopusa umangoyimba zamavutoako cholinga akupatsendalama ndiweopusa

  • @LuciusLungu
    @LuciusLungu 10 часов назад

    Iyayi onsewa ndi manyazi a boma ndilomweli, akudziwa kuti mcp sizikuyenda.. Wayiwonela patali.

  • @GetrudeMsusen
    @GetrudeMsusen 6 часов назад

    😂😂😂😂kma kumeneko

  • @ClementeJorje
    @ClementeJorje 19 часов назад +2

    Ndiwopenga nkasa

  • @LesterNtolilo
    @LesterNtolilo 6 часов назад

    Komatu nkhaniyo ndiyoona achair anayetsetsa si manyaka enawa

  • @JosephSamuel-f6f
    @JosephSamuel-f6f 19 часов назад +1

    Nkasa2 amangofna ndalama basi koma mutu sugwira bwno

  • @AmakaBAbie
    @AmakaBAbie 7 часов назад

    Chair ❤❤❤❤

  • @WilliamsChifundo
    @WilliamsChifundo 8 часов назад

    Nkasa akunena zoona ulemu wanu a chair

  • @jamestimothy1537
    @jamestimothy1537 10 часов назад

    Vuto linali lonamizidwa galimoto koma leadership analin1 even mkasayo akudziwa

  • @LuciusManyambaJunior
    @LuciusManyambaJunior 17 часов назад +1

    Ndidolo❤

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 4 часа назад

    Zamphavu 🔥

  • @IgnatiousFote
    @IgnatiousFote 18 часов назад +2

    mkasa mutu wake sumagwla ai chitsilu chenicheni

    • @PiliraniBanda-c6z
      @PiliraniBanda-c6z 8 часов назад

      Ndiwe galu kwabasi

    • @AmakaBAbie
      @AmakaBAbie 7 часов назад

      ​@@PiliraniBanda-c6zGaru wake wachitenenensotu😂😂😂😂

  • @ZahirMatiya
    @ZahirMatiya 3 часа назад

    Wosokonesa uyu mkasa

  • @MphatsoLuka-gn3lr
    @MphatsoLuka-gn3lr 10 часов назад

    Chisilu chipagidwa promesi chimadikila ochejejela amapagazake

  • @KelvinMatiki-r2m
    @KelvinMatiki-r2m 9 часов назад

    Apa mpomwe ndadziwa kuti kumalawi kuli maluzi eeeee km tiyaluka

  • @LilNestaTambo
    @LilNestaTambo 8 часов назад

    Achitsiru a mkasa komwe kuli ndalama ali komko

  • @SiliAmanu
    @SiliAmanu Час назад

    Mikasa ndiopenga

  • @seyoDavid
    @seyoDavid 17 часов назад +1

    😂😂😂😂😂

  • @HerlbertKaalis
    @HerlbertKaalis 8 часов назад

    Zoona zake akudziwa yekha

  • @AdamMakala
    @AdamMakala 17 часов назад +1

    Kukhumba ndalama😂😂😂😂nkasa

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 7 часов назад

    Zoonadi bingu anali pangolini

  • @ernestobenissonizocomabebe8113
    @ernestobenissonizocomabebe8113 4 часа назад

    Zona

  • @johnyassin-je8rv
    @johnyassin-je8rv 18 часов назад +1

    wachamba mkasa

  • @FelixHenry-l6o
    @FelixHenry-l6o 16 часов назад

    He is foolish man zamaziwa chomwe amachitaa in Short ndithira kuwirii kwawoneka anapambaza makofi kudowa 😅😅😅

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 15 часов назад

    Nkasa akuhonga galimoto

  • @InnocentKanseu-u4j
    @InnocentKanseu-u4j 6 часов назад

    Akukumbusa galimoto ija amaneyo

  • @SanudiNdawala
    @SanudiNdawala 6 часов назад

    😂😂😂😂😂😂😂

  • @ZachariahMpacha
    @ZachariahMpacha 10 часов назад

    Yonse bho

  • @JulietKapata
    @JulietKapata 6 часов назад

    ❤❤❤

  • @AngellahKapimphi
    @AngellahKapimphi 19 часов назад +1

    Km guys chezan bwn

  • @AubreyMgundo
    @AubreyMgundo Час назад

    Ndadabwa!!

  • @BuzayaKanyenga
    @BuzayaKanyenga 9 часов назад

    😂😂😂😂

  • @CollinMkhonza
    @CollinMkhonza 19 часов назад

    Chisilu chamunthu....wangokula

  • @KwandaMthethwa-j3m
    @KwandaMthethwa-j3m 10 часов назад

    Mbambande mkasa

  • @TesiaMdoka
    @TesiaMdoka 18 часов назад

    Munthu saipa zonse bakilidi anali munthu

  • @raphaelmatias7194
    @raphaelmatias7194 17 часов назад

    Nkasa wasowa kolowela

  • @MussaAli-h4i
    @MussaAli-h4i 17 часов назад +1

    Kkkkkkk

  • @JacksonALICK-z4r
    @JacksonALICK-z4r 18 часов назад

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @Umalikandu
    @Umalikandu 14 часов назад

    Umakwana mkasa

  • @DicksonEvance-h6g
    @DicksonEvance-h6g 18 часов назад

    Power of soda

  • @BandaJames-e4f
    @BandaJames-e4f 17 часов назад

    Umakwana nkasa

  • @JimsonChisi
    @JimsonChisi 18 часов назад

    Miss

  • @LuwizaChika
    @LuwizaChika 18 часов назад +6

    🥰🥰🔥🔥🔥🔥🔥

  • @PatrickDalikeni
    @PatrickDalikeni 11 часов назад

    😢😢😢😂

  • @LastonMaere
    @LastonMaere 16 часов назад

    😅😅😅😅😅😅

  • @KachingweGolden-n3k
    @KachingweGolden-n3k 17 часов назад +1

    Nkasa😅😅😅

  • @giftmukona
    @giftmukona 19 часов назад +2

    Kwa omwe mukuonela mukunvela nyimboyi 2090 i was here before you and this is kind of music we were like to listening osat zanu mukunvela panozi

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 17 часов назад

      There was no such 2090 That was 1990 ok

    • @MathiasJoseph-xv1hj
      @MathiasJoseph-xv1hj 10 часов назад

      2009kapena2090?

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 7 часов назад

      @MathiasJoseph-xv1hj Were you there 2090? When was 2090?

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 6 часов назад

      @MathiasJoseph-xv1hj it's up to you you know it

    • @MonicaMkomanya
      @MonicaMkomanya 5 часов назад

      2090😂

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni 19 часов назад

    😂😂😂😂😂 uyu ndi wamisala bas kkkkkk

  • @ChristianMalingamoyo
    @ChristianMalingamoyo 18 часов назад

    Ngati Pali munthu wakuba ,waononga dziko ndi muluzi,ankasa mukuzionongera luso

    • @AngolaChinga
      @AngolaChinga 10 часов назад

      Aaaaaa iwe mapwala ako aaa bamboo ako wava galu iwe chitsilu cha mcp iwe bakili muludzi anaononga dziko kut chitsilu iwe pwala lako la bamboo ako nyini iwe

  • @MissyThobve
    @MissyThobve 9 часов назад

    Iii yokha sinandiwaze anamva ija inalibwino hevy

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe 6 часов назад

    ❤❤❤❤❤❤