We have many rich people in Malawi but are stingy and greed...Bravo Madam Mpinganjira for being generous! There is a blessing, if not blessings that await you: Luke 6:38 (KJV) Give, and it shall be given unto you; good measure, pressed down, and shaken together, and running over, shall men give into your bosom. For with the same measure that ye mete withal it shall be measured to you again.
I don't see no problem coming with cameras and the whole social media team man, that's an initiative that needs records, she need to report to her boss ain't nothing to do with fame, patha kuzafunika ma audits nthawi ina yake remember its an initiative she can't handle it on a personal level, a team is needed man, stop badmind, komanso ma camerawo ndofunika cuz enaso akaona pa social media kuti someone is doing this kinda good job nao atha kupangidwa motivated nkuyilowaso nawo kukathandiza wina wake pena pake, zinthuzi zimachitika kwambiriso ku maiko aanzanthu koma sitimayankhula koma poti wapanga ndi mmalawi eeeeee😅 anyway I ain't got no prob with the woman who rejected the offer, I ain't got no problem with Triephornia, I ain't got no prob with you either, the problem I have right now is that am out of weed😢
1) Mpinganjira akukanika kupereka ngongole kwa ma contractors. 2)Koma mkazi wake akugawa ndalama kwa anthu. 👆Izi ndizidabwitsa. Ndalamazo akupangira ma rituals. Osalandira ndalama za anthu ngati Tri-hule
We are witnessing politicians dishing out Malawi Kwacha 2000 notes and their bootlickers are busy enlarging such as works of generosity. The Mpinganjira family are what they are taught by their religious leaders. Ambuye akudalitseni Mayi Mpinganjira...you have walked the talk...and not talked the walk!
Komano mayi uja chifukwa chimene adakanira akuchidziwa ekha. Tisamaweruze ena please. Tivomereze kut tili mu Nthawi ya Ma Camera. Tikanakhala mu 90s kunalibe kujambula chifukwa ma camera kunalibe. Technology is advanced.
Spina Bifida and Hydrocephalus. I covered this story last year at Blantyre Sports Club when they were celebrating World Day. She can talk to Blessings Chapweteka, Executive Director of Child Help, they are helping children born with Spina Bifida and Hydrocephalus.
Kaya ndi umbuli kapena ai zilibe ntchito, mai anakana ndalamawo ndi ufulu ndi maganizo awo ndipo sanalakwire munthu wina aliyense ndi mmene anaonera. Palibe chifukwa chowanyozera asiyeni chisankho cholandira kapena kukana chinali chao
Muli anthu ambiri Ku mwanza kwawo akuzizika kupeza ndalama za businesses osathandiza Bwanji? Okalamba aku mwanza osowa chithandizo alipo ochuluka koopya Bwanji sayenda Ndi banja lake lonse kuti Taiwanese chikondi pamenepa Pali mafunso ochuluka Kwa aMalawi aku mwanza kwawo
Mmene ndaonera mayiwa ndzot akana ndalamayo mchmbulimbuli ndthi even inuyo mukuona...munthu amaliplilidwa ndlama nd anthu ena more than k500000 Ku xool ot si achbale ake kwa 4 years or more than ndye k500000 nkachan? Osamaganiza mozizila wina akamapanga chnachake ayi don't blame her plz
Ndipo mayi uyu wakana ndalama uyu ndi wa mzeru kwambili ndipo God bless that mama ❤❤ wothandiza sayenda ndi camera 📷
Mmmmm inu do you think God can come to you in person
Zako izo koma zomwe wapanga mayi uyu ndi zofunikila kwambili because helper don't take photos that is not helping but lough on you
'ndipo 😂😂
Ndipo live
Mai Mpinganjira aziganizireso okha fukwa munthu akugulitsa tomato kukana za ulele iwowa akanangowagula tomato yense pamtengo wabwino ndekuti mayiwa akanalandira ndalamayi momasuka kunena zoona zaulele sizimapindula sikuti awapatsaotu apindula nazoyi thukuta LA azako limavuta kulipindulira
@@shinyrobert2003 Nzeru💯🤜🤛
Nde akanagula tomato akanatani naye. Tomato ali naye kale mu Ekhaya.
Eya ndizona@@msatisi.reangfordphiri
Chilipo chomwe anaona maiwo pekana ndalama 😮😅
Mai wazelu kwambili Wachita bwino kukana🎉😂😂
Anthu olemerawa akuopsa masiku ano. Palibe ndalama yo dza mwaulere. Big up mama kunsika wa mbulumbuzi
Don't take chances for poor people..... to me she did a good job n she teach them a good reason and I appreciate
God bless and protect the poor lady ❤
That's true
God will never come to you in person
Mwaiona anabwerera kumagunabe ndalamazo let's change our mindset please za camerazo mulungu ndiye akudziwa
Uli ndi umboni kuti anabwerera kuti akalandire? Mai mpinganjirawo analankhula chifukwa Cha manyazi chabe@@josephmsyali
Zachifundo amati dzanja lamanzere lisadziwe. I like the woman rejected to receive unknown money
Amen
Ndalama zobwela chonch pena zimaopsa kumene ine ndkuwavesesq😂😂
Kwambili 😂😂😂
We have many rich people in Malawi but are stingy and greed...Bravo Madam Mpinganjira for being generous! There is a blessing, if not blessings that await you:
Luke 6:38 (KJV) Give, and it shall be given unto you; good measure, pressed down, and shaken together, and running over, shall men give into your bosom. For with the same measure that ye mete withal it shall be measured to you again.
You are right
Mai akutha diza awa. God bless her works and her charities 🙏🙏
Kuthandizako she is doing so good. But next time drop the cameras at home.
Mayi wa dxiko, okongola ndi mtima omwe ....a Malawi 🇲🇼 zikhulupiliro zomwe zomatisaukitsa...
Life is not easy sikadza kokha kaopa kulaula. Ndalama zimenezo ndisabwino or pang'ono
Pure evil 😂😂😈
Chopeleka chili pa wiri poyela kapena mwachisisi Koma kupeleka poyela kumalimbikisa ena kupeleka
Mai ujatu wakana ndalama zija ndi komwe zachikako,sizinachoke thumba loyenera,kumaganiza
She did good, why camera and whole social media when doing good charity?she is doing it for fame, too bad
I don't see no problem coming with cameras and the whole social media team man, that's an initiative that needs records, she need to report to her boss ain't nothing to do with fame, patha kuzafunika ma audits nthawi ina yake remember its an initiative she can't handle it on a personal level, a team is needed man, stop badmind, komanso ma camerawo ndofunika cuz enaso akaona pa social media kuti someone is doing this kinda good job nao atha kupangidwa motivated nkuyilowaso nawo kukathandiza wina wake pena pake, zinthuzi zimachitika kwambiriso ku maiko aanzanthu koma sitimayankhula koma poti wapanga ndi mmalawi eeeeee😅 anyway I ain't got no prob with the woman who rejected the offer, I ain't got no problem with Triephornia, I ain't got no prob with you either, the problem I have right now is that am out of weed😢
Zopanda ntchito izi anthu ena azafa osaukadoaiko akunja akamatithandiza amjabula bwanji 😊
Mukafuna kuthandidza km cameraman popo dzoputsa bas akutameni athu Kama dziwani tinadzipedza ndipo tidzadzitsiya bas
@@LouisShaffie-sp2xu The whole of this essay pa social media ngati pano and a mere comment for that matter who has got time to read the whole of this?
@Jimmy-e6r9x If you ain't got nuh time don't bother reading lad, go look for money. Happy new year. Am still out of weed tho🤦🏽♂️
1) Mpinganjira akukanika kupereka ngongole kwa ma contractors.
2)Koma mkazi wake akugawa ndalama kwa anthu.
👆Izi ndizidabwitsa. Ndalamazo akupangira ma rituals. Osalandira ndalama za anthu ngati Tri-hule
Musiyeni m, zimai abale wanena yekha kuti zomwe Ali nazo zimamukeanila abale athu enatu amadziwa mayu amulungu kukana suchifukwa
Nkhani izitha aaaaa,mayi uja zomwe ali nazo zimamukwana
Koma inu ananena mombeka bwino kuti zake zomwe amapeza zimamukwaniraa nde kaya nkhaniyi sikutha bwanji?ngati kuti iyeyo ndiwoyamba kukaniridwa ndalama aaaaaaaaaaa Malawi nkhani simawatheratu awaaaa
Samalani ndi zaulele muzagulitsa nazo sogolo lanu,zikoli likuyendesedwa ndi satana samalani abale
Ai sitiwadziwa ndi kanyama kanji mpinganjira😂😂😂
She did well,to the beginning of the year receiving money for free charge mmmm that's questionable.
😂😈
Ndimayi wabwino .. aliyense ali ndi ufulu okana kapena kulandila .
First comment today mayi mpinganjila amapanga bwino kwambiri azapaseko ines kuno 😂😂😂😂❤❤❤❤
Muzigwila nchito osamadalila zopasidwa
Anakati sapereka bwezi akuti ndiwowumira oro ali olemera...amayiwo kukana ndi ufulu wawo ndipo ndi pempho langa kuti Mayi Mpinganjira apitirize kuthandiza ovutika chifukwa alipo ambiri..
Ndalama za magazi😈😈😈😂😂😂
Mmm munth akufuna kuthandiz zoyankhula mbweee walakwitsaso. Asathandize anthu walakwitsaso iiii munthu ndi ovuta sure
Ntima wa zongopasidwa mmaiyu alibe🎉
😂 madalitso sasochera
We are witnessing politicians dishing out Malawi Kwacha 2000 notes and their bootlickers are busy enlarging such as works of generosity. The Mpinganjira family are what they are taught by their religious leaders. Ambuye akudalitseni Mayi Mpinganjira...you have walked the talk...and not talked the walk!
Yes is true you cant give someone on front of cameras thats risks people are watching
Kupeleka ndalama kapena thandizo lililonse kwa munthu sikolakwika coz mulungu amatiphunzitsa kuti tikhale anthua achifundo komano zimangofunika kupeleka thandizoli moyenera pokhala kuti mulungu anati chochita zanja LA mania lamanzele litsaziwe kotero kuti sikoyenera kuulura zomwe zanja lamanja lachita pakuti ichi sichipereka mdalitso etu so apapa sizinachitike bwino nkhani sanagwiritse ntchito njira zabwino popereka thandizoli coz kutenga anzathu awailesi zakanema komanso zoulutsa nkhani sizabwino popeleka thandizo coz zimaitanilanso chiopyeso kwa olandila thandizoli and zimaonesaso kuti ndikufuna kuzitchukisa kwa munthu woperekayo komanso kupereka chiopyeso kwa olandila etu.
Komano mayi uja chifukwa chimene adakanira akuchidziwa ekha. Tisamaweruze ena please. Tivomereze kut tili mu Nthawi ya Ma Camera. Tikanakhala mu 90s kunalibe kujambula chifukwa ma camera kunalibe. Technology is advanced.
Mai wa mzeru kwambiri
Ndpo Trifonia mulungu azmudalitsa amwene! Kumbali yake akuyesetsa kuthandiza anthuu🎉 receive ur flowers mamie
Azimudalisadi ndiochepa anthu olemela omwe amathandiza anthu
Aaaaaa zikhulupiliro vuto lake azimai inu pali dzuwapa kukana zosezo
Mrs mphinganjira kuli ana ku queens amene Ali ndi nthenda imene amakula mitu akufnika chithandizo,za operation,mwina mutathandizilako kumeko ZIkomo
Spina Bifida and Hydrocephalus. I covered this story last year at Blantyre Sports Club when they were celebrating World Day. She can talk to Blessings Chapweteka, Executive Director of Child Help, they are helping children born with Spina Bifida and Hydrocephalus.
It's part of life kukana koma eeee mwai wina ukat ukufikire kkkkk
No easy money around the world given to someone without the benefit from the giver.There is something behind
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Koma ine mwayi umenewo kungondigwera ndingathokoze kumwamba eeeee way things are hard😢😢
Mayi uyu kukana sanalakwitse ayi.
Thandizo sitilenge ayi chomaika pa camera ndi chani ngati mwapereka zeni zeni
Nde adathamanganso anvekele ndipatseni😂😂
Madam mpinganjira bweran kwaineyo mami ,ndikusowa ya business ine,mwana wanu wa fdh
Mmmmm poverty will always give us limits 😂😂
The way people of Malawi r suffering eshhh.
This woman has disgraced her blessing indeed
Pali zinthu zina umayamba kuchita mulungu akakuyendela zitha kutheka kuti momwe anali ku gine mo amapanga zinthu zosayendela nde kupeleka ndalama kwa anthu kutha kukhala njila imodzi yoti mulungu awakhululukile komaso pali anthu ena otembeleledwa mwina maiwo anatembeleledwa
Inu musiyeni mai uyo ngati anakana musiyeni Vuto kuno kumalawi kuriusataniki ndeno anthu ena akuopa kumarandira ndarama akuopa.kufa ngati mene anafera grece chinga iya masataniki inu mukufuna magazi
Mai mpinganjira mulungu akudalitseni nanenso mundiyendere kuno kulikoma
Poyamba tidziwe komwe Amayi okana ndalama yu kwao ndi kutiko. Pali dera lomwe Mzimayi amamulowo kuti akwatiwe ndiye pamakhala Malamulo omwe,amapatsidwa. Ndi kuganiza Amayiwa adaopa gulu lomwe amaliona loperekeza kuti, akayankha chiyani kunyumba komaso Mbiri yoti wachifundo akugawa Mpamba, adali asanayimvepo. Dziwani Mzimayi akaweruka kogulitsa malonda, watopa, sakhalaso ndi nthawi yomvera wailesi kapena kuonera TV, amathamanga kugwira ntchito zina pakhomo. Wotereyu, mmawa wake kukangolandira mulendo pa bench pake, kwinaku ma Camera, kumapatsidwa ndalama, mchifukwa mantha adamugwira.Mbiri zathu a Malawi nzakuti, timayika maganizo a zikhulupiriro kamba kosadziwa, galimoto yofufuza network from MACRA paja wanthu amkayithawa mkumati yopopa magazi, mmadera mu, kkkk!!! Ndiye osadabwa nazo, mindset development tikadali kutali chifukwa cha illiterace kwathu kuno tikadali nayo yaikulu ndipo Boma likanali ndi chintchito chambiri yoti athane nayo. Patsogolo zidzakhala zikondwerero tikalandira Alendo mwadzidzidzi ndi thandizo.
Salaam
But otherwise the bible tells us kuti zomwe wapanga nkono wa manja wamazere usadziwe why cameras kulipo akufuna akaone? 😢😢
Mwati siusokera
Munthu opeleka zinthu in front of cameras samandikala .
Chuma chimakoma kudya NDI abale Ako.
Koma ngati achibale sukuwagawira ndiye sizili bwino
Kk ari Bwino mzimayi, m'daritso siwake wanenawanena
Popeleka chithandizo sitiyenera kupeleka thandizo.
Eeeeee good woman inuyo mmantha amai
Kuchoka pa mai wakana uja palibenso atakane anakana coz samayembekezera kuti kupempha Kuja zitheka pompo anali ndi mantha chabe
Aliyese ali ndi ufulu olandira kapena kukana mphatso iliyonse.
Mai Mpinganjira pititiridzani kuthandidza anthu ochepekedwawo
Kudalila zopasidwa ngakhale boma lanu achewa likudilila kupempha
Gawani ndithu mama ifeso kuno mutipeze
Mai uyu musiyen apume
Ndiufulu wake kulandira kapena kukAna
Ayi msiyeni munthu wokana ndalama mayiwu sanalakwe ndipo mayiwu amangoziyalusa motere Ndi wachikhalidwe chachimalawi
Faifi Handede Sauzande
Fafi handede amwene kuikana koma ndasekatu
Mpaka police kokathandiza azimayiwa anyway
Ine ndikuona ngati mayi uyu wapangaso regret kut ndikanadziwa ndikanatenga
Easily come, easily gone
Ine muwauze andinthandize
Eeeee ine nde ndlibe chonena km mzimayi uja sndkumuona nd vto ine
Kodi mai mpinganjila azibale awo onse anawapasapo ndalama?
Kaya ndi umbuli kapena ai zilibe ntchito, mai anakana ndalamawo ndi ufulu ndi maganizo awo ndipo sanalakwire munthu wina aliyense ndi mmene anaonera. Palibe chifukwa chowanyozera asiyeni chisankho cholandira kapena kukana chinali chao
Abweretse kwaine ,eish kukana ndalama
Triphonia sanalakwe
Mpaka documentary nkhani yomwe ija? Eh eh
Ambiri ali ndi nsanje alaona munthu alupeza bwino koma iwowo ndi nsima yomwe sanyambe ampasapo munthu koma kulongolora kwake.
Siyani Nsanje zikuphani mwamva?
Mwasowa zochita eti?
Muli anthu ambiri Ku mwanza kwawo akuzizika kupeza ndalama za businesses osathandiza Bwanji? Okalamba aku mwanza osowa chithandizo alipo ochuluka koopya Bwanji sayenda Ndi banja lake lonse kuti Taiwanese chikondi pamenepa Pali mafunso ochuluka Kwa aMalawi aku mwanza kwawo
Sometimes we don't how opportunities comes in life and this woman is very ignorant about the development
Mwaiwala kunene kuti mayi uyu anapempha yekha ndipo atapatsidwa anakanso yekha. Please report properly
Koma uphawi ukuphani mayiwa sanalakwe samafuna zopasidwa ndichifukwa amapanga geni
Mwanena zoonadi
Mai mpinganjilao abwele kuno azatigaile Ife kuno tikusowa mpamba okwanila
Why not donate to people Who are living in the bushes,under bridge. Is enough wat she is getting from the benge lake osati strange money. Pickitup mom
❤
Tsoka la wina ndi mwayi wawina ndithu.
Pantudzu panu mayi chokanila ndalama chani???
TRIPHONIA BWERESA NDALAMAZO KUNO KU RUMPHI KASALASALA MARKET
Ukamathandizila Nja lamanja linalo lisaziwe usamapereke kuti uchuke ayi
Ndipo sangalote kut ineyo ndikuifuna koma
Anachita bwino, tsoka la wina ndi mwayi wa wina.
Mayi wa nzeru sakopeka ndi zongodusa ngati madzi amukwawa mayiyu ali ngati Nyanja maganizo ake ndi okhazikika
Mmene ndaonera mayiwa ndzot akana ndalamayo mchmbulimbuli ndthi even inuyo mukuona...munthu amaliplilidwa ndlama nd anthu ena more than k500000 Ku xool ot si achbale ake kwa 4 years or more than ndye k500000 nkachan? Osamaganiza mozizila wina akamapanga chnachake ayi don't blame her plz
Mayi wakana akufuna koma mantha
Opusa.mukupereka.kutauni.nanga.akumudzi.muwatani
AMALAWIAN MUSAMANGO LANDILA NDALAMA KWA ANTHU ANTHU AWA NDI WA SATANIKI SAMALANI
khan yokana ndalama ija mpaka yafika koseku kkk ai taaah
Ndi opemphera kwambiri mzimai ameneyu
Tiziona mtsogolomu
Tamabweretsani zinthu zomwe zili zapompo osamabweleza zinthu zomwe anzanu zinaponyedwa kale plz
ndiochokera ku Neno not mwanza
Mapelekedwe andalama owonetsera chonchi awawa anthu antha kuphetsana kunjaku kuli mavuto
Ndipo nde wandidabwitsa
Ndalama yopasidwa ndi yowopsa kwambili ambili amaliza moyo
Chimalora opanda mano
Andipatse ine amene sakuzifuna ndqlama
Mayi awa amakwana