I'm originated from Malawi my father was from Machinga yao tribe I'm in Zambia the truth must done the life of human being is important as a creature of God very sad Goo bless 🎉you sir 😭😭😭😭
What is the aim of this briefing? To bring evidence or chaos? Or campaigning for somebody?Bwerani poyera anamiwa. Politics behind bungwe lomenyera ufulu
Bwanji amalawi timafuna kumazungulila pankhani ya chilungamo, Akasambala ndi ose amundege aliyese amadziwa ku ndi a mcp anapha anthu amenewa nde chomazungulila ndichaniso apa.
Nonse amene mumati mumapanga kafukufufuku wa ngozi ya ndege ija mukonzekere kuzabweza ndalama zomwe munadyazo chifukwa mumapanga zopusa Kodi akanakhala kuti adaphedwa aja nda Ana Anu inuyo mukanaisaya chonchi nkhaniyi? Zopusa mudapangazo musamale nde emwe anakutumaniyo God is able wait until the end.
Robert Edward,,,,,, tikonzereni chizungu,,,( fighting from within and not from "without" sitimati from without but from outside,,,,,, according to the context. ,,,,,,, ndibwino kufunsa mafunso mchichewa
Namiwa has a party he is supporting. Mtambo was vocal because he supported Tonse Alliance. Trapenzi anali vocal chifukwa amasapota DPP nthawi ya PP. A Namiwa adzakhala chete utsogoleri ukadzasintha. CIDED ndi stepping stone yawo.
Zaziii??? Iwe ompusa kwambili ufune usafune chilungamo chidziwika we will support Mr Namiwa mpaka chilungamo chitadziwika anakafa bambo ako anakati zaziii! Usanditukwanitse galu iwe
Inuyo ndiamene mungatiuze choona nanga munathawiranji mu inquiry muja..Thats where your stupidity is,you missed and opportunity ndiye pano mukukhala ngati mzeru mulinazo pamene ndinu empty tin which only makes noise
Ndiwe chitsiru di mau ako iwe ndindani kuti ukakese anthu asamachule dzina la Chilima ndi pamene ubgadziwe kuti anali dolo amene uja komanso anthu sazasiya kuyankhula mpaka zitatuluka chomwe anafera
@@LinlyMathewe iwe mbuzi bwanji why are you taking it so personal...galu iwe kwambili ...go and cry your people kwanu it will do you better.....ndindale izi sitizitengela personal thats why politicians fight today tomorrow mkuzakhala mchipani chimozi ...abankha ngati inu mmazitengela kukhosi ngati manyi achiwala
Here you need to stop nonsense about!. How much you guys ready to spend because of someone who is died already. As you sitting there with all those surrounded you at the end of the day you need money. People are dying out there and no press briefing about them noooo men enough now really tired and exhausted. History is good to waist your time. Iiiiiiii you People please forgive me but I've done my side and no more hearing about chilima!.
Amalawi please let's support this guy, nkhondoyi siya Namiwa koma tonse💪
Koma Namiwayu ndi katundu, let's support this guy.
Yes 💯%Namiwa bravo bravo I think umapindadi Ku church kukafuna mayakho thank
Mr Namiwa ur our Pilar proceed it, and we really appreciate the job u doing
Ulemu wanu mr namiwa inuo simuika chigamba ayi kumeneko ndie kuyankhula❤❤❤❤
May God continue to bless and protect Namiwa.
Chilungamo sichimasowa namiwa ndi dolo no1 like him in malawi pori malawi timadana ndichilungamo timuda namiwa pa top
Namiwa ndiwe shasha kwambili ❤❤❤❤❤
Namiwa you are very sharp and brilliant
Khokhokho mawu amenewo 🎉🎉🎉🎉🎉
NAMIWA GOD BLESS YOU BIG .YOU SPEAK VERY NICE THAN CHIKANGAWA
Boma lazitsiru president chitsiru nduna zake zitsiru
Nàmwiwa short of support but he is brave ,,,more 🔥🔥🔥🔥🔥
Namiwa ndi dolo guys
Nduna ikakhale zikhale ngoma😂😂😂😂😂
God bless you ❤❤❤💥💥👌
Why must we accept documented lies and crimes like this and just move on tomorrow it will be you and me. Thank you Mr. Namiwa.
Mr Namiwa mumatiyimita ife a Malawi 🇲🇼 ❤❤❤❤❤
Malawi sikusowa anthu ophunzira ayi,koma likusowa anthu otchula tchimo ndi dzina lake.
Our pillar
Chakwera must step down he is useless
God has to protect you Mr namiwa
Uyu ndi Julius marema wakuno ku Malawi😂😂😂
Let's support him .A Malawi tinafatsa mombwambwana kwambiri
Ndipo nde sitingaone anzathu Mozambique aaah tinapusa
Pls mr. Namiwa timakunyadilani kwambiri , ndipo tikadakhala ndi anthu 10 kapena 20 ku Malawi ngati Namiwa bwezi kuli chilungamo.
Brilliant guy
I'm originated from Malawi my father was from Machinga yao tribe I'm in Zambia the truth must done the life of human being is important as a creature of God very sad Goo bless 🎉you sir 😭😭😭😭
Boma lopambana maina onse onyansa
Chakwera step down is not president for malawi : ndi mfiti chakwera uyo munthu osayamika
😂😂😂😂 achekwela ndi antchito athu komaso mphabvutu tangwabwereka
🔥🔥🔥🔥💪💪💪💪
Mwabwera chief
What is the aim of this briefing? To bring evidence or chaos? Or campaigning for somebody?Bwerani poyera anamiwa. Politics behind bungwe lomenyera ufulu
Awa ntchito yawo samayidziwa ayi
Nyau yalira
Kwanukuja mtambo uja amkataniko? Usatiophyeze
Katundu madzi mkudzatulukira tsopano well come Mr Namiwa
Watulutsa Joker kkkkkkkkkkkkk
Namwiwa katudwu weniweni
Achoke kumene
Ishaaa km uyu
Silvester Namiwa, and Samia Suleman athu amenewa amayima pachilungamo and atakhala kuti ndi azisogoleri ziko lingayende kwambili
Bwanji amalawi timafuna kumazungulila pankhani ya chilungamo,
Akasambala ndi ose amundege aliyese amadziwa ku ndi a mcp anapha anthu amenewa nde chomazungulila ndichaniso apa.
Namiwa tithandize pankhani yandege aziwike OMWE anapha chilima
Namiwa ndi katundu weniweni eeeeeeeee!
Powerful
Umu muli confidents
Chekwela must go is gosht
Chilungo muchiziwa inu atolankhazi chakwela anapha chilima ama muyankha zosaveka apa poti imfa simuyiziwa saulosi anafa ifa yopweteka
Nonse amene mumati mumapanga kafukufufuku wa ngozi ya ndege ija mukonzekere kuzabweza ndalama zomwe munadyazo chifukwa mumapanga zopusa Kodi akanakhala kuti adaphedwa aja nda Ana Anu inuyo mukanaisaya chonchi nkhaniyi? Zopusa mudapangazo musamale nde emwe anakutumaniyo God is able wait until the end.
Robert Edward,,,,,, tikonzereni chizungu,,,( fighting from within and not from "without" sitimati from without but from outside,,,,,, according to the context. ,,,,,,, ndibwino kufunsa mafunso mchichewa
My friend Robert, the English is alright... Ndipo nchothyakuka bwino.
That pistol was used it disappeared so to clear wonga..everything about that denge and what happened before is very peculiar.very strange 🤔
That's true
Pyeeeeeeeeeee😂😂😂😂😂😂😂....
Chikangawa group ituluse black box nkhani yatha
Adonawo serious yabwanji
Nzoyona. Zake. Basi
Mazeze mafunso amphamvu
Tiyen nawoni apulewo chilungamo chiziwike bas.
Ndipo Pharaoh ameneyu akufunika awone achule,mdima,madzi amagazi,imfa yaana oyamba kubadwa
Nzoona
Chakwera nd olephera
Sangawachose chifukwa anapha nawo chilima mix akuopa kuti azaululana ndiyeno akubakilana
Straight
Boma ndi lomweli la madrama
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥💪💪💪💪💪💪💪
Namiwa lncluding Anabel mtali manja
SKC💔💔
Dziko lapasi mphavu chaluka kwambili chikakhala chosangalatsa mulungu akanamanga Ekha athu amene anepanga chiwembu chilima thawi yama vote isanakwane mwazifundo zake yehova zitatelo sizingalakwike
Achoke kumene hiiya
Mulungu akudalitsen anamiwa
A Chakwera kumaposedwa ndi kamwana Ka Zaka 36 Traore kulamulira dziko zomvetsa Chisoni
Namiwa
Apanidwe achakwerawo anene bwino yemwe anawauza kuti ndege inafika ku mzuzu
Sangacotse munthu chifukwa a2 osewa akukhudzidwa ifa ya a2 9 include kasambala
A Namiwa ngati muti muphedwe Malawi waphedwa mwankhanza.
Hope big CDEDi
Namiwa has a party he is supporting. Mtambo was vocal because he supported Tonse Alliance. Trapenzi anali vocal chifukwa amasapota DPP nthawi ya PP. A Namiwa adzakhala chete utsogoleri ukadzasintha. CIDED ndi stepping stone yawo.
Azako akuyakhula chichewa iwe kuziva sukulu kwambili bwanj
Waiting for demos
Ukulamula ngati ndani? Poti unathawa enquiry kukapeleka umboni
Fuseck zako iwe ulibe mzeru kupusa sikwabwino pongoyakhula mosamvesera kuti utorepo mutu wakhani ,nuyakha zazeru chifulwa watolapo zazeru , ukuona ngat anthu adaphedwera muja amalawi tikhale chete?
Koma Nami Wawa ngat susitha zomwe ukupanga zo ukoza zikoli ndipo pitilizani ase iwe dolo
Chikangawa is nonsense president 🙄 😒 😑 😐
Tangotilusani black books ngati ite achikangawa
Mbuzi ya munthu namiwa ango panga mademo ku Lilongwe kuno
Inuo nzeru mulibe zomwe akukamba namiwa zi ndizoona zokhazokha
Utsogololeri olephela,okupha, muchoka basi
Komatu Anthu osewa akutchulidwawa ndiye mcp yo,,,zosatheka kuti chakwela achose anthu amenewa,,,koditu chakwela wangokhala ngati chikwangwani cha mcp koma amene akuyendetsa mcp ndi anthu ake amene atchulidwawa
Kunali achina mtambo anaima kuthandizira mcp kulowa m'boma anapatsa chibrend anagonja kunali ziiii awaso relo ngachilunga come tomorrow adzasowa awawa nmmmmmmm malawi
274 days left kuti chakwera ndi azake akupha aja akalowe ndende life prison
Mr nawiwa mumakwanat km
Namiwa uremu wako inzizi zikufunila choncho. Koma Mcp eeeeee yatiwonongera athu ambiri.komaso anakatisakabe kuti atiphe mtsogoreri nkukhara chakwera.koma koma iweyo siwe wamuyoya
Za ziiiii
Achitsilu inu tapitani uko,
Achikhala kuti munali bambo ako bwezi ukuva bwanji garu iwe
Zaziii??? Iwe ompusa kwambili ufune usafune chilungamo chidziwika we will support Mr Namiwa mpaka chilungamo chitadziwika anakafa bambo ako anakati zaziii! Usanditukwanitse galu iwe
Zotentha zili mkanudula mwakomo
Zaziii zili Kunyumba kwanu chitsiru iwe dziko ndi laling'ono zizatuluka mulungu simunrhu musathe mau
Iwe ndi kupedza ndi microphone yako iyo. Galu iwe.
Great namiwa patalike pafupike amangidwa,, mcp never win again.
Ziwanda zachuluka ku Malawi Satana anaponyedwa ansi kuchoka kumwamba uja bola akanamupheratu bwenzi chikondi chiliko ku dziko
Mbuzi iwe onse omwe wawatchurawo kunalibe.kuchikangawa
God bless you
Mbuzi yoyamba ndiiweyo kape iwe mxeew
Mbuzi yayikulu ndi iweyo Linda madzi aduse mulungu simunrhu zizatula ndithu
Ngat ukut kunalibe analiko ndamai ako?
Anthu ena mumamutenga kut Namiwa ndiozungulira mutu koma iye amapta pachilungamo
Munthuyuu amayakhula koma ntchito yake sioneka ma dem amalephera palibe chomwe amachita aaa
Kod madem atheka bwanji pamene anamachende azikwanje akumakhapa anthu
Inuyo ndiamene mungatiuze choona nanga munathawiranji mu inquiry muja..Thats where your stupidity is,you missed and opportunity ndiye pano mukukhala ngati mzeru mulinazo pamene ndinu empty tin which only makes noise
Ndipo akudziwa komwe aliko amenewa a mcp
Iwetu cadeti sunavoterepo m c p ndiye usamatinyase
Big cadet
Kuvotera MCP ngati kape
Akavotere Mcp ngati chitsiru chipani cha ma savechi kagwere
Inu nde anxeru ? Mmmm tamaonani zinaxi osamangotukwana
Olo atatenga zikwanje zonse zomwe anagulazija sitinga votele mcp😮😮😮😮
Mr president step down alephera kutilamulira Ife amalawi
mwayi anakupasani anamiwa musatizunguze
Ndipo inu
😂😂😂😂😂 mmene munayambila chilima chilima kamuzusenitu isaaa musatibhowe
Iweyo ukagona lero mawa sudzuka blv me
@tingamasi106 😂😂😂 i am protected by the blood of Jesus my guy ...back to sender on that
Ndiwe chitsiru di mau ako iwe ndindani kuti ukakese anthu asamachule dzina la Chilima ndi pamene ubgadziwe kuti anali dolo amene uja komanso anthu sazasiya kuyankhula mpaka zitatuluka chomwe anafera
@@LinlyMathewe iwe mbuzi bwanji why are you taking it so personal...galu iwe kwambili ...go and cry your people kwanu it will do you better.....ndindale izi sitizitengela personal thats why politicians fight today tomorrow mkuzakhala mchipani chimozi ...abankha ngati inu mmazitengela kukhosi ngati manyi achiwala
@wisdom20mkango49 galu wamkulu ndi iweyo koma bakha weniweni ndi iweyo who ateyi kuti ukandibene ine bakha kagwere mwana W njoka iwe
Here you need to stop nonsense about!. How much you guys ready to spend because of someone who is died already. As you sitting there with all those surrounded you at the end of the day you need money. People are dying out there and no press briefing about them noooo men enough now really tired and exhausted. History is good to waist your time. Iiiiiiii you People please forgive me but I've done my side and no more hearing about chilima!.
Nosence what about those useless faithleaders