kwanthawi yaitali nyimbo iyi yakhala ikufunidwa yonse dalitsikani tsopano.From daughter of zion

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 янв 2025

Комментарии • 287

  • @Flavoured-one
    @Flavoured-one 3 месяца назад +5

    This is my every day song, it gives me hope,, it draws me closer and closer to God

  • @maishamsiska7836
    @maishamsiska7836 23 дня назад

    Thank you Jesus for your love, and that you care so much for my life my family as a whole, keep caring 4 us,my Mum passed away when we were just kids ,at 12 i could still see that there is no hope anymore 4 growth or anything good, it was painful no heart can tell,t'was first to loose someone close, but God really cares and raises someone you never thought can do motherly love, an Angell my Dad at 45 he gave up all his youthfull and took care of us then last born was just few months old, and he did a great job God planted a heart of love and care now we r all grown up ,we just give glory to God alone, Inde Asamala

  • @AngellaKuntindiNkhoma
    @AngellaKuntindiNkhoma 9 месяцев назад +3

    To God's closeness this song brings me...
    Feeling like being in upper room all day...

  • @VioletMbale
    @VioletMbale 6 месяцев назад +4

    Ndinu dalitso pa moyo wanga because I always listen to your worship songs zimandilimbikitsa each and every time

  • @ChristopherJamesumali
    @ChristopherJamesumali Месяц назад +1

    Each and every time I listen to this song I feel like I'm already in heaven, so touching

  • @ot6fo
    @ot6fo 9 месяцев назад +4

    Mkwiyo wanu sukhalitsa koma chifundo chanu chamuyaya.. daily listening Yesu ndi thanthwe ndi pousila chimphepo all the way from USA Washington DC

  • @LucyEndmond
    @LucyEndmond 14 дней назад

    This has been my song, it gave me hope and. Comfort, mwayenera ambuye kulandila ulemu ndi matamando.❤❤

  • @AngellaMhango
    @AngellaMhango 15 дней назад +1

    Nyimbo imandipangitsa kulambira mulungu iyi olo oti sindimafuna kutero❤

  • @citimbaisah8262
    @citimbaisah8262 2 месяца назад +1

    None is like you Jehovah, you are worthy of everything 🤲🤲

  • @FrankSomba-lr4rq
    @FrankSomba-lr4rq 9 месяцев назад +17

    1000 times can watch this song

    • @Gabrielmahete6700
      @Gabrielmahete6700 7 месяцев назад +3

      And that is on daily basis....Ambuye atamandike ndithu

  • @AnnieBanda-zk8cj
    @AnnieBanda-zk8cj 9 месяцев назад +2

    Amen pa repeat ambuye azaze chikho chanu ndipo chisefuke

  • @MphatsoJalison
    @MphatsoJalison 9 месяцев назад +2

    Amen kulibe ofanana naye yesu , pitilizani kutipatsa nyimbo zotsitsimutsa mama

  • @molokabeckson8634
    @molokabeckson8634 3 месяца назад +2

    1 million times watching this worship.

  • @hascardjere
    @hascardjere 9 месяцев назад +1

    U always bless me with ur powerful & encouraging songs,may the Good Lord continue to bless ur talent in Jesus name.

  • @matlidaphilimon1719
    @matlidaphilimon1719 4 месяца назад +1

    So touching song, am blessed, indeed kulibe ofana nanu Yesu amen and ame

  • @HabrilMalaya
    @HabrilMalaya 2 месяца назад

    Amen kulibe ofanana nanu Ambuye mwasintha nyengo yanga Ambuye kunthenda yomwe imandivuta kuchoka 2021 pano ndine mufulu kumwamba kulemekezeke palibe ofanananu ndimulungu wazatheka bwanji inuyo

  • @meganabigail-ye7fw
    @meganabigail-ye7fw 9 месяцев назад +3

    Thank you so much my Dear sister nyimbo znu Zimakhala zonditsitsimutsa nthawi zosw

  • @TawinaLuwayo
    @TawinaLuwayo 4 месяца назад +1

    Mulungu azikudalitsani nthawizonse mum, munyimbozanu muliuthenga wamphamvu omwe umandisendezela kufupi ndi mulungu nthawizonse... Mulungu akusungeni mphaso yomwe mulunguanaika mwainu isazafe 🙏

  • @TiongecomfortMuwanga
    @TiongecomfortMuwanga 4 месяца назад +3

    Pamene simunyozela pemphelo laolungama losweka mtima,,,ndipo zambuye zikutivesa kukoma

  • @PromiseNamalawa
    @PromiseNamalawa 9 месяцев назад +1

    Lovely..... keep it up....mumatisimusa mum

  • @TinachedumisaniBanda
    @TinachedumisaniBanda Месяц назад

    Amen, oyera ndinu nokha Yesu palibe ofanananu

  • @FreddieKanyerere
    @FreddieKanyerere Месяц назад +2

    Nyimbo imandidalitsa kwambiri mulungu azikupatsani moyo wautali mama

  • @EnessMponda
    @EnessMponda 2 месяца назад

    Power Gob bless u timakukondan mulungu aptirize kukuza malire anu

  • @NjiyeziChirwa
    @NjiyeziChirwa 4 месяца назад +1

    Ooh 'YES' There's no one like u and will never be🙌🙌❤. To GOD be the GLORY 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌

  • @oscarmmanjamwada755
    @oscarmmanjamwada755 5 месяцев назад +2

    A song so soothing touching where the bone marrow and the flesh meet.Powerful words 💪💪💪💝💝💝

  • @chikondimagombo-p1e
    @chikondimagombo-p1e Месяц назад

    Misozi imangotuluka yokha when lm listening this song munandidalitsa nayo

  • @luciamwanjawala2153
    @luciamwanjawala2153 9 месяцев назад +1

    You can produce a good hit ndi Clara ngulube,,, I love you mama
    Simukhudwitsa

  • @IreenBanda-g5b
    @IreenBanda-g5b 9 месяцев назад +1

    Nice song , ihv blessed with this song

  • @getrudeminikwa9636
    @getrudeminikwa9636 9 месяцев назад +1

    Amen so powerful and kulibe wina ofanana Nanu yehova ndipo sadzapezekanso

  • @ruthchikavumbwa2236
    @ruthchikavumbwa2236 4 месяца назад +5

    This has been my song ,it gave me hope and comfort

  • @maxwelljuwaophiri
    @maxwelljuwaophiri 6 месяцев назад +2

    I like this song.
    God bless you worshiper

  • @oscarmmanjamwada755
    @oscarmmanjamwada755 5 месяцев назад +1

    Oyera ndinu nokha yesu kulibe afana nanu .❤❤❤

  • @ChimwemweBottomani-hc5ju
    @ChimwemweBottomani-hc5ju 9 месяцев назад +1

    Ooooh yes mwayenera yesu and kulibe ofanana nanu ....oyera olungama amene muli mulipo ndipo mudxakhala nthawi zonse ...mmmm ndikudalitsika nanu mayi mang'anda may God enlarge your territory

  • @MaureenDombola
    @MaureenDombola 5 месяцев назад +4

    Ooh yes, there is no one like You God

  • @Stephanie-gd1jt
    @Stephanie-gd1jt 3 месяца назад +2

    Nyimbo iyi amasuntha moyo wanga👏

  • @MilliamChikwembani
    @MilliamChikwembani Месяц назад

    Mbali zano nde imakhala pa repeat pitilizani mama kutidalitsa. Ambuye akulitsebe luso lanu

  • @GnessBanda
    @GnessBanda 4 месяца назад

    Hallelujah,,💪palibe ofana naye ,,,nyimbo yolombikitsa kukhala chifupi ndi Mulungu.

  • @MercymariaMapiko
    @MercymariaMapiko 23 дня назад

    Ambuye yesu mwayenela ...pothawila panga panthawi ya msauso

  • @lydiajackson5942
    @lydiajackson5942 9 месяцев назад +2

    Amen 🙏 powerful ❤

  • @eddahmphoolahzulu3194
    @eddahmphoolahzulu3194 9 месяцев назад +1

    Wooow thanks a lot God bless you

  • @ChifundoKayuni
    @ChifundoKayuni 3 месяца назад

    Palibe ofanana nanu Yahwe am a living testimony...You have done alot God I salute

  • @MposaLucy
    @MposaLucy 4 месяца назад

    I'm blessed with this song, kulibe ofanana Nanu zoonad 😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @ChisomoKaoloka
    @ChisomoKaoloka 4 месяца назад

    Hmmm woman may the Lord increase you I'm so blessed to listen to this msg iv bn craving for it, to God be the glory

  • @DalinessMabaso
    @DalinessMabaso 2 месяца назад

    Nyimbo yopeleka ulemelero kumpando wake,Hallelujah

  • @Alinafe-o1u
    @Alinafe-o1u 5 месяцев назад

    Ulemu ndi matamando zikhale kwaiye sopano ndikunthawi zosatha Amen

  • @oscarmmanjamwada755
    @oscarmmanjamwada755 5 месяцев назад +1

    Dzina lili ndi mphamvu lokhazika zonse bata 💪💪💪💞💞💞

  • @ivynkalo3483
    @ivynkalo3483 4 месяца назад

    Powerful song it surely gives hope am blessed

  • @JosieShumba-n1t
    @JosieShumba-n1t 9 месяцев назад +1

    Ndipo we needed this song

  • @YamikaniKyson
    @YamikaniKyson Месяц назад

    Amen and amen kulibe ofanana nanu yesu

  • @elizabethmazengera5274
    @elizabethmazengera5274 9 месяцев назад +1

    Well done mama thanks for blessing us with beautiful songs

  • @GeraldVansneakMgala
    @GeraldVansneakMgala Месяц назад

    🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌 mukuleeeee Jehovah ine ndichepeeeeee 🙏🙏🙏

  • @hatredkavumba-o1j
    @hatredkavumba-o1j 5 месяцев назад

    Mulungu awonjezere luso Ili pa inu ndimatothoze kuchilitsidwa ndi utumiki wanu.❤

  • @mosesskajawo9351
    @mosesskajawo9351 4 месяца назад

    So touching 😭🤲❤️
    The sing of all seasons, mwayenera ambuye ❤❤❤❤

  • @RejoiceKamanga
    @RejoiceKamanga 6 месяцев назад

    🎉 you are blessed Mom 🙏. I likes your songs

  • @Josephinekalipo-hp4jf
    @Josephinekalipo-hp4jf 7 месяцев назад

    Kulibe ofana nanu Yehova .. This is so powerful!!

  • @duncanmailosi4786
    @duncanmailosi4786 8 месяцев назад

    Iyi nde timati nyimbo ya uzimu,I love songs of worshiping our Lord Jesus christ

  • @georgenkhoma6898
    @georgenkhoma6898 5 месяцев назад

    Tiyamike kumwamba potsegula chidzalo cha luso komaso luntha pa kapekedwe komanso kalalikidwe, pemphero ndi pembedzero zotere mmoyo wanu, tili nao umboni wa mdalitso wa utumiki wanu pa miyoyo yathu. Ambuye apitilize kukuchitirani chokoma natsanulira kudzodza kwake kochuluka muutumikiwu. Mwayenera Yesu!!

  • @TendaiMvula-g2n
    @TendaiMvula-g2n 7 месяцев назад

    Amen nyimbo zanu mama zimandifupikitsa chifupi ndi mulungu ❤

  • @NoriaSingini
    @NoriaSingini 8 месяцев назад

    Great worship.....my soul says yes to you Jesus Christ....It soothes my spirit

  • @DorisLupiya-wh9mi
    @DorisLupiya-wh9mi 9 месяцев назад

    Ndipo kwabasiiiii.ndinali mmodzi wa Iwo, oyifuna nyimbo iyiyi. "Mwayenera YESU". God bless you daughter of Zion. Much love❤❤❤

  • @Olivekapote
    @Olivekapote 5 месяцев назад

    Powerful song I can't stop listening to it ❤

  • @JaneThewe
    @JaneThewe 8 месяцев назад

    Powerful, l adore you Mama, indeed kulibe wofana ndi Yehova. Mulandire ulemu Yahwe

  • @Rasheeda-l3z
    @Rasheeda-l3z 4 месяца назад

    Amen kulibe ofanana nanu ambuye😢

  • @mercynina6288
    @mercynina6288 9 месяцев назад +2

    ulemelero ukhale kwa Atate. zikomo kwambiri mayi wanga kumvetsera kuchokera Germany.

  • @faithchanunkha5396
    @faithchanunkha5396 8 месяцев назад

    What a powerful worship!!! Kulibe ofanana nanu mulungu wathu..

  • @PriscillaBakili
    @PriscillaBakili 8 месяцев назад

    I praise Abbah father for this song I have been searching for this full song , indeed there is no one like God❤❤❤

  • @mwayikambiyayoutubekambiya3731
    @mwayikambiyayoutubekambiya3731 9 месяцев назад +1

    What a beautiful song

  • @Nyausiska
    @Nyausiska 3 месяца назад

    Nyimbo ZANU olo kumvera tsiku lonse ❤

  • @AngelMbewe-xh1iw
    @AngelMbewe-xh1iw 5 месяцев назад +2

    Indeed no one can compare to you jesus our lord

  • @oscarmmanjamwada755
    @oscarmmanjamwada755 5 месяцев назад

    Worshipping at its best . Godbless this daughter of Zion❤❤❤

  • @eunicechawinga8613
    @eunicechawinga8613 9 месяцев назад +1

    Powerful song, Amen

  • @LINNLYMBETA
    @LINNLYMBETA 6 месяцев назад

    OHOOOO YES MWAYENELA YAHWEH KULIBE WOFANANA NANU HALLELUJAH YOUR GREAT FATHER 🎉🎉🎉

  • @ShakespeareKanthiti
    @ShakespeareKanthiti 8 месяцев назад

    I love your songs my sis and hope to hear more worship songs

  • @SteveMdalajunior
    @SteveMdalajunior 9 месяцев назад +1

    Yes no one else like him❤

  • @wligomeka1
    @wligomeka1 7 месяцев назад

    Amen 🙏 nyimbo zanu zimandifupikisa chifupi ndimulungu

  • @maishamsiska7836
    @maishamsiska7836 23 дня назад

    Kulibedi Ofanana naye Yeso Okoma uyu opatsa mtendere weniweni wachikondi Chenicheni

  • @GraceChapola-ez3dx
    @GraceChapola-ez3dx 5 месяцев назад

    Kilibedi angafane nanu. Inu wosakwiya nsanga wodzala ndi chisomo. This is powerful

  • @thokozanibanda71
    @thokozanibanda71 9 месяцев назад +2

    I even request on TikTok eish l really need it
    Thank you mum

  • @LydiaZibamagombo
    @LydiaZibamagombo 3 месяца назад

    Inuyo mulungu azilemekezeka pa inu ,kuzoza kwa yehova kupitilire pa moyo wanu,nyimbo yokhuza iyi yozoza

  • @KennedyKanthumba
    @KennedyKanthumba 3 месяца назад

    The song is so powerful. 🔥🔥

  • @GloriaGunde-xo4rf
    @GloriaGunde-xo4rf 5 месяцев назад +2

    Indeed there is no one like our God.

  • @margrettukulani4730
    @margrettukulani4730 4 месяца назад

    been looking for this song 🥰

  • @candidakawerawera6971
    @candidakawerawera6971 9 месяцев назад

    Kulira kosatha kumulambira Yehovah... thank you very much Phalyce. You are a blessing!

  • @MalaniNkhoma
    @MalaniNkhoma 8 месяцев назад

    A very good song with well balanced voice as well as guitar

  • @AlinaChauluka
    @AlinaChauluka 9 месяцев назад

    Zoonadi palibe ndipo sazapezekanso ofanana ndi to yesu amen🙏🙏

  • @gilberthachisambabaila9956
    @gilberthachisambabaila9956 9 месяцев назад +1

    Thanks for song ❤

  • @eunicemtenthaonga2075
    @eunicemtenthaonga2075 5 месяцев назад

    I miss u Portia my Sister ulendo unanyamuka iwe ukuwawa zikuvuta kuiwala....seing u rapped in ur own bedsheets, carrying ur body to the mortuary living u in mortuary room zimangondionekerabe ngat ndikulota😢😢..seing my self shaking ur head and calling ur name thinking that ur just unconscious...trying opening ur eyes and mouth...all for nothing..just like that ur gone for good and three weeks yakwana chikusiiren kumanda kwawekha..mhu.life is so cruel😢😢😢😢

  • @daughterofzionphalycemalik1296
    @daughterofzionphalycemalik1296  9 месяцев назад +2

    Mwayenera yesu kulibe ofanana nanu

    • @oscarmmanjamwada755
      @oscarmmanjamwada755 5 месяцев назад

      He is worthy of our praise . There no one like him. He has the power of changing unchangeable ❤

  • @BridgetLuwanika-n6l
    @BridgetLuwanika-n6l 6 месяцев назад

    Amen this song is very powerful ccter ❤❤❤

  • @dalitsokays7596
    @dalitsokays7596 6 месяцев назад

    My praise and worship song every morning since I heard it❤

  • @JohnMama-u3n
    @JohnMama-u3n 8 месяцев назад

    Mamie ndili ku Capetown..mwayenera praise songs take me into deep holly spirit of God...wonderful touching song❤ndikubwera ku malwi..l want to meet you just to hug u .lets keep on praying abale.

  • @PeterTembo-ej6sz
    @PeterTembo-ej6sz 8 месяцев назад

    Mwayenela baba🙏🙏🙏🙏 Good track

  • @EnessMponda
    @EnessMponda 2 месяца назад

    Amen powerful worrshiper

  • @Madalitso-r6k
    @Madalitso-r6k 9 месяцев назад +1

    Yes kulibe ofanana nanu

  • @phillgwedera3755
    @phillgwedera3755 6 месяцев назад

    you are a great Worshiper. woman of God esh!!!

  • @LenneKatundu
    @LenneKatundu 9 месяцев назад +1

    sadzapezekaso Ngati yesu

  • @RichardNkhoma-d2f
    @RichardNkhoma-d2f 2 месяца назад

    Ndipo osati masewera nayisaka 100times ,we thank GOD now it's out

  • @marthabanda6937
    @marthabanda6937 6 месяцев назад

    No one is like you Lord, you are worthy to be praise. You are faithful let your name be lifted on higher

  • @RuthMtunga
    @RuthMtunga 9 месяцев назад

    Thanks mama for blessing us we really enjoyed it 🎉

  • @shanitahpiuschikaphonya
    @shanitahpiuschikaphonya 5 месяцев назад

    Mwayeneladi Jehovah ndipo mumatimeyela nkhondo 🙏🙏