Daughter of Zion-- song Kodi yesu asamala

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 27 янв 2025

Комментарии • 295

  • @AnnaMtonga
    @AnnaMtonga 9 месяцев назад +4

    Ambuye asamala aliye ofunta na fiti yonse kuti amuziwe mulungu ndi yesu

  • @TadalaChithope-yg9fo
    @TadalaChithope-yg9fo Год назад +5

    Zowonad yesu asamala l lost my dad 2014 eish moyo unali olimba koma yesu zowona amasamala 🙏🙏

  • @evetalikukuta1487
    @evetalikukuta1487 2 года назад +88

    When my Dad passed away in 2020 11th February....i used to ask "kodi yesu asamala"? Coz i was not ready to face reality that my dad has gone....but God has provided us with more wisdom to take care of each other...Ambuye asamala

  • @JosephChimwano-eu8sk
    @JosephChimwano-eu8sk Год назад +11

    Sometimes I ask my self "Kodi yesu asamala?" Looking at situation am passing through that all my agemate I used play when we were young they are are all rich and they stays in their own house

    • @JohnSelemani-me3sx
      @JohnSelemani-me3sx 9 месяцев назад

      When am reasoning gospel songs am blessed

    • @hellinamwimba9839
      @hellinamwimba9839 6 месяцев назад

      He cares for you. Have you ever asked yourself why God is keeping you alive while some whom you played with are dead?

    • @maishamsiska7836
      @maishamsiska7836 Месяц назад

      Thats gives alot of questions and we tend to ask ourselves maybe i have sinned a sin that cant be forgiven , but really God cares and he is serving you from alot that may have taken your life, have joy of the Lord as long as there are no altars speaking against your destiny it will pass you will enjoy peaceful worth from God, and kneel and cry with thanks giving, lets not give up zikayandikira zimawawa, and God will give longtivity to your joy in Jesus name

  • @thokopangani7854
    @thokopangani7854 Год назад +12

    Today she came at our church ( Life Giving Spirit Church) to pray and ended up singing for us , The first song was Thanthwe , my sister you are minister .. The moment you started singing I felt the presence of the Holy Ghost.

  • @lizzyhuyser2768
    @lizzyhuyser2768 Год назад +7

    100/ kusamala kwake yesu ❤❤❤❤🎉🎉ndine bone amunanga namwalila kunisila tiana tatichepele koma you can't belive pano yesu asamala abale 🤗

    • @lindanimbewe1118
      @lindanimbewe1118 Год назад

      Amen

    • @JeanChimbiya-ef1vc
      @JeanChimbiya-ef1vc 3 месяца назад

      Komaa nyengo iiiiiiii zikati zisause groly to god

    • @Sheila-sh1td
      @Sheila-sh1td 20 дней назад

      Bambo anga atamwalira ndimangoona ngati dziko Latha ..
      Koma mnamuona Mulungu akutitola mkulera ..lero timalera ena

    • @harrykhomz3372
      @harrykhomz3372 2 дня назад

      Amen

  • @MadalitsoEvanceMatemba-e4c
    @MadalitsoEvanceMatemba-e4c 24 дня назад +8

    Who's watching in 2025 let's gather here ❤

  • @FatnessThom
    @FatnessThom Месяц назад

    My favorite song ❤yesu asamala munyengo zonse tikudutsa with my family 😭😭😭

  • @EstherMchawa-q2l
    @EstherMchawa-q2l Месяц назад +3

    Ambuye ndiziwitsen kut mumasamala poyankha nyengo zomwe ndikudusamo Amen🙏

    • @FatnessThom
      @FatnessThom Месяц назад +1

      Same here ambuye andiyankhe tikudutsa mumzowawa😢😢

  • @harrykhomz3372
    @harrykhomz3372 2 дня назад

    My favorite song ..He has been there for me and for my family. Amasamaladi ndili nawo umboni...

  • @ritabani274
    @ritabani274 Год назад +6

    Ooooh Yesu amasamala mai anga anamwalila 1996 tinali ana 10 koma Yesu anatisamala amen

  • @festerchinula7806
    @festerchinula7806 Год назад +4

    Ndimakhala ndi funso limeneneri kodi yesu asamala pamene makolo anga onse anamwalira chaka chimodzi 2022. Misozi sikutha maso mwanga koma poti mulungu asamala.

  • @limbitsokamba6324
    @limbitsokamba6324 Месяц назад +1

    Inde Yesu asamala. Ngakhale nthawi zina timaiwala ubwino wake koma iyeyo amatisamalirabe🎉

  • @GrevazioAuspiciousJacob
    @GrevazioAuspiciousJacob 3 месяца назад +1

    Uku ndie kuimba uku 🔥🔥🔥❤️❤️

  • @HenryHenock-lz7wu
    @HenryHenock-lz7wu Год назад +2

    Yesu asamalad inalipo nthawi imene ndinali ndi mkuluwanga kuchipatala mpaka anamwalira ndikuona ...Ndinalira mosweka mtima mkumamufusa ambuye kut walorelanji 😭but mu zose yesu asamala

  • @mwebembezijonas
    @mwebembezijonas Год назад +4

    I love the song from Uganda 🇺🇬 🇺🇬

  • @idahmasanjala6329
    @idahmasanjala6329 Год назад +1

    Inde amasamala umboni wa moyo wanga ku dziko lachilendo with my child Koma ndinamuona mulungu akusitha nyengo zanga
    Nyimbo zanu women of God zimandipatsa chilimbikitso

  • @RebeccaMalunda
    @RebeccaMalunda Год назад +7

    Jesus 😢😢 thank you for everything 😢😢 im passing through alot but one thing i know is that you care for me alot

    • @RonelyPatricks
      @RonelyPatricks 15 дней назад

      Hello.. I hope you are doing great in Jesus' name

  • @MikeMerecah
    @MikeMerecah 2 месяца назад

    I ❤❤❤❤❤❤ this song so much and ndinaivera dairy may God bless u mum moyo wanga umasuthika Mulungu Amasamala tachoka kutali ndi moyowu.😊

  • @LeyahPhiri-sd9xj
    @LeyahPhiri-sd9xj Год назад +3

    The powerful worship song ever!❤️❤️❤️❤️

  • @marthamafunga6329
    @marthamafunga6329 Год назад +1

    Yesu amasamaladi🎉ndipo amawona nyengo iliyonse yomwe timadutsa

  • @SamiaManganda-gj3zh
    @SamiaManganda-gj3zh Год назад +1

    Komanso iyiyi ndi one. Mumatisuntha mama continue

  • @LizzieMalie
    @LizzieMalie 9 месяцев назад +1

    100% asamala.Mulungu ndizoona ndipo ndiokhulupilika kwambili❤ daughter of ziyoni.nyimbo iyi yamphamvu kwakukulu🎉🎉🎉

  • @DeliaChalela
    @DeliaChalela 4 месяца назад

    Yes asamala ndine mboni, I lost my mom when I was 8yrs then my dad wen I was 10 yrs nyengo zakhala zolimba koma aaaa yesu amasamala wakhala Thandizo zaka zonse za moyo wanga😢

  • @AlefaChomanika-oh8ds
    @AlefaChomanika-oh8ds 10 месяцев назад +1

    Zikomo chifukwa mumasamala ambuye😷😭😨🙏

  • @daughterofzionphalycemalik1296
    @daughterofzionphalycemalik1296  2 года назад +10

    Yesu akusamala nyengo zonseee

  • @MemoryyMunanga
    @MemoryyMunanga 3 месяца назад

    Am really thank God for your life....your songs brother they give me courage and hope....keep the fire burning 🔥🔥🔥

  • @victoriakamowa1116
    @victoriakamowa1116 Год назад +1

    Ambuye musamala...ndlibe mau

  • @RhodaKalumbi
    @RhodaKalumbi Год назад +1

    Nice song God bless you my sister

  • @LaitoneJefitala
    @LaitoneJefitala 8 месяцев назад +9

    Mulungu ndiwadongosolo anthu ena anawalengadi Kuti adzatumikile kudzera mkuimba ndimakumbukira imfa ya m'bale wanga amene tidaabadwa mapasa yemwe anafa ndimphenzi koma Mulungu amasamala ndizovuta kuiwara koma Yesu amasamala

  • @RoseNgwira-v8q
    @RoseNgwira-v8q 6 месяцев назад +3

    Jesus christ cares I have story about my life and whenever I think of it I really appreciate to you Lord !🕷

  • @KondwaniRichardNkhongoza
    @KondwaniRichardNkhongoza Месяц назад

    Ndizoona amasamala Ana ake ndipo alibe tsankho. Nyimboyi imandikumbutsa nyengo Ina imene ndinadutsamo koma mulungu anandisamalira.

  • @LeticiaMtema
    @LeticiaMtema 3 месяца назад

    Zoonádi yesu amasamala,ndamuona akukhala okhulupilika pamoyo wanga, inuso ambuye akusamaleni panyengo muliyo,Amen .

  • @emilyhulani8673
    @emilyhulani8673 Год назад +3

    I feel the presence of God with this song, I can't sleep well without to listening to this song. This song touches roots of my heart. Lord you always protect us I my trust is in you my miracle actor...❤❤

  • @mercynina6288
    @mercynina6288 Год назад +1

    Asubuh na usiku huu ndio wimbo wangu! Mungu ananitunza kila wakati

  • @TammahKhama
    @TammahKhama 2 месяца назад

    Mulungu thawi zonsedi asamala nyimbo iyi imandilimbikitsa pamene ndinali kudwala end pano nachila yes asamala amen

  • @MemoryZimba-tx5xp
    @MemoryZimba-tx5xp Год назад +1

    Kip on burning sis💪💪💪

  • @aliceshawa3677
    @aliceshawa3677 Год назад +2

    My mother loved this song. 😢😢

  • @PhiriHenderson-in9hs
    @PhiriHenderson-in9hs 2 месяца назад

    Based on true story yes ndimalimbikitsika ndi nyimbo iyi may almighty God bless you Daughter of Zion

  • @alinafesathawa-yr3gj
    @alinafesathawa-yr3gj Год назад +1

    God is faithful there times we feel God has left us but he's right there taking care.... Powerful song

  • @JeanChikwatula
    @JeanChikwatula Год назад

    Ndinali mu nyengi yowawa kwabasi Koma yesu ameneyu wandidutsitsa ❤

  • @cosmaskachitenji-o9n
    @cosmaskachitenji-o9n 3 месяца назад

    Nyimbo zimemene zikuthandizila kutsekula makomo anga aaaaa what a powerful song, your so blessed

  • @richardmalumba857
    @richardmalumba857 Год назад +6

    My greatest testimony. Yesu amasamala. We are coming from far. Only God knew where we will be.

  • @lizwikhanyile5091
    @lizwikhanyile5091 8 месяцев назад +1

    Yesu amasamaladi ....ndimakumbukira mamuna wanga atamwaliw pa ngozi kundisiya ndi mwana wakhanda koma mwa zisomo mwana wakula shes 3 years old now yesu amasamaladi... May God bless u sis

  • @MemoryMissi
    @MemoryMissi 4 месяца назад

    This song brings confide and hope in my heart and I really enjoy it ,Jesus is always there for me and you ❤

  • @georgenkhoma6898
    @georgenkhoma6898 6 месяцев назад +2

    Songs that speak to broken souls, spirits and minds! Yesu Asamala, another excellent piece Phalyce! more grace to you!

  • @malingamussah5934
    @malingamussah5934 Год назад +2

    There is power in this song nyimbo yomwe amaikonda sister wanga rest in peace my lovely sister

  • @oliviatbonongwe2544
    @oliviatbonongwe2544 Год назад +1

    I needed masamala dzinthu zikafika polimba ndi pamene wataya ciyembekezo.

  • @JestinaKunkuyu
    @JestinaKunkuyu Месяц назад

    Does Jesus care? Yes Jesus Cares, i love this song

  • @EmmanuelBanda-s2t
    @EmmanuelBanda-s2t 4 месяца назад

    May Almighty God bless you as you are doing his work in Jesus Christ Name

  • @christopherchilufya1954
    @christopherchilufya1954 Год назад +1

    Yes Jesus cares.Nice song indeed.thou I'm Bemba I can get the message.

  • @NdazionaKumcheza
    @NdazionaKumcheza 9 месяцев назад +3

    Yesu amasamala amene amasamalaso za yesuyo mulungu ndi chikondi

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq Год назад

    Nyimbo zainu Mama ndimwala mwala zedi ulemu wanu ndithu keep it up❤❤❤❤🛐

  • @RashidOsman-d8l
    @RashidOsman-d8l Месяц назад

    I remember my mom powerful song amen

  • @ElizabethMangani-e4w
    @ElizabethMangani-e4w Год назад +1

    I like this song almost every morning iplay this song

  • @wligomeka1
    @wligomeka1 Год назад

    Nice song ndipo kwambili kwake yesu amasamala amen

  • @eltonnankhwere3284
    @eltonnankhwere3284 Год назад

    Ineyo i had stress koma the moment istarted listening this song all the stress inapita Yes inde Yesu Asamala ndithu

  • @wligomeka1
    @wligomeka1 Год назад +1

    Ndipo nyimbo iyi imandipasa chimwemwe thawi zonse ndipo imandilimbikisa

  • @blessingsemulyn638
    @blessingsemulyn638 Год назад

    Nyimbo iyi imandipatsa chiyembekezo nthawi zonse ndaimvera. He really cares.

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson 6 месяцев назад +1

    Yesu asamala ndadusa mnyengo zovuta ine kuyamba ndili wachichepere bambo ondipeza samandifunira zabwino pamoyo wanga koma yesu asamala

  • @DocusChibwe
    @DocusChibwe 2 месяца назад

    Nyengo zikulimba ambuye 😭😭😭mukusamalabeeee??? 🗣️

  • @NancyZgambo
    @NancyZgambo 3 месяца назад

    RSA 🔥🔥. I love the song so touching 😍🤗

  • @MikeChikalema-f1n
    @MikeChikalema-f1n 2 месяца назад

    Zikomo kwambili ambuye coz munyengo zanga zonse mumasamala🙏

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq Год назад +1

    Wow!!!! ❤❤❤ Powerful powerful Mama athu mumatiimilira ndithu asamaladi nthawi zonse n Amen 🛐

  • @FagessWilson-jt9nb
    @FagessWilson-jt9nb Год назад

    Yes amasamalirad ,since I lost my husband 2012 akundisamala pamodzi ndiana😱😱😱🙏🙏🙏

  • @victoriakanyimbo5628
    @victoriakanyimbo5628 Месяц назад

    This questions comes with the situations you are passing,it really gives some questions but Jesus is there for us.

  • @TinenenjiWakudyanaye-ib3zs
    @TinenenjiWakudyanaye-ib3zs Год назад +1

    My best song ever!!! I cry over it!!!!!

  • @EishoeOppoz
    @EishoeOppoz Год назад +2

    Wen my sister passed away in 2022 August....I used to ask Kod yesu asamala😢😢continue to rest in peace maria sis

  • @RossanaMitha-tl9in
    @RossanaMitha-tl9in 4 месяца назад

    I really love this song,,❤

  • @hellinamwimba9839
    @hellinamwimba9839 6 месяцев назад

    My favourite worship artist ❤

  • @brightkampeza1430
    @brightkampeza1430 3 месяца назад

    My BEST Son Ever!

  • @VeronicaKhuleya-zh1if
    @VeronicaKhuleya-zh1if Год назад +1

    This is my favorite song,I can listen to it day and night.

  • @chiccahkatanga9359
    @chiccahkatanga9359 Год назад +3

    Nyimbo yotonthoza mtima

  • @phillipchiotcha3197
    @phillipchiotcha3197 Год назад +1

    Nyengo zomwe zowawisa ndikudusa panapo ndinyimbo yomwe ndimamvera and kuonera everyday

  • @EdnaSaidi-u2b
    @EdnaSaidi-u2b 22 дня назад

    Nthawi zina ndimazifunsa " kodi yesu asamala za mavuto anga" chifukwa cha mavuto koma yesu asamaladi ndipo chilichonse chimachitika ndi cholinga

  • @KondlyChindenga
    @KondlyChindenga Год назад +2

    God cares for us regardless of any situation

  • @DeborahBinamu-v9z
    @DeborahBinamu-v9z 19 дней назад

    Yesu asmala ndaonela ine aaaa yesu asamaladi 🙏🙏🙏🙏

  • @GraceKanyenge
    @GraceKanyenge 8 месяцев назад

    Ambuye osakhumudwitsaa kwa iye kulibe cholepheleka 🙏🙏🙏🙏

  • @FELICITYCHIRWA
    @FELICITYCHIRWA Год назад +1

    Yesu asamala nthawi zose AMEN

  • @AGRIHOLD
    @AGRIHOLD 6 месяцев назад

    i heard your song kwa neighbour till i searched you here, Beautiful mama

  • @chikondizimba9085
    @chikondizimba9085 Год назад +3

    There is anointing of God in your songs. Keep it up

  • @harrietkamwambeni-mv9ki
    @harrietkamwambeni-mv9ki Год назад +1

    Ngakhale mu nyengo ya cyclone ambuye atisamala👏👏👏

  • @NancyZgambo
    @NancyZgambo 3 месяца назад

    Ooh , Yes.!! Yesu asamala. ❤🤗

  • @mwayikambiyayoutubekambiya3731
    @mwayikambiyayoutubekambiya3731 Год назад +4

    Indeed Jesus cares for us day & night🙏🙏

  • @samueltkalima8317
    @samueltkalima8317 11 месяцев назад +1

    I enjoy listening to this song

  • @JaneNgulube-rm2ot
    @JaneNgulube-rm2ot Год назад +1

    Your songs heals me

  • @susankadulira4559
    @susankadulira4559 Год назад +1

    Indeed God cares what I am today it's all about God

  • @willielimited
    @willielimited 2 месяца назад

    Its only Jesus christ who take care of us indeed

  • @Martha1436
    @Martha1436 2 года назад +1

    Mwanditsitsimutsa. Yesu asamala no matter what? 🙏🏾🙌🏾

  • @clyviakalivea9188
    @clyviakalivea9188 2 года назад +2

    Ooh yes amama powerful songs 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @DorisNkwanda
    @DorisNkwanda 7 месяцев назад

    Amen. Jesus cares about my family , my life

  • @MaulidiFebbie
    @MaulidiFebbie Год назад +1

    We may think that God has forgotten us but he still cares indeed he cares love this song

  • @MartinChilomo-hz6cs
    @MartinChilomo-hz6cs 10 месяцев назад

    Ndine mboni, Yesu amasamala ndithu. Ndikukumbukila mu chaka chowawa Cha 2021 pomwe ndinadwala convid. Koma ndinaona Mulungu akundichilitsa. Yes Yesu asamala

  • @tamikazulu7285
    @tamikazulu7285 Год назад

    This used to be my mom favourite.... may her soul rest in peace 😢... i love this song becouse i know he really care about me..... he has been with me when i thought had no future 😢

  • @marthamandionga1919
    @marthamandionga1919 8 месяцев назад

    Inde Yesu asamala. Thank you Lord Jesus 🙏

  • @smartchiotcha2558
    @smartchiotcha2558 Год назад

    In every situation he is always by my side,,, i don't loose hope in good and difficulty situation. Mbuye asamala

  • @EsnartMajiya-t7y
    @EsnartMajiya-t7y 11 месяцев назад

    YEHOVA I know mukusamala za matenda anga 😭😭😭 May you take control Lord.
    thanks phalyce for this song it strengthen my heart

  • @MauChipande
    @MauChipande 9 месяцев назад

    Ijust love the performance today 😊 it was something else 😊 mudzibwerabwera mammie😊

  • @MacdonaldNamero
    @MacdonaldNamero 5 месяцев назад

    Khulupirirani Yehova Mulungu wathu ndi Yekhayo wacilungamo wolungama wacikondi wazisomo ndi wocidza indedi atsamala munyengo zonse

  • @estawilson9998
    @estawilson9998 Год назад +7

    Ndine mbon kut Yesu amasamala Amen amen kuyambira 2015 kuzafik 2020 mmmm moyo umawawa kwambir ndimagonera jolly jus ndiana anga ndasi limodzi kunyemana kkkk kma Yesu ameneyu zomwe anandichitira dziko silikumvetsa ,pano zakudya sinkhan azibale anga pano akudalira ine Hahaha Hahaha ,ngt mlipo ena mlindifunso ngt ili ayi ndingt Ambuye akuonekeren kut nanu mkhale ndiyankho Amen mdalitsike mama.