Pena ngat ndinene kuti the best songs pa nyimbo za king James phiri koma ndikakumbukikanso MUKUMANE NDI MOYO WANGA ,,,,,,eeeeeeee God bless you man of God nyimbo iliyonse yainu ndiyabwino
Nyimbo iyi ndinaiona pa TikTok anyamata ena ake atapanga ka clip koma zoti ndiya king James phiri sindimadziwa eeeeeeeeee chisomo cha king james chisefukile kwa ine in Jesus mighty name
Now listening for ten times mmene ndayipezela Ku RUclips ndikungopanga repeat eish wat a powerful song
Pena ngat ndinene kuti the best songs pa nyimbo za king James phiri koma ndikakumbukikanso MUKUMANE NDI MOYO WANGA ,,,,,,eeeeeeee God bless you man of God nyimbo iliyonse yainu ndiyabwino
Powerful song, Matthew 7 v 7 ugogode nditsegula, undiitane ndiyankha🔥🔥🔥🔥🙏🙏❤❤
My Mama's favorite artist. Every time I visit her she asks me to play King James. God bless Apostle
Massive. Congratulations King James.. what a powerful Song. Indeed no man shall pull me backwards, Forward ever no matter the challenges.
Awa ndi machine awa , anabwera kudzaimba pa Malawi , keep it up sir ,, following u from Gaza city peni peni pa BOMA
Amen Worshiper
Powerful song 🔥🔥🔥
Chipulumutso ndi wekhadi. Thank you apostle, tikudalitsika nanu. Mulungu apitilize kudzoza ndi mafuta a chikondwelelo chenicheni.
Really gospel music song Mulungu alemekezeke 🎉amapiano atichedwetsa
Chipulutso ndi wekha powerful song🎉🎉
Nyimbo iyi ndinaiona pa TikTok anyamata ena ake atapanga ka clip koma zoti ndiya king James phiri sindimadziwa eeeeeeeeee chisomo cha king james chisefukile kwa ine in Jesus mighty name
So touched with this song,well done,King
Once again congratulations brother dressing idzifana ndi uthenga ulimunyimbo mwavala bwino zosachititsa manyazi Ngati ma gospel artists enawa
I have been waiting for this❤ a powerful song
Been waiting for it, thank you so much, powerful song
Powerful Song 🔥🔥🔥🔥.... Same powerful anointing!
The song of the year end. God bless you Apostle King James for this song. CHIPULUMUTSO NDI Q
WEKHA
So powerful amen am blessed....my testimony song of 2024
Same wit me 2024 ws a very tough year ambuye ayankha chaka chikupita kumaoeto simungamvetse
🗣️🗣️🗣️ ngati ndikonguwa kuti enawoooooooo..... This song🔥🔥🔥🔥
Welcome back man of God,this is powerful
Indeed chipulumutso ndi wekha Ambuye ndiwabwino this is powerful encouragement words in this song
This is powerful song 🔥🔥🙏🏼❣️
What a powerful song!!!
Wow beautiful munasowatu atsogo mwaphulitsa bomba osati chibwana🙏
The gospel song we have been waiting for 😊
Powerful song🔥🔥🔥🔥
Chipulumutso ndi wekha ... that's great brother I feel like ndilikumwamba kale with Tate Abraham,Elijah,Moses and many more......see more
I was waiting for this song❤
Anointed music!!! Spirit filled
Totally in love with the song, God is always good
This is powerful. Chipulumutso ndi wekha
The Best song 2024 ma award mwapanga changu
❤❤❤❤❤ Big up my broh
A master piece 🔥👌🙏 awesome job man of God 👏👏
Keep it up my Apostle! Ndalimbikitsika
Nice one, Nyimbo yolimbilitsa kuti munthu usafooke
I waited like oooooh my God am so Excited
Powerful song❤
Amen Apostle we blessed
The only remaining gospel artist who compose his songs, enawa amangoimba za mu hymn 😢
Ndipo zenizeni enawa ma copy n paste
Wow...powerful messages
Zilibwino man of God chipulumutso ndiwekha sure
Powerful. Am looking for Ondisamala by You. How do I get it
Am frm Uganda am inluv WTH the song thou idnt get chichewa…..Komatu akulu awawa amatha kupeka nyimbo osati izi za avocado
Great message 🎉🎉
So powerful ❤❤❤❤❤❤❤❤
Powerful brother 🎉❤
Cangratulations Bishop
Powerful man of God❤
amen, a powerful song
Amen..Moyowu awusunga ndi Mulungu.
Indeed chipulumutso ndiwekha❤❤❤
Every time am listening to his music,I feel good ,,
On repeat.🔥🔥🔥
Olo namondwe adzee komabe tiyen chitsogolo
Mumatha Chief Apostle King👑👑
Chipulumutso ndi wekha nice song😊
This is amazing 🎉
Sweet music❤
More grace my brother
Eishiii nyimbo iyiyi mwapha,ikuchita kundilakhulira chilichonse 😥
Zoonadi awo andichedwetsa,, powerful💪🔥🔥
Nyimbo yabwino kwambiri 🔥🔥🔥
Powerful 🔥 ❤
❤ Powerful one
This is a spirit bathed song
The wait is over🔥🔥🔥
Very powerful 🔥
Powerful🔥🔥🔥
Powerful 🎉🎉🎉
Welcome back inuyo mumatha🔥
Ndaikonda nyimboyi. 🙏
Ameeeen ! 🔥🔥🔥
Powerful song
The song has come on time,,,,,,
Amen amen that's powerful
So powerful 🔥🔥🔥🔥
Powerful ❤
Ndipo yesu yekha ndiye bwenzi
Powerful 🙏
Powerful man of God
powerful song
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤Amen
Oh yes❤❤❤
Moyo amasunga ndi Mulungu 🙏
Yeeees! Palibe ondithandiza
Wow just wow
Ikanakhala ya secular bwezi ma views Ali ambirimbiri😭, Amalawi tizitolere eeh🙌
Ndipo this song is very nice .......very powerful.....
Mbambande 🔥
Za power
Hallelujah
Congratulations
Amen
💪🔥🔥🔥🔥🔥
Very powerful
Powerful
😊😊😊
❤🤩
Good vibes
Mwatilimbikitsa mulungu akudakitseni