Mwayamba chani a great Engels aaaaaaaa mwandifooketsa ine tisakunyengerereni apa tikuuzeni chilugamo munayamba bwino kma apa mwapita kuzenje kulibeso za umfumu wakumwamba
Pepani mama. Ziwanda zapadziko sizikufuna kuti mudziwe chilungamo chokuti gospel ilibe ubale ndi za secular. Go read the Bible akulu kuweluzanso nkololedwa you just quote the verse out of context
@@AishahSenjekwa Mateyu 7:20 Yesu anati chirichonse chimadziwika ndi zipatso zake. Sikuweruza kunena Kuti mtengo uwu ndi wa mango when we clearly see Kuti muli mango okhaokha mu mtengomo.
MATEYU 7 : 18 Sungathe mtengo wabwino kupatsa zipatso zoipa, kapena mtengo wamphuchi kupatsa zipatso zokoma. MATEYU 7 : 20 Inde chomwecho pa zipatso zao mudzawazindikira iwo. MATEYU 6 : 24 Palibe munthu angathe kukhala kapolo wa ambuye awiri: pakuti pena adzamuda mmodziyo, ndi kukonda winayo; pena adzakangamira kwa mmodzi, nadzanyoza wina. Simungathe kukhala kapolo wa Mulungu ndi wa Chuma. When you put the word of God in a song, I doesn't make it a pure Gospel song. This is a secular song and Heavenly angels cannot take this song and sing it face to face with God on His highly exalted throne
Tikuyenera kudziwa kusiyanitsa pakati pa maimbidwe a business ndi maimbidwe omusitha munthu kumbali ya gospel iyi ndi business chabe great angel inali kale koma poti anthu alinkukonda kuyamikira zopanda pake
Complain take u no way let angels be angels if you not happy how the sing now day don't listen there music please tisangojaja anthu osalakwa akayimba kwa bushido is it crime shem on Brothers tiyeni tizindikile
@@SaisonMwendaapo mwalakwa. It’s better to correct a brother to walk in a right path even if it doesn’t please him than to applaud him when you know he’s following the ungodly path . You’ll be held accountable for letting the devil take him away
Abele great angels yavala zikopa eeee koma imfa iwe unatenga producer wathu Joseph tembo ndikutisiila ziwanda zama piano izii😭😭😭😭😭😭😭😭 mwina akanakhala wamoyo Joseph tembo bwezi zosezi kulibe ine ndikamaonela nyimbo ija ya maliro ija anatulusa pompano usiku sindigona kuopa mavalidwe aja ngati ndili pasi pa nyanja basi kutusaso iyi mavalidweso azikopa zomwe zija ambuye abwezeni ana anu a great Angles komwe akupitaku atitha for sure mumalo moti tizisisimuka ndi nyimbo tikumapanga nao mantha eeeee great Angles kumbikani pomwe mwagwela iyi si njila yanu tilalikileni uthenga oyenela ife ana anu a Malawi nyengo tikudusamo izi zopweteka abare azanga ndapita kuseliku ku album ya ndasankha👋👋👋👋
Chabwino ndikhare mbuni ndine,,, Koma na Pano great angels simandiwaza, nyimbo zinali zomwe zija gwiren zanja,,,, msalorere,,, Usiku kwacha kopanda dipo,,,,, Koma Pano mmmmm 0 pa 10,,, mlungu Wanthu Nd wansanje safuna kumusakaniza
Kusakaniza mchani big?
Ndipo zalowa chani chani uko akuzisisa mawait
Ndipo simukunama ine sindizisimuka nawo maimbidwe achochi zomikisa ndichoncho
Ndipo singaposeso zayawe .akumilirandani .musalore mmm very nice nyimbo iyiyii ilibwino poti muli aleluyayoo
Ndipo great Engels yathapo basi
Alipo wina amene amapiano yamutopetsa🙌🏾 ayimike nkono
Ine pano 😂
Tilipo angapo
😂😂😂😂😂 ine kuno
Zotengela zaeni 😂😂😂😂😂😂
Yafika pobowa
Your old songs are the best
Ndipo kwambiri
Lemme not hide I am in deeper love with this song especially on the verse
Keep it up nkhani ndi uthenga basi I love the song
Mwayamba chani a great Engels aaaaaaaa mwandifooketsa ine tisakunyengerereni apa tikuuzeni chilugamo munayamba bwino kma apa mwapita kuzenje kulibeso za umfumu wakumwamba
😂😂😂😂😂
From Grace to Grass why doing that Great Angel. Tangovomerezani kuti munatha 😂😂😂😂
Asanduka agalitiya choonad achitaya
Music is dynamic and this simply shows how dynamic great Angeles have become ❤❤
Ndirande Angrican Voices my VOTE
Koma iyi ndi great Angels
@@BlakRedGrin😂😂😂😂😂😂😂
@@BlakRedGrinNdirande Angrican number 1 iweyo kazivela zakozi
Thank God for Great for even preaching the gospel to young generations of today. You are doing a great work.
Ulemelero wa Yehovah udasamuka palibe zauzimu, apa mukulambira milungu yanu yachilendo😢
zoonadi Mulungu mwamuyiwala
Ndirande Anglican voice 🔥🔥🔥🔥🔥🔥sipembeza nawo mafano
Moto buuuu
I suppose ndirande Anglican voices is purely a church choir,, pomwe awa it's business
Ndipo munthu sangakhulupilire kuti iyi ndi great angels yomwe imaimba bwino ija aaaaaaaaah bundle yanga ine🗣️🗣️🗣️🗣️😭😭😭😭😭😭
Anthu muli nkuweluzatu ngati ndinu a phwawo a yesu😢
Kkkkkkk
Pepani mama. Ziwanda zapadziko sizikufuna kuti mudziwe chilungamo chokuti gospel ilibe ubale ndi za secular. Go read the Bible akulu kuweluzanso nkololedwa you just quote the verse out of context
@@AishahSenjekwa Mateyu 7:20 Yesu anati chirichonse chimadziwika ndi zipatso zake. Sikuweruza kunena Kuti mtengo uwu ndi wa mango when we clearly see Kuti muli mango okhaokha mu mtengomo.
🔥🔥🔥 Kell Kay top fans gather here
Ife pano🔥🔥
Here we are🎉
Here🎉
Ife pano
Wow this is great I like the message n the dancing itself ❤
Munayamba mwa uzimu mwasiliza ndi kuthupi why great Angels
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭✨😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Phenomenal!!!
Well Done Kelly Kay and Great Angels
From Zambia we confirm that it's a certified hit and banger
🎉❤
Kalikonse tikaona,,, Ambuye ndamene Akudziwa chilichonse tili munyengo ya Agalatiya!!! 🙏
MAN joy.... la(apala,Mwandikondera ija ndi 💥💥💥*
Great jam there❤Kell Kay i give my flowers ❤❤
From Zambia🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Wow the song is hitting inuyo ambuye❤❤❤❤
Kele kei ndwe dolo adh..... Ma angels fire Pati♥️
Great Engels yakale ija mwina yatuluka ina mwayamba zobowa
Tachoketa Kwa Pule Chikatiko.✋
Koma zili nnyumba mwanu yehova nnyumba mwanu....in Doc's Voice
The fact that you let the song be on the great angels choir channel ❤ very inspiring ❤❤
Let's gather for Kell Kay 🎉🎉🎉
Who's here for Kell Kay! 🙋🇲🇼
Kell Kay to the world 🔥🔥🔥
Ati nchani kod great angels abale🙆💔💔
😂😂😂😂😂
Zausatana zeni zeni gospel song imakhara chocho great angel inali choir yabwino kare
Beautful song. Keep it up!
What a great song of the year
Nice tune. Great angels. My favorite choir❤
MATEYU 7 : 18
Sungathe mtengo wabwino kupatsa zipatso zoipa, kapena mtengo wamphuchi kupatsa zipatso zokoma.
MATEYU 7 : 20
Inde chomwecho pa zipatso zao mudzawazindikira iwo.
MATEYU 6 : 24
Palibe munthu angathe kukhala kapolo wa ambuye awiri: pakuti pena adzamuda mmodziyo, ndi kukonda winayo; pena adzakangamira kwa mmodzi, nadzanyoza wina. Simungathe kukhala kapolo wa Mulungu ndi wa Chuma.
When you put the word of God in a song, I doesn't make it a pure Gospel song. This is a secular song and Heavenly angels cannot take this song and sing it face to face with God on His highly exalted throne
@@MMK-p3y zoona ndipo mwanena chilungamo
This is 🔥 my favorite gospel song of the year..... Sutuziba family Zambia
Hallelujah ndakula ndkuva za Inu
Great angels apa pokha ndye mwanyanya sizinandisangalatse umu simomwe mukuyenera kuimbila
Mwangotiwonongela GREAT ANGELES NDIMAPIANO ANUWA😢
good tune olo yesu sanasangalatse onse.
keep up
Jersey got beautiful voice.❤
Great Angels inatha ngati bozatu💔💔Lord have mercy upon us 🙏
Nyimbo ili makora waka 🎉🎉🎉🎉 keep it Mr Kelly
Beautiful 🥰 church ❤
Tikuyenera kudziwa kusiyanitsa pakati pa maimbidwe a business ndi maimbidwe omusitha munthu kumbali ya gospel iyi ndi business chabe great angel inali kale koma poti anthu alinkukonda kuyamikira zopanda pake
Choyankhula chagwera mkati😢😢
@@Aminayaumi.in8tn ndipo iwe Uli Ngati ine sindinayimalize kuyimvera
Especially kumalawi kuno 🙌🙌. Chilichonse kumangoti yes munthu wina akanena kuti pakuti palakwika amati nsanje
Very beautiful song
Massive hit from Kelly K and Great Angels, mwatyimila
@kell Kay & #great_Angels thanks for this great piece of art
Amazing song.... powerful message
Great angels my fav Gospel singers
I love it already fire
Great angels mwatero...
Being listening to this guy for a long time ❤️❤️
Fire kell kay
Ambuye bwerani muzaweruze dzikoli illumination yadzadzadzikoli 😢😢😢 God help us
Iyi si Gospel amwene...Illuminat yeni yeni.
Ndipo inuuu mhhhh anthu ankayimba bwino awaaaa mhhh
More love from Zambia 🇿🇲 kuchalo
Best collaboration so far
Kellz that verse imandiwaza moipa 👏
Mau oti. hallelujah aja is a heavenly word indeed....nyimbo yonse yakoma pokhapo😂
Great great choir and the best artist indeed,,,onuyo mmakwana🎉🎉🎉
Song of the year 🔥🔥🔥
Koma kell Kay umayimba mosakakamiza 🔥🔥I love the song ❤️
The outfit did it for me🥰🥰🥰🥰 nice song too❤
This is a work of art 🎨 ✨️
Iwe umati, Kell Kay ukutiwaza ku Moçambique 🇲🇿
Iyiyi yakazingidwa serious, tonse takula tikunva za iye indeed ✊✊🕺🕺
GOAT for a reason
Kodi kuphatikana kwake mkuti pakati pa kachisi wa Mulungu ndi mafano?
Efereimu waphathana ndi mafano; mulekeni!
Ngakhale pamene zakumwa zawo zatha, amapitilidza kuchita zachiwerewere; atsogoleri awo amakonda kwambiri njira zawo zochititsa manyazi. (Hosea 4 : 17 - 18)
Watching 👀 straight from Capetown 🇲🇼 🇿🇦
It's giving amwene 🎉🎉🎉
🔥🔥 favourite choir and artist
My favourite of all times ndipo ndimaona kuchedwa foe this vedio
Mwapanga chani Great Angels aaaaaa
Kelly key hes so talented 🔥🔥🔥🔥
This is great song my country people ❤😊😊
Fire🔥🔥 Great angels nakusowani ma dolo. Mr Kell Kay matha
Eeehh Tricky ujaa🙌🙌
This is a master piece🙏🙏
Umatha anse big up Mr kell kay
Woyimba yemwe amandiyimbira boh Kelly Kay ❤
Ooh yes powerful song 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤❤❤❤❤❤
Amen ñice tune dearest
Been listening to this song since 2022🥰...ndipo imandiwaza koopsya😍..all this while i thought the title was Inuyo... anyway beautiful video🔥🔥🔥🔥
The video is massive ✔️🔥🔥🔥
We listen but we don't judge,ambuye oweluza ndinuyo🙏
I love it
Hallelujah 🗣️🗣️🗣️ awesome 🔥🔥🔥🔥
The voices are on 🔥
Nyimbo yosakoma Ana abushiri omwa magazi zitsiru nose apa
Bishop apa mwafika 🔥🔥🔥🔥 KellKay
Kell Kay music from Malawi style is powerful 🤝 I love you from Zambia any one to like my comment I will come back to watch this video ❤
😲😲 nice song
Excellent ❤❤@@RaymondProsperDouglas
❤
Complain take u no way let angels be angels if you not happy how the sing now day don't listen there music please tisangojaja anthu osalakwa akayimba kwa bushido is it crime shem on Brothers tiyeni tizindikile
@@SaisonMwendaapo mwalakwa. It’s better to correct a brother to walk in a right path even if it doesn’t please him than to applaud him when you know he’s following the ungodly path . You’ll be held accountable for letting the devil take him away
Beautiful visual
Nice one my favorite...... sutuziba family from Zambia
Kell Kay dolo katatu, my friend forever
This is Hit well done guys
Wow that’s wow 😮 amazing kell Kay this song is really good. Like my comment so that I’ll come to watch this video again and again ❤
Kell Kay all the way🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
izitu zitha kubweretsa ziwanda mu deni!
Ziwanda apo zasikira kare