ASATANA ANDALE AYALUTSIDWA NDI DJ MUNYANANE KUWAYANIKA PA DZUWA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 15 сен 2024

Комментарии • 61

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Месяц назад +3

    Umakwana DJ uli ndi voice yabho ❤❤❤

  • @eliaskhofielias8152
    @eliaskhofielias8152 Месяц назад

    😂😂😂😂 best dj munya nane and you got nice voice.

  • @BhekiLithuli
    @BhekiLithuli Месяц назад

    Zikunveka bho❤❤

  • @IssaLazack-ij1gf
    @IssaLazack-ij1gf Месяц назад

    Ndikanakonda ndithakona ngope amunyanae mundfikapo

  • @OssmanGuevarra
    @OssmanGuevarra Месяц назад

    Aaaaaa DJ munyanane apatu nde mwaing'aluratu zoonadi beni Longwe ndi satana kapolo wamunthu

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Месяц назад +1

    Ben longwe amachinda ana ake yakumbuyo

  • @amadichembe4068
    @amadichembe4068 Месяц назад +2

    Mwaswela bwanji,ngati muli bwino dzikomo,koma ineyo kuno ku Zambia muku mveka 10%

    • @amadichembe4068
      @amadichembe4068 Месяц назад

      Sorry ninali EMBA 10% pepani pepani mukumveka 100%

  • @mariamahamadu8402
    @mariamahamadu8402 Месяц назад

    Mavuto kumalawi kadziko kachepelanji koma nkhani dzomwe zikuchitika🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌 Komatu ndive tomwe tinkavotela chakwela chiyipa chizata Eni ake chipandakumvomela kumvota kawiri Kaja zibwesi Lero tiri chontchi koma aMalawi Ife ayi

  • @james-zd2nz
    @james-zd2nz Месяц назад

    watching from jhb loud n clear

  • @SAMARTEDWART-b1j
    @SAMARTEDWART-b1j 23 дня назад

    ✦✦✦♥︎♥︎♥︎♥︎♥︎✦✦✦
    ☆☆☆☆☆☆☆☆☆☆
    Inu ndi akatundu

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn Месяц назад

    Malawi is a very had country to leave specially the citizens than visitors

  • @MussaNgoma-r2k
    @MussaNgoma-r2k Месяц назад

    Proud of u keep it up the great work ❤❤

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn Месяц назад

    Panopa mzukulu wanga ali ku prison ku Thyolo atamupanga transfer kumuchotsa ku Blantyre ndikumupititsa ku Thyolo nkhani yake amakatola nkhuni ku phiri lina lake ku Blantyre pamene anthu omwe akuzunza a Malawi ndikuba chuma cha boma khoti lomwelo silikuwamanga

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Месяц назад

    ❤❤❤❤ DJ munyanane nyimbo wabayayi imandiwaza ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @Machemba-b7s
    @Machemba-b7s Месяц назад

    Loud and clear. In Pretoria north west in south Africa, umakwana

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 Месяц назад

    Uli super Munyanane

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b Месяц назад

    Clear. From Zambia chakwela should go

  • @ChristinaSimwaka
    @ChristinaSimwaka Месяц назад

    Chautaaone

  • @MerryWayson
    @MerryWayson Месяц назад

    Kumenekoooooo timakunyadilani Mr Munyanane kuno Ku South Africa Box B Kuli bwino, Kuing'alula mosawona apongoziiiiii kkkkkkk

  • @HappyBirchForest-zy8nq
    @HappyBirchForest-zy8nq Месяц назад +1

    🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-dg5pc6rz1b
    @user-dg5pc6rz1b Месяц назад

    Exactly

  • @Uncle_B265
    @Uncle_B265 Месяц назад +2

    Ziko lapasi limakomera anthuu oipa

  • @AiameAdamo-su1nt
    @AiameAdamo-su1nt Месяц назад +2

    Loud and clear from Mozambique.

  • @Patgregorymanyumba
    @Patgregorymanyumba Месяц назад

    Loud and clear @ Winnie Mandela, Pretoria

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe Месяц назад

    Eya a chakwera anaba chimangadi nkiukagulitsa ku tanzania ndiponso iwo ndi nduna zao anaba mao za Sattar Gate koma kumgomugwira Saulosi klaus chilima yekha.!! Bwanji kodi ? Afiti inu

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Месяц назад

    Mmmmmm koma abale kumangidwa chifukwa cha nkhuni koma Mcp nde mukusowa zochita tu kuchititsa manyazi munya simudzawina 2025,apolice sakuyidziwa ntchito yawo palibe chomwe akupanga

  • @DalisoulThom
    @DalisoulThom Месяц назад

    Mulungu alowelelepo azimai amenewa ayenela kutulusidwe

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim Месяц назад

    Mmmmmm mwinatu ndi maaaa iiiiiiii sorry mr vp

  • @HaliJana
    @HaliJana Месяц назад

    OSAMANGA ANAGWESA NDEGE KU CHIKANGAWA BWANJI,ENA KU BUTI 3MTAR OSAMANGA BWANJI

  • @user-ny3it3jp9l
    @user-ny3it3jp9l Месяц назад

    DJ ❤❤❤❤❤💯💯💯💯💯

  • @DanielJuwawo
    @DanielJuwawo Месяц назад

    Ulemu upite kwa tv mulungu ntanyiwa ndi Dj munyanane

  • @JacksonMahafu
    @JacksonMahafu Месяц назад

    Kkkkkk uzibwelabwela

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Месяц назад

    Satan's anali m'busa 😂😂😂 panoso akungokwera akazi a eni

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje Месяц назад

    Ndimachedwatu

  • @MphatsoChangata-ti9ru
    @MphatsoChangata-ti9ru Месяц назад

    Munyanane woyeeeee!

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v Месяц назад

    Dj yomweyo ipase moto asakufuna akagone

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda Месяц назад

    🔥🔥🔥

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Месяц назад

    Ng'alura

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 Месяц назад

    Moto dj

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Месяц назад

    Ndipo ziko la pasi Lokomela achuma ndipo zoipa zimachitkila abwino zabwino zimachitikila zoipa koma tose ndi ake ndithu

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Месяц назад

    Ma jaji akumalawi.naonso ali ngati asilikali NDI a Police anasankha kugwira ntchito ndi chipani kusiya kulemekeza malamulo , komaso Ben longwe AMENEYU AZIYENDA mosamala timutchola nsagwada dziko si lamake kapena chakwera ,

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje Месяц назад

    😂 koma ili madzi mcp 😂 komaso iwe ndimoto mr lomwe ukukwanilatu😂😂😂😂 owulule onse mr lomwe

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Месяц назад

    Do ndipo live mukuveka bwin ndiripano kukusatirani benlongwe ndisatana uyu palibe omwe angachivere chimenechi dj mulibho

  • @AngozoMalunga
    @AngozoMalunga Месяц назад

    Tikukuvani kwambiri kuchokela kuno ku eastern cape mthatha

  • @DanielJuwawo
    @DanielJuwawo Месяц назад

    Uku kuli zabwino so chonchi

  • @IdressaMussa
    @IdressaMussa Месяц назад

    🎉🎉🎉🎉🎉

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w Месяц назад

    Mwanzi ugwila nchito

  • @EzekiaMnkhondya-bc5bs
    @EzekiaMnkhondya-bc5bs Месяц назад

    Achimwene tikumvani kuno kutanzania mukumveka ndipo mupitilize

  • @AngozoMalunga
    @AngozoMalunga Месяц назад

    Dj wabho uyu

  • @JeremiahKainga-rm2np
    @JeremiahKainga-rm2np Месяц назад +1

    DJ Munyanane,how can I get the instrumental playing

  • @ellahmwams831
    @ellahmwams831 Месяц назад

    Umakwana DJ Munyanane🔥🔥🔥

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o Месяц назад

    Tinya nawedi sure

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Месяц назад

    Dj munyanane mballi yanji mulli iweyyo ullibho nanga ennawo allibwanj osawopha osavowonka ndive amalawi mtanyiwwa osawopha bakili muluzi TV osawopha mulungu adalise wina aliyese astaguffllal yha Allah tiutseni soona shonde

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o Месяц назад

    😂😂😂

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh Месяц назад

    Amasulidwe with immediate effect

  • @promisemussa4891
    @promisemussa4891 Месяц назад

    Hiw can I get into Ur WhatsApp groups?