BREAKING NEWS NKHANGA ZAWONA PA LIMPOPO FM NDI COMRADE NTANYIWA KWABWERA MA ISRAEL 11 pa 15 SEP 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 17 сен 2024
  • NKHANGA ZAWONA PA LIMPOPO FM NDI COMRADE NTANYIWA CHIGAWO CHA USIKU,KWABWERA MA ISRAEL 11
    Izi ndi zomwe wayakhula

Комментарии • 69

  • @HappyLighthouse-hj8qw
    @HappyLighthouse-hj8qw 3 дня назад +3

    Thanks Mr ntanyiwa God protect you all the time

  • @ReubenGama
    @ReubenGama 3 дня назад +6

    Koma social media osazaiyiphweketsa guyz

  • @ChikondiChimwaza-i8l
    @ChikondiChimwaza-i8l 2 дня назад +3

    Kodi asilikali ntchito yawo ndi chani,eeeee koma ngati nkulu wa asilikali wadya ndalama,akanangotula pansi udindo wake, mmmmu atipwetekesa galu ameneyi

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh 2 дня назад +2

    Mcp zopha chilima,ma plan anayamba chaka chomwe tinavota coz nkati mwawo munali dyera ndi ugogodi.

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k 3 дня назад +4

    Guys kodi tikudikila chani? Tatiyeni kumsewu chikangawa akufuna kuyambitsa nkhondo inu simuona? Mbuzi imeneyi akutiona a malawife kupusa

  • @Edithmchinza
    @Edithmchinza 2 дня назад +1

    God protect you mr tanyiwa,why God

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi 2 дня назад +1

    May ALMIGHTY ALLAH protect Mr Ntanyiwa 🙏

  • @user-ov4wt4qs3x
    @user-ov4wt4qs3x 3 дня назад +1

    Thanks mr Ntanyiwa God bless you

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 3 дня назад +2

    Big Up brother ❤❤❤

  • @AishaIshumael
    @AishaIshumael 3 дня назад +2

    Tiyeni pa nsewu basi chakwera wationjeza

  • @SamuelBhanda
    @SamuelBhanda 3 дня назад +2

    Siteti house ija kwasanduka kosugirako zigawega basi

  • @JjeradiAricki
    @JjeradiAricki 3 дня назад +2

    tiyeni marawi tidzuke tisango chonde chonde mandem chakwera wanjaira machendeake osadura

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 3 дня назад +1

    Mtanyiwa ndi #1🎉🎉🎉🎉🎉

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 3 дня назад +1

    Achoke uyu bas Chikangawaaaaa watikwana Panseu amalawi

  • @wezzieneba9238
    @wezzieneba9238 2 дня назад +1

    If there are organizations that help countries, please, come and help Malawi. I don’t want to face this….war. We are tired of crying. We don’t want to cry again. God help us.

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 2 дня назад

    We have been waiting for this continue to give us the best analysis of what is happening around the world

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika 2 дня назад +1

    Basitu I now believe that Ntanyiwa stays in heaven...

  • @BenardThomas-p6o
    @BenardThomas-p6o 2 дня назад

    Mbambande boss

  • @HOMEAWAY-h7t
    @HOMEAWAY-h7t 3 дня назад +1

    Limpopo FM ❤ nkhanga zaona

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 3 дня назад +1

    ❤❤❤❤ tikadali maso sitinago

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 3 дня назад +2

    Tiyen pamsewu basi chakwera achoke

  • @Friday-o4u
    @Friday-o4u 2 дня назад

    Apuresdent chepesan kubwelesa alendo ankhondo mudziko lamalawi sizabwino anthu amatopa mukakhala mukumbukile za kukenya chonde Mr puresdent

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 3 дня назад +1

    Big brother

  • @JohnKukulu
    @JohnKukulu 3 дня назад +1

    Comrade ingondipatsa ineo ndivere that audio cfkw ndatopa ndi manyi akubiba cakwerawa

  • @OmmarAbdullah
    @OmmarAbdullah 3 дня назад +1

    Umatiimilila comrady mtanyiwa

  • @BrightLuciano
    @BrightLuciano 2 дня назад

    Panseu athu munafooka athu opangisa mademo anatha

  • @JanaJovian
    @JanaJovian 2 дня назад

    Timakukondani❤❤❤❤❤

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 3 дня назад

    Tingangowotcha Start House 🏠🏠 Yoo bas iyah asatitopese Chikangawa pathako pache

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 3 дня назад +1

    Wel come

  • @JohnMakinah
    @JohnMakinah 3 дня назад +1

    Zikachitik tivera kwa inu ❤❤

  • @ToothyWebb
    @ToothyWebb 2 дня назад +1

    Koma zoona tidikile mbozi zilowe mmutu mwanu comrade??? Release the audio!

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 2 дня назад

    Alore alore akane akane welcome comdred mtanyiwa

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 3 дня назад +1

    Comryde ntanyiwa in,galuleni basi aziwe kut inuyo simuthu wamba

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 3 дня назад +2

    Akumatiwonjeza munthu uyu ateromo akufuna kupha anthu ena nde munthu uyu zufunika kukawotcha Stars House komweko aaaa atithano mmalawimu

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 3 дня назад +1

    Aaà a MCP sakugona ndi notse mukuwulula dzotsisi za MCP nangao nyumba yaboma yasandika kolandikula dzigawenga KOMATU MA ISRAEL AWA KUTSAFE MUNTHU ONTCHUKA AMALAWI MWAWONA KUWAWA MASOKA ENAWA OTSAMAYAMBA DALA mwina abwela kuthandidza pa nkhani yobela chitsankho ngati dzili idzo nde amalawi mudzawadziwa 2025 kuti akachepa kayenda MCP tsamalani idzi mukupanga magadzi achaka chamawa

  • @elishamael-shadai
    @elishamael-shadai 3 дня назад

    Umakhwwana heavy Comrade Nthanyiwa,usazafe ,uzangosowa like Enoch mu bible. Pliz audio imeneyo plizzzzzzzzzzz uyiphulise ,agalu amenewa akukoza osagwirira😂😂😂😂😂

  • @JaneNdamela
    @JaneNdamela 3 дня назад +1

    Chifukwa chale awagenda kusanje

  • @BlessingsMarley-l2x
    @BlessingsMarley-l2x 3 дня назад +1

    Antanyuwa mumatiyimilila mwa wa angaga uku ku nsika wanjala timenyele nkhondo amalawi

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 3 дня назад +1

    Chakwera the maphia

  • @IdahKamwanga
    @IdahKamwanga 3 дня назад +1

    Iiiihhh sad

  • @Aaron-w9x
    @Aaron-w9x 2 дня назад

    Antanyiwa tapangani za ma audio amundegewo kut tione kuti tichita motani

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 2 дня назад +1

    Eeeee koma chakwela

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 3 дня назад

    ❤❤❤❤

  • @HaroonWalusah
    @HaroonWalusah 3 дня назад +1

    Work up guys 🤔🤔

  • @JjeradiAricki
    @JjeradiAricki 3 дня назад +1

    chakwera machende ake akufuna kubweresa khondo muno eti machendeake abambo ake

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 дня назад

    ❤❤❤❤❤❤ ntanyiwa your my mfumu

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 2 дня назад

    koma Kodi kuribe anthu wotithandiza kuti atiyimire Kodi anthu wose agurika ndindarama koma ziko rathu rikupita kuti abare tose tiri ziii zinthu zikuwonengeka 😢😢

    • @morisndalama6380
      @morisndalama6380 2 дня назад

      Vuto tilibe Atsilikiraki olimba mtima kuti ayambise kuukira,,anakayambitsa ife tili ready kuwathandiza kuti tithane ndi chikangawa

  • @louismagongwa
    @louismagongwa 2 дня назад +1

    kod ntchit ya MDF ndichan 😂😂😂😂😂

  • @SamuelBotolo
    @SamuelBotolo 2 дня назад

    Zopanda umboni izi

  • @EphiehkariPhiri
    @EphiehkariPhiri 3 дня назад

    Ine aluya akamadana ndi dziko la Israel ndi ngati ndi anthu odzikonda koma panopa nazindikila chowoonadi kuti anthu amenewa ndi Haram

  • @EphiehkariPhiri
    @EphiehkariPhiri 3 дня назад

    Tangoponyani asanaphenso anthu ena please maliro atikwana ife eeeeeee

  • @MosesBemah
    @MosesBemah 3 дня назад

    Mmmmm koma malawi

  • @MosesBemah
    @MosesBemah 3 дня назад

    Kodi ya ng'ombe ijah simunafufuze kuti zafa ndi chani chongo Kona iwowo
    Zabwana issa zijah

  • @khoviwaedward
    @khoviwaedward 3 дня назад

    Koma asilikali ah Malawi Defense Force akumva bwanji nkhani ngati idzi? Koma Chakwera galu wa munthu kwa basi

  • @blessmarleystech5712
    @blessmarleystech5712 3 дня назад +1

    Chenene

  • @wendaemily3179
    @wendaemily3179 2 дня назад

    Eeee koma chakwera

  • @AllanMwakalenga-wn5ib
    @AllanMwakalenga-wn5ib 3 дня назад

    Mademo...akufunika a violence,ngati achina mtambo aja,ndipamene angature pansi udindo

  • @PempheroAlli-v8y
    @PempheroAlli-v8y 3 дня назад

    tiyen pa msewu guys achoke chikangawa atipha kenako tonse

  • @AmissKumakanga
    @AmissKumakanga 3 дня назад +1

    Uremu wanu❤❤❤❤

  • @McMillanMillanzi-uh6ov
    @McMillanMillanzi-uh6ov 3 дня назад

    Kuankhula koma simu chitapo kanthu anthu oipa inu

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi 2 дня назад

      Ndipo zoona zake nanga titani tikanva zimatiwawa

  • @patriciajangaza675
    @patriciajangaza675 2 дня назад

    Kodi asilikali alikuti? Kuti azinthandiza dziko muno abale mulungu wanthu atinyhandize

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 2 дня назад

    Kidi asilikali a mw tchito yanu ndi chani mwangokhala ngati mwagon bwanji

    • @morisndalama6380
      @morisndalama6380 2 дня назад

      Ndipo inu,,, tikungofuna silikali oti atilimbise mtima akhale kutsogolo kwathu ife tigwire ntchito

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e 2 дня назад

    Tulutsani odio yo tive

  • @yobesaikonde6166
    @yobesaikonde6166 2 дня назад

    Choka wa wa chamba