MICHAEL USI ANAPITA KU MA OFFICE A ADMARC LERO NDIPO WASAMBWANZA OGWIRA NTCHITO MOTERE

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 28 янв 2025

Комментарии • 77

  • @ggrrtyTyne
    @ggrrtyTyne 10 дней назад +2

    😂😂😂😂 koma kuli kuthamanga iiii

  • @Sadckchigomile
    @Sadckchigomile 10 дней назад +1

    Osusa milimbikile mwina mcp yayamba kuva suleman is power

  • @MarkMuvula-q2m
    @MarkMuvula-q2m 11 дней назад +1

    Kodi amene mumamuda vice usi , amakulakwirani chiani ?, Mukanyozanyoza pomaliza , mukadya soya pieces, tea wamadzi , pogona , ngati pogona nkhumba posalongosoka , tikambe , zazibale Anu mavuto mbwerekete , mudzipanga zanu ,osamalimbana ndi munthu omwa tea wa sitrober ndi nesqueck. , Zomunyozazo zichepe

  • @wakisamsukwa9918
    @wakisamsukwa9918 10 дней назад

    Actor in action. Why would you need a camera with you for official duties..

  • @JamesYusufu-l6d
    @JamesYusufu-l6d 12 дней назад +2

    zamatama. ngati. zazeru. ndalama ndiye mwabamo bomamo loko adimakiyo ilibe chilichose. zachamba akutcheni oziws nthito palibe zaziiii. adimaki simupezeka chimanga mukutanganidwa ndizopanda nthito. anthu akusowa chokuja

  • @StoneckJali-s3n
    @StoneckJali-s3n 11 дней назад +1

    Uku ndiye kugwira nchito osangoti phwii mu office

  • @vinceynyone6693
    @vinceynyone6693 10 дней назад

    Cover the short boi😂😂😂

  • @JuweriaMussa
    @JuweriaMussa 12 дней назад +2

    Ndewapolice wina mwamusiya kumbuyoko sakuthamanga kkkk njala kapena kunenepa

  • @DuniaBanda-by9gt
    @DuniaBanda-by9gt 10 дней назад

    Vitumbiko ndi Manganya ali ndi mu MCP komano mzimu wawo Kaya uli Pati,,,

  • @AimanTwalid-o6o
    @AimanTwalid-o6o 11 дней назад

    Ndpo wayambilanso usi aja mumagona mma office aboma samalani

  • @ishmaelimedi7363
    @ishmaelimedi7363 11 дней назад +1

    Tikufelanji kwa admac😂😂😂

  • @KenChissah-pp2lk
    @KenChissah-pp2lk 7 дней назад

    Mumafuna kuti magalimotowo aziyenda azikanyamula chain poti mu admac chimanga mulibe

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 12 дней назад +1

    Zonse mukupangazi amalawi sitikuonapo kathu tili ndi chidima chanjala mr short one

  • @ISHMAELCHITENJE-ri9rq
    @ISHMAELCHITENJE-ri9rq 11 дней назад

    Iye wasazika ndani kuti akafike kwadimark?nayeso achosedwe basi kuyalusa boma uku,mmalo moyankhula zachimanga akukamba zamagalimoto kkkkkkk,mbutuma zadziko

  • @Dellingsmunthali
    @Dellingsmunthali 11 дней назад

    Anthu awa ndiye ofunika kuthamangisa malawi mmm malawi wafikapa mmm zikufunika changamu osangogona ku state house mkonono

  • @InnocentMtewa
    @InnocentMtewa 12 дней назад +1

    Awanso nde yayi ndithu. Bola Mumba uja😂😂😂

    • @MarkMuvula-q2m
      @MarkMuvula-q2m 11 дней назад

      Osati akanakhala bambo Ako ukadayamikira , nyonzo unyoza iwe ana Ako adzaona zonga zomwezo

  • @AllanMwakalenga-wn5ib
    @AllanMwakalenga-wn5ib 11 дней назад +1

    Akujambula filimu yanji nkuluyu

    • @MarkMuvula-q2m
      @MarkMuvula-q2m 11 дней назад

      Kwanu kukhale ophuzira udzadziwa kuti ichi nchiani. ?

  • @GreyChandilanga
    @GreyChandilanga 12 дней назад +1

    Can this help Malawians Mr?

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 11 дней назад

    Palibe chingathandize malawi apa olo pang'ono ngati kulikuluko sikukulongosola

  • @MoosaAyileni-u5k
    @MoosaAyileni-u5k 11 дней назад

    Akuyenda ngati akupita kumaliro bwanji 😂

  • @noelanaker7340
    @noelanaker7340 12 дней назад

    Admarc inayamba ndi kamuzu wa congress yatha ndi Chikangawa wa congress hahaaa

  • @DanielAdson-g1o
    @DanielAdson-g1o 12 дней назад +1

    Eli

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 11 дней назад

    Koma utsi akudzudzu apolice abale ndiye chani ichi hhhhh

  • @alfasibriancornwell8685
    @alfasibriancornwell8685 11 дней назад

    Zitamatele ndikukhulupilira kuti dziko lathu likhoza kusitha ndithu.

  • @FrancisSilia
    @FrancisSilia 11 дней назад

    😂😂😂😂😂 ndizoonadi akuononga chuma cha boma aaa 5

  • @SaisonMwenda
    @SaisonMwenda 11 дней назад

    Ndi chifukwa timakonda achinyamawa amayenda pasi osangoti ndiyimaso muthu wskalamba azikangomubela mafana

  • @AlidiNgalande-ou7ig
    @AlidiNgalande-ou7ig 12 дней назад

    I like the guy. Munthuyu pa ground akutipula

    • @MoritiouseJefita
      @MoritiouseJefita 12 дней назад

      Ndimene zimankhalila munthu akamasaka mavote tuu😂

    • @JohnstonNyirenda-zw6jd
      @JohnstonNyirenda-zw6jd 10 дней назад

      Kutipula akutipulako tazifunseni kuti wawonga ndalama zingati ulenfpdo wakewo

  • @ashankagwa668
    @ashankagwa668 11 дней назад

    Tadziwako ntchito za nduna through Usi ndi Mumba.

  • @MartinCaptain-qr7of
    @MartinCaptain-qr7of 12 дней назад +1

    Awa koma kuvina ndi azimayi

  • @PatrickNampota
    @PatrickNampota 12 дней назад

    Tikuferanji yalowa mu admac kkkk koma mzimbabwe uyu ayi ndithu

  • @lucksonmoonga4426
    @lucksonmoonga4426 11 дней назад

    Ma drama akupitilizabe.anazolowela 😂😂

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 12 дней назад

    Za ziii mwagundika ndi mabodza kufuna kuputsitsa amalawi

  • @InnocentFadweck-i6n
    @InnocentFadweck-i6n 11 дней назад

    Koma bvuto mwaziyamba mochedwa athu atafa

  • @YusufMapata
    @YusufMapata 12 дней назад

    wofuna kukalipilidwa nda nduna akawale chifukwa ndiwunduna wawo akumphela sakotha kulondoloza zinthu zimene zowonongeka muwunduna wa zamalimidwe

  • @VincentJohn-z1t
    @VincentJohn-z1t 12 дней назад

    Kufuna kuziyeretsa kumeneko? Ayi Ife sitiinva muchoka basi.

  • @EnerstMwitha
    @EnerstMwitha 12 дней назад

    Undasi sikaloti kutima kuyela kuti beye chifukwa anapeleka skc amafuna izi koma boma tisitha basi ngati abiyeni palibe ine ndisitha basi chifukwa zanga sangakhale chikangawa andimpa ndithu chipani choipa ndithu mbili sitidzawala ndipo tidzampizitsa ana athu 6

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis 12 дней назад

    Za zii kazikangopangani tikufelqnji. Ndi make sikono izi asiyileni a Vitumbiko Mumba

  • @TechnicKingsly
    @TechnicKingsly 12 дней назад

    Iiiiiiiiiiiiiiiiiiii koma dziko ili manganya lelo vaisi pulezidenti oooh gooooo

  • @jamesmukhula5643
    @jamesmukhula5643 11 дней назад

    Strategic mafias

  • @SuedMdoyi
    @SuedMdoyi 11 дней назад

    Ndi camera yandani imajambula izi?😂😂

  • @ThomasChiona
    @ThomasChiona 12 дней назад

    Ministries drama after drama kkkkkkkkkk

  • @FrancisSomanje-k8j
    @FrancisSomanje-k8j 11 дней назад

    Njala yambiri mbiri chochita chosaoneka

  • @hlyby2657
    @hlyby2657 12 дней назад

    😂😂😂😂 Ati Vuto talipeza Tanvana 😂😂😂😂 a choir nyimbo

  • @MACDONADLITIA
    @MACDONADLITIA 12 дней назад

    Azichotse boma ligule galimoti zina izi alimi akagule ku mudzi azikanyamulila manyowa

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi 12 дней назад

    Mmalo mofusa za chimanga agalu usi kungowonga ndalama za boma

  • @SydneyDrinkson
    @SydneyDrinkson 12 дней назад

    Akeendera ngati mulichimanga

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi 12 дней назад

    Cha nzelu ndi chani apa koma ili likusewelesa ndalama zazi nduna mupangiletu ndalama mukupita basi

  • @DelubyMarko
    @DelubyMarko 12 дней назад

    Tidzakukumbukani kukazafa as of now akuti ndi Tikuferanji

  • @MphatsoNak-wq2kd
    @MphatsoNak-wq2kd 12 дней назад

    Kd akuluwa sewero sadasiyebe???

  • @FredMagalas-d5h
    @FredMagalas-d5h 11 дней назад

    Kutokota kopanda manyazi

  • @blessingsNyirenda-pj3rs
    @blessingsNyirenda-pj3rs 12 дней назад

    Same same with mumba

  • @hlyby2657
    @hlyby2657 12 дней назад

    😂😂😂😂 😊

  • @Markbanda-q3y
    @Markbanda-q3y 12 дней назад

    Nice one

  • @stephanongalaukabanda2step867
    @stephanongalaukabanda2step867 12 дней назад

    Akuzikozera malo akuziwa zakusogolo

  • @patrickjaenda8288
    @patrickjaenda8288 12 дней назад

    Anthu onse munawachosa ntchito ndie asamale ma phapao ndani

  • @UsumanLuwayo
    @UsumanLuwayo 12 дней назад

    Nde nzichani mufuna kuti anthu aone ngati Pali cha nzeru

  • @MandelaMaganga
    @MandelaMaganga 12 дней назад

    Dramatically country kkkkkkkkk

  • @mosewallace9717
    @mosewallace9717 12 дней назад +1

    zopoira kupita ku admac kumakapaza magalimoto pali cha nzelu pamenepo m'malo mòpanga za chakudya.,ndi fetereza

  • @FrancisSomanje-k8j
    @FrancisSomanje-k8j 11 дней назад

    Zopanda pake

  • @cosmaschitimbeladson460
    @cosmaschitimbeladson460 12 дней назад

    Za ziiiiiii

  • @phiphiraTamandani
    @phiphiraTamandani 6 дней назад

    Usso

  • @TechnicKingsly
    @TechnicKingsly 12 дней назад

    Ngati zenzen2

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 12 дней назад

    Now you are the Dr Usi I know and admire