Anthu awa akuyenera kukwezedwa udindo komaso akufunika chitetezo.....mulungu oziwa kusamala akutetezeni mu zonse pamodzi ndi ma family anu.... AMEN AND AMEN.U DESERVE AWARDS GUYS.
Tithokoze aT/A ndi Mr. Manjolo polimba mtima kupulumutsa moyo wa mwana ku imfa ngati imeneyi. Enatu anakakonda ndalama kusiyana ndi moyo wa munthu. God bless you.
Mmmmm! MR MANJOLO and the headman they need to be on the better position and please my fellow youths do not be influenced in such calectors even if things can be bad in life try your best to do the right thing like what MR MANJOLO and the village HEADMAN.
Dziko la Malawi atulusidwa amenewo, chisanzo nachimpanti anamutulusa kale Ali kuno ku South Africa, nkhani ngati zimenezi athu m'boma zimakhala kuti zikuwakhuza
That's great, we need such good and courageous chiefs like this one. God bless.
TA you are more a patriotic citizen.May God bless you.Malawi is lacking such leaders even in religious and political fields.
Ulemu wanu manjolo and hands up to Ta. TA you are wise like king Solomon may God bless you with more wisdom
Anthu awa akuyenera kukwezedwa udindo komaso akufunika chitetezo.....mulungu oziwa kusamala akutetezeni mu zonse pamodzi ndi ma family anu.... AMEN AND AMEN.U DESERVE AWARDS GUYS.
😭😭😭😭YESU akuchedweranji kubwera koma?AMBUYE akudalitseni A/T ndipo akupatseni moyo wautali and Mr manjolo God bless you mukhale wotetedzedwa anthuwa
Ambuye akule ife tichepe mmm anthu akuopysa kuposa mkango
Nde amati A/T
My God bless you mr manjolo ndi
T/A mukhale ndi moyo fumu❤
This guy is really true Malawian legend.. Wapulumutsa moyo wamwana. The government should recognise him, awards is coming bro
For sure 😊
Koma zoona this man must be recognized as a legent
Mulungu akudalitseni amfumu ndi manjolo
Mumagula inu guys
Anakakhara Ngati Maiko anzathuwa aindithu anakapangapo kachithokodzo ndithu kooneka pa Mfumuyi NDI azakewa Koma🤔mmmm h Malawi a Magadzi mmmm ndukaika anakakhala mwina NDI dzina Lina otsati Malawi coz ma🔥gahena mmmmmh ayi ndithu kuteloko lakwiya bomalo akumipandoko 😂😂😂😂😂😂 Kuti ena apulumutsetso mwana?coz iwowo NDI👹👿👺kare kupha NDI kuononga 😂😂😂😂😂 wafikapo aise Ma🔥lawi iwe🙌ndakuponyera kukhara ngati unalengapo munthu Malawi👹👿👺🤔😔
Good job Mr Manjolo & T/A❤
Amen Ambuye alemekezeke, amfumu abwino okonda amalawi anzawo!! Ambuye akudalitseni a amfumu
long live amfumu ndi Manjolo..Ambuye akutetezeni
May God bless you all as well as the chief ❤in Aroma 13v1
I like this program. Watching from zambia, Moses
That's ws good pran AMALAWI
Am John from Lusaka Zambia
God bless you manjolo and the T/A for job well done im watching from lusaka zambia❤
Manjolo he deserve an award,,,well done Mr Manjolo and T/A
Really appreciate nkhani izikhala in full video osabisa maina olakwayo ndiokhudzidwawo.
Ngt ku zilipati kubisa mwina amapeka aaah
a T A Mr manjolo mulungu akudalitseni, a T A kuyambira lero ndinu mfumu Solomon.
Mr TA well done mwagwira ntchito mafumu ambiri amakonda ndalama and mchitidwe oterewu umakula chifukwa mafumu amatenga nawo gawo koma Inu simunatero ulemu wanu ndi Mr majolo
Tithokoze aT/A ndi Mr. Manjolo polimba mtima kupulumutsa moyo wa mwana ku imfa ngati imeneyi. Enatu anakakonda ndalama kusiyana ndi moyo wa munthu. God bless you.
You did a great job
Chilungamu chiyende ngati madzi, AT ndi mr manjolo mulungu akudalitseni.
Yes this guy and the TA must gain some thing from the the government for rescued the boys who was about to lose his life,
😂😂,😂koma Lawez 🙌wafikapo eeeh!dzikomo amfumu Mlungu akupatseni moyo wautali ndithu
Manjolo and T/A they deserve a medal
Munabwera Inuyo
Manjolo atetezedwe ndi mwazi wa Yesu
Ndikutha kuwona kuti moyo wake uli pa chiopsezo koma Ambuye wanthu ngwa moyo ndipo ndi mgonjetsì
Mlu dzikomo kwambili mulungu Akudalitseni 🙏🙏 ine ndili Joz
Mafumu a smart❤❤❤
Manjolo akhale wa police am JOHN daka from Lusaka Zambia
Our T/A is great man
If all Malawians were like Manjolo and the TA, such cases could have been on the decrease.
People are very hard hearted.
😭😭😭😭😭 God bless you my brother all the best in your life 🙏
God bless u mr manjolo.
T/A akutetezeni Mulungu ndi manjolo akupatseni moyo wautali
Thanks to the TA for exposing the criminals and protecting the nation
This guy s a hero
thats true your heros boma likuyenera kukuthokozani kuti anthu ena akawona atengelepo phunziro
Pakufunika apasidwe unduna wa za chitetezo mdziko mino.wosati zisilu zomwe chakwera azisankha zija
Mulungu akukwezeni afumu ndakutukulilani muma ja a yehova
Akanagwirisa mawu ot opha nzake aphedwe bas
Very disappointed about this a Malawian killing each other because of money aaaaaash what if this man to be taken to court
Stupid person
Government give thanks to the people for sure they did great job 👏
Inu ndi akatundu odziwa kufufuza nkhani, you deserve a medal
God is revealing himself to people,,,that child is just innocent and God is watching upon him
Ulemu wanu mr manjolo❤❤❤
Boma lichitepo kanthu, big up Manjolo and T/A
Well done Mr T/A
Title of the song please
Great job
Nyimbo anapanga play kuti mwana uja amvere title yake Ndi chani??😢
God bless you
Chochi ndi kumati lamulolonyonga lichoke nooo am saying nooo!!!!! Athuawa akuenela kunyongedwaaja ndiawa for sure ❗❗❗❗❗❗❓❓
That true my bro wapha mzake naye aphedwe chifukwa kuchotsa moyo wamzako sichinthu chapafupi
Keep it up Manjolo and T/A. May the almighty God, bless both of you.
Nanga Judgement yatha bwanji? Nanga anthu 5 womwe akugulisapo ndi ati? Amagulitsira kuti? Nanga anthu amenene anagula Boma lichita nawo chiyani? We need Justice. Manjolo Ambuye Akudalitse komanso a T.A pamaganizo yawo ya bwino yofuna munthu wamoyo, tikana luza mwana.
Yall deserve honors
Munthu amene anafika kwa munthu wachilungamo amene anauza aT/A ndiye amene wachilungamo zikomo
Mwana obweresa nxakeyu asatuluke cz anauyamba kale
GOOD JOB BRO🙏
Well-done Manojolo
Afumu anzelu mulungu akudalitseni
Jesus
Tidziwe bwino lomwe kuti ziwalazo zimagwira ntchito yanji?
Good job may God bless you guys
After so many years now the secret is out, my question is is the police keep secrets also?
Ndukuuzani aname what a sad story
They do most of them ma deal awawa amapanga nawo
on my way to Mr manjolo and Mr T/A they deserve it🏃🏃
Strong man manjolo💪
Manjolo u are a king
Nkhani yogulisa ziwalo zinayamba kale kale ndipo ine ndikukumbukira boma likuopyeza anthu kuti anthu asiye kunena boza kuchitisa anthu anzao mantha. Pano anthu ngati Manjolo ndi a T/A ndi osowa. Nchitidwe umenewu uthe mulungu achite nao opha anthu .
Zikomo a Ntola nkhani Ambuye akutsogolereni mu nchito imenei. Mwapulumusa ena.
Ine ndimaona kuti boma litenge mbali ogula ndiogulitsa azirandira chirango chachikuru
Zikomo kwa bwana TA and the team who helped to rescue the boy
Kodi nkhaniyi idatha bwanj???
Boma lidachtapo chan
Dziwalo zimapita ku boma asaname
Malawi akufunika atsogoleri ngati awa agog Mulungu akudaliseni
Thyolo chilazulo maboma aukape kwambiri kamalawi watunthu alomwe zisiru zokonda kupha anthu moyo wawo ndi waku Mozambique basi
Kuyankhula mopusa kwinako anthu saphana mxieeee
Mbola yanu malowesa ndale ndikusankhana mitundu eti anthu akuchikwawatu kuthyolo ndikubwalo
mboliyanu amwene dikila timuchose chakwela matumbo
Mmmmm! MR MANJOLO and the headman they need to be on the better position and please my fellow youths do not be influenced in such calectors even if things can be bad in life try your best to do the right thing like what MR MANJOLO and the village HEADMAN.
Amfumu ndi Manjolo apanga zaumunthu. Boma liwathokoze basi
It's really fine
Dziko la Malawi atulusidwa amenewo, chisanzo nachimpanti anamutulusa kale Ali kuno ku South Africa, nkhani ngati zimenezi athu m'boma zimakhala kuti zikuwakhuza
So touching
Bwana minjolo ulemu wanu ndipo mu kufunika kukhala wa police
. iyi ndi program ya bwino.isathere pa njila.( Ndine chikumbutso Sande : ck/T/A NGABU ,GVH SANDE ll SAOPA.
Malawi is no longer at ease.Laws have to revised
Anthu oterewa akuyenera kukalowa mundane moyo wawo onse chifukwa ndizoipa kupha munthu osalakwa
T/A ndi mr manjolo muyenera kulandila award, boma liyenera kukuganizirani, tsoka boma lathuli ndilopondereza
Tikuyeneradi kudziwa mmene chigemulo chakukhoti chinayendera abale inu
Ooooo my god 🤔🤔🤔🤔kama amalawi 🇲🇼 mmmmm
Ineyo ndikuyamika a T/A ndi A police amumudzi mulungu awa tsogolele
Mmmmmmm My god 😢😢😢
Don't forget the big buyer also hails from the same.........'.............
Mukuloleranji ambuye anthu oipa mtima awa azichita bwino dziko lolenga nokha
Chonena ndilibe 😭😭😭
Please those who are doing this dirty thing should face the law.
Malamulo nkhumi amulungu;Usaphe ";
Big up to Mr manjolo and the t.a, 4such a good job done.❤
Amalawi tiyeni tigwilane manja kupewa nkadza Kwa abale athu tiyeni tikondani wina ndinzache
A tiye Wawa ndi anzelu kwambili
Km a T/A awa ngofunika award
Moti zigawenga zija zikanatutumuka manjolo anali pamavuto agulupu aja akanamutembenukilanso kt iweyo mission ija wailepheresa pazifukwa zilibwino ubale wamanjolo ndi a T/A panopa kamba mission yatheka nduthu
Nyamatayu Boma limupase kagalimoto
Mwanayo mudamupeleka kwa makolo wake?
Zimenezo zinali nthawi ya kamuzu,yemwe anali ndi lamulo okupha wina naye aphedwetso.democracy yafika ndi zithu zoipa kwambili.
Koma nanga mabwana omwe amagula Ku nchalo Ku chikwawao tiwadziwe nawo ife kwathu mkomweko
Manjolo wanena zoona kuti boma ndilo vuto lalikulu anthu ena atagwidwa koma pano anamasulidwa
Well amfumu amchacha
True hero
Manjolo deserves a reward from the government
Tili.mmasiku otsiliza 2timonthy3v 1.....end
Mulungu awaonjezere zeru Mr majolo and a T/A