KWAGWANJI KWAYAKA MOTO 16 October 2024 KULIBE KUNYENGELERA |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 окт 2024

Комментарии • 40

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 День назад +7

    Best program forever Times Tv is the best 🔥

  • @BonfaceMpokosa
    @BonfaceMpokosa 2 дня назад +4

    Even the MEC chair herself knows that things are not going fine but seems like she is just there as the name, the salary and allowances only.She is just doing and even said what she always told but in her head knows the truth.
    My God be with our Country, Amen

  • @kadijachilwan967
    @kadijachilwan967 День назад

    Munatiyankhulira gyz keep it up ndipo mulibembali

  • @AkimChangaya
    @AkimChangaya 20 часов назад

    andevu mumayamkhura moveka mogwira mtima mwachikond kmaso mwachilungmo

  • @MuhamadYassin-ye4hn
    @MuhamadYassin-ye4hn 2 дня назад +2

    Ashibale ashinawanda amenewo akunama ndithu

  • @RemitterFlik1130
    @RemitterFlik1130 День назад +1

    Mmmm asaname sakumalemba zolongosoka anthu timangobwezedwa kuti chimatchini chaonongeka

  • @NAKHWAIYANA
    @NAKHWAIYANA День назад

    Mphatso Sambo ukuzitenga ngati wochenjela kuposa Atimes Machendeako

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o День назад +2

    Kodi jene ansa anali wadpp bwanji sananene kuti uyu ndi wadpp adpp mwachulusa zonena

  • @HaroonMKWANDA-r4x
    @HaroonMKWANDA-r4x День назад

    NRB chilungamo chikukuvutani ma guy 2018-2020 MEC and NRB amagwilira ntchito limodzi and applications form ija ya NRB sticker ija imatuluka pompo pompo 😅

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o День назад

    Nkhani ndiyoti winaaliyense akalembetse mu kaundula wa chisankho basi. Nkhani ndiyoti umboni ulionse ukagwile ntchito, ngakhake chikalata chakwamfumu .

  • @elijahkasawala9122
    @elijahkasawala9122 День назад

    DPP yaluza tisanavote😂😂😂😂

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 День назад

    Kikikikik koma Brian amaziwa kutsila mchere😂😂😂😂

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam День назад

    Inu kupoto ndikubwela kulibe athu ochuluka ndikubwela ndiye sitheka bwanj kuchuluka athu ku central ndikupoto 2m kumwela 8k koma mcp anjaila kwambili amec agulidwa ndj nrb agulidwa ndi mcp uyuyu wameyu wagulidwaso koma mcp isalowe boma mulungu yankhani pembezelo langa

  • @allahslave7177
    @allahslave7177 День назад +1

    BT anthu osakwana even 1 mita eti koma LL ndiye mpaka kuthamangira 2 mita eeeeeee kuli zinthu eti !!!!

    • @JulietMunthali-g9b
      @JulietMunthali-g9b День назад

      I don't understand why Lilongwe mean ku BT anthu aliko omwewo basi kkkkkkkkk ayi sizoona ndekutu the hole Malawi anthu ambili amakhala ku Lilongwe zaboza iziiiiiiiii inu mwatani bravo times ❤❤❤❤❤

    • @elijahkasawala9122
      @elijahkasawala9122 День назад

      Akuphatikizatu ndi a 2020 aja

  • @JustinMpunga-c8b
    @JustinMpunga-c8b День назад

    Sakuyankha mfunsolo amenewo abwanawo ayankhe momveka bwino

  • @FrankMakulumiza
    @FrankMakulumiza День назад

    Afotokoze zoona aNRB akapanga zibwana 2025 atiziwa kuti ife sitifuna zibwana tiliononga ndi zipolowe ife si Ana am a 1940 ife ndi a ma 2000 aphunzira mcp sitikuyifuna yatizunza pakwana.

  • @FelistasNkasalaMakumbo
    @FelistasNkasalaMakumbo 19 часов назад

    Ine ndinajambulitsa mu march up to date id sinatulukebe

  • @geoffreykankhomba
    @geoffreykankhomba День назад

    In time of DPP mec and NRB were working hand in hand polembetsa chovotera opanda ID amapita kukalembetsa awa akufuna atisokoneze

  • @faroukmejah.9169
    @faroukmejah.9169 День назад

    Chifukwa chani ku Lilongwe analebesa ambiri more than ma boma ena even osakwana one million ma ndela ena

  • @MosesChazima
    @MosesChazima День назад

    Aziwona RRB amayenda mbali

  • @FloraMakoka-r9i
    @FloraMakoka-r9i День назад +2

    DPP ndi yakuba Jane assah komanso jean mathanga onsewa ndi a DPP panopa onsewa Ali ndi ma udindo kuchipaniko

  • @TrezzarSmart
    @TrezzarSmart День назад

    Iwe wa N R B bwanji kusalima sunabwele kuzalembetsa komaso tikalimbetsa sakumatuluka mukumawasiya kut inuyo

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl День назад

    Agwirizana basi ndi boma kuti abele

  • @SamuelKaphwit
    @SamuelKaphwit День назад

    Kumalawi munthu akawina u president amarephela kuyamba kupanga chitukuko amayamba kupanga ukampen mwalo momanga chitukuko saulosi chilima adalakwa chani inu achakwela kupanda saulosi chilima mukanawina inu relo mukurephela kufotokodza mkhani ya ndege why

  • @allieadam3235
    @allieadam3235 День назад

    Guys mumatiyimirira ndithu,
    Tili ku Pretoria koma timadzitsata through Times

  • @RestarUmi
    @RestarUmi День назад

    Zisiluzi zaonjeza kongoelekeza kubela nde aliyese azipanga zake Malawi muno

  • @Kamwachale
    @Kamwachale День назад

    Where are the ID cards printed. Zokondera ndizaona, umboni ndili nawo Ndithu. Amaweruka 3 okoloko and I even called one of the Officer and all the people that came after 3 o'clock were referred to the district NRB head office

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam День назад

    Aaaa mcp kunena mwachuchu mcp tikufuna mubela ndithu

  • @PhyllisMambo
    @PhyllisMambo День назад

    NRB ikugwira ntchito yawo mokondera nalembesa 2022 koma mpakana pano ID yanga sinabwere ndayendera kutopa akuti zinabwera koma anabwera kuzazitenga kukazisiya ku Lilongwe mwezi uliwonse ndikumayendera koma kumangobwerera phone ndaimba ndaimbaso

  • @MadaMamo
    @MadaMamo День назад +1

    Kwqchematu

  • @saidimwanyali8969
    @saidimwanyali8969 День назад

    Kulilongwe ndikumene ali anthu ochuluka papenepo

  • @DannyMkochi
    @DannyMkochi День назад

    Koma tisayiwale kuti tinapanga mademo kuti dpp yichoke,ndye palibepo wabwino apa

  • @MuhamadYassin-ye4hn
    @MuhamadYassin-ye4hn 2 дня назад

    Sanalembe moenela

  • @PatrickMghogho-go2pn
    @PatrickMghogho-go2pn День назад

    U r waisting