KWANGWANJI - BRIAN BANDA WANG’ALURA MODETSA NKHAWA ANTHU PA TIMES 360

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 17 окт 2024
  • KWANGWANJI - BRIAN BANDA WANG’ALURA MODETSA NKHAWA ANTHU PA TIMES 360

Комментарии • 8

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 21 час назад +2

    Komaditu its a free advice take it or not

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 21 час назад +2

    We're proud of you guys you speak for the people who can't do it

  • @EnockTheu-dp8ep
    @EnockTheu-dp8ep 17 часов назад +1

    Good and free advice

  • @LawrenceMakataNgwira-xt5hv
    @LawrenceMakataNgwira-xt5hv 11 часов назад +1

    Kuno ku Nkhata Bay munthu akafuna kulembesa akuti akhale ndi kalata ya mfumu komaso akhale ndi anthu awiri amene Ali ndi ma ID ngati mboni.
    Ndiye pali chilungamo apa?????

  • @MalizeniOliviaBridan
    @MalizeniOliviaBridan 15 часов назад +1

    Kodi kudandaula kwa zipani zotsutsa chipani cholamulila bwanji safuna kudandaulinao limodzi anzaowa kusonyezakuti iwowa adziwapo kanthu

  • @ruthmpunga6331
    @ruthmpunga6331 17 часов назад +1

    Chachikulu ndi matha komanso akuziwana
    Mavoti a 2025 azakhala aphokonsonso Chifukwa zipani zonse zikufunitsitsa mcp ichoke pa mpando ndiye nkhawa ya a Malawi ndiyakuti zipanizo atsogoleli ake akuchokela chigawo chimodzi
    Ma chair onse angotula pansidi maudindo awo kuti tisavotenso kawiri komanso maphokoso achoke

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 18 часов назад +1

    Koma lets go truth ,apa lamulo likuti bwanji?wopanda ld ayenela kuvota kapena ayi woooo!koma ine kuno ku r.s.a nthawi imene ndidalibe ld i was not allowed to vote.koma pano i do have en ndikuvota.

    • @jomochirwa
      @jomochirwa 18 часов назад

      Wonder is so brilliant ,alibe mbali ngati ine,koma brian esh zikuwoneka kuti uli ndi mbali 😂