KAYA MCP IMADALIRA MYAU.A OPPOSITION NONSE KACITIRENIADEMO KU LUMZU CHIFUKWA KU LUNZU NDI KU CHILEKA KWAO KWA A DALITSO KABAMBE KUCHILEKA NDI KULUNZU.NDI KWA MAKATA ZILIPONSO. NDIYE MADEMOWONSO AKACHOTIDWIRE KU LUNZU.ZIKAKHALA NJUCHU ZIKALENGEDWANSO KUTI ZIPHAPHALITSE A MCP NDI CĤILANGAWA YU
NDIYE A NTANYIWA WAWA MADEMOWO MUDZAZITETEZE NONSE OPANGA MADEMO NDI PEMPHERO LOSWEKA MTIMA KWA YESU MNKHRISTU KWA ATATE MZIMU WOYERA KUTI ALEMEKEZEDWA NDIPO MUGWORITSE ZITSAMBANSO REFER REVEALTION 22 VS 1 TO 10 AND VS END KUTI MUTETEZEDWE KUZOOPSYA ZA MCPZO.EG MOSES used his Wooden rod which helped him.all way..
Sindikumvesa,akuphunzisa kabeledwe ka zisankho,otengela brack box kupita nayo kunyumba ya Kamudzu Ndi Mc Falen,mafunso anga nao,Kodi zakuphedwa kwa mai ake kuchikangawa,sizikunkhuza?akuthandiza chipani chomwe chamuphera mai ake kuti chipitililebe kulamula?mmmmm sizikundimvekela bwino apa pokha
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa God bless you sir
😅🎉kkkkk
Limpopo you are the best
Let's gathering here please
Mwana ameneyo zake zimenezo
😂😂😂😂
Koma chipanda inu a Mthanyiwa yaaaaa! Kukanavuta tikanatha.
Ndipo mwana ameneyo ndi chitsiru zoona MCP inamuphera Mayi ake basi ndikumatumikiranso
Number one 1⃣ tanyiwa
Zilengwa lengawa😂😂😂😂😂😂😂😂😂 go ahead
MCP ndi yankhadza oook
Ambuye tipulumusen
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Ufiti umenewo nduona ngati ngwabwino......andiphunzitse...
Chimwendo naye ndi kama jekete look at him
😂😂😂😂😂😂😂😂 alongezedwe muthumba ndithu kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Mutu mwake simukugwila Ayi
Zianthuzi ndi zitsiru kwabasi
KAYA MCP IMADALIRA MYAU.A OPPOSITION NONSE KACITIRENIADEMO KU LUMZU CHIFUKWA KU LUNZU NDI KU CHILEKA KWAO KWA A DALITSO KABAMBE KUCHILEKA NDI KULUNZU.NDI KWA MAKATA ZILIPONSO. NDIYE MADEMOWONSO AKACHOTIDWIRE KU LUNZU.ZIKAKHALA NJUCHU ZIKALENGEDWANSO KUTI ZIPHAPHALITSE A MCP NDI CĤILANGAWA YU
NDIYE A NTANYIWA WAWA MADEMOWO MUDZAZITETEZE NONSE OPANGA MADEMO NDI PEMPHERO LOSWEKA MTIMA KWA YESU MNKHRISTU KWA ATATE MZIMU WOYERA KUTI ALEMEKEZEDWA NDIPO MUGWORITSE ZITSAMBANSO REFER REVEALTION 22 VS 1 TO 10 AND VS END KUTI MUTETEZEDWE KUZOOPSYA ZA MCPZO.EG MOSES used his Wooden rod which helped him.all way..
My comrade
Wasala manganyayo
Keep it up mtanyiwa tipulumutseni Ife amalawi
I think mc fallen mutu wake siuli bwino m'malo molila mayi ake ndi izo ayamba kumuwukilazo
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
❤❤❤❤❤
Akulimbuli let's gather here😂
Koma ambuye vumburusani chirichose chiwonekere poyera abare zowona mpakana kumpha anthu wose awa zowona ambuye rowereranipo baba anthuawa ayaruke mzina ra yesu
Mmmh koma mavuto alipo ndithu
Mulungu si Jemus zidziwika
Ndi chifukwa chani anthu ambiri amakonda kugwlitsa ntchito dzina loti mulungu si jemes kodi maina ena kulibe
Achakwela azapenga misala
Mizimu ya anthu 9 osarakwa zonse ziwonekera.
Njuchi not njuchu..akachitidwire not akachotidwire
Sindikumvesa,akuphunzisa kabeledwe ka zisankho,otengela brack box kupita nayo kunyumba ya Kamudzu Ndi Mc Falen,mafunso anga nao,Kodi zakuphedwa kwa mai ake kuchikangawa,sizikunkhuza?akuthandiza chipani chomwe chamuphera mai ake kuti chipitililebe kulamula?mmmmm sizikundimvekela bwino apa pokha
Mwina sizikumukhudza chifukwa ndi step mother not omubereka
😢😢
Kkkkkkkk timakudalirani
Live comrade ntanyiwa
Hi
😭🥱🥱🥱😭😭😭🤷🤷🤞
😭😭😭😭