KUMANGIDWA KWA NTOLANKHANI WA TIMES __4 December 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 11 дек 2024

Комментарии • 254

  • @gmxplayboy6559
    @gmxplayboy6559 8 дней назад +22

    Yaaaa! Yaaaaaa! A Ndevu za Mwayi mwawonetsa chamuna. Anthu awawa akumati apolisiwa osamawasekerera kapena kuwanyengerera

  • @MakabaBauleni-c2i
    @MakabaBauleni-c2i 8 дней назад +16

    Wonder safuna kunyengelera Muthu,vuto mkulu wa police,mkulu wa mdf , mkulu wa MEC , mkulu wa ACB , mkulu wa NRB ndi mkulu wa ma judge onsewa ndi a Mcp nde ife. A Malawi tisayembekedzere kuona ndi kumva zithu za bwino tidzuzika koopsya mpaka titatsitha president ndi cipani September 2025 .Cipanda apo nde mmmmm tidzuzika

  • @giftkayome3568
    @giftkayome3568 8 дней назад +23

    The problem is that police are working for MCP not dziko.

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka 8 дней назад +13

    Wonder you stand for Malawians thus the people we need in our country

  • @RightwellZumbwe
    @RightwellZumbwe 8 дней назад +14

    Andevu zamwiyi kumangidwakwa ntolankhaniyo ikufunika hot kalent muwasambwazebasiiii😂😂😂

  • @dinganinedsontchongwe610
    @dinganinedsontchongwe610 8 дней назад +21

    100% MR wanda just hit the nail on its head kalaya kaya chilaya ndinu munthu waboza

  • @vincentmakotho
    @vincentmakotho 8 дней назад +12

    Ndevu za mwai akanakhala pafupi ndi Peter kalaya akanamupasa khofi 😅😅😅😅😅😅

    • @AliceGeorge-il6ig
      @AliceGeorge-il6ig 7 дней назад +1

      Ndipo zoona,,akanalilandila mbama

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr 7 дней назад +1

      Wonder zachibwana safuna ndipo akanawaswadi awawa. Komansotu a police a Chakwera mutionjeza a Malawi, ilitu ndidziko zinthu zimasintha. DPP inkazunza anthu ndikubowa koma not like this MCP leadership is doing, becareful for what you do cz God is watching 😢

    • @SleepyGolf-wx1wh
      @SleepyGolf-wx1wh 7 дней назад

      Straight

  • @ChipMkombezi
    @ChipMkombezi 7 дней назад +6

    Wandaa. Ulemu wakooo❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ kalaya wachukusapo boza pamenepo

  • @jozyomar5361
    @jozyomar5361 8 дней назад +7

    Mr Wanda 100% wosawopa these people are too much amakhala ngati enafe ndife alendo mudziko lathu Mr what ever sikhani yomaseka iyi be serious at ones for crylound. We pay you.

  • @WhyteSmart
    @WhyteSmart 8 дней назад +9

    Kuyankhula kopanda mantha ndikomwe kukufunika ndipo ndichilungamo

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt 8 дней назад +9

    Ndiponso amakanika kumanga azikwanje aja bAsi ndikumanga munthu ngati uyuu!!.

    • @lacksonsiyadi943
      @lacksonsiyadi943 8 дней назад +2

      Eti eti azikwanje aja osamangidwa koma nkhani za ziiii nde changu afiti achabe chabe awa

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka 8 дней назад +6

    Tikufunika mapemphero pamkhani ya mphezi no body can control that except God the cleator

  • @aubreypiyo-m4k
    @aubreypiyo-m4k 8 дней назад +6

    Comrade Wonder Msisha

  • @MavutoChipanda
    @MavutoChipanda 7 дней назад +4

    Azachitetezo muzikwanisa kukagwila ntchito za emergency popandakudikilila chilolezo kwa bwana ntchito yanu ndikuteteza anthu ndi xolengedwa zonse za mziko nchifukwa munalephela kupita kukafufuza za ngozi ya ndege ku chikangawa podikilila kuuzidwa chochita. Apapa mukuti mukufufuza zakumangidwa kwa ntola nkhani issue is straight forward,wa police waphwanya lamulo apasidwe chilango molingana ndi malamulo anu.

  • @DANIELMakangala
    @DANIELMakangala 8 дней назад +5

    ngat chakwera akuphwanya ufulu wa tolakhani kuli bwanji iwe ndi ine

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363
    @dhaoudhiabedinegomaseko2363 3 дня назад

    Allah titetezeleni ku chilengedwe chanu.
    Imfa siyibisalidwa and kufuna kwa Mulungu kumakwanilitsidwa koma omupempha ndi Mulungu yekhayo chitetezo.
    Kumangochi dzulodzuloli yawomba mphezi mnyumba

  • @MuhammadSamson-yz1kl
    @MuhammadSamson-yz1kl 7 дней назад +2

    Wonder congratulations 👏👏👏 osamanyengelera mbuzi zimenezi

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q 8 дней назад +4

    Nanga za azikwanje aja sanawafufuzebe?

    • @GraciumMdala
      @GraciumMdala 7 дней назад

      Still investigating mweneee till Jesus kufikaa hmmm this ppo aiii

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 8 дней назад +3

    Wonder umakwana and PK nonse ndinu mbambande

  • @aubreygrant99
    @aubreygrant99 7 дней назад +1

    Ndevu zamwayi ngwachikulire❤

  • @worldfamous_23
    @worldfamous_23 8 дней назад +2

    Ok wonderer ipase moto

  • @ShareefKalima
    @ShareefKalima 8 дней назад +2

    Mukufufuzza chan pa nkhan yojambulayi sono azikwanje aja ku Lilongwe mwawachaja zaka zingat? Ali police yanji? Malawi wawola

  • @EsherMike
    @EsherMike 8 дней назад +2

    Kupewa kwa mphedzi the best way is kumudza mwini phedzi Kut akuteteze...tingathe kumvera malangizo a zanyengo Koma opan Jehovah protection will follow you

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 7 дней назад

      Mphedzi zake zathumbazo,,kumachinga,kwa mbere inapha bambo ndi mayi ndikuwosha katundu yense nyumba komatu makolowa anakhala mosiyana mayi amapita kumadzi bambo nyumba ndi ana, what is that's

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 8 дней назад +4

    Police is corrupt in malawi and they take law in their hands.Un profe

  • @kekeaufi9834
    @kekeaufi9834 8 дней назад +2

    *Allahummah sayyiban nafi'an*

  • @HamuzahRoben
    @HamuzahRoben 8 дней назад +4

    Ndemvu zamwayi sanyengelela zopusa😂😂😂

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q 8 дней назад +1

    MDF ,MPS,MEC,NRB plus ACB all from Central region

  • @YasinMmadi
    @YasinMmadi 8 дней назад +2

    We as Malawian should know kuti mziko lathu lino tilibe well qaulified police officers I mean this is from above

  • @FelixMapemba
    @FelixMapemba 8 дней назад +2

    Wonder samafuna zachibwana
    But i can feel the pain

  • @McphersonBedi
    @McphersonBedi 5 дней назад

    😮😮Satana walowa mumphezi kuti anthu asadziwe mntchito yasatana mulungu akule ife tichepe *Amen.

  • @alickkachepa3801
    @alickkachepa3801 8 дней назад +4

    Wanda more fire 🔥

  • @SliviaJosephy
    @SliviaJosephy 7 дней назад +1

    Phedzi izi ndizathumba olo kumachinga,kwachikwewo inapha bambo ndimayi onsewa ananyamula ana,chodabwitsa chakuti ana sanamwalile ,,amalawi tiyeni tizikondana bcz izi sizabwino

  • @hackwellkagolo6614
    @hackwellkagolo6614 8 дней назад +1

    I agree with wonder to ask ngati akutenga thawi pazazing'ono mkotani nanga zazikulu

  • @KalongaWhy
    @KalongaWhy 7 дней назад +1

    Apolice muzingosowa mmozi muona tizamalizili chikangawa maganizo opusa osamanga azikwanje koma apolice inu tiye komatu kuno kunali mademo ku south Africa kumenya Ethiopia chifukwa anapha mmalawi what more kumalawi mukanena zafuti anthu alinazo komaso zimadusa maboda momwemo

  • @FrancisChitsulo-f2d
    @FrancisChitsulo-f2d 7 дней назад +1

    Always anthu awa apolice amazolowera kwambiri ndipo amakonda kuyakhura motero

  • @andreabanda7838
    @andreabanda7838 7 дней назад +1

    Sanakwiye. Koma ndi okhumudya the Malawi police service is working.

  • @JudithKatungwe
    @JudithKatungwe 7 дней назад +1

    Apolice gwirani ntchito yopeleka chitetezo,,osati yophwanya lamulo,,,1 day adzakhala ali m'bale wanu,komanso dziwani kuti kumwamba kuli mulungu

  • @AlexisKantondo
    @AlexisKantondo 8 дней назад +1

    Pk you have mental and physical stamina

  • @chipilirotepulachizuzu6619
    @chipilirotepulachizuzu6619 7 дней назад

    Hats off Wonder Msiska for telling the truth on the matter. Police ya Malawi aaaaa, ili chabe

  • @AlexBanda-w6x
    @AlexBanda-w6x 4 дня назад

    Awa ndatolakhani 🤝

  • @JOHNOlesmasCosmas
    @JOHNOlesmasCosmas 7 дней назад

    Ndevu zamwayi you are represent us❤❤❤

  • @PetersKondana
    @PetersKondana 4 дня назад

    I like Wanderer so much

  • @JamayakoJamayako-rv2he
    @JamayakoJamayako-rv2he 7 дней назад +1

    Following with patient

  • @lewisdicksonmlozi130
    @lewisdicksonmlozi130 8 дней назад +2

    Police ya malawi ndiyomvuta kumvetsa

  • @HassanSaid-q8q
    @HassanSaid-q8q 8 дней назад +2

    Kumwalila kwa anthu pa chifukwa cha phenzi..musadabwe pajatu ndi mCP ndiye sacrifice yawo

  • @ChikumbutsoDzukwa
    @ChikumbutsoDzukwa 3 часа назад

    Ndi wonder ameney safuna zachibwana😂😂

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 7 дней назад +1

    Apolisi a mmalawi kumanga mtolankhani kulephera kumanga zigawenga zazikwabje

  • @JoyceMoyo-mp3de
    @JoyceMoyo-mp3de 7 дней назад +1

    Kukupatsani mpata wa chani iwe police,iweyo panyapako ndithu 😊😢

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 7 дней назад +1

    Mulungu anakwiya ndi usogoreli,wa falawo anatumiza mulili ochuluk,nden vuto ili azitibweresera ndi sogoreliyi

  • @SamsonKhobiri
    @SamsonKhobiri 7 дней назад +1

    Kalaya ndwe mbuzi ya munthu kwambiri, zomwe ukukamba sizikunveka

  • @cassimedward9315
    @cassimedward9315 5 дней назад

    Big up wonder🎉🎉

  • @MichelleSambakunsi
    @MichelleSambakunsi 8 дней назад +3

    Kodi azikwanje aja munafufuza aaaaa

    • @omarlux3434
      @omarlux3434 8 дней назад

      Kkkk akuti akufufuzabe sakuziwa kuti chinachitika ndi. Chani kkk

  • @evansjohn7766
    @evansjohn7766 8 дней назад +2

    Kodi azikwanje aja sanapwanye malamulo?mukuti ukaphwanya malamulo ndimulandu

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l 7 дней назад +1

    Kalaya ndigalu sakuziwa kuti kulikucha ndiusiku

  • @ShareefKalima
    @ShareefKalima 8 дней назад +1

    Apolice kumalawi ko kulibe. chifukwa akusakaniza ndale ndi ntchito yawo zinthu zikhala bwino tikachosa nyasi yilipo yi

  • @abelkayange866
    @abelkayange866 7 дней назад +1

    Koma Times ikuyenera kufunsa pa air nkhani imeneyi?

  • @louisgolden
    @louisgolden 8 дней назад +1

    A wonder boma ili ndila mbuzi olo mutapanga bwanji

  • @emmanuelkwelepeta-uu3dk
    @emmanuelkwelepeta-uu3dk 8 дней назад +1

    Wonder ali pa Hot Current! 😅😅😅

  • @gertudebandah1758
    @gertudebandah1758 8 дней назад +1

    MCP police panopa ufulu unatithela 😮😮😮Ndevu zamwayi atsukuluzeni awa

  • @Saushaba
    @Saushaba 8 дней назад +1

    Wonder msiska katundu muzito

  • @lucianokantchembere6758
    @lucianokantchembere6758 8 дней назад +2

    Ilowe pa hot current ya Isaac Salima yo

  • @ZakiyyaMphiri
    @ZakiyyaMphiri 2 дня назад

    Afinyidwe ameneyu awulule akuzitenga kuti mphavu.

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani 8 дней назад +1

    😂😂😂😂😂koma wanda ndikatundu

  • @LameckGamah
    @LameckGamah 7 дней назад

    This is simple issue I gree the point. 💪

  • @Otisi-t3y
    @Otisi-t3y 8 дней назад +1

    Mkalipileni kalayayo opepera ameneyoo

  • @NelsonMzoma
    @NelsonMzoma 8 дней назад +1

    Chilungamo chija pena pake umakhala ngati mwano

  • @thatgirrroskrr3570
    @thatgirrroskrr3570 8 дней назад +4

    A police pano sabale anthu. Tikwapulana nao 2025 ameneo. Wonder more fire

    • @EdsonMuhango
      @EdsonMuhango 7 дней назад

      Ndiye tilima bwanji ambuye timenyereni nkhondo kuti vula yizigwa bwino tiyeni tipempher kwa kuya mulungu wakwiya

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 7 дней назад

    Inah lilah wainah lilah rajiunah

  • @AnnaPhiri-b8t
    @AnnaPhiri-b8t 7 дней назад

    Zigawenga ndizomwe zili ndiufulu, sizikumangidwa

  • @SteveKanongwa
    @SteveKanongwa 6 дней назад

    Kodi abale sitingakamutenga wonder msisha akuti ndevu zamwai akhale president chifukwa pomwe wafika malawipa tufunika anthu ngt awa osanyengelera zinthu zopusa ai

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 7 дней назад

    good job wonder ndi nzako ❤❤❤

  • @CharlesFeston-r1v
    @CharlesFeston-r1v 7 часов назад

    Kalaya kamaya iww kalayaj ndakuyitana kangati ok

  • @nawenaconstruction
    @nawenaconstruction 8 дней назад

    Ndevu zamwai, p. K mulibhoo heavy

  • @ExtensionWork-vq9pt
    @ExtensionWork-vq9pt 4 дня назад

    Chifukwa chomangira ntola nkhan wa time ndichan amalawi chikuchitika

  • @EdsonMuhango
    @EdsonMuhango 7 дней назад

    Kumwamba ambuye akutiva pemphero lathh lifike kwanh phezi yisawombe atate muli mwambamo ivani pemphero lathu

  • @LoveKasema
    @LoveKasema 7 дней назад

    Wondler,
    Awawa akachedwa nkufufuza kwawoko inuyo mungowaonetsa kuti no one is above the law. It's ether Salima akawasumile as a person or Times ikasume ngati company komanso paja atolankhani ali ndi bungwe lawo, bungwe limeneli lisakhalepo chete please.

  • @RachealPongolani
    @RachealPongolani 7 дней назад

    Malawi mhhhh🙌🙌

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 6 дней назад

    Kalaya akusamalira mchere wake, akudikira yankho kuchokera ku MCP

  • @PreciousKARINGANIZA
    @PreciousKARINGANIZA 7 дней назад

    Apolice amarawi mumagwira tchito ngati ya gogo Anu😢😢

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 6 дней назад

    Nanuso uhule uli tho nkumati kunjaku kuli mulungu osasiya machimo bwanji zinthu zadziko dzasatana kumangochula dzina lamulungu zaziiii

  • @IreenAK
    @IreenAK 6 дней назад

    Maybe we have very high expectations for the Police. Police yokuti it took them 24 hours kuti apeze Doniya 🚁 ya Abwana. Investigation iyoyo itenga 2 days kah 😂😂😂😂

  • @RobertChikawonda
    @RobertChikawonda 7 дней назад

    Apolicetu akufunika kumathila timiyala pang'ono

  • @AliceGeorge-il6ig
    @AliceGeorge-il6ig 7 дней назад

    Mbuzi zimenezi zimasulidwe,,agalu a apolis

  • @daviechapweteka4759
    @daviechapweteka4759 2 дня назад

    Malawi police service panopa , kwachuluka anthu omwe amagwira monama chifukwa saziwa chomwe akupanga , how come mukumanga tolakhani pamene mukugwira naye ntchito limodzi , mufuna azikuwopani, kapena mufuna atolakhani azigwira nthito ma nyumba mokha

  • @KalongaWhy
    @KalongaWhy 7 дней назад

    maeki 47 ali mmalawi momwemo kodi malawi other time will see tizapanga bwanji nkhondo kaya izachitike na ndiulamulilo wachakwera tiyenazo

  • @ChristopherMasamba-bs5ms
    @ChristopherMasamba-bs5ms 7 дней назад

    Kkk bwana kalaya atsekatu
    Koma akudziwa ndithu kut wawoyo walakwitsa paja ma bwanawa kupepetsa amaona kuthipa

  • @WillardMpasu
    @WillardMpasu 7 дней назад

    There's no way that a very simple issue like this akakhale 24hrs kufufuza ...Mr Kalaya is an inspector general..why he couldn't just make a call ndikufufuza kut zinakhala bwanj ..popeza munthuyo ndiwodziwika..

  • @FelistusTaulo
    @FelistusTaulo 7 дней назад

    Palibe chanzelu chomwe akuyankhapo mungotaya nthawi

  • @mayamikocharlie
    @mayamikocharlie 3 дня назад

    Ku MCP kulibe munthu wa chilungamo uku kuli Ng'ona zokha zokha palipose ndale kumaso kuopyseza mzika zadziko

  • @JovitastoloBridane
    @JovitastoloBridane 7 дней назад

    Azanyengo alindimabodza izindizakwamulungu awa ndimbuli amafuna pongodyera ndalama

  • @NelsonMhango-j1d
    @NelsonMhango-j1d 6 дней назад

    Kumenekoooo

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 7 дней назад

    Ndipo malume wonder wakwiyilatu sakucheza ndakalaya

  • @MauriceMukona
    @MauriceMukona 8 дней назад

    Times radio,Zodiak,Born kalindo, Timothy Ntambo, Sylvester Namiwa,Late Dr SKC,PAC ineyo ngati mMalawi ndzakudani moyo wsnga onse .ndinuyo munaika dziko lino pamoto with your 2019 destruction demonstrations

  • @MichaelHastingsGodfreyMvula
    @MichaelHastingsGodfreyMvula 8 дней назад

    Ayambilenso kuika ma Lightening gard nyumba zonse za magetsi. Komanso azitalika kupitilira ma dish a ma TV.

  • @johnfikilini.88
    @johnfikilini.88 5 дней назад

    wapolisiyo sanayakhe mafuso

  • @annembepula
    @annembepula 7 дней назад

    Ulemu wako wonderful umatiyimilila

  • @DeavncKapesi
    @DeavncKapesi 8 дней назад

    Big up mr ndevu zamwayi👊🔥💯

  • @SaedJafari-z7r
    @SaedJafari-z7r 8 дней назад

    Mphenzi it's a natural thing
    Trying to stop mphenzi is the same as trying to stop rain ,, can you??

  • @SailessjuniorTchuwa
    @SailessjuniorTchuwa 7 дней назад

    Koma ziko lathu lanyanya kumanga anthu mopanda zifukwa

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 7 дней назад

    Kalaya yemwe mukuti ndi wa polisi ndi chitsiru komanso apolisi omse ndidzitsiru