DPP MEGA RALLY LIVE - MPAKANA ZAFIKA APA? MUSOWA KUILAMULA NDIRANDE IDZACHITE UPO MCP IKADZABWERASO

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 14 дек 2024

Комментарии • 28

  • @giftlisimba6628
    @giftlisimba6628 5 часов назад +2

    Waiting

  • @CatherineMsaya
    @CatherineMsaya 55 минут назад

    Waiting for nankhumwa to join us

  • @RoseThindwa
    @RoseThindwa 3 часа назад +1

    Boma iloooo 💙💙

  • @handsomenkonde2552
    @handsomenkonde2552 5 часов назад +1

    We here

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 34 минуты назад

    Dpp ma vote

  • @MosesChazima
    @MosesChazima 4 часа назад

    My vote

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 36 минут назад

    Dpp imandiwadza 😂😂😂

  • @JummahBlaqboi
    @JummahBlaqboi 4 часа назад

    Nawoso akuti adzafera mbendera !

  • @AfriStorycom
    @AfriStorycom 4 часа назад

    Kodi bwana Mwanamveka alipompo??

  • @JummahBlaqboi
    @JummahBlaqboi 4 часа назад

    No akulu akulu muphana ndthu kay amoyo adzaziona

  • @BlessingsNdawo
    @BlessingsNdawo 4 часа назад

    Ndiwe galu ndi mcp yakoyo mudakathamangisidwa

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 4 часа назад

    Aaaah mcp boma,boma la mako iwe mbuzi ya munthu iwe

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 4 часа назад

    Amayika muthu pa mpando wa u president ndi mulungu osati anthu muwona chaka chamawa

    • @PatrickTimothyh
      @PatrickTimothyh 3 часа назад

      So you think God choose the wicked to inflict His people? You think God is a dictator??? Mind your tongue buddy when talking about God!

  • @ChizeweEdwin
    @ChizeweEdwin 3 часа назад

    Mcp boma ndare zamutondani

  • @MathewsMakina-z6n
    @MathewsMakina-z6n 4 часа назад

    Mwambi ovuta kwambiri nkazi ofuna mwana sagonandizovala kkkkkk

  • @jirehchiwaya1796
    @jirehchiwaya1796 4 часа назад

    MCP boma

    • @phindiswatshibo7101
      @phindiswatshibo7101 4 часа назад

      Agalu ma plan Anu akungoonekera poyera no secret under the sun mwayaluka muopa chani boma ilo dpp woyeeeeeeeeeeee

    • @ChriNyirenda-he1sx
      @ChriNyirenda-he1sx 3 часа назад

      Boma ndi mapwala akowo

    • @ChriNyirenda-he1sx
      @ChriNyirenda-he1sx 3 часа назад

      Ati boma ndilomweri zapa nkolokolo

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 4 часа назад +1

    Ndipo fetereza wandipangisa kugulisa Njinga ine chifukwa chofuna kugula fetereza ukwerayu mmmm Chakwera must fall down indeed

    • @WelingsLongwe
      @WelingsLongwe 3 часа назад

      Wosadalira zolandila kulimbika kugwira ntchito

    • @NicolasKamunga-rv9vr
      @NicolasKamunga-rv9vr 3 часа назад

      Iwe ndiopusa eti athu tikugwira ntchito koma malipilo ndiomwewo zinthu zikukwera kodi tinene kuti sitikulimbikira kodi?

    • @JACKSONHULUWA-j2n
      @JACKSONHULUWA-j2n 2 часа назад

      @@WelingsLongwe ndani wakuuza kuti tikufuna zolandira? We are saying katundu wakwera not tikufuna za ulere

    • @JafarWiati
      @JafarWiati 2 часа назад

      Koma ziliko

  • @BensonBanda-xo1bz
    @BensonBanda-xo1bz 3 часа назад

    Olo atandithjra doom mkamwa singavotere dpp ,mmangowapuzitsa anthu akundirande