DPP MEGA RALLY - NDIRANDE YAYAKA MOTO KOMA MWATI MCP UKUKU IDZAPITASO?? DPP ILI NDI AMAYI ONG’ALULA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 14 янв 2025

Комментарии • 18

  • @JacobMiley-r4v
    @JacobMiley-r4v Месяц назад +3

    Ma bruez for ever

  • @GeorgeBanda-x6l
    @GeorgeBanda-x6l Месяц назад +4

    mmmm koma ndi anthu kapena njuchi kkkk kkk chimwendo banda ukunva bwanji ndi manganya wakoyo

  • @PatumaCassim
    @PatumaCassim 29 дней назад

    😂😂😂😂koma nde kuli nyimbo ku dpp 😂😂😂

  • @MariaKumwenda-q3c
    @MariaKumwenda-q3c Месяц назад +2

    Bola pamenepo mulungu atithandize amen adadi abwerere pamupando mulu tithandizeni mulungu

  • @DippedJob
    @DippedJob Месяц назад

    Yomweyo ichoooooo

  • @MlambeLodge
    @MlambeLodge 29 дней назад

    Chonde ambuye itsogorereni dpp kuti ibwererenso m'boma

  • @KinziWindasoni-h4b
    @KinziWindasoni-h4b Месяц назад

    Dziko tatenga kale iyi kkkkkkkkk kuli chakwelako akungotsela mmimba

  • @patriciajangaza675
    @patriciajangaza675 Месяц назад +2

    Koma jomo kkkkk ng'ona ilibe mabele kkkkkkk

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 29 дней назад

    Wina akunya manyiii pano kkkkkkkkkkk

  • @EdgarBuleya
    @EdgarBuleya Месяц назад

    kma dpp yayaka moto eeeeee

  • @DoreenLivata
    @DoreenLivata 28 дней назад

    Dpp boma

  • @DippedJob
    @DippedJob Месяц назад

    Koma Jomo iweyo unabwera kkkk

  • @Howa1-t9m
    @Howa1-t9m 29 дней назад

    Mcp yachep

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile Месяц назад

    Chonde ambuye musalore kut dpp yizalamulileso Malawi muno

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 29 дней назад

      Shame ambuye wake uti inuuu😢😢😢 ndakulilirani ndiinu omvesa chisoni

    • @PatumaCassim
      @PatumaCassim 29 дней назад

      😂😂😂mulungu wake wa chakweratu koma osati mulungu yemwe ndikumuziwa ine wa Abraham wakwiya ndi ulamuliro wa chikangawa 😊😊

    • @Maria-nv8ev
      @Maria-nv8ev 28 дней назад +1

      Adadi omweo

    • @NoelTruman-n1k
      @NoelTruman-n1k 7 дней назад

      Mulungu wake utiyo inu