Mr President you said Malawi is for all but why in your cabinet is full of central region where you are coming from?? Why you are choosing your friends, partners, relationships, relatives and your same church people into the different departments others as Malawi embassy in the different countries.??
Aaah za zii panyoo pako chikangawa ndi ndani chisilu chopanda tchito ngati chimenechi. Iweo ndi zako chikangawayo mwachita chani cha mzeru mmalawi muno dzisilu inu?
@kaphika iwe ine si mtundu wamva! Kuteloku sptembe inuo nde muliladi chifukwa bomali tikupeleka kwa ena osati inu mbuzi za anthu mukuona ngati smart matic muyigwilitsa ntchito? Iwe ndi mcp yakoyo panyoo panu anthu opanda ntchito inu
Kape wama president mu Africa we never had in history
Anthu akufuna black box
Our next former president
Kkkkkk koma ase nde wandiwaza bwanji koma zoonadi ukunena zoona
Mbuzi yamunthu 😢😢😢achite mutu rwaaa ngt namzikambeee🙄🙄🙄🙄🙄
Chilembwe sanali munthu oipa mtima komanso wadyera ndi wakuba ngati iweyo chikangawa ndi team yako ai
Mulibe nzeru umu....
Our Next former president good kape sort time is over
Boma loyendesedwa ndi chisilu komanso chigawenga .....munthu woyipa uyu kwambili
Iweyo chakwera matama poyankhula sikuchingawa uku nd mwambo wamaliro okumbukira john chilembwe mfiti iwe uzingothokoza chilima kukuika pampando galu nyau yakupha
Kodi galu iwe Ibrahim Traore siukumuona chinkhope chouma chimutuso chouma mbuzi
Tayankhirani Chichewa inu osamankhara ngati zizunguzo muli nzelu pomwe ndi ziro pa 100
Chimunthu chonyasa kukamwa ndi mtima omwe galu
Amalawi sakufuna English akufuna kudya zazii
Chiksngawa m'manja mwawo muli magazi
Muziyang'anako zomwe akupanga anthu ampingowo, sizikuwasangalasa konse
Panyapanu nonse amene mukuombera manja zithu zasetenu mwava....mukuona gati ife zomwe akuyakhula chitsilu chanucho zikutisangalatsa....nyumba zasete...boma ndilomweli lakokhalira kwanuko eeee....or tikamakamvota muona gati tizikamvota titasidzina kapena masomu atatithilamo sabola....phechepheche mwanjomvu muthu siumadutsamo kachiwili.....amalawi ife sitingamvoterenso iwe wa mcp wamva,,,atakumvotere ndiomwe akukuombera manjawo osati ife ayi wamva
Lero simuphwasula zithufya ? President wazithufya
Congrats Mr President! Chakwera!
Congrats for what ??? Clapping hands for a murder ?? U are also one of them! Mzimu wa chilima ndi athu ena 9 pamutu pakepo
kodi mesa anthu akuyang'ana inuyo chifukwa munatenga udindo ogawa ndrama zathu! Nanga zija munkalonjeza amalawi pa campaign zija. Aaa awa ndochimwitsa bwanji? Achokepo akuluwa pampando zawakanika
Mr President you said Malawi is for all but why in your cabinet is full of central region where you are coming from??
Why you are choosing your friends, partners, relationships, relatives and your same church people into the different departments others as Malawi embassy in the different countries.??
Tachiwoneleni kuchikamwa ngt mbale
Ndie pitala tingamukambe bwanj kukamwa kopanda mano kuja???
..mwapezelapo mwayi olakhula zakukhosi...awuzeni kuti chilembwe ndi uja mudamupha ku chikangawa..
Uyu ndiye watisala amalawi tonse ndinthu
Ngati opephela tu mm
bigy mumakwana boma ndilomweli
Chakwela,akuku dziko lakukanikani,just resign before the elections chifukwa muzapanga manyazi,palibe ndi Mmalawi olo wamisala yemwe azavotele inu bwana
Koma John adali m'busa osati president end amachita kuwapatsa anthu chochita komanso samapha abale ake ai koma amayanjanitsa
Paja apule wa mwat anakhalapo mbusa pa dziko lapansi pano???
12:35 12: kodi iweyo ukuona ngati AMALAWI mzitsiru??
Palibe fundo yachilimbikiso""
Ndipo kuipa ndimtima omwe ambuye akukukanthe galu iwe
Fundoless dzeru mwa inu a chakwera mulibe
Zopanda mzeru izii tulutsani black box
Akuombera mmanja ndi a Mcp basi
😂😂😂😂😂😂😂 amandinyasila inemo sindimafuna kumva zoyankhula zake
Anthu wonsewo kumbamanja atatuwokha kkkkkkkkk chiguluchosecho zikuwanyasa ngati angokuwatu kt achookeee😂😂😂😂😂😂😂
Kkkk koma ndiye achokeee
Chakwera chikangawa omuphaa chilima , manyazi ulibe ndithu iwe mfiti
Nice speaking Mr president....
ngati Pali munthu opusa ndi chakwela kumbali ya dzelu
Chisilu cha munthu ichi
Kape wa kumalawi we don't want to head your speech ma mphwala Anu Asani maso mwanu ntatopa ndi inu manyi Anu ndamene amakulembela history
Owoneka auzimu koma mphamvu yake adayikana
Iwe ndipo sungafikire pa John tembo iwe ndi chimfiti kwabasi
Iwe usamapangeko comment zaumulungu,akukanthe mulungu mfitiwe
Wayambaso zandale
Kukugendani ndichiziwiso chokuti mwalephera
Kodi amamulembera ma speech Mkulu ameneyu ndani? Sindimatha kuzilumikiza zoyankhula zake amangolowa apa ndi apa poyankhula
amakanika kuti anene straight forward chifukwa chosowa mfundo. Traole uku akungomenya kugwetsa. Siizi ayi
Nonse amene mukunena chakwela mudziyang, ane
Aaah za zii panyoo pako chikangawa ndi ndani chisilu chopanda tchito ngati chimenechi. Iweo ndi zako chikangawayo mwachita chani cha mzeru mmalawi muno dzisilu inu?
@@ChipiliroMsanyama aaaaa nazikambe iwe ukugonaso ndi njala paliwepo
Uyambe iweyo wadziyangana mapwala akowo wamva,,,ndiye tizimalizila ife
@ElizabethDinala iweo ndichitukuko chanji wayika chikangawa ku nyini kwakoko gwape iwe? Pankholo pako ndi chikangawa wakoyo kuphatikizapo mcp yonse anthu opanda tchito inu
@@WarriorKB-l3iine singalimbane ndiiwe ndi agalu azakowo wamva
Galu kwabasi uyu atipha
Chokani inu mgwala wanu chifiti
Mandenga ako iwe amampwala
My president
President wakoyo ndi chisilu ....p0peza zisilu zokhazokha zimachitana support ndiye kuti iwenso ndichisilu ..
Mwauzeni mosabisila kuti nonse inu sisilu
NDIPO umuuzenso wamva
Aflobalomiter....pack akatolika musamale
Mkamwa mwa matewemo
Mulungu akudalitseni a President, great speech. I think Boma ndi lomweli.
Chakwela is a good person but people around Him they're bad
@@hassanchome they are bad I can agree to that, they are not helping him but he is a good President
Iwe panyoo pako boma ndilomweli la mako? Ca mzeru mwapanga mmalawi muno ndicani dzisilu inu?
@@WarriorKB-l3i Mtundu wotukwana basi ndakuziwani, mulira kwambiri posachedwapa September wayandikila.
@kaphika iwe ine si mtundu wamva! Kuteloku sptembe inuo nde muliladi chifukwa bomali tikupeleka kwa ena osati inu mbuzi za anthu mukuona ngati smart matic muyigwilitsa ntchito? Iwe ndi mcp yakoyo panyoo panu anthu opanda ntchito inu
Komatu icici nchotopetsa
Boma ndi lomweri
Boma ndilomweli lakuthumbooo kwamako...utazamvotere chitsilu chizakocho ndiiweyo ndiomwe amaombera manja anja wamva
Uzeleza pera...
Vindere chomene vanthu ivi
Futsek
Tiyambe kumugendano munthalika akuwona ngati ife sititha kugenda timatha tiyambe kumugenda ndiye yanu ndinkhalamba ingathawe tiyambe kubwezela muziwona
galu iwe ulibe dzelu
Musiye kuzunza kumangomanga anzanu , why DPP only?
Amfunse bale mbuzi za anthu izi amalephela kuwamanga nthawi yonseyi awona kuti tayandikila kudzisankho ayamba kumanga a dpp sinanga akuwaopa
Ichichimandi nyazabwa
Magalasi m'maso, mbuzi ya munthu
Chakwera mboleyake
Panya pako
You just know how to speak English koma kuyenda dziko mulibe mphatso
Nanga bwanji anthu akumangochi kumakanjira mumasalabe mpaka pano simunakhozele nsewu wamakanjira😢😮
Mfundo less
Chisilu cha president nde iwe umasatila yesu osati chikangawa Gali iwe chipha maso basi
Mmesa anthu akati aku thandize ukuwaphanso ndiye ukufuna titani chakwela mwalephera basi ndiye nkhani apa
Chikumbu Mtima chikugwire pamenepo Chilima unamupha uja, Sidick Mia unamupha uja, Kasambara unamupha uja, Shanil Dzimbiri unamupha uja Komanso Anthu Ena Onse kuphatikiza Onse umawachita tintini chakuseliko.
Munthu Woyipa iwe mwana wa njoka Chakwera.
Ukhalepotu mpaka 2050 pa mpandopo tikuonera. Mthudzula Dzithuphya, mphyodza Magazi ndi mikodzo 👹👹🐊🐊
Mpumulo simukaupeza