Nkasa is an artist, he can be hired to go and entertain people at any function. Musamunyoze chifukwa choti wayimba nyimbo ku msonkhano wa chipani chomwe mwina simugwirizana nacho. Next time he can be called to entertain people ku Convention ya UTM, DPP, UDF, AFORD or any other party. So izi nzabhobhoo. 🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Nkasatu ndi oyimba ali ndi ufulu opanga kuti zake zimuthekele nane kwathu ndi ku alomweko koma ndikugwilizana ndi mfundo za chakwela tonse ndife amalawi osayang'anila mitunndu
Tisazabwereleso kuchipani cha family. Amalemela ndi ochepa mudziko...2025 muvutika.koooopa nose achipani cha ma family ichi...dziko linabwerera kwawo. Mistake yamakolo.athu inakozedwa 2019😅😅😅
A Mkasa a Mkasa, munkati Chiyani inu zotamanda a tsogoleri a ndale? Pano mwayambilaso? Aaaaaaa, APA mumuuza chiyani mwini WA luso lanu Mulungu? Mukupitilizabe kumukhumudwitsa ifeso mwatikhumudwitsa. Mwaphwanya lonjezo lanu Mkasa. God for give you. Come back to him my brother Mkasa
Panyake ukavu ungachepako munyumba ya Nkasa wakukhumbako ndalama panji watolako chikwama eeee ndipo ndalama zithu zikuperekeka wayambapo kusewereska Sono ni nyengo yake yakugula wanthu kuti panji vote yingazasangikako so ninjani wangapulikila chindere Cha Joseph
@@actuarialscience2283 you're such a useless person ase,, that's according to me, i haven't said u shld like him too,, drop ur opinion but don't embarrass urself by insulting others..
Ndikumummvetsetsa nkasa akupanga mchere basi ❤️
Mkasa amadziwa kutembenuza chikwangwani! Change goal! Beautiful song, beautiful composition, wise timing!
Kkkkkkkkkk true
Wapanga zimenezo poyang'ana thumbs la ndalama lomwe labooka ku MCP
Miyoyo ikuvina kuyiwala ogogo anga akufa ndi njala
Koma ndalama anakonza ndithu zomwe akuchemererazo za ziiii aaaaah
yomweyoo ,,, wawulesi asadyee ,,, amene salimbikira pa yekha nde zimuwawa ,, dikira chakwera azakulimira ku Munda kwako
Akufuna ndirama ameneyo umphawi wamukwana
Nyimbo ikukoma iyi,, Ife tikunva kukoma Enawo akunva kuwawa eish 🎉🎉🎉🎉
@@mphatsochitimbe2205 🥰🥰🥰🥰💯
Tikumvadi kukoma mcp yomweyo
Wakwiya ndi mfiti 😂😂😂 opha malubino iyaaa
@@mphatsochitimbe2205 kukoma osati maseweraa ,, tiye tithamange pa ground basi
The song deserves a video, nice one in that matter, with all the infrastructures included.
He is brilliant. He supports the President of the day.
❤❤❤ amukasa mamveka tili namwe
Nkasa is an artist, he can be hired to go and entertain people at any function.
Musamunyoze chifukwa choti wayimba nyimbo ku msonkhano wa chipani chomwe mwina simugwirizana nacho.
Next time he can be called to entertain people ku Convention ya UTM, DPP, UDF, AFORD or any other party.
So izi nzabhobhoo. 🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@@martinndawala8125 iwe nde chimunthu choganiza boooo 💯🥰🥰
Nkasa yemweyo 🎉🎉🎉
Chikachepa ponya nkamwa akakhala galu kuyan'gana ndikwake 😂😂😂😂😂 nkasa ndikatundu
@@GeraldChisamba😂😂😂😂
APM 2025 MY VOTE💙💙✅
Komatu Amkasa zandale zizakuphani
Mukaona nyau zikuvina mudziwe kuti wina akutamba masana.
Chipolopolo kumalawi pamaimbidwe mcp wooooyeeee 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 big up
Ulova kupasa nzeru makemu Thomas chibade sananame
Ku MCP zaphweka bola plan ,salute Nkasa panga mchere
It's hot out there! he's doing it for survival
Live
But here is hot less
Exactly 💯
Pamalawi ndalama zilibe ntchito ndithu xikuchita kundindozana ngati akukapereka kuguwa la tcharitchi munthu ndi phuji zoonadi
Ine ndezandisangalatsatu wakwiya ndimfiti😅😅
Nkasa is a legend indeed amatha kuzisaka
😂😂😂 kudzaaapopa apule
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 mkasa yemweyo
We all need money to survive ,,and he is doing this for survival
Ine ndingowerenga ma comment basi 😝🤪🤪🤣🤣🤣🙌
Mkasa afera ndalama
ndukuuzan adha uyu ndi galu kwambili
Nsip@@IzzyAsirndipo ndi mbuzi yayimuna ndithu😅😅😅😅😂😂😂
Mchape wachabe uyu
Ndani safuna ndalama, sanje ayi inu pangani zanu zochita zopezera ndalama
Anaimba Kale lasdema
Nkasatu ndi oyimba ali ndi ufulu opanga kuti zake zimuthekele nane kwathu ndi ku alomweko koma ndikugwilizana ndi mfundo za chakwela tonse ndife amalawi osayang'anila mitunndu
Mkasa samakwera yakuphwa uyu amaonera patali mita akutanthauza china chake chachikulu mawu akulu akoma a kagonera.
Tisazabwereleso kuchipani cha family. Amalemela ndi ochepa mudziko...2025 muvutika.koooopa nose achipani cha ma family ichi...dziko linabwerera kwawo. Mistake yamakolo.athu inakozedwa 2019😅😅😅
Gule uja wayambapo tchito yake🙌😂
Nkasa doesn't know his Password 😅😅osamamutengera.
Brain is the measure of the mind
Atsogoleri kumalawi alibe vuto koma alivuto ndi iwo amavota
Ndikukaika ngati amadziwa chimene akusankha
Chikachepa ikamkamwa 😅😅😅😅😢😢😢😂😂😂🎉 😊😊 akakhala galu kuyqng'ana kwache
APM my vote
A Mkasa a Mkasa, munkati Chiyani inu zotamanda a tsogoleri a ndale? Pano mwayambilaso? Aaaaaaa, APA mumuuza chiyani mwini WA luso lanu Mulungu? Mukupitilizabe kumukhumudwitsa ifeso mwatikhumudwitsa. Mwaphwanya lonjezo lanu Mkasa. God for give you. Come back to him my brother Mkasa
He is a good composer ofcourse nothing he can do it's apart of surviving
😂for the sake of his survival Nyimbo yabwno 😍🥺😅udyapo zambiri aise
Ndiye anthu mukumutukwana vuto lanu ndi chani 🤣🤣🤣 inuso imbani yanu yatamanda adad anu aja 😂😂😂
@@asiatubrown8410 🤣🤣🤣🤣🤣🤣 eti bwaaaa
Komadi sis ayimbe yawo yotamanda nkhalamba yawo adadawo munthu wosatha kuyankhula chichewa nkumati Kodi ndi mmalawi ameneyo akamayankhula ngati waikamo nsima munthalika wakalamba s asiile achinyamata aimilile nkasa yemweyo moto kuti buuuuu olo mumutukwane amalawi inu ndichoncho bola mzanuyo zikumuyendela khalani ndi nsanje wanuyo Kodi add anuwo mukuti akuomboleni mavuto Kodi mayesa analimomwemo Kodi ankatani Kodi mwina amagona ????
@@NancyNyirenda-v9o iyaaa asatikwanepo ife
@@JoziMaulana 😂😂😂😂koma ndaseka
Kkkkkk kumeneko ndikumalawi kuona mfundo zimene akunenazo nyumba za police kkkķkkk
Nkasa sadzamva ndithu😂😂😂😂😂 mmene anamukhomera nthawi ya Amayi😂😂😂😂
Sikale panja amanyodza chakwera lero 😢akumuyimbila nyimbo nkasa sadzatheka
Ndyee akut a pure athetsa njala malawi munooo ayiií ndichfkwa achair adamuwonetse nyekhwee
Nyimbo ya mbembatu moto kuti buuu🔥🔥🔥🔥bomalilo
Nkasa amalemba kusokerela nyimbo with catchy hooks Talented guy, 🎉
Eya akugwiradi nthito zabwino zokupha, kuononga,kugwesa ndalama komanso kugwesa ndenge
Mmmm kutaya a Malawi, kodi nyau imavita???
Fungo losamva perfume lija latha 😂😂😂 zipange ndalamazo but chakwera alibe mbili yabhoo
Fungo lija lathadi mwinu
Mmmm 😂😂😂😂😂 kunyoza kwabwanj uku mukatero zakunyasan bola akanayimba zochemelera ena aja 😂😂😂😂
So sad mulomwe dzathu mkasa mwati mukuchemelela chani,eeee Koma ndalama ndisatana
Chakwera my vote
Nyimbo yo it doesn't matter,what matters ndi thumba walandira kuti apezeke pa stage.
Uyu ndee mnthu panopa aliyese amapanga zomwe mtima wake afuna
Wadyera uyuuu mmmm munthu opanda mbali
Koma ndalama eishiiii ai zikomo koma iziz sizachilendo nkasa akati wadya kwao ndindale basi mapazi ake
Amene akulowa chaka chammawa sitidzalola kuti udzamuimbile nyimbo chifukwa mbali yomwe uli sitikuiziwa
Zaziiiii nyimbo mumati yabwinoyo ndiimeneyiyi aaaa kupusa ubwino wake chilichonseso chakwera
Nkasa same same Brown Mpinganjira kumangopanga zokuthandiza that time basi😂😂😂😂
Awaso inu imphawi sizinthu aa nyimbooo ,, ntchito yake itii nanu za ziiii
@@PatricaTchuwa kkkkk iwe nde sungawonepodi or chimodzi chifukwa mukati mwakomo mwadzadza nsanje
@@NancyNyirenda-v9o😂😂😂😂😂 nsanje ija anakoza
@@GeraldChisamba ndipo ndi chinthu choipa🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂 koma Nkasa ndi dolo
Ichoooo kuswa kuswa anwene
Eish koma aise ayi sikomo
Kod nkasayo wayiwala koma aziwe kut akamasewela ndi mikango aziwe mikango imadya😢😢😢😢
Akayanjana aleke
Kupanga khobili pa town Mkasa 😂😂😂
😂😂😂ankasa kumeneku mwatola chikwama kkkkkk umphawi sikanthu
Kapena kuopa kupotokoledwa khosi
He loves our president musically
Akasa nayenso kukadyanawo 😂😂😂😂
Kodi mesa ankati sazaimbanso za ndale pa interview ya Brayani Banda
all the best mr president God help you
Ankasa ngati chili chamba kumazimitsira, coz zomwe umanga umakhala ngati sumadzidziwaso wekha, Kodi ndi mtundu wanjinwa munthu uyuuu
Ankasa mumkati simuzaimbaso za ndaletu lero bwanji nanga mmmmm koma umphawi sizithu ataaa
Zachisoni 😮 koma awa
Sanalakwitse, iye ali pa business ndi mmene yabookera kwacha.
Aaaah koma 😂😂
Chindere Cha Joseph chasowa vakuchita chasowa ndalama
Kodi kesa ankati sazaimbanso zotamand andale😢😢😢 aaaaaaaaaaaa!!
Mkasa it's not about poor bt he's crazy seriously
Pure Madness
Bola alandilepo bx ❤❤❤
ANC
RAMAPHOSA MY VOTE KKKKKK. TSEKI CHAKWERA
Panyake ukavu ungachepako munyumba ya Nkasa wakukhumbako ndalama panji watolako chikwama eeee ndipo ndalama zithu zikuperekeka wayambapo kusewereska Sono ni nyengo yake yakugula wanthu kuti panji vote yingazasangikako so ninjani wangapulikila chindere Cha Joseph
I like it 👌
Wasala pang'ono kumwalira uyuu🤣🤣🤣
RIP Lucius Banda
Awa nde azafela zayen srs
Kkkkkk koma mkasa ndiwakuba
Padzana zinali bwino popeza anayimba yotamanda Mfumu yanu. Lero wayipa popeza wachemerera mdani wanu?
Ndizimenezo amalawi mukuononga dziko chifukwa chokonda ndalama maso timva Kuti mkasa ndi vice President. Note that mukuononga dziko koma
Chopusa chidyeleni chikangawa yoeee
Chakwera my favorite 👏🥳
Mukuphwisa ndi pakamwa inu a namanyini.
@@actuarialscience2283 you're such a useless person ase,, that's according to me, i haven't said u shld like him too,, drop ur opinion but don't embarrass urself by insulting others..
Akapusa adyele aise ndi nthawi yako naweerr😂😂😂😂😂😂😂, ndalama zaphweka uku
Legend umakwan 😂
That's why zikukudukirani ufiti kutamba kwambiri
Kuyankhula kwa Anthu ANDALEE amati “there’s no permanent enemy in politics “.
Nde J. Mkasa adzituwa milomo pomwe ku MCP vinyo alipo.
Ngati nditukwane kuti mboli yake ndithu uyu ndi galu kwabas😌😌😌
I don't blame mkasa he has nothing to do for survival iye basi ka 100k ka Andale kamamukwanila kkk
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Amakaka kkkkkk kwao gule
Mmene kulili kumudzi panopa bola kulimbikila ku pephela basi no voti is coming from my familly
Zinazi sizifunika ma Cadet pafupi iyai chifukwa atsegula nazo mumimba
Titenga ngongolezo koma sitibwezaaaa!!!!!
Big up mkasa
Akulu awa dyela lidawakulira
Zinazo pambali koma sound iyi nkasa wapha eeee
Chineke 🙌🙌🙌🙌🙌🤣🤣🤣🤣
koma Mkasaaaaa
May his soul continue rest in piece SKC 💔
Ife mcp ndi boma lathu 2025 motoo❤