Akuyankhula ndikupanga zinthu,NDI zinthu ziwiri zosiyana ,Akabambe anali muboma,NTHAWI yomwe Amalawi anawachosa,ngati anali abwino bwanji anachita kuwachosa,mwina Amalawi timawombera mfiti mumanja,AJoice Banda pompano anati munthu zikakuvuta umakapempha Kwa neba pamene umaona zoti upange, Koma anthu ena amasokoneza Dala zinthu muboma kuti ena agwire njakata, ndibwino apeze njala zawo tione ngati mupiteso kukawawuza kuti musawapasa Mafuta,opposition will oppose,asiyeni inu muli mu Boma pangani zothandiza Amalawi,koma paliso ma tv station ena kaya NDI A opposition kaya,monga Times Tv,NDI ena,ayi musalimbikese umbuli NDI kuti anthu azimanyana .Ndale sikuyankhula mowopseza anthu zimapangisa udani NDI nkhondo,
Gayz ku dpp kumachoka anthu azelu kms kabambe ndi munthu ozindikila zed ndpo fundo za mtogoleli izikhala yogwira mtima kms izi khala yokwanilitsak osat kungo dziwa kuyankhula km osat kupanga zofuna anthu no aple sauthandiza anthu avomelz.
Iwe udali ku DPP nyanja kunalibe? Akulu ngati ndi njala ya u president mugwa nayo chifukwa iweso ndiolephera kale mbuzi nangati kutsutsa kwake kukhale kumeku iwe uli ku RBM sumadziwa kuti ku malawi kuli nyanja?
Mtsogoleli koma ameneyu Mulomwe ndi oganiza bhooo more 🔥🔥🔥🔥 koma osamangoziwa kuyankhula mukalowa mboma kumalephela kupanga zomwe mumalonjeza
More 🔥🔥🔥 mr kabambe ana zawakanika kwawo ndi kuba ,kupha ndikuwononga zikwanje zabwera ndi MCP ndizomwe amakhapira chilima ndi anthu ena 8 aja
We smart people like you Mr Kabambe pls kuyendetsa dziko si chalichi ayi
Well done dalitso kabambe❤🎉
Kabambe is Genius kunena chilungamo
Dzikomo kwambiri poganizira mpoto pa khani ya ma company abwere komaso airport ikozedwe
Keep it up 😊
Amalawi sitikumvesa pati kuti tilibe sogoleri anthu okalamba fertilizer akamutenga kutiko
Koma chakwera mwamupanikizatu 😂😂😂
I like this man
Tili ndi president koma wosati tsogoleri…😟
Amalawi tikokole kuti mbuli iyi ipitile kuti lamulila alibe nzeru, saziwa makaka kuti kukhala Mtsogoleri wa dziko kumafuni channi
Kabambe nd number one
Kabambe is very intelligent eehhhh
Kabambe ndi number one
Koma chisilu Anabel uzatinyase apq makina anu ayamba kugwira ntchito zopano poti abwerela kwanu kulilongwe sopano akupanga changu makina anu omwe kumwela asamafuna kulemba anthu pakati alibweno tsopano makina anuwo ndeno tichoke kumwela tipite kulilongwe tikalembetse chifukwa ndikomwe akugwirila ntchito sopano
Chakwera akuti sikomanda wa police
Uyu wachita misala ndithu
The president akangosankhidwa amakhala mkulu wa sitikali ndi apolisi
tilibe president sure
Tili mu nyengo wa gule wamkulu tilibe president
Kabambe uli ndi vote yanga kale iwee
Akulu makwana❤
Mfundo less chakwera ngongole mukudziputazi atazabwenze ndani?
Koma inu mukusitha pano munali muboma zikakuvuta nana muthu koma anakoza kkkkk
Koma ngongore zomwe akuziparamura Chakwela u adzabweza ndan?🤔🤔🤔
Ayenda bwino chifukwa ndi kwanu ku Lilongwe zopusa nanga kumwera kumpoto zikuvuta pati
President angadandaulire apolice
Chakwera mutu wake sumagwira ndithu
Kabambe ndi katundu, ndipo Chakwera mutu ngoima suyenda, sakukwanila kukhala President wa dziko ai, kutalitali.
Sitima imaphweka akamayendesa wina
Check Google. Who is the chief in charge of Malawi police service?
😂😂😂koma ndiye
Chakwela apa mfundo palibe ganizani bwino
Tikulamuliridwa ndi gule wa mkulu
Ndiye kuti kuchipani cha mcp kulibe wina aliyense wamzelu ???
Zangokomanako ndondocha zokha zokha
Chakwera vuto ndi lakuti mukuoneka ngati munakwatila hule mkazi wanzelu amadzuzula mwamuna wake
amalawi. asanduka amasikini chifukwa. chakuba kwaboma lachakwela. chiwawacho. akuyambisa ndiye. chisilu. achoke apha. anthu. sogoleli olephela kukhala openphapenpha masikini
DK ❤❤😂😂
Kabambes press briefing was the state national address compared to the pathetic speech by Chakwera
Choncho ndie akukakamila kulamulila ameneyu atichimwisatu
Nzelu zilimo ena kumatama Mcp zitsilu zawanthu
Ndipo uchisiru masewera
Kngoti alephera utsogoreli kukwamwa ngati khumba yopanda m.zeru
Chitsiru Anabel ukuti matchine akupanga changu chifukwa ndimbali yakwanuno
Zitsiru za anthu izi zalemphera kuyendesa boma kuba
President chakwela ndi mbuzi yamunthu watule pasi udindo
Chakwera ndi talimanja pantumbo pano
Koma zikanakhara awine chakwera kuti anthu ena azachite manyazi
Speech ya chakwera zero Pa 10
Akuyankhula ndikupanga zinthu,NDI zinthu ziwiri zosiyana ,Akabambe anali muboma,NTHAWI yomwe Amalawi anawachosa,ngati anali abwino bwanji anachita kuwachosa,mwina Amalawi timawombera mfiti mumanja,AJoice Banda pompano anati munthu zikakuvuta umakapempha Kwa neba pamene umaona zoti upange,
Koma anthu ena amasokoneza Dala zinthu muboma kuti ena agwire njakata, ndibwino apeze njala zawo tione ngati mupiteso kukawawuza kuti musawapasa Mafuta,opposition will oppose,asiyeni inu muli mu Boma pangani zothandiza Amalawi,koma paliso ma tv station ena kaya NDI A opposition kaya,monga Times Tv,NDI ena,ayi musalimbikese umbuli NDI kuti anthu azimanyana .Ndale sikuyankhula mowopseza anthu zimapangisa udani NDI nkhondo,
Ndangwilizana name zithu zinazi ndi sabotage kupanga zoti wina aoneke kape pamene anthu akufa akuvutika ma TV awa ufulu wao unabzola mulingo thawi zonse zokakamba zoipa zokha zoona zithu sizili bwino koma kodi zabwino palibe olo chimodzi ku times akuti kung'alula zithandiza chiyani
Natali manual atuli pansies kod akukamila chiya
Akuoneka wanzerutu kabambeyu
Zimene ananena mpaka pano sindinatole kena kali konse
Palube kuvota....ndikupusa chabe kupusisa amalawi mwantundu utelewu pomwe ntalimanja akudziwa kuti zikathela ku court ndi ma judge omwe atakasankhe owina 2025 election so whay wasting resources for campaign and elections funds pomwe mukudziwa kuti mudzawina already
Gayz ku dpp kumachoka anthu azelu kms kabambe ndi munthu ozindikila zed ndpo fundo za mtogoleli izikhala yogwira mtima kms izi khala yokwanilitsak osat kungo dziwa kuyankhula km osat kupanga zofuna anthu no aple sauthandiza anthu avomelz.
Inu achakwela amasankha kulu wa Police ndi ndani mutiuze?
Mulugu akudaliseni akabambe maso pasogolo musamudandaule usi usiyu sanamalizeno kulidya thupi la Dr saulosi chilima aziona kuti mulugu aliko
Tikumvoterani tione mbali yanu akabambe
KODI CHOMWE MUKULEPHELERA KUMUCHOTSA CHAKWERAYU NDI CHANI?
Iwe udali ku DPP nyanja kunalibe? Akulu ngati ndi njala ya u president mugwa nayo chifukwa iweso ndiolephera kale mbuzi nangati kutsutsa kwake kukhale kumeku iwe uli ku RBM sumadziwa kuti ku malawi kuli nyanja?
Dpp in anabwelesapo njala ngati mene mukupangila agalu inu
Palibepo chazeru chomwe anarakhula
Kabambe moto kuti buuuuuu
Iwe mtali manja manja ataliataliwo usamatipusise sife wana mesa mavot mudaponya kare apa mumangot phimba maso
Mtalimanjao pantumbo pake
DPP inapanga kale zomwezo B
Kunama iwe, mcp out
Dpp sidachirisepo MANYANZI amalawi
Ndpo timadya kutaya msima mkati@@SteynMaduka
Dpp sinabwereko pa podium kumavesa chisono kumapempha
@@GiftMusorola-l2o garu iwe usatinyase mesa mumati mukonza zinthu asatana inu or satana yemwe sadzakukhululukiran mwamposa ziwanda
Mungovutika chakwera is still ruling this country in 2025 to 2030 mudztsimikiza izi zitachitika ,ngati ndikusauka ,tisaukabe mpaka 2030
Osusaboma ones ndimbuzi za anthu
𝑴𝒃𝒖𝒛𝒊 𝒏𝒅𝒊𝒘𝒆 𝒏𝒅𝒊 𝒇𝒂𝒎𝒊𝒍𝒚 𝒚𝒂𝒌𝒘𝒂𝒏𝒖
Amuchita bwino