Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Mastenwo eeh knows how to act
I have loved how Masteniwo handled the whole convey Wow
Ngat uzingopanga daily tu coz umabebesa mandota😂😂
Eeeish ache mandota kumapetoko anangoti ndwiiii 😂😂😂😂
Mastern amenewo kuyambira kale ndi nkhani Zina. Proud of u Mai Chandiyang'ana amatiimilira Ku Namiyango Bangwe
Fire fire mabomba.Che Mandota mukutimvetsa kukoma keep it up
As a matter of fact I lavuzi you Che Mandota 💝💝
iwe ndi dolo ase 😂😂😂 eti amayi muli ndi mwana owoneka bwino😂
😂For the first time che mandota kundiwaza hahahah🔥🔥Masten ndi dolo
Tiyeni tiziwalemekeza anthu akulu akulu ayayaya 😂😂🙌🙌🙌🙌 mqndota
😂😂😂😂akuzensa ngati mtolo wa nsimbe Mandota kunooo😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣Amkulu ku umfiti, kodi ndiwe wamkazi wamuna
KKK zina umangoona waziyamba ndithu. Nice one brother
Koma ndie kathera pafupitu❤😂
Umakwana iweyo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Masten awawa nd one,,I love her 😊
Koma mandota iwe aise siuzatheka serious ndaiwonela ka 10times I wish to see u face to face Inshallah
"As a matter of fact"good actor💥
Zina umangowona waziyamba😂😂😂
Iwe watengaso award 🏅 chaka chino🔥🔥
Kkkkk inu Dr Mandota ndi more fireeeee
Mandotatu ndiwe dolo kwambili
Koma mandota palibetu gemu mudzawine kumangolunza basi😂
Anawawo akut mamawo msawi kkkkkk😂 niyeleyo asimene nayo
Che mandota amwene chonde siku lina tizakhaleko nawo amwene chonde ❤❤🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏
Koman achimwene mutiganisileko 🙏
😂😂😂 puma poyangula mwawonat as matter of fact your are the best iyi lavusi yu too mashiii
Kkkkk ambassador wayikidwa pa phuzi
Love this kuno ku america
Morogeni akuti olo nkhukuyo iwotchedwe sakufuna mukadya masamba😂😂😂😂
One day I wish to be one of your team member ❤
Kumasamala kkkkkk eish! Apa ndi akita akukafadi kkkkkkkk Great lesson. Keep up the god work
Iwe ndidolo
Zina umangoona waziyambatu🤣🤣🤣🤣🤣
Kumu lipilira okamu menyaso 😂😂😂 eeeeh 🙌🙌🙌🙌
Koma mwayamba kutipanga tatigupi tima comedy ti
Maso Award taitetedza bas🎉🎉🎉🎉🎉
Anambewe ndinu number one mumatha chemandota apa mwatinvetsa kukoma Blantyre moto kuti buuuuu
Kkkkkk mayi you wakwanilatuuuu ...unampasa ndalama zingati 😂😂😂komano iweyoo ndi dolooo😅😅😅😅
In love with King Troy's reactions❤😅
😊😊😊 thanks
@@user-tf4wz1mm5r uncle Troy, i see u❤
Keep it up!! Mandota 😂😂😂😂 muli phunziro Mu khaniyi
😂😂😂😂😂 akuti unali kotamba
"As A Matter Of Fact" Munthu Wankulu Kwambiri😅
Komatu apanza anangodekha, amachalira nthawi yoyenera😂😂😂
Ati kodi iwe ndinu amuna kapena wankanz 😂
Akundibalalisa BP mutumu😂😂😂
U r # 1.
Iweyo ase umakwanira koma
Great
Nde tizisamala zotuluka nkamwa maka tikakhala pa gulu la wanthu.Akulu akulu nde akita wafaaaa😄More love and respect for you Che Mandota from Lusaka Zambia 🇿🇲
Nice ❤
King of comedian chemandota... Acting ya Agogowo nde mwakazingiratu bwino ngati soya meat 💥🤣🤣🤣🤣🤣🤣🙏
Nkhope.. iweyo mukuoneka kuti ku ufitiko mumatamba nkhope yakanika kubwelela 😂😂😂😂😂😂
Yiyi ndiye yandisangalasa umanta kkkk
😂😂😂😂 Kodi masten wo ndiakuti
😂😂😂😂 mandota umaganiza mwa thinking iweyo
Iweyo ndidolo
ndizo muzimalize 🤣🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂 mandota kuchenjeletsa akusenzatu akakupanga kanyenya kkkkkk nice ati akundisomoneza bp yanga mmutumu kkkk
Kulongolora nawe 😂😂😂😂😂waziona
Okay ndaseka😂
Kumayankhula mopasana ulemu koma 😂😂😂😂😂😂🎉🎉
Nice one
Chinanchina iyiyi bulasa munaphaaa ndithu, naye Mologeni akati amtuluke munthu😂😂😂😂 alibe kuti tili limosi tuuu😅😅😂😅😂
Aah wangotilawisa iwe😂😂😂
koma yiyi comedy mwapa ndithu
Koma iyi waphamandota umatha pamozi ndi makosana enawo kumeneko
Mwaiche kutama mwenjo kkkkkk
😂😂😂😂😂 nde mwati nkhope yalephela kubwelera kkkkk
Kkkkkkkkk ndota wava bazi
Big up my elder😂😂😂
Munthu wamkulu amayi sangatambe kkkkkkkkkk koma mandota
Amayiwo ndi katundu amatha
Hiiìiiiì ine phwete ndisamalize kuonera🤣🤣🤣🤣
😂😂🤣🤣ndiwe Dolo kwambiri
to say the fact I don't know what walking I your head always ma concept ako amandpasa chidwi. Big up even atenga mbali onse eeeeeeh aziwika okhaokha
Singasiye kuonela ma video ako
Kmatu Mandota iweo unadzaaaa
Che Mendota mudzapalamulatu inu ndukuuzan 😅😅😅😂😂😂
Umapusa ukawanene Masten kt Afiti😂💔
Aka ndikabho man😂
Kma uyu amwene 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂mwazionatu che Mandota....mumakwana inuyo
Koma ndiye ndaseka
Amazing one 👍👍
Nthawi ikumachepa kwambiri. Keep it up guys 😜😜
Koma mwayambaso kupanga ama minutes ochepa bwanj ☹️
Ngat kuli ka Ufa asakanize ndi madzu??😂😂😂😂osat nsima
😂😂😂😂 wakumananazo mandota
Moto unandi 🔥🔥🔥
Good
😂 koma mandota suzatheka ma scandal...nice one
Lifidiyoli linavupikatu muntu wankulu
😂😂😂😂 mbasada 😊😅😅😅
Kkkkkk ndilib chonena
Anzawowo akut ndianthu abwino awowo kkkkkkk
Dope
😂😂😂😂😂😂😂😂 koma ndaseka
Mandota ndi mologeli muzafela m manja mwa anthu 🤣🤣🤣🤣ngani yanguku kkkk mumakwana 💗💗💗💗
🔥🔥actor wafwa
yama legendz🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Mastenwo eeh knows how to act
I have loved how Masteniwo handled the whole convey Wow
Ngat uzingopanga daily tu coz umabebesa mandota😂😂
Eeeish ache mandota kumapetoko anangoti ndwiiii 😂😂😂😂
Mastern amenewo kuyambira kale ndi nkhani Zina. Proud of u Mai Chandiyang'ana amatiimilira Ku Namiyango Bangwe
Fire fire mabomba.
Che Mandota mukutimvetsa kukoma keep it up
As a matter of fact I lavuzi you Che Mandota 💝💝
iwe ndi dolo ase 😂😂😂 eti amayi muli ndi mwana owoneka bwino😂
😂For the first time che mandota kundiwaza hahahah🔥🔥Masten ndi dolo
Tiyeni tiziwalemekeza anthu akulu akulu ayayaya 😂😂🙌🙌🙌🙌 mqndota
😂😂😂😂akuzensa ngati mtolo wa nsimbe Mandota kunooo😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣Amkulu ku umfiti, kodi ndiwe wamkazi wamuna
KKK zina umangoona waziyamba ndithu. Nice one brother
Koma ndie kathera pafupitu❤😂
Umakwana iweyo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Masten awawa nd one,,I love her 😊
Koma mandota iwe aise siuzatheka serious ndaiwonela ka 10times I wish to see u face to face Inshallah
"As a matter of fact"good actor💥
Zina umangowona waziyamba😂😂😂
Iwe watengaso award 🏅 chaka chino🔥🔥
Kkkkk inu Dr Mandota ndi more fireeeee
Mandotatu ndiwe dolo kwambili
Koma mandota palibetu gemu mudzawine kumangolunza basi😂
Anawawo akut mamawo msawi kkkkkk😂 niyeleyo asimene nayo
Che mandota amwene chonde siku lina tizakhaleko nawo amwene chonde ❤❤🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏
Koman achimwene mutiganisileko 🙏
😂😂😂 puma poyangula mwawonat
as matter of fact your are the best
iyi lavusi yu too mashiii
Kkkkk ambassador wayikidwa pa phuzi
Love this kuno ku america
Morogeni akuti olo nkhukuyo iwotchedwe sakufuna mukadya masamba😂😂😂😂
One day I wish to be one of your team member ❤
Kumasamala kkkkkk eish! Apa ndi akita akukafadi kkkkkkkk Great lesson. Keep up the god work
Iwe ndidolo
Zina umangoona waziyambatu🤣🤣🤣🤣🤣
Kumu lipilira okamu menyaso 😂😂😂 eeeeh 🙌🙌🙌🙌
Koma mwayamba kutipanga tatigupi tima comedy ti
Maso Award taitetedza bas🎉🎉🎉🎉🎉
Anambewe ndinu number one mumatha chemandota apa mwatinvetsa kukoma Blantyre moto kuti buuuuu
Kkkkkk mayi you wakwanilatuuuu ...unampasa ndalama zingati 😂😂😂komano iweyoo ndi dolooo😅😅😅😅
In love with King Troy's reactions❤😅
😊😊😊 thanks
@@user-tf4wz1mm5r uncle Troy, i see u❤
Keep it up!! Mandota 😂😂😂😂 muli phunziro Mu khaniyi
😂😂😂😂😂 akuti unali kotamba
"As A Matter Of Fact" Munthu Wankulu Kwambiri😅
Komatu apanza anangodekha, amachalira nthawi yoyenera😂😂😂
Ati kodi iwe ndinu amuna kapena wankanz 😂
Akundibalalisa BP mutumu😂😂😂
U r # 1.
Iweyo ase umakwanira koma
Great
Nde tizisamala zotuluka nkamwa maka tikakhala pa gulu la wanthu.
Akulu akulu nde akita wafaaaa😄
More love and respect for you Che Mandota from Lusaka Zambia 🇿🇲
Nice ❤
King of comedian chemandota... Acting ya Agogowo nde mwakazingiratu bwino ngati soya meat 💥🤣🤣🤣🤣🤣🤣🙏
Nkhope.. iweyo mukuoneka kuti ku ufitiko mumatamba nkhope yakanika kubwelela 😂😂😂😂😂😂
Yiyi ndiye yandisangalasa umanta kkkk
😂😂😂😂 Kodi masten wo ndiakuti
😂😂😂😂 mandota umaganiza mwa thinking iweyo
Iweyo ndidolo
ndizo muzimalize 🤣🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂 mandota kuchenjeletsa akusenzatu akakupanga kanyenya kkkkkk nice ati akundisomoneza bp yanga mmutumu kkkk
Kulongolora nawe 😂😂😂😂😂waziona
Okay ndaseka😂
Kumayankhula mopasana ulemu koma 😂😂😂😂😂😂🎉🎉
Nice one
Chinanchina iyiyi bulasa munaphaaa ndithu, naye Mologeni akati amtuluke munthu😂😂😂😂 alibe kuti tili limosi tuuu😅😅😂😅😂
Aah wangotilawisa iwe😂😂😂
koma yiyi comedy mwapa ndithu
Koma iyi wapha
mandota umatha pamozi ndi makosana enawo kumeneko