BON KALINDO LERO PA 18 OCTOBER 2024 |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 окт 2024

Комментарии • 81

  • @BasheerPhiri
    @BasheerPhiri 13 часов назад

    Timakunyadilani kwambiri ndipo mumuyankhula zinthu zothandidza dziko lathu koma yambani kuchita osamangochita mademo apakamwa. Let's work up My fellow Malawians.

  • @giftmakwale-n5d
    @giftmakwale-n5d 21 час назад +7

    Chilima thought was very clever but his actions proved he was not. He was just emotional, greedy and revengeful. He helped MCP for his own benefit not for the betterment of Malawians. Had it been he was clever, he wouldn't have been stuck to the alliance amidst all those ill-treatments. Look how it ended, he is history now

    • @Sherrie-b5s
      @Sherrie-b5s 21 час назад +1

      Chilima Phuma linamuphetsa

    • @vincentbankam6406
      @vincentbankam6406 20 часов назад +1

      ​@@Sherrie-b5sakanakhala wa phuma sakanalora kukhala vice kwa Chakwera.....
      And kukhala waphuma, did it mean mumuphe?

    • @Sherrie-b5s
      @Sherrie-b5s 20 часов назад

      @@vincentbankam6406 nde phumalo amatani kudikira 2025

    • @Sherrie-b5s
      @Sherrie-b5s 20 часов назад

      Ine ndi wa UTM

    • @LouisChikhadzula-k1k
      @LouisChikhadzula-k1k 19 часов назад

      U must be a fool

  • @IanAllstal
    @IanAllstal 12 часов назад +1

    Mwachidure Tiribe President ife

  • @SandraChibaka
    @SandraChibaka 13 часов назад

    President uyu ndi mafiyaa 😂😂 chikangawa party

  • @richardmahata5523
    @richardmahata5523 23 часа назад +4

    Big up DC the real Man , the Last Man Bon Kalindo

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 22 часа назад +1

    The DC we love you ❤❤ chilungamo chokha ichi, mukunenechi apita bwanji? Mesa anapha ndi iye yemwe chikangawa wo eish mr chakwera alibe nzelu or pangono kom Ambuye ndi wabwin ndithu tsikuli kuzacha, ndithu,

  • @HopeLuwangakaunda
    @HopeLuwangakaunda 18 часов назад

    The last man standing Bon KALINDO mwana oopsa kwambiri ❤❤❤❤

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 18 часов назад

    Ben longwe ali pamankhwala otaliktsa moyo sikukalamba kumenekuja

  • @TottiesJackie
    @TottiesJackie 23 часа назад +1

    Cant wait Mr DC Ndodo ituluke basi

  • @gertudebandah1758
    @gertudebandah1758 19 часов назад

    Ndodo ituluke bs 😮😮chilungamo chokha chokha inuyo mau anu sapita pachabe you're number one

  • @ShamilahSaizi
    @ShamilahSaizi 23 часа назад +3

    Wado Wado emweyo Mr dc

  • @constancemkandawire7378
    @constancemkandawire7378 20 часов назад

    Za dondo tapangani changu pa ground pasanakhe mwazi wina chondeee

  • @GiftNgwira-e8l
    @GiftNgwira-e8l 16 часов назад

    😂😂😂😂😂😂😂 Bon kalindo more fireeeee

  • @TrishaPhiri-x2y
    @TrishaPhiri-x2y 17 часов назад

    The DC ang'alure basi nde zofunika

  • @YasmeenYalabi-b2c
    @YasmeenYalabi-b2c 14 часов назад

    Umaitha pangolin wathu

  • @DadyPatrickMtondo
    @DadyPatrickMtondo 16 часов назад

    kkkkkk! chipongwe😂,mpaka Happiness 😂

  • @DicksonKamwendo-b9f
    @DicksonKamwendo-b9f 21 час назад

    Ndodo ituluke basss mwna ikhoza kuzakhala ngat ya mose ,,kutipulumutsa kwa akadzidzi amenewa

  • @DoriceMagawa
    @DoriceMagawa 22 часа назад +3

    Ovota ndife yeah km ngat apposition sakupangapo kathu ife ndindan. Of course sitikumufuna chakwela km ngat wakoza zobela ife tingatani. Tiyike mmanja mwa ambuye dziko ili kt aweluze ndi mlunguyu

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er 23 часа назад +1

    Mr born kalindo mumakwana ndichoncho ndithu

  • @PatienceHarry-z7h
    @PatienceHarry-z7h 22 часа назад +1

    Kkkkkkkk koma ndiye benirogwe watha gati makatani akuchimbudzi

  • @CosterMustafa-m6h
    @CosterMustafa-m6h 23 часа назад

    Bon kalindo tangotulusani ndodo yanuyo plz aaaa nafenso tatopa naye sono zoona matemba pamsika pakana Mk2000 iii malo oyezatu amenewo kt udye ndiwo yabwino ndy kt 10 pini km Malawi 😢😢

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio 9 часов назад

    Timakunyadilani big

  • @sharifhenderson6982
    @sharifhenderson6982 20 часов назад

    Kutulusa ndodo 😂😂😂😂 Koma DC

  • @MphatsoGeorge
    @MphatsoGeorge 20 часов назад

    Ulemu wanu bwana winiko😊

  • @LastonMmanga-r2u
    @LastonMmanga-r2u 19 часов назад

    Nibe angokhala ngati m'nyawupe mu sowetomu😂😂😂😂😂😂

    • @TakalaniGlenda
      @TakalaniGlenda 13 часов назад

      Ali ku nkhatabay malawi ananena yekha don't lie bro

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 19 часов назад

    Tulusa ndodo DC 🔥😅

  • @Concerned320
    @Concerned320 22 часа назад

    The DC amayankhula za nzeru kwambiri..

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 19 часов назад

    😂😂😂😂 dala dala booooon kalindoooooo the DC

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 22 часа назад

    😂😂😂😂 koma lweyo ayi taa unena Ben Longwe 😂😂😂

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 19 часов назад

    Koma za MACRA nzoona?

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 22 часа назад

    ❤❤❤❤ koma iwe Bon Bon Kalindo😅😅😅

  • @KAYDJAMES
    @KAYDJAMES 21 час назад

    The DC mumakwanila ❤❤❤

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 21 час назад

    😂😂😂😂😂 ndodo ibwere bas

  • @KentWilliam-r2v
    @KentWilliam-r2v 23 часа назад

    ❤❤❤😂😂😊The DC umakwana

  • @VictorMateyu
    @VictorMateyu 23 часа назад

    KKKKKK 🤣🤣 IWE NDI PREDIDENT WATHU BASI ASA

  • @muhammedcharley300
    @muhammedcharley300 22 часа назад

    The D C the only man🎉

  • @MtisungeMoyo
    @MtisungeMoyo 21 час назад

    Umakwana iweyo❤

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 23 часа назад

    itulutseni ndodo Dc tathopa nawo anthuwa

  • @chanjubanda8861
    @chanjubanda8861 23 часа назад

    Ndipo abale just like that basi anthu 9ayiwalidwa ...

  • @RodgerChaula-r5z
    @RodgerChaula-r5z 23 часа назад

    The D C more 🔥

  • @YahayaKondwan-mo8hu
    @YahayaKondwan-mo8hu 19 часов назад

    Kkkkkkk

  • @AbusheGabure-q2y
    @AbusheGabure-q2y 22 часа назад

    🔥 d c

  • @AustinBornface
    @AustinBornface 23 часа назад

    Wado Wado

  • @JohnDon-f1l
    @JohnDon-f1l 23 часа назад

    Umakwana the DC

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 22 часа назад

    😂😂 😂😂😂😂😂😂😂😂 anibe 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @DeviLinya
    @DeviLinya 23 часа назад

    ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 23 часа назад

    Zilibe ntchito zimenezo sizinayambe lero zimenezo

    • @donbastora854
      @donbastora854 23 часа назад

      Woputsa iwe eti

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 21 час назад

      @@donbastora854 amako ndiye opusa

    • @TracyBanda-i2g
      @TracyBanda-i2g 21 час назад

      Osamvera ma v n ADC baba ngat muli MCP muzikomoka ndi bp ndiy at ndodo ikutulukat mufera MCP azanu akupita kuli tsogolo

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 20 часов назад

      @@TracyBanda-i2g phone yo ya kunyini kwa mako kuti ukandiwuze zochita nayo galu iwe panyapako

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u 20 часов назад

      ​@@SaidiMbawa-st6bjiwe galu mwana wa hule unyatu 2025 ambuyako Ali ku maximum zomba prison 😂😂😂

  • @ElsaMalunga
    @ElsaMalunga 23 часа назад

    Mademo kwanu koko ku Dz zopusa zanuzo ayi buzi wakutumaniyo kuno ndi kumachine kwa Mcp samarani km cz mcp iyi ndiyozikonda izi zitivuta ifeyo a Mcp tivutika nawo alomwewa osewa akurakhura lakhulawa ndi alomwe anthu awa kulima ayi km ulesi km kulandira zaurere agulu akumwera mudzirima kd uresi basi zisitu

    • @BeatriceSaulosi
      @BeatriceSaulosi 22 часа назад

      Eeeee mwayakhulatu ngati inu mukugula zotchipa ana a njoka 😢

    • @MaggieCement
      @MaggieCement 22 часа назад

      Kupepera onga uli nkathu mxiiiiiii

    • @ViolaPhiri
      @ViolaPhiri 21 час назад

      Kuzolowera nyau ndi president wakoyo basi ukati Kuzolowera zolandila umawadyetsa ndiwe

    • @BeatriceSaulosi
      @BeatriceSaulosi 21 час назад

      Ndipo inu ku dedza kwawo kulinso athu ambiri olandila za ulere za ziiiii kuyakhula mopusaaa​@@ViolaPhiri

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 20 часов назад

      Nde ngt mkuti mumalima mpunga wabwera bwanji kuchoka ku India?? Alandira ndi alomwe okha ife achewa sitilandira nao?? Kulankhula mopusa basi mmene dziku likuyenderam basi mukagulilidwa data muzilankhula mokhuta ngt uli kokunya kuchimbudzi

  • @SympathyChikwanda-ck7mk
    @SympathyChikwanda-ck7mk 23 часа назад

    Namapephaa

  • @officialturfrican_ent
    @officialturfrican_ent 21 час назад

    This guy must shut up watikolela, Akadongoyamba campaign ya dpp this waste of his time

    • @Kamwachale
      @Kamwachale 9 часов назад

      Better just close your ears, mouth and eyes

  • @BENJAMINNYIRENDA-um9cu
    @BENJAMINNYIRENDA-um9cu 21 час назад

    Kkkkk