KWAVUTA A UTM AKUNG'ALURA UKU MOSAOPA MUNTHU|

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 сен 2024

Комментарии • 39

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz Месяц назад +4

    Imfa ya chilima was very painful ndithu koma let God be da judge

  • @ELIOTMUNYAMAPEPAKAZIZWA
    @ELIOTMUNYAMAPEPAKAZIZWA Месяц назад +2

    Mwayamba kupembeza mafano sopano

  • @user-xg5dg7jj4d
    @user-xg5dg7jj4d Месяц назад +1

    Imfa ya chilima ayensa ngati njila imodzi yopangila kampeni 😢😢😢

  • @JamesMjathu-dg4ep
    @JamesMjathu-dg4ep Месяц назад

    Fredokis Traore Kalua... Mwana wa mkango ndi mkangonso

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 Месяц назад +5

    Voice ngatitu Joyce Banda

  • @user-ln5hw7dn9g
    @user-ln5hw7dn9g Месяц назад +3

    Our Chilima 😢😢😢😢😢

  • @isaachoward6311
    @isaachoward6311 Месяц назад +1

    Spiritualism

  • @user-bw2cv9sd7x
    @user-bw2cv9sd7x Месяц назад

    skc forever 😢😢😢

  • @enocklayelo2316
    @enocklayelo2316 Месяц назад

    Our chilima is still with us, mzimu wake suzafa mwaifeeeeee❤❤❤❤❤❤

  • @brightkwenje-ib7yo
    @brightkwenje-ib7yo Месяц назад +1

    Wakufa sadziwa kanthu palibe munthu mzimu kukhalaso ndi moyo ukamwalira ndale zanu muziwerenga kaye bible

  • @ManalYahya-q6o
    @ManalYahya-q6o Месяц назад +2

    Ndipo mzimu wanu uwakathe onse amene anatengapo gawo pa imfa yanu mzimu wanu uuse muntendere

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 Месяц назад

    Amen indeed mama mzimu wa Chilima ndi mizimu yonse yawanthu aja adafa mu Chikangawa ipitilize kuusa mu mtendere ndipo muzitipempherera 😭😭😭😭

  • @brightkwenje-ib7yo
    @brightkwenje-ib7yo Месяц назад +1

    But the bible says munthu akafa kwake kwatha ndipo palibe kukhalaso ndi moyo kwinakwake , paliponse even mzimu wa munthu ochimwa sungapiteso kumwamba fumbi ku fumbi lidzabwelera

  • @SusanPilingu
    @SusanPilingu Месяц назад

    Musamanene kuti mzimu wa achilima uuse mumtendere achilima sanafe ali pakati pathu mukati wuza kuti anafa bwanji ndi pamene mzimu wawo uwuse mumtendere

  • @user-kt5bq2wg6v
    @user-kt5bq2wg6v 3 дня назад

    Amayi awa awufunika wina apite kukalalikila atembenuke mtima. Awuyankhula Ngati awuzimu koma mmmmm alikutali nda ambuye

  • @user-vx5kv8dz3d
    @user-vx5kv8dz3d Месяц назад

    President aziyambila zaka 21 . Pushani anyamata

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o Месяц назад +3

    You. are. an. Inspiring. lady I have. been impressed here. In chitipa

  • @ChipiliroKasakula
    @ChipiliroKasakula Месяц назад

    Komatu akubanja anena zoti osamapangira campaign dzina laimfa ya yaokondedwa wawo eti

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i Месяц назад

    Mulungu alipo amawopa osafowoka zimu wachilima utiteteza kuzela kwa mpulumusiwathu ambuye ndipo pephelo ndichida chokhacho chogochesela akumidina achina chakwela ndi manganya

  • @DesireLuka-nf5is
    @DesireLuka-nf5is Месяц назад

    💥💥💥💥💥💥💥💪💪💪💪🇲🇼🇲🇼🇲🇼

  • @jogechawa6192
    @jogechawa6192 Месяц назад +1

    Chilima iiiiih ndimamulira

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Месяц назад

    Amene 😭😭😭😭😭mama

  • @Stevekatiwa-tp3oq
    @Stevekatiwa-tp3oq Месяц назад +1

    Chakwela wasemza thembelelo loopsya pamutu Pake ndithj

  • @user-lt3xl7cv5n
    @user-lt3xl7cv5n Месяц назад

    Boma lake litiro ukunenaro

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Месяц назад +1

    Mulungu watsala thawi yochepa mulungu atiyakha mapepala athu ndipo atiyakha posachedwa mulungu sagona saozela

  • @user-rl5zq1qr4d
    @user-rl5zq1qr4d Месяц назад

    Tiphunzire kuyamika Mulungu nthawi zonse ndikuwapemphera chikhululuko nthawi zonse Mulungu ndi yekhayo amene amapereka zimene timamupempha osati munthu kupempha thandizo kwa munthu wakufa palibe kusiyana ndi kupembedza mafano koma kumufunira zabwino amene watisiya ndizoloredwa ndithu koma osati kupempha kwa anthu akufa mwai wina uli wonse ndizosatheka

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Месяц назад

    Chakwela azafa imfa ngati galu sure 🤞🤞 iwe chakwela iwe chakwela ngati Pali anthu akuwuza zopusazi zomwe ukupangazi you ll regret one day and palibe azakuthandiza

  • @user-ld8gb9xm7v
    @user-ld8gb9xm7v Месяц назад

    Ka chakwela wakawa Nadi mubusa nthena

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl Месяц назад +1

    Mayi uyuyu asazakumane ndi chakwera paja chakwera samanyengereraru

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus Месяц назад +1

    Pemphero la mzimayi uyu ayankhidwa ....ndi Mulungudi wa zolengedwa zonse ..osakaika mama...ndi Yemweyu wa Abraham, Isaaac and Jacob (mtendere wa Mwini Chisoni ukhale pa iwo onse)

  • @ChikondiCharles-b4o
    @ChikondiCharles-b4o Месяц назад

    Kuyankhura mwa mnzeru

  • @JamesChiphwanya-tb3tq
    @JamesChiphwanya-tb3tq Месяц назад

    Mwana wa mkango ndi mkango basi Fredo osaopa osafooka ife nga ndiinuyo

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba Месяц назад

    Chakwela wafika pobowa akakhala zothela kuswana naye boxing nnakozeka

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Месяц назад

    Uchisilu kodi munthu akafa amavaso or zimu wake ungagwile ntchito

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Месяц назад +4

    Iiii MCP ili NDIMAMVUTO MAGALIMOTO NDI NDIMAYETSA AMAGULA ALIPODZI NDE BWANJI SAMALANDA NTHAWI IMENEYO LELO CHIKWA ATULUKA BOMA NDE ALANDE KKKK KUYAKUKA UKU CHILUNGAMO PALIBE APA WANYANAYO CHAKWELA APATU DZAMVUTA