Zipani Zinalandila Ndalama Ya Chipepeso? Why??? 😯

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 22 дек 2024

Комментарии • 23

  • @MdokaJames
    @MdokaJames 2 дня назад

    iwe ndiwa DPP choka apa

  • @AliNtolera
    @AliNtolera 3 дня назад

    Ayao plus bakili muluzi atupele muluzi ndi mbalame komanso opanda mzeru

  • @Blessings31
    @Blessings31 3 дня назад

    For the sake authenticity,next time time to bring actual words spoken by someone so people knw they are viewing a something which is true

  • @FladielMwase
    @FladielMwase 4 дня назад +1

    Bwanji osapepesa utm or kubanja la malemu skc

  • @kondwanlackson8319
    @kondwanlackson8319 4 дня назад +1

    nanga chipani Dpp sadachipepeseko bwanji

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 4 дня назад +1

    Atupele ndi wadyela ndichifukwa chake samadzudzula boma la mcp atupele sangawine olo atapanga bwanji

  • @muhaspader3593
    @muhaspader3593 3 дня назад

    Kunali kwatseka pakamwa kut asayakhulepo
    Pazaifa ya chilima

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 4 дня назад +1

    Kd munthu akafa mwadxizi afiti onse amangoulurana okha okha ndye sikunati bola moyo timva zambri Mulungu atisungre moyo wina adzaulura yekha yemwe anapha Chilima

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 4 дня назад

    Aaaa mvuto ndi mcp otsati dzipanidzo CHISILU CHAKWLA

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 3 дня назад

    ( Ndalama ) olo yesu alibe nayo mau

  • @EliasKamanga-y8l
    @EliasKamanga-y8l 3 дня назад

    Aku banja 1 m zipani 14 m for what

  • @ThannabMtendere
    @ThannabMtendere 4 дня назад

    Wamanyi uyu dpp muvulala nayo sizawinaso kambakoti ozuzula ambili akulimbana ndi udf osati mcp olo dpp

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 4 дня назад

    Zipani zonse zinalandila ndalama Why mukupatulapo DPP 😂😂😂😂

  • @LinlyMathewe
    @LinlyMathewe 4 дня назад

    Nde chipepeso cha ndalama ku zipani kutanthauza kuti chani???

  • @AbrahamsMlelemba
    @AbrahamsMlelemba 4 дня назад

    Alibe manyazi a malawi

  • @FransBanda-z9g
    @FransBanda-z9g 4 дня назад

    Baseless article

  • @MathewsMakina-z6n
    @MathewsMakina-z6n 4 дня назад

    Pp nayonso ndiyakupha

  • @VeronicaSekobi-is6dk
    @VeronicaSekobi-is6dk 4 дня назад

    ❤🎉