Lake Malawi Yalandidwa Ndi Tanzania Koma Boma Palibe Chomwe Lakambapo, Nanga Chakwera Akuti Bwanji?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 23 дек 2024

Комментарии •

  • @MohemmedSanud-c3o
    @MohemmedSanud-c3o 7 часов назад +4

    Chakwela ndi gululake likudziwapo kanthu

  • @SindisiweMendu
    @SindisiweMendu 7 часов назад +3

    Wagulitsa ndikudabwa kwacha ikungokwela

    • @WiliWili-y2d
      @WiliWili-y2d 5 часов назад

      Kkkkkkk Nawe ikukwera ikugwa wachamba Iwe Eti

  • @benmagulula4522
    @benmagulula4522 8 часов назад +3

    Ziko lathu ndi lomvesa chisoni ndithu chilichonse timangolephera ndithu

  • @KabalideHenz
    @KabalideHenz 4 часа назад

    Mmmmm TZ inathandizila kuma Floods aku Malawi cifukwa amanyengelela kulanda Nyaja🙉

  • @KabalideHenz
    @KabalideHenz 4 часа назад

    Which Boma we dnt hv Government in Malawi😤

  • @EsChinombo
    @EsChinombo 4 часа назад

    Khalangati ulibe fundo sudziwa chomwe ukufuna kuwauza amalawi

  • @AndyKawaliza
    @AndyKawaliza 36 минут назад

    Please God my Lord I berg in the name of Jesus don't let our lake to go like that Amen

  • @OwenMindozo
    @OwenMindozo 2 часа назад

    Chonde a Malawi tsegulani ma Baibulo anu andi kuwerenga buku la Mafumu 21:1-4, God hear our cry we are sinking in deep waters

  • @LISUNGUCKMITHI
    @LISUNGUCKMITHI 7 часов назад +1

    Chakwela uyeza masimba kakhulu

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 9 часов назад +1

    Oh my Malawi

  • @JustinMakoka
    @JustinMakoka 8 часов назад +1

    Akuziwapo kanthu

  • @EmilyNkhonjera
    @EmilyNkhonjera 5 часов назад

    Kuthandiza ndi nyanja sizikugwilizana

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 8 часов назад +1

    Ku Malawi kulibe president chakwera mapwala ake asatiputsitse nyanja wagulitsa

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 9 часов назад +1

    Wagulisa ndlama zake zija amagulira achina Dan Lu

  • @WysonChilonga
    @WysonChilonga 7 часов назад

    aona kuti president wa Malawi mchidzete😢

  • @ShamimaWilliam
    @ShamimaWilliam 7 часов назад

    Dziko lamalawi pamapu athu timaimila nyanja sono chasala ndichani?😂😂poorest country 😢😢😢😢😢

  • @StevenMbera
    @StevenMbera 6 часов назад

    Wagulixa pwala lake chakwela

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 9 часов назад +1

    We have president not leader.... APM tone😂😂😂😂

  • @EmmanuelBonongwe-g2c
    @EmmanuelBonongwe-g2c 7 часов назад

    Only Historians will understand this.

  • @finchiadriano
    @finchiadriano 9 часов назад +2

    Zosatheka nyanja ndiyathu

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 7 часов назад

    Azitola nkhani athu mkuchitapo chani afuseni akumipandawo osamangopanga blame president yet ife tomwe ndamene tikungoonelera zinthu andalewa akamachita manyaka awowa

  • @abdullahmansadia8656
    @abdullahmansadia8656 7 часов назад

    Amalawife kupepha kwaonjeza tikadalirabe uku ndikuyamba

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 8 часов назад

    ALANDA BWANJI MALWYER ATHU ASANAKAMBE MULANDU .MOLINGANA NDI MA RECORD A DR H KAMUZU BANDA

  • @ChisomoBanda-jo4ix
    @ChisomoBanda-jo4ix 9 часов назад

    Boma razitsiru chakwera arimachende rende koma kunyenga Anna ndiko amadziwa iye

  • @BiswickChotsani
    @BiswickChotsani 9 часов назад +1

    Chakwera iwe panyero pako ufune usafune 2025 sukutenga boma!!!!!!!!!

  • @VeronicaSekobi-is6dk
    @VeronicaSekobi-is6dk 9 часов назад

    ❤🎉

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 8 часов назад

    Bvuto losakhala ndi presdent mziko ndilimenelo, tikadakhala kuti tili ndi presdent izi sidzikadacitika koma lero munthu wa mai watilanda nyanja cifukwa tilibe tsogoleri

  • @PhlipsPhi
    @PhlipsPhi 9 часов назад

    Koma sizoona. As big as Tanzania you're not serious Chakwera

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 8 часов назад

    Osatheka chakwera akabweza ndalama imeneo awonaso iyeo ndi dyela yakeyo

  • @GOSH-c8y
    @GOSH-c8y 8 часов назад

    Nkhondo ndi Tanzania sitikwanitsa tingopita kuma court

  • @HwiwhHahaha
    @HwiwhHahaha 8 часов назад

    Just making noise in the society to innocent pple kusikukalalatila otbera what a shame gvt is this

  • @LabKazembe
    @LabKazembe 7 часов назад

    Ndilakwapo apa tisade chakwera koma maudindo onse panya panu nyini zamanu nonse amaudindo abomanu ndipo chakwerayo bumbu lamake

  • @IssahOsiman-ob5ym
    @IssahOsiman-ob5ym 9 часов назад +1

    Zikuchitika chifukwa presented wathu ndi wajela kwambali ndipo ndichizilu kwambali ndpo mapwala ake ndi akwaowose machende ake kwambil 😊

  • @MaryTchapo
    @MaryTchapo 8 часов назад

    Ngat adatithandiza chikhale chifukwa chotibera?

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 9 часов назад +1

    U know what bro, zonsezi because kukhala ndi president osadziwa history ya ziko.ndi,angati ma president alowa pa udindou,izi zosatheka,koma uyu chifukwa cha dyela,ndiye ndi zimenezi.

  • @GiftMusorola-l2o
    @GiftMusorola-l2o 7 часов назад

    Nyanja sinalandidwe

    • @WysonChilonga
      @WysonChilonga 7 часов назад

      mudzimvetsa chichewa nanunso akuti gawo lina, shame on our president 😢😢😢😢

  • @KelvinSamboSambo-m1q
    @KelvinSamboSambo-m1q 8 часов назад

    Zazi

  • @WeaponChilungo-y4i
    @WeaponChilungo-y4i 8 часов назад

    Kodi nanu mwadya chibazi eti!!! Kugawana nyanja kamuzu anati nyanja ndiyathu