Anyamata a zikwanje alephera kuteteza Nyanja ya Malawi.Tanzania yalanda akuona ndi maso

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 21 дек 2024

Комментарии • 387

  • @EvanceHorresie
    @EvanceHorresie 14 часов назад +32

    Area 30 amakwiya koma amawonelela bakili muluzi tv ngankhale amakwiya koma history is the best teacher

  • @mikephiri4092
    @mikephiri4092 14 часов назад +26

    Ifenso TV ndiyomwei sitikusitha❤❤

  • @TysonMwenye
    @TysonMwenye 13 часов назад +18

    Ndewu yomenyana pachibale mumapatsa mpata wadela.Chifukwa ifa yachilima ijatu idaulula chisisi chadziko lonse la Malawi. Nanga mpaka asilikali umayenda wapasi akut upita kokafufuza VP kusowa ndege zonyamula asilikali.Ndiye choncho muona ngat asilikali akumalawi angamenye nkhondo?? Aaa ndiye yolanda makala kuthumatu 😂😂😂 HISTORY IS THE BEST TEACHER BAKILI MULUZI TV ❤ EVER.

    • @joshuaagabu3032
      @joshuaagabu3032 10 часов назад +2

      Tinkanena ife kuti nkhani yangoziyi tikuchedwa kulozana ufiti pali zinthu zimene zaululika zoti tikonze Koma ife busy ayi awuje akulhidzidwa ayi kunali ma Israeli kunali magnet and BM TV was one of the proponents of such stories. The issue was kodi ndege Zanthu Za nkhondo zili kuti, bwanji Tsiku limelija sizidauluke kukamusanka vice president, as you have asked.

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 6 часов назад

      100 % my dear

    • @TysonMwenye
      @TysonMwenye 5 часов назад +2

      @@joshuaagabu3032 ukati tinkachedwa ndikulozana ufiti ukutanthazanji? Potitu kulozana zala kudadza kutengera ndimomwe President adaziyendetser kuchoka tsiku lomwe ngozi ija idachitika.Chitsanzo,President ngozi kuidziwa yachitika 10 am koma avekele ine ndiyankhulapo midnight.Komaso asilikali ndi asilikali kufufuza ndege angatenge mpaka 24hrs malo ake amene ajawo poyer ngt pamene paja zoona 🤣🤣

  • @AdyasiMaulana
    @AdyasiMaulana 14 часов назад +11

    History is the best teacher chakwela anabwela kudzapha kuwononga komanso uchigananga ndi ufi

  • @ShayMdoka
    @ShayMdoka 14 часов назад +12

    Ndaipanga lipiti kwa 2tyms best TV ❤❤

  • @CharlesMmanga-v4w
    @CharlesMmanga-v4w 6 часов назад +3

    Amalawi chimene timadziwa nkulimbana tokhatokha lero ndi izi talandidwa nyanja, HISTORY IS THE BEST TEACHER

  • @JamesSaidi-rw6ek
    @JamesSaidi-rw6ek 8 часов назад +11

    Ingotengani Malawi yose tikhake ku tanzania😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

    • @Yoxym
      @Yoxym 5 часов назад

      Iwe nde wangolasa

  • @JumahKanjombi-ug4sh
    @JumahKanjombi-ug4sh 14 часов назад +7

    Ndimadikila inu nchimwene
    History is the best teacher

  • @AffickChaona
    @AffickChaona 13 часов назад +9

    The best TV in Malawi bakiri Muluzi TV

  • @MadalitsoChibisa
    @MadalitsoChibisa 14 часов назад +9

    History is the best teacher

  • @ImranWyson-e9o
    @ImranWyson-e9o 14 часов назад +7

    Ndipange like sir 🎉 you're best content creator ever best TV 🎉🎉❤💯💯

  • @YusufJafali
    @YusufJafali 7 часов назад +4

    Zosakhala bwino chakwera chakwera mmmmmmh ndiye tili ndi mbuzi Zina kuno ku Malawi A police ndi Asilikali eeeehe ogona okhaokha panafika chakwerapa akanakhala mayiko akunja uyu atachosedwa pa mpando ndipo uyu atamupapalitsa ndi makofi 😢😢😢😢 Dziko langa la Malawi ukupita kuti Innah Lillahi Wa Innah Illaihi Rajiun....

  • @ChemandandacassimMilanz
    @ChemandandacassimMilanz 4 часа назад +2

    History is the best teacher sir

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 14 часов назад +4

    History is the best Teacher 👌 👍 ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @JamesKadango-qs3ej
    @JamesKadango-qs3ej 13 часов назад +4

    History is the best teacher 👊

  • @KimulaniImani-z4j
    @KimulaniImani-z4j 13 часов назад +5

    Malawi wanga akupita kut 😭😭🇲🇼 History is the best teacher 💪🏽💪🏽

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w 13 часов назад

      Eee inu sir number 1

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w 13 часов назад

      Iiiiii chakwera watigulisa

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w 13 часов назад

      Bwanji osaitana asilikali aku islaili aja anagwetsa ndege awathandize kulanda nyanjayo

  • @GodsFavourite1
    @GodsFavourite1 13 часов назад +9

    Mmmmh ndakulila Malawi wanga, ukutha ngati silipasi😢

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 7 часов назад

    This is the best teacher
    You open my ears and i gree with you
    Ationa kuti tili wiki zoona
    Mafuta kulibe olo mutapita kukamenya nkhondo
    Mafuta muwatenga kwani
    Forest mulibe mungayite nkhondo inu MCP
    Zimene mukulimbikitsa kwambiri ndi kagulu kazikwanje
    Malo mogula zipangizo za atsilikali

  • @MilajiZondani-h6u
    @MilajiZondani-h6u 14 часов назад +4

    Keep more blessing to you

  • @henryibrahimsailes4638
    @henryibrahimsailes4638 3 часа назад

    Tilibe mtsogoleri ku malawi when they saw those people with panga knifes in public without the police or mdf involved to protect people, satana ameneyu wayalutsa dziko lathu ,history is the best teacher.

  • @AdizzMadizo
    @AdizzMadizo 14 часов назад +2

    History is the best teacher my best tv ever since ❤️ ♥️

  • @IbrahimAbeck-n9u
    @IbrahimAbeck-n9u 14 часов назад +6

    Mpaka timagonatu❤❤

  • @spartalemani4389
    @spartalemani4389 14 часов назад +3

    We're more guys let's der with dem 😢 history is a best teacher

  • @ChisomoKampingo-f3u
    @ChisomoKampingo-f3u 37 минут назад

    History is the best teacher 🎉🎉🎉🎉

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 3 часа назад

    History ndiphuzisi wakulu thax abro

  • @martinkasamba1576
    @martinkasamba1576 13 часов назад +3

    Understandable statement shuwa

  • @JummahNelson
    @JummahNelson 14 часов назад +2

    Welcome to back big man

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 5 часов назад

    Zosayendatu kwabasi.... BM TV forever ili pano kuulura mbiri bas❤

  • @juliusidaho3262
    @juliusidaho3262 14 часов назад +4

    Salute comrades

  • @GivenMuhunga
    @GivenMuhunga 5 часов назад

    I love u daddy bakili muluzi nimakuverani thawi zonse from Zambia

  • @AbdulNyambi
    @AbdulNyambi 5 часов назад

    Full of good history big up Mr bakili muluzi TV

  • @dorothymkandawire
    @dorothymkandawire 4 часа назад

    History indeed is the best teacher, tv of the year 2024.

  • @Mohammed-sk1fy
    @Mohammed-sk1fy 14 часов назад +3

    Nyanja yaputa bas aaaah dziko lathu amalaw tilowela kt ife 😢 😢😢😢😢

  • @SPEARJAMES-r7y
    @SPEARJAMES-r7y 7 часов назад +2

    Pompano akufunika atumize army yathu ndiimene iyenera kuyang'anira dziko lathu ndi zonse tilinawo dziko la Malawi 😢😢😢😮😮

  • @Africaourmotherland
    @Africaourmotherland Час назад

    You are a genius 👏 🙌 ❤️

  • @GiftBonomali
    @GiftBonomali 5 часов назад

    Mwadzuka bwanji sir, ndimakunyadirani ndikamva mau anu❤❤❤❤

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 3 минуты назад

    HISTORY IS THE BEST TEACHER.

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 12 часов назад +3

    Big Up brother ❤❤❤

  • @MdalaJuma-w4j
    @MdalaJuma-w4j 12 часов назад +3

    History is best teache ❤❤❤

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 12 часов назад +2

    Big up brother man!!

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 3 минуты назад

    I support Bakili Muluzi TV

  • @Augustinoblessings
    @Augustinoblessings 14 часов назад +3

    21 seconds ndaona kale izoooo big umakwana ❤❤

  • @VeronicaSuliwa
    @VeronicaSuliwa 6 часов назад

    Abakili muluzi more fire mumatha continue

  • @hendreson
    @hendreson 13 часов назад +3

    U a the best TV

  • @IbrahimJackson-i8h
    @IbrahimJackson-i8h 5 часов назад

    History is the best teacher basi nyanja yapita paubusa paja akoza naposo guys

  • @AbuMussah-wi7gb
    @AbuMussah-wi7gb 3 часа назад

    100% my big boss mashaallah mashaallah mashaallah

  • @KametaClement
    @KametaClement 14 часов назад +2

    Hy bwana wanga ndakusowan hvy❤❤🎉🎉

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 5 часов назад

    Bakili muluzi TV iyi idabwera basi 🎉🎉

  • @JuniorTV1997
    @JuniorTV1997 Час назад

    Long live Bakili Muluzi TV

  • @JosephMakatha
    @JosephMakatha 13 часов назад +3

    Kulumikiza nkhani no discount..mmakwana chief

  • @GILBERTMGJMTUMBULAH
    @GILBERTMGJMTUMBULAH 13 часов назад +2

    Ndikulira nyanja yanthu 😢😢.

  • @YasinterKapinga
    @YasinterKapinga 7 часов назад

    Itsanana yomweyo history is the best teacher 😢😢😢 malawi wanga

  • @AkibuSaidi
    @AkibuSaidi 13 часов назад +2

    ❤❤❤
    Much love

  • @ChikhaondIssah
    @ChikhaondIssah 4 часа назад

    Bakili muluzi tv we following you history is just tiv

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 14 часов назад

    God bless you mr bakili muluzi tv 🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @GogoPreciousChibwanaEP
    @GogoPreciousChibwanaEP 14 часов назад +2

    ❤❤❤❤ Bakili muludzi tv

  • @FelixMwakhula-u8m
    @FelixMwakhula-u8m 6 часов назад

    You are great researcher!

  • @ConnexKhomba
    @ConnexKhomba 3 часа назад

    😂😂😂😂😂 ndine wa police olo chipolo polo samachiziwa maonekedwe

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 3 часа назад

    Pano aliyense akumamvela Bakili Muluzi tv❤

  • @AdamMleke
    @AdamMleke 13 часов назад +2

    ❤❤BM tv komad we Are very weak

  • @LytonGalison
    @LytonGalison 4 часа назад

    Tzichosa zgawenga zmenez ❤❤ bakili tv

  • @MisheckChinjala
    @MisheckChinjala 14 часов назад

    History is best watching from Cape town Stellenbosch ❤

  • @KELVINGezakanjan
    @KELVINGezakanjan 13 часов назад

    All the best Bakili Muluzi Tv 🎉🎉

  • @ChanceZambika
    @ChanceZambika 4 часа назад

    Zabwino zonse boss ❤❤❤❤❤

  • @JahmanJames
    @JahmanJames 4 часа назад

    Bakili muluzi TV number one

  • @JafarAnusa
    @JafarAnusa 14 часов назад

    Ndigone tsopano my best TV ever

  • @junasssabiwa1996
    @junasssabiwa1996 14 часов назад +4

    Bg makwana

  • @ahmedmsume1489
    @ahmedmsume1489 29 минут назад

    Koma ase ndiwe dolo kwambiri & you're qualified to be minister of information

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 7 часов назад

    history is really best teacher

  • @FladielMwase
    @FladielMwase 14 часов назад

    History is the best teacher ❤❤❤❤

  • @ChisomoYosefe
    @ChisomoYosefe 14 часов назад

    history is the best teacher indeed

  • @Aisha-n5e
    @Aisha-n5e 4 часа назад

    Good journalist❤❤❤

  • @SamisonJoseph
    @SamisonJoseph 14 часов назад

    I was waiting for you brother kuti ndinve zoona panopa ndiknkhonza kugona🎉🎉❤❤❤❤ kept up.

  • @JazakaPhiri-j3h
    @JazakaPhiri-j3h 14 часов назад

    ❤❤❤❤❤❤❤ mumakwana100% voice

  • @DennisKankhuni-b8l
    @DennisKankhuni-b8l 14 часов назад

    History is the best teacher😮😮

  • @IkilaIbula
    @IkilaIbula 4 часа назад

    Za bundle sindimadanda cos umandivetsa kukoma ❤❤❤❤❤❤❤

  • @INESAMchisoso
    @INESAMchisoso 14 часов назад

    Following boss and God bless you and protect you ♥️

  • @StephenPhiri-x6g
    @StephenPhiri-x6g 5 часов назад

    Rouder and crear best wishes to you father

  • @Moses51
    @Moses51 3 часа назад

    Only best TV we have in Malawi

  • @JosephPhiri-pw1kt
    @JosephPhiri-pw1kt Час назад

    Malawi ndiziko laring'ono koma kamba nyanja ya maliawi ziko lamalawi ndi lalikuku ndiye Tanzania ndiziko lalikulu munu mu Africa. Nkutenga nyanja Yamalawi yikhala nkhondu yayikulu Zambia 🇿🇲 tinthandizeni. Even we don't have more nuclear weapons but God will be to our side

  • @ChrispinSanudi-d7h
    @ChrispinSanudi-d7h 14 часов назад +4

    Mumakwana bigy

  • @RichardZakaliya
    @RichardZakaliya 13 часов назад +1

    Akuluakulu pa history mmmmm

  • @MemorieMwasinga
    @MemorieMwasinga 5 часов назад

    The best teacher

  • @NovemberMmangathayo
    @NovemberMmangathayo 14 часов назад

    Bwana bakili muluzi tv ❤❤❤❤❤

  • @JasonMailos
    @JasonMailos Час назад

    Mmmmm kalang INE chakwela pathakopeke ndithu, nkhani kulimbana NDI dpp basi

  • @NathanHalineck
    @NathanHalineck 14 часов назад +2

    My best tv

  • @IdrisahChuma
    @IdrisahChuma 5 часов назад

    The best tv in Malawi

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 6 часов назад

    Bakili TV number one good ❤

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 4 часа назад

    History is best 😮

  • @YamiZingani-ij5kj
    @YamiZingani-ij5kj 5 часов назад

    Well analysed

  • @Dee-h7c
    @Dee-h7c 7 часов назад

    LONG LIVE BAKILI MULUZI TV 🎉🎉🎉🎉

  • @JameNdex
    @JameNdex 14 часов назад +2

    First comment

  • @HawaDayton
    @HawaDayton 27 минут назад

    The best teach

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc 5 часов назад

    Chisilu kwabasi chakwera aaaaah, ndipo izi akupangira dara kut ayambise khondo mulandu wakupha upondelezedwe wawusilu waziwa kut zamuvuta akhoza kumangidwa

  • @ElsaMalunga
    @ElsaMalunga 6 часов назад

    Km kuba aMCp cz apapa zovuta achakwera ature pasi udindo ndiye kubwere pure wina oti ateteze nyanja yathu anthu zeru alinazo kt antha kuteteza nyanja km akanyimbi awa makani ntchito kuba matama ziwerewere ndiolephera njara zinthu kukwera kupha ndiye ntchito zasatana ndarira abuye mutithandize amen

  • @HopefulCoralReef-tx4vx
    @HopefulCoralReef-tx4vx 5 часов назад

    Ulemu wanu big man

  • @ShukuranAMadu
    @ShukuranAMadu 14 часов назад +1

    Yachabetu yele🎉🎉🎉

  • @ChristinaJustin-j4c
    @ChristinaJustin-j4c 38 минут назад

    Salute big

  • @lazarousmabote7780
    @lazarousmabote7780 14 часов назад

    Mabote listening 🎧 from Zambia

  • @PeterJafali
    @PeterJafali 13 часов назад +2

    Kkkk kkk 😂machende akoooooooo chakwera