NOTE : WABETSA was recorded last year 2024 before Cretik Released USAZAMB'ISE... he's an artist,he does all genres,incase you'll be wondering what he's doing on a drill song..thank you
A MELLZ MWALAKWISA KU DROPPER THIS SONG COZ YOU HAVE DROP IT AFTER CRETIK WAPANGA TREND AND HE IS A LOCAL ARTIST SO ZOMAMUPASA DRILL ZITHA KUMUCHOSELA MA FANZ COZ MWANAYO MUSAMUIWALISE CHOMWE ANTHU ANAMUKONDERA,,,,COZ TINAMUKONDA COZ OF LOCAL SO ,,,,
Inu man cretik ndi wa drill kuyambira kale iweyo ndi amene usakumuziwa koma cretik ndi mellz apangira zithu zambiri limodzi amamujabura ma vid video kuyambira kale
Nde mwaganiza zoyipanga release pano fukwa watchuka 😅koma kunena chulungamo mumuonongela fan base anthu akanona cretik we expect vibe yomwe watchukila osat izi sizili bho
Inu nde iyeyo sumamuziwatu , zoti drill yake pa channel Africa , amayika uziwa channel O ?? Nde simukumiziwatu iyeyotu..genre yake ndi dril check out lighter shot by mellz emweyo ku MUST..that video imayikidwa pa Trace axse...
Drill nde ndkudya kwake kuposa chitelela chija ndi dolo cretick❤
Kumpanje🏋️
NOTE : WABETSA was recorded last year 2024 before Cretik Released USAZAMB'ISE... he's an artist,he does all genres,incase you'll be wondering what he's doing on a drill song..thank you
Nice concept kms nyimbo ili Hard 🔥🔥🔥🔥🔥
Za harddddd!!!
Zifufu pa nyimbo yaanzanu.... Mellz tracks yabho iyi 🔥🔥
Kaka pumbuyo pa meeeellz
Koma mellz kumpanje iwey ayi umatha
Nyimboyi nde yabaya heve 💥💥💥💯
A mellz muzisinthako style
This is fire they can’t put out, apapa ndudikira Lifidiyo🎉
Nyimbo yachabe 🔥💪🏽
Cholinga mumuyamwe Mwanayu😭😭
Cretik ndiwa Drill kuyambira kale mumuziwe enanu muti amufwifwitsa ndaniyo..pa ujeni mixxiii zili bwino bwino iziiii fire kumpajje
Wabetsa pa repeat 🔁
Hook yokhayo aaah iwe okey credit iiiiih cretik ❤❤❤
Ana achepa
Chinyimbochi chilibho chaniii
Cretik waika bh kolasi
Nice🔥
Aaaaa ase mufuna kusokoneza Mwana yo ndy zichani
I used to know him with "LIGHTER". So in short this ain't to my surprise
Nice
A MELLZ MWALAKWISA KU DROPPER THIS SONG COZ YOU HAVE DROP IT AFTER CRETIK WAPANGA TREND AND HE IS A LOCAL ARTIST SO ZOMAMUPASA DRILL ZITHA KUMUCHOSELA MA FANZ COZ MWANAYO MUSAMUIWALISE CHOMWE ANTHU ANAMUKONDERA,,,,COZ TINAMUKONDA COZ OF LOCAL SO ,,,,
Inu man cretik ndi wa drill kuyambira kale iweyo ndi amene usakumuziwa koma cretik ndi mellz apangira zithu zambiri limodzi amamujabura ma vid video kuyambira kale
Or account wabesa 😂😂😂😂🍾
Akuti wabetsa ndi account yomwe😅😂😂😂
Mwabwela inuyo
😊😊😊
🇲🇼🔥🔥🔥
Kma benadetta 😂😂
Kumpanje
Funa tadekha
Good drill
Nde mwaganiza zoyipanga release pano fukwa watchuka 😅koma kunena chulungamo mumuonongela fan base anthu akanona cretik we expect vibe yomwe watchukila osat izi sizili bho
If you wanted to feature the kid it would be more better jumping on his genre,coz ndiyomwe akumaipweteka osati drill yi
This song is older than those songs....komanso his genre is this one...zinazo wangoyamba kumene..thank you
@@MellzKumpanjeTV ndikape mtayeni
Inu nde iyeyo sumamuziwatu , zoti drill yake pa channel Africa , amayika uziwa channel O ?? Nde simukumiziwatu iyeyotu..genre yake ndi dril check out lighter shot by mellz emweyo ku MUST..that video imayikidwa pa Trace axse...
Subscribed madar
Thank you
Macheen kumpanje