Dr Kabambe please make a joint alliance government with DPP cos your not enough on your on and you will second to president and the president selected will hand over the presidency to you and you will choose your vise from AFORD in my visionary I see that
Dr kabambe is strong man
Vote kabambe🎉🎉
Dr D kabambe ,the best replacement ever
Mr Kabambe very strong leader, let's give him chance to rule the nation
Wachepa
My vote kabambe more
UTM my vote 💥💥💥. DK2025
I respect you kabambe more fire
Njawala is a machine
Kabambe my vote basi....
More fire Kabambe, ndili nganganga pambuyo Pako!
My vote
Kabambe my vote
Kabambe ndi mbambande💥💥💥💥💥💥
My vote Dr kabambe
My vote
Kabambe anabwera kuzakhala
Kabambe nd kasongo😊
Sindikusamala kuti alibe nfundo kaya ndale kwaiye nkumazereeee, koma sindidzavotera anthu amene analamulapo kale, akulamula pano njeeee, vote yanga kwa amene sanalamulepo basi
Iweyo uli ngat ine coz onsewa tawayesa kale DPP inatizuzaso macadet amabowa
Ineso ndidzavotera amene sanayimepo
Ubwino wake vote yakoyo ndiyimodzi nde sadzawinabe oyamba kumenewo 😂
I like your point or ineso vote yanga Mr DK woyeeeeeeee
Ndikugwilizana ndi mawu amenewa ndithu
Best president
President ndiyemweyi, koma ndi mmene pa group palili zachidziwikire kuti APM will be pule. ❤❤❤- Dk vice pule
Waionera patali bwanawe😅
My vote Mr ❤ DK
Chakwera must go .....very very mbolatic
Our own president
Dr Kabambe 2025 boma UTM my vote ❤❤❤❤❤
My vote DK
Much respect to Dr Kabambe 👏
Dk my vote❤❤❤❤❤
My vote ❤❤❤❤❤
Chakwela eeeeee🙌🙌🙌
We move together guys❤❤, we have to be strong.
Uyu bola timuvotere ndi wanzeru ❤
mBEU ya DK NDI YO BELEKA IYI
like the message
More fire Kabambe my vote
SKC oyeeeee!!!
The hope
Kabambe kabambe more fire
My vote 🔥🔥🔥 zokongola
Kabambe my vote 2025
DK....Chokonoka bwino❤
😂😂😂😂
Chobeleka mapasa!!!
Our own
DK🔥🔥
As a shadow mp for UTM, for Zomba Malosa.... tikudikira kuti bwanawa atiyendere kuti atitsogolere kutipula. Anthu akufuna awawone. Chonde, chonde. Kamodzi kokha kwinako tizitipula .
.
My vote ✅ UTM
I can't wait for it, i see you FredoKiss , join lovely with the leaders Ife tili pambuyo panu
Kalembeseni guys timuvotele uyu kugwa kwa kwacha komanso kusowa kwa Forex kwaononga Malawi
Incoming president of Malawi
DK 2025 boma💪💪💪💪💪
Chaka chikuchedwa kuthabwanji voti yanga ikunyowa nimvula kkkkkkk UTM mofire 💃💃💃💃💃💃💃💪💪💪💪💪💥💥💥💥
UTM oyeeee!!!!
Utm my vote
More fire utm
Ndipo ndizoona boma ndi lomweli tizangosintha president basi.
Dk. Tiwombolen. Bas. Manja. Mwawoyipayo
ipatseni moto kumeneko kkkkkkk 💪💪💪💪💪💪
Osakaiwara kut aipase moto opanda usi ungaphweteke anthu usi plzzz
My vote 2025
good audience adults only
Mr DK tilikumbuyo kwanu
Zili bwino 😢
Ndizakuvora Kabambe ine anthu akupha toto
Boma iyo my vote
Zili bwino kwambiri, APM my vote.
Boma ilooooooo🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ine ndimafuna ndisavote koma ndi vota chifukwa Cha kabambe
Nane nkangovotera yemweyu ndithu aaa...enawa taaonapo kale ulamuliro wawo...tatopa ife
The chosen
Cokonoka tidzale DK basi 2025 DPP zinawalepher MCP zawakanikilathu tiyese abwanawa
Ndipo ndadula kale chomuvoteracho
Timpatseko chinthuchi achilamulireko ena atilephera
Adad my vote
Uýu ndikatundu waboma
Kkkk bwanji msimudayende wa pasi
Kkkk komwe kwa pita Apm anthu akumapita komweko
2 molo will register, l have found a president not an the oldest man
Eti bwa😂😂😂😂
Koma ma guy mmajambula bho
Moto wamapesi
Felix wang'alura
Utm ndichipani cha anthu anzeru manganya yekha ndiyemwe anali kape
Tawapatsa Michael usi ndamene akuonekako basi enaonse manyaka
Alibe molaro kape wanuyu
Yomweyo boma
Sindyankhula ndngopeleka mon mpaka,8 min 😊
Koma kulakhula UTM ilibwino ndithu
Ipase motp
Zinangolakwa kumwalira kwa chilima mwina akanathandiza dzikoli koma enawa eshii angofuna utsogoleri koma zoti angamange bomali mbava zokhazokha
U lier
Bodzatu iwe
Dr Kabambe please make a joint alliance government with DPP cos your not enough on your on and you will second to president and the president selected will hand over the presidency to you and you will choose your vise from AFORD in my visionary I see that
Let's go clean ziyambe ndi inu kupanga chisankho chabwino chokonda dziko lanu..... numbers won't be an obstacles
Muli kutali nd ndale ana inu
Kabambe the choosen one, big up man
Tivotera iwoo
Koma anthu ammamidzi kuvuta kupangidwa convince....eeee koma kabambeyu timupatse mpata
Anthu kumamidzi kuuma mitu iih😂
Kambambe yemweyooo
Kwa kumene kude komweko
Motooooo
Kapambe timuyese
Koma ngati sazatithandiza azatilikwara kwamber
Azatithandiza Mulungu salakwitsa broh
Kavote u will believe my words
Mbava izii
Chipanichi Bola chisaphatikizanenso ndi zipani zina,zimasokoneza
Vice president wakumwela ndiwanzeru muli fundo
Yankhulani za nzeru, auzeni zeni zeni osati madzala mpuno
Palibe chimene mukunena
Why is my kaliyati
Kususukira munthu wa chilendo pa nkhani ya ndale ndi izi lero za chikangawa zikuvutazi.
Asatana ntchito yao ndi bodza kuononga ndi kupha, ndale ndi uchitsiru